Tap to unmute

GWEDEGWEDE WA DZULO ANATOKOTA MWA NYOO ~ KOMA POLICE SIWAITANA AWA? EEH CHAKWERA ASAMVE NAZO CHOONDE

  Рет қаралды 13,633

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@EliasKhofi
@EliasKhofi 14 күн бұрын
Stevie and Selina your true sons of the soil for malawi,mumatimilira kwambili 🤝🙏👏🤛🙌
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 10 күн бұрын
Heavenly Father there is bliss in Your Throne I witnessed on June 9 2011. Bring it here it in Malawi.it's not a prayer but my heartfelt affirmation. Amen!!!
@OsmanSamu
@OsmanSamu 11 күн бұрын
Respect guys
@JailosKantonya-e1y
@JailosKantonya-e1y 12 күн бұрын
More fire guys alankhuleni anthuwa zinthu sizikuyenda
@AnnoyedClover-pp7gi
@AnnoyedClover-pp7gi 15 күн бұрын
Gwede gwede ndipodi zoonadi mwatokotadi adzaluzadi mavoti ambili asiyeni apilize adzaluze sitiwafuna awawa achoke
@kejescompany-zi1ft
@kejescompany-zi1ft 10 күн бұрын
Malawi okomela Lilongwe
@FridayKabade-t7x
@FridayKabade-t7x 15 күн бұрын
Eeeee koma kuzayambila bwino pameneviwo athela inu kuyayamba popo selina and sitve God bless you
@TadalaBirsonkanjanga
@TadalaBirsonkanjanga 10 күн бұрын
Mumatiimilila ma gyz
@ChrissieNyasulu
@ChrissieNyasulu 11 күн бұрын
More🔥
@TadalaBirsonkanjanga
@TadalaBirsonkanjanga 10 күн бұрын
Azanga tiku commenta ,chilima adpp anamusiya ndimoyo ,koma lazalo ndazake anamumpha ndemukhoza kumalakhula zopanda zelu ndithu
@rashidadan2533
@rashidadan2533 12 күн бұрын
Let's talk about pangolin ,,,, His exllence professor Peter muthalika The president of the republic of Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 🌹The winner of 2025 general election 🌹 Whether you like it or not but DPP is every Malawians hope .
@Andy20247
@Andy20247 12 күн бұрын
Anthu inu mukupita ku MBC nonse next year
@AlliSikweya
@AlliSikweya 11 күн бұрын
Mwalakhulabwino komaosapa
@duncainjimmy
@duncainjimmy 15 күн бұрын
Gwedegwede apa mukuima pa Chilungamo, aliyense wachita zolakwika adzudzulidwe posaona chipani
@StevenDastan-f5y
@StevenDastan-f5y 15 күн бұрын
Zoona zake
@GumuleKandawala-g7k
@GumuleKandawala-g7k 12 күн бұрын
Anthu amene alibe utsogoleri amalimbana ndi anthu odalitsika ndi utsogoleri
@PaulSimpamba-v3n
@PaulSimpamba-v3n 11 күн бұрын
Ngati nkhondo yayamba tibwela
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 11 күн бұрын
Kulibe ftereza kumwela palipose ndipo ili ndiboma la ng'ona zokhazokha akazizi enieni ndipo soka kwaanthu omwe anatengapo gawo povotela chithuphya kumwaba simukalowa
@DoreenLivata
@DoreenLivata 11 күн бұрын
Amcp azanva kuwawa akachoka boma
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 12 күн бұрын
Anthu inu mumakhwana , mumayankhula zoonadi
@johnkambala692
@johnkambala692 11 күн бұрын
1.7 trillions
@BashiruAdamus-l2b
@BashiruAdamus-l2b 15 күн бұрын
zowona chilungamo
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba 12 күн бұрын
