HOT CURRENT YA LERO UTHA KUMANGOSEKA ASAMBWANZA ALIYENSE OPANDA KUOPA MUNTHU AWA ALIBE 2 KOLOKO

  Рет қаралды 77,966

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 119
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 2 ай бұрын
Zachipani ndiye kuchezera president uja, koma vice president atasowa kuimitsa operation yofufuza😢
@marthachakoma4558
@marthachakoma4558 2 ай бұрын
Papàappppaapaďpp,źxd'ź,,,,
@retirementtoafrica
@retirementtoafrica 2 ай бұрын
Thank you mr pankuku for not being bias
@NchebeMilliyano
@NchebeMilliyano 2 ай бұрын
Chikangawa sadzawinaso ,Mr chikangawa where is Mr chilima kafana koganiza bho Kali kuti ?
@EnockChembe
@EnockChembe 2 ай бұрын
Moti aukufziwa komwe adapita chilima
@mazumabekumwenda3876
@mazumabekumwenda3876 2 ай бұрын
I support, the idea Mumba to be considered in the cabinet. I believe he can deliver
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 2 ай бұрын
Tinavota chifukwa Cha chilima osati iyeyo Mr chikangawa
@imraanJafal
@imraanJafal 2 ай бұрын
Koma bwanji sanapite ku chikangawa kod kuonetsa utsongoleli PA bwino pokha pamavuto ai
@DumisanMkandawre
@DumisanMkandawre 2 ай бұрын
Good message to Mr President
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 ай бұрын
And it's good a leader must show a strong leadership not to keep quiet where things are not going well, he must talk where things are not ok
@MOGAMW
@MOGAMW 2 ай бұрын
Chikangawa era ija bwanj sanachezele nawo instead anaimisa operation rescuë
@violetkamvanthupi2443
@violetkamvanthupi2443 2 ай бұрын
Watching from nsipe
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 2 ай бұрын
Ndikadakhala a Chakwera , anyamata akalewa ndikadaganizira mozama chifukwa anagwira ntchito yayikulu kuima nawo limodzi pa nkhani ya ngozi ya ndege yaku Chikangawa .
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 2 ай бұрын
Kuchezela ku vote zikungowoneselati kuti MCP kulibe m'gwilizano ,,,,a peter or asachezele zilibe ntchito bola ngati anthuwo akugwiliza ngati chilungamo chilipo,,,,,, komaso kodi achilima atasowa munangona kusonyeza kuti mcp yose inali ndi plan yokupha chilima
@DeeHMugonya
@DeeHMugonya 2 ай бұрын
Too later..kumanena za CHAKWERA lero tizimuyamikira munthu chifukwa sanagone!! MALAWI tachangamukani chabwino sanagone, koma ziganizo zake ndi zogona ndiye chabwino nchani?.
@JustinWBanda
@JustinWBanda 2 ай бұрын
Koma chakwela kungomupasaso mpatu olamulila chaka chamawa tili mmazi
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 2 ай бұрын
Zosatheka brooo
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 2 ай бұрын
Sakulamulila ameneyo 2025
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 2 ай бұрын
Gule kwawo bc 4 sure
@AgnessJonas-zt9wp
@AgnessJonas-zt9wp 2 ай бұрын
Kuti awine chaka chamawa iiii angazasimbwe ndikutukwana komwe yoooooh
@MillyKachepa
@MillyKachepa 2 ай бұрын
Ngat anat tonse ikutha amamuoheranji nzawo 😢😢😢
@isabelmartin7567
@isabelmartin7567 2 ай бұрын
Mr chikangawa 😥😭
@ChikondiBanda-r4h
@ChikondiBanda-r4h 2 ай бұрын
Aaaaa Inu muchemelela kuti sana gone chakweleyo bwanji chilima anagona kuthengo usiku wose kuchikagawako iye anali kuti zachamba sitingayiwele 🎉🎉🎉
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 ай бұрын
Chakwera zoma zoona kupha chilima mochita kukhapa zoona munthu anakuikani pa mpando Ambuye akuoneni ndithu RIP Chilima
@yankhonsaiwa
@yankhonsaiwa 2 ай бұрын
Is our democracy growing achunga...
@JonasMsungambeu
@JonasMsungambeu 2 ай бұрын
Kodi Makosana, zoti voice ya intro yo siimveka zimenezo simudziwabe mpaka pano?
