Pa nkhani yakufutsa ma president onse pa nthawi imodzi zinganthandize kwambiri kwa ife ovota ndipo ngalani ndi hot 🔥 current imeneyo tawayitanani onse mzawagagade ndi mafunso
@KatengezayobuАй бұрын
Kunena zoona nkhani yakamba Mai Joice Banda ndiyoona ndithu aliyense amene akufuna kuima u president azifunsidwa zomwe wapanga Cian pa history yake eish izi tapita nazo kupompho eishi chakwela wapha Malawi yonse Mmmm za chisomo
@KinziWindasoni-h4bАй бұрын
Inu musapite patali prezdent wa nzeru NDI peter MUTHARIKA .zinazo NDI manyaka.aaaaa mukuchedwa bwanji
@JustinMpunga-c8bАй бұрын
Kmanso chain of command ukuenela kusatidwa kwambiri coz ena amalimbikila kugwira ntchito ngati deputy now senior akachokapo MOTi deputy alowepo pano akutenga Malo ndi wina zimatero zimabwedzeretsa mbuyo kulimbikila kugwira ntchito
@DickensManda-td9bnАй бұрын
Our towns are filthy due to these plastics. In Tanzania there use were banned long time ago
@GiftJulius-gx2kbАй бұрын
Kumumvesesa kotani.naye uja mesa ndigalu.ndiye kaya akuyamkhula zopusa timvesese
@MakeSunshine100Ай бұрын
Mtsogoleri analipo. Ndi uja anaphedwa.
@AngelaMphinjiАй бұрын
Iyi. Ndi. Hot. Current ija!!!! Ndizoona. Zoti. Akukhuthulirani. Zindalama. A. MCP. Eti!!! Mwadya. Chibanzi. Chotentha. Guy's zawonekaa
@GreenBadaniАй бұрын
Kkkkkk 😂😂🔥🔥🔥💓
@JustinMpunga-c8bАй бұрын
Nkhani imenei makosana eee mwandifika kwambiri ndipo ndizoona mlandu mpaka dzaka 12 kutha judgement osatuka mpaka lero chonde ayankhureni asithe timawadalira
@tabithamlangeni2890Ай бұрын
Akatelo azizati ma file anasowa
@VincentRobert-c5cАй бұрын
Kungot osaukafe
@DjshukulanGiftАй бұрын
Za chakwera anali kwina uko and sanakharepo wakulu wa boma,even u khasala sanaimeko,relo kungot balamathu