Koma program ndimayusatira koma yayamba kubowa
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 11 күн бұрын
Kudana ndichilungamo 😂😂😂😂
@NokiaNokia-e2t
@NokiaNokia-e2t 15 күн бұрын
Mbambande
@AcctyhBuno
@AcctyhBuno 15 күн бұрын
Kodi iwe gwedegwede unali kuti osamasowa timadalila inu
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 15 күн бұрын
Mulungu a dziku dalitsani stev ndi Selina
@YoungMwacho
@YoungMwacho 12 күн бұрын
Chawezi Banda aziwonelanso anzake mwina angaseguke mutu.
@sibomasina330
@sibomasina330 12 күн бұрын
Wayufi uja iñu😂😂😂😂
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 12 күн бұрын
apa,tukudandaula,zachihana,adanyozedwa,nda,dpp,kuwatukwana,kt,atumbuka,sangakhale,nysogoleli,wadziko,atumbuka,nimbulizokhazokha,lelo,wakopeka,chihana,ndi,dpp,walolela,kunyozetsa,ntundu,wake,wa,atumbuka,umufuse,atupele,adakhaula ndi,dpp,
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 12 күн бұрын
zoti,munamuthamangitsa,chilima,ku,dpp,mukuona,ngati,tidaiwala
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 11 күн бұрын
Bola kumuthamangitsa kutsiyana ndi kumupha muthu
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 15 күн бұрын
Anthu inuyo mulungu akudalitsen ndpo akuze malire amoyo wanu
@rhodrickchinkhali4233
@rhodrickchinkhali4233 11 күн бұрын
Mmakamba zopanda nzeru inu
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 12 күн бұрын
zosezi,tikuziona,apazi,ndimbava,zokhazokha,winayo,am,manga,chifukwa,chabodza,winayo,am,manga,chifukwa,chakuba,kusalima,suga,440,biliyoni,munthu,m,modzi,omweo,nkumatukwaba,boma,kt,suga,akusowa,
@DonaldMunthali-d5i
@DonaldMunthali-d5i 12 күн бұрын
DUMBULA NDI KONDA NDINU ANA A CHILUNGAMO NDIPO PITILIZANI ANTHU ABOZA AWA TATOPA NAWO PA 16 ONSE A MCP NDI WAKUMALEMBE KU CHIKANGAWA
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 12 күн бұрын
chilima,kt,apite,ku,mcp,kt,ayambitse,chipani,chake,chifukwa,cha,dpp,kumuchitila,nkhaza,chilima,lelo,nkumati,timankonda,chilima,km,a,dpp,eeeee
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 12 күн бұрын
ddp,ikadakhala,imalemekeza,,malamulo,achipani,mwana,veka,akadamuchosa,ndalamayo,idachuluka,440,biliyon,km,suga,nkuvuta,kumalawi,,dpp,itaba,ndalama,zankhaninkhani,dpp,yomweyo,nkumaipitsa,mbili,yaboma,,,,kt,lakanika,kuyendetsa,dziko
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 12 күн бұрын
km,mcp,ikulamulabe,npaka,2030
@JoyceKasongo-s8k
@JoyceKasongo-s8k 12 күн бұрын
Mbambande
UNTV: Hataw Balita Ngayon | January 24, 2025
47:32
UNTV News and Rescue
Рет қаралды 43 М.
Жездуха 42-серия
29:26
Million Show
Рет қаралды 2,6 МЛН
БАБУШКА ШАРИТ #shorts
0:16
Паша Осадчий
Рет қаралды 4,1 МЛН
SLIDE #shortssprintbrasil
0:31
Natan por Aí
Рет қаралды 49 МЛН
ZOMWE AYANKHULA MAI KALIATI 😱 😱 __17 January 2025
27:20
GWEDE GWEDE | 16 JANUARY 2025
31:11
Malawi News Update
Рет қаралды 27 М.
Жездуха 42-серия
29:26
Million Show
Рет қаралды 2,6 МЛН