@FRANCISKAMPIRA
@FRANCISKAMPIRA 2 ай бұрын
Good news
@MercyKatongo-p9b
@MercyKatongo-p9b 2 ай бұрын
😂😂😂 guys you always make my day
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 2 ай бұрын
He can talk but no will to make it. Corruption now is beyond measure which was one of the songs be4. We have seen people playing around with public funds and he even backed up Chithyola no action was taken. Words vs Actions
@MitchChanza
@MitchChanza 2 ай бұрын
Khala ngati Unifrom Ya Lunzu Secondary tu 😂
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 2 ай бұрын
MCP is a divided party .From the women's dressing you can tell that some are continuously loyal to the first founder of the Party than the current leadership .
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
Joyce Banda tamuwudze kuti adzikango peleka yakumbuyo kwa banda iya sangakhaleso president
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 2 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣 She's is too old and fat to manage that kkkkkk
@Vascomw
@Vascomw 2 ай бұрын
🔥🔥🔥
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 ай бұрын
2 late chikangawa we never forget Malawians waiting for report and we know who is chakwela
@juliochiwalo
@juliochiwalo 2 ай бұрын
Is chifundo zimba in Malawi or abroad
@haroldchirombo7918
@haroldchirombo7918 2 ай бұрын
Background music mwina itasikako bwana ikumazasokoneza pomvesela koma timakunyadilani
@Fredoh10
@Fredoh10 2 ай бұрын
DPP my vote (Adad)
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 ай бұрын
Ndipo mcp ibwita izi ndikunenazi muzavomereza coz anaophyeza pachilima
@AugustineTheu-of6nv
@AugustineTheu-of6nv 2 ай бұрын
Chakwera is active to the party (MCP) and not to the government of Malawi. The government needs active and wise person not like Chakwera
@ElizahMadi
@ElizahMadi 2 ай бұрын
Adadi athu Ali ndi ana ambiri atumiza ana tikachezera 😂😂😂😂❤❤
@MtshubunguClemence
@MtshubunguClemence 2 ай бұрын
Ada sangathe kuchedzera chifukwa sanapangepo overnight prayers kkk
@LanceLance-mj4kc
@LanceLance-mj4kc 2 ай бұрын
Anazolowera nchitidwe oipa wazikwanje,kom izi nindale sibwino kutero,zikwanjezo zimabwera bwanji
@AnthonyChirwa-t4g
@AnthonyChirwa-t4g 2 ай бұрын
Ada kanikilanji kugona itasowa ndege ya chilima koma uko paka kuchezela osaopa osafowoka osagonja ndizafela ndembela UT ikuwina mzimu wachilima uuse mtendele
@vussoh00
@vussoh00 2 ай бұрын
With the new alliance if they fall out they should vote again if the fall out is less than 50%+1
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 ай бұрын
Kodi chakwela anapha dala chilima ndipo Malawi waiting for u chakwela
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 2 ай бұрын
Achunga mukuti democracy ikuyenda just because Chakwera anangoti aloleni akumpotonso avote basi aaaah aMalawinso timaiwala mwachangu bwanji
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 ай бұрын
Palibe kulekanitsa mphamvu pakati pa Executive ndi nyumba yamalamulo Gotani Hara is compromised.
@kadijachilwan967
@kadijachilwan967 2 ай бұрын
😂😂 mpaka mutharika angachezere😂😂😂😂
@burnetkalembere4528
@burnetkalembere4528 2 ай бұрын
Anyamata mumakhazula osanyengerela koma kamajekete asamupatseso unduna
@retirementtoafrica
@retirementtoafrica 2 ай бұрын
Bring back obanda to chair awa amapereka ma restrictions
@MosesNkumaniza
@MosesNkumaniza 2 ай бұрын
Awa sangalongosole zinthuchifukwa Cha anthu womwe amati chipani ndi Cha makolo kunyoza tsongoleri
@LanceLance-mj4kc
@LanceLance-mj4kc 2 ай бұрын
Zoona ndithu aakamayendera mbali zonse kumafunsa ndikuona momwe zinthu zikuyendera ,akakamadzionera okha kusiyana ndikumangonvera zomwe anthu okuzulira akunena
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 2 ай бұрын
Kudana ndiatsogoleri zimaonetselatu kut iweyo umafuna zithu zongopatsidwa mmalo mogwira ntchito
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 2 ай бұрын
Channel yanuyi ndiyabwino koma nyimbo ya pasi pansiyo aaaaà
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 ай бұрын
Mwaitambasula bwino anyamata, ndipo ine waiting kuti mukapiteso ku mkumano wa Dpp. Tikaoneso zawo
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
Chakwera ndi chisilu kumaliro achilima analephela kugona chifiti cha munthu 😢
@brotherfrancissuwali455
@brotherfrancissuwali455 2 ай бұрын
Nanga yemwe anakhapidwayo si munthu ,it means kuti kunalibe mtendere musatinamizepo apa
@BatumeyoChikopa
@BatumeyoChikopa 2 ай бұрын
Anthu akatopatu amafika potopa yatsala 2025 general elections 😮😮
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 2 ай бұрын
Akunama amenewo j b akadali ku MCP
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 ай бұрын
Chifukwa chiyani utsogoleri wa MCP sunatsutsidwe? Malinga ndi mgwirizanowu utsogoleri wa UTM udayenera kutenga udindo. Sitingakhulupirire MCP mumgwirizano uliwonse.
