Sawe are on your side, keep well, wishing you all the best
@FosterChilumbaАй бұрын
Nzerutu izi from the leader simwantere mwantere coz he speaks his English from the nose English is a language even pple who did not go to school can speak English A Malawi anabesa posankha Lazaro
@ophlexmkondowe8107Ай бұрын
Welcome back APM,I didn't see anything bad with you.
@lindiwematanya9716Ай бұрын
That is very true Sir APM global problems are there in world everytime
@lindiwematanya9716Ай бұрын
Bwana APM mukunena zoona zoti zikalata zokavotera zitakhalanso monga: chauzika, passport, kalata ya kwa Mfumu ndi driving license zingathandizetu kuti a Malawi akhale ndi mwayi woka vota
@user-lz6lr8bv9tАй бұрын
A p m kuyankhula mwanzelu komaso mwamphavu kuposa, mbuzi chakwera
@user-do2cs8nf4bАй бұрын
I silute you ADAD may the almighty God give you a long life❤
@olivemalomboza9010Ай бұрын
I also sit on chair because of my back pain Is there anything wrong with that??
@mashallahleonard2793Ай бұрын
Adad osaopa ndpo osayang'ana mbuyo maso patsogolo Boma mwalitenga ilii🔥🔥🔥
@kazembewailesiАй бұрын
Powerful interview, APM my vote.
@HarryChizengoАй бұрын
Ngati sunapite ku xool sukuyenera kumakamba nawo za anthu ozindikira ase DPP ❤
@user-vo7cb4cv5d24 күн бұрын
1 Billion imeneyo aimaliza agaru ali panowa
@DamianoKapachika-ft1yeАй бұрын
Big man
@YusufuKaifa-fr4wtАй бұрын
❤ ❤❤ my vote to adadi long life
@thomasyohane987Ай бұрын
My vote ❤❤❤
@InnocentMtakulamusi27 күн бұрын
The best person to rescue this country
@user-eu1cx9gp5wАй бұрын
Brian Banda wakumana ndi machine a boma, Peter Mutharika,adadi ndi katundu
@user-fr4gb4bq6qАй бұрын
❤❤❤❤ you Mr APM God bless you and protect you
@shayrafernandeslatif9556Ай бұрын
I agree wt APM we are a failed state n worse
@mollymasangano473Ай бұрын
It was abig mistake for my fellow MALAWI 🇲🇼 today the COUNTRY is in the HOT SUPU 🔥 🥵 ADADI receive my VOTES ❤🎉❤🎉❤🎉❤
@WilsonLimited-os1xdАй бұрын
Tikavota opanda ID nrb ikutiputsitsa kwambili
@SandraBanda-hd1liАй бұрын
Adad. aaaa. ndagoma. nanu. njala. anthu. Kumafa nayo. chifukwa. chosowa ndalama. yogulira. Chakudya koma. President. a kuona..., what. nonsense. Chakwera
@user-uc1pd1tc2xАй бұрын
Our only Dad, my vote❤❤❤❤❤❤❤
@LusunguMkandawire-fh5eqАй бұрын
Long life dad 🥰
@user-vh9uk1jy7wАй бұрын
Long life dad
@user-wd9yd1bg9nАй бұрын
Man in action
@YamzyAmos10 күн бұрын
Ndife ana ADADIIIII❤
@jamesphillipo9952Ай бұрын
He is a genius
@LukaThaweАй бұрын
Mbuziiii Peter aliyese amapita kumanda samakhala pampando kumeneko ndikupusa. Iye angonena Kuti sangayime nthawi yayitali wakalamba iyaaa
@JaneJames-rb6jsАй бұрын
We really want u Adad
@DalitsoTanganyika-gw9qiАй бұрын
Mafumu komanso abusa amakhala pa mpamdo Ku maliro,akanakhala mpasi ndiye omwalirayo akadadzuka?
@SteveriaChakalamba28 күн бұрын
Adad woyeeee❤
@andrewkalukhoАй бұрын
Boma 💙💙💙2025
@user-oq5rg5mz7qАй бұрын
Mbavu💪 chimakhala chibadwa, sakuwelenga pepala koma akuyankhula zambavu, akanakhala chakwela ndi peplalake zaziiiiiii 😢 AMP my vote
@user-wx1jt5fd2jАй бұрын
Tikukumvesesani adadi liphuleni ziko lamalawi pa moto amalawi tisazachitenso mistake awiri komanso zakhaleni ndi ma adivaiza okonda kuthandiza anthu awo osati adyera opanda chisoni opanda chifundo ongoona Bola zawo zikuyenda mafuno a bwino no kwa adadi God be on your side
@MackenzieChipetaАй бұрын
Koma kuimba atakuima koma kampeni akwanitsa kuyenda paliponse ndithandauza kuti a former president ndi akulu
@AhmadumkomaTambala-lr9gpАй бұрын
❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
@marryphili5419Ай бұрын
We're waiting for you adadi mwina mungazatichotse ku bagamoyo kuli mavuto wochuluka
@HendersonNkhomaАй бұрын
Big boss AMP more fire🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@georgempondaАй бұрын
A leader with skill never condemn other than find solution to solve matters thats Peter Munthalika... I think Malawians have learnt a lesson from mcp government.....
@YusufuUsumaniАй бұрын
❤
@JonesChingaya-yf4ggАй бұрын
Thus the voice of the President to be, God is keeping you for a reason. Good answers from APM,
@user-po6ir6eh4zАй бұрын
Apm more fire its my vote
@dusterelias680521 күн бұрын
A malawi amaiwalakwambili mukuziwa Congress party inalienable ya chabe mukuziwa zimenezo inu mmalawi munabvotelanso yomweyo simunaganize bwino
@FractionSylessАй бұрын
❤❤❤
@aarondickson70Ай бұрын
