TONSE ALLIANCE... UTM is OUT

  Рет қаралды 6,494

Malawi Page

Malawi Page

Күн бұрын

Пікірлер: 19
@wezzieneba9238
@wezzieneba9238 5 ай бұрын
This is great news. Mwachita bwino mwatuluka though late, but God has a purpose for everything. But the issue is what next? Malamulo akuti chani? I believe the law should state that Dr Lazarus Chakwera has to step down and a referendum MUST take place now since he is on the seat because of the alliance. Please, tikudalira inu akulu akulu ku chipani uko, make a move on the case of our president, Dr Saulos Chilima and may his soul rest in peace. The government should NOT make these distractions so that so that the truth should be known.!Justice should be done for the sake of these souls that were lost in Chikangawa forest.
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 5 ай бұрын
Chokani inu mukutenga ngati chipani chanu , muthesa chipani ngati ma curtain
@wellingtonaugustin8314
@wellingtonaugustin8314 5 ай бұрын
koma amalawi mwawafunsadi? Mpungwepungwe mukupangawu ukugwetsani.Dr SKC zimenezi akadakhala moyo kodi akadasangalala nanu?
@ChimwemweGomani-yu4io
@ChimwemweGomani-yu4io 5 ай бұрын
UTM will not die the seed of SKC the seed of Tsogolo lowala was planted Ku SKC is the Symbol of Malawi's brighter future and Malawi will Be Transformed for Sure 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥
@umalimaganga
@umalimaganga 5 ай бұрын
From now I will keep ndevu in honor of SKC
@louisemsowoya8235
@louisemsowoya8235 5 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥osatopa ,osafooka🎉 tiyeni chitsogolo❤❤❤
@LeviChakwira
@LeviChakwira 5 ай бұрын
Great move❤❤❤
@umalimaganga
@umalimaganga 5 ай бұрын
God will be with SKC spirit and UTM 💪
@OwenBanda-e7d
@OwenBanda-e7d 5 ай бұрын
Osaopa osaoka osatopa
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h 5 ай бұрын
Eya kaa nanga mumachedwa pati out of alliance and be free
@FrancisBanda-g9v
@FrancisBanda-g9v 5 ай бұрын
Mwacita bwino kutuluka cifukwa nkhuku ndigola sakhala pamozi and fisi sangagone ndi mbuzi khalani orimba mulungu Ari mbari yanu Zikomo sindine malawi
@PeterGabriel-uh2lh
@PeterGabriel-uh2lh 5 ай бұрын
I quote, aliyese wasunga ndevu ndi wa UTM
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 5 ай бұрын
Zikomo kwambiri tamva za maganizo anu ngati UTM. Ndikuwona chipani chanu chikutha, chifukwa munatitengela kwa mbusa okupha . Ndiye basi mubalalike basi, osati muzipitiliza kutiputsitsa ndi bodza lanulo . Basi No more UTM palibe kutinso mungazawine ayi. Pepani nonse koma mauwa ndiowona ndithu.
@wezzieneba9238
@wezzieneba9238 5 ай бұрын
@@HamiltonwaNamuwah thx though. It’s not about chipani as for me but rather the loss of SKC. I hope you are happy but God is watching. Olo chi the chipanicho do you mind the way the wife and the children are feeling? Do you think it will be easy for them to forget what happened? As the vice president of the country dying as a nobody, naked, in cold…. I know how Chikangawa can behave… are you sure you talk like this ? You are heartless!!! God have mercy!!!!
@ChimwemweGomani-yu4io
@ChimwemweGomani-yu4io 5 ай бұрын
You are lying you don't know what you are talking about UTM will never die SKC is on the Red part of Malawi Flag 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@nellikkmwenda7087
@nellikkmwenda7087 5 ай бұрын
Mwachita bwino kutuluka
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 5 ай бұрын
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@jamesgama5489
@jamesgama5489 5 ай бұрын
Bola kusakhale utm A ndi utm B
@umalimaganga
@umalimaganga 5 ай бұрын
Real ones will stay opita apite tikunganabe
Гениальное изобретение из обычного стаканчика!
00:31
Лютая физика | Олимпиадная физика
Рет қаралды 4,8 МЛН
小丑女COCO的审判。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:53
超人不会飞
Рет қаралды 16 МЛН
Assista na íntegra o Resenha Semanal 29/12/2024
MIRAMAR
Рет қаралды 1,5 М.
MICHAEL USI WAYANKHULA IZI KU CHIRIMBA LERO
30:20
Makosana
Рет қаралды 15 М.
Ndamkana - St Lawrence Catholic Chemusa Choir Malawi
6:32
Chifundo Sauti
Рет қаралды 6 М.