@MukhozenjiKalimanjira
@MukhozenjiKalimanjira 2 ай бұрын
Sangapite kwa Tate koma mwaine ,koma ndaseka
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 ай бұрын
Chikangawa chakwera apusisa anthu
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 ай бұрын
Alliance izakhalako after mavote thats what mai Banda mean mukutanthauzira molakwika
@calvinjamal7117
@calvinjamal7117 2 ай бұрын
Adangogwela 4yrs downwards walephela kuyendetsa dziko kwao kwatha
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 2 ай бұрын
Anamachende awa amangolimbana ndi dpp bas
@OsbertPangani
@OsbertPangani 2 ай бұрын
Apatu the TV Manager khaze khaze munakwana! Kkkkkk
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 ай бұрын
Palibe osatinamiza chakwela ndi mbamva komaso okupha
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 2 ай бұрын
Kodi tikapanga comment,,,zimafika atolankhaniwa pazomwe takomenta,,,kapena timapanga comment kwa iweyo basi,,,ndiye umawuza zomwe anthu akupanga comment😢😢😢
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 ай бұрын
Ndinu 1 Iyaaaaaa ana achepa
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 2 ай бұрын
Chakwera wachezerera mavuto akuchipani kwake koma ku Dpp kulibe choti tsogoleri achezere
@AlleyNomakanjani
@AlleyNomakanjani 2 ай бұрын
Ine kukamwa kwangondiuma
@humphreysidie4747
@humphreysidie4747 2 ай бұрын
Stop the background music, its irritating
@NabeelAlie
@NabeelAlie 2 ай бұрын
Mpaka agogo
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 ай бұрын
Komaso apa tikusowa blayan banda
@Ndendendlovu
@Ndendendlovu 2 ай бұрын
Chakwera is not a good leader 2025 akagwele ukoo
@JamesNalifu-wz2lu
@JamesNalifu-wz2lu 2 ай бұрын
Akulu akulu mukamapi chitetezo chilipo mukutathauza chani athu anapezeka atafa aja mukuakumbukila kundilande okuba amafuna kukaba kwa wapolisi kundilande aja umbava mene wakulila pano mukuona kapena mukukamba za inu nokha atolakhani kuti chitetezo muli nacho paja mumati mumayakhulila amalawi ndikufuna ngatidi mumayakhulila amalawi bwelaniso kuzakamba khani ya chitetezo kuti amalawi avesese kuti mukamati kuli chitetezo mukutathauza chani
@MexcoJepter-p5f
@MexcoJepter-p5f 2 ай бұрын
Yedzekani kaye yachakwerayo
@tasmania527
@tasmania527 2 ай бұрын
Awa nchifukwa chake Peter Mutharika amafuna kuwamanga nkhani ya Cashgate kkkkkk.
@AlickChikaonda
@AlickChikaonda 2 ай бұрын
Kuchedzera kin covension sizikutanthaudz kuwina
@FractionMailosi-p3n
@FractionMailosi-p3n 2 ай бұрын
DPP zivele mtolo
@GeorgeNamonde-sy5ue
@GeorgeNamonde-sy5ue 2 ай бұрын
Anachedwa
@raymondchilimba7010
@raymondchilimba7010 2 ай бұрын
President Chakwera not just A Chakwera, mwatani Kodi?
@MzadziWanga
@MzadziWanga 2 ай бұрын
😂😂😂. Nde chomwe chingasinthe nchani mweteremu , mwadya nyama??
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 2 ай бұрын
Kod chakwera ndindan Mr chikangawa not president President amakhara ndichifundo ndi anthu ena koma upule wakubanja kwake kokha chifukwa chake anthu amangot chakwera chikangawa
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 nkhalambadzo bwanji sizingakhale kunyumba yoh
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 2 ай бұрын
Anamusiya nzao akuphupha ndi moyo ku chikangawa Iwo kumagona koma kwinaku osagona
@bernardzgambo1317
@bernardzgambo1317 2 ай бұрын
Inu munali kuti kukampulumutsa mmene ankaphupha?
