Mwapupuluma a UTM kutuluka msanga mu mgwirizano musatengeke ndi achinyamatatu .Anyamatatu sa voter . Examples:- Malema in South Africa amadzazitsa ma stadiums ndi achinyamata zotsatira mwaziona? Malemu Chilima bwanji nthawi ya campaign 2019 achinyamatatu amadzaza zotsatira munaziona? Anyamata amangofuna kusangalala basi .Wakunamizaniyo tu apindula chifukwa chakuthetsa mofulumira mgwirizano muti musapindule ndi inuyo a UTM. UTM imeneyi pomafika 2025 itatsala dzina lokha. Osankha kusamva asamve akumva amve.Mwina mumezedwa ndi chipani china chake chomwe chinaimaliza UDF.Uko ndiye simukafulukuta.
@user-rj7yv3eu4b25 күн бұрын
I don't understand
@user-rz9rm4cb8x25 күн бұрын
Iwe ndi wa mcp khala chete
@PaulLackson25 күн бұрын
Akuluwa ngakumalawi koma?
@Edson-sj8vn25 күн бұрын
Ife achinyamata tikavots mwaunyinji tatopa ndi mcp utm woyee!!