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 2 ай бұрын
Fuseni chakwera wanuyo kuti chifukwa chani anachezera usiku onse ku convention anasiya kuchezere kosaka ndege ya vp ndi anthu onse 8 tinaluza kuchikangawa kuti tima kruck inu
@benjaminmvuma-rk6mu
@benjaminmvuma-rk6mu 2 ай бұрын
Amusiska mpaka nthena
@BostonMalack
@BostonMalack 2 ай бұрын
Kkkk gogo amene ujayu sangachezere ngati chakwera akagona uko kkkk
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 2 ай бұрын
Kodi simungafunse achakwelawo kuti atulutse report lakuchikangawa
@FrenceTsitsani
@FrenceTsitsani 2 ай бұрын
Kkkkkkkk mpaka kunkhapana zilipo tiziona angati akudana pa umodzi wawo ulendo usadayambe zili bwanji mmene ziyambire
@retirementtoafrica
@retirementtoafrica 2 ай бұрын
A pankuku sakupatsidwa mwai wo yankhula
@MercyKatongo-p9b
@MercyKatongo-p9b 2 ай бұрын
Chikangawa chakwela party
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 ай бұрын
Komaso osatinamiza apa which democrats u toiking about
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 2 ай бұрын
Inuyo madolo atola khani muli zelu
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 ай бұрын
Koma Kunkuyu kamajekete amenewa anthu anatopa nawo Koma mumba anachita bwino kupeza ma vote oposa ena amaudindo awo
@wadsoncontinue3017
@wadsoncontinue3017 2 ай бұрын
Fundoless. Anachita bwino ngat anadzivotera 😅😅😅
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 2 ай бұрын
Chikangawa party (mcp)
@JamesMaduka-wk8xi
@JamesMaduka-wk8xi 2 ай бұрын
Zomwe zawonetsakutichikondi ndinzawouja analibe chilimaanachitakumupha ameneangatsutsezimenezi ndisatana weniwen
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev 2 ай бұрын
Chakwela is a good leader mpaka 2030💥💥💥💥
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@NchebeMilliyano
@NchebeMilliyano 2 ай бұрын
Ngati ukuti adzawina chakwela wakoyo where is Mr chilima Mr chikangawa ? Sadzawinabe bale wakoyo pokha pokha mukantenge chilima uja
@ConradccjSokoSoko
@ConradccjSokoSoko 2 ай бұрын
Mwazukuta mwaukadaulo
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki 2 ай бұрын
Chakwera is like chameleon,he changed everytime today is talking that tomorrow this. Imagine what he said about chikangawa saga now quite is an idiot.
@humphreysidie4747
@humphreysidie4747 2 ай бұрын
The background music is irritating pls stop it in you nest episodes
@holdings2022
@holdings2022 2 ай бұрын
Ur right ✅️
@lastonaloni5680
@lastonaloni5680 2 ай бұрын
Komatu usi wasala momo sanatuluke
@veronicagullo9373
@veronicagullo9373 2 ай бұрын
Chakwera a good leader
@Carodaimon-h6g
@Carodaimon-h6g 2 ай бұрын
Zubeba
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 2 ай бұрын
Kkkkl
@ZaccheousPetrol
@ZaccheousPetrol 2 ай бұрын
Ndekuti ma delegates ndi amene amamvota osati anthu 1400 anja.ndichichifuka anthu amalandila zikwama nthawi yamamvoti
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 ай бұрын
A siksya mwatanthauzira molakwika ma banda said sikukhala alliance koma aliyese apite ekha...
@atusayemwandelile8307
@atusayemwandelile8307 2 ай бұрын
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 ай бұрын
Chakwera is a good leader
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Bola inu abambo Anu achakwela 😂😂
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 35 МЛН
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 262 #shorts
00:20
How it feels when u walk through first class
00:52
Adam W
Рет қаралды 25 МЛН
🕊️Valera🕊️
00:34
DO$HIK
Рет қаралды 14 МЛН
News At 10 | 21/10/2024
45:13
Channels Television
Рет қаралды 28 М.
Exclusive Interview with Reverend Alexander Kambiri
30:56
TIMVENI TV
Рет қаралды 13 М.
MUIMBI HOSIAH CHIPANGA MUDARE RAMAMBO MUTASA VS LEON MATESVA  KARANGANDA TV KUTORWA KWEMUNDA
18:01
Brian Banda full interview with politician Ken Msonda on Times Radio
24:24
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 35 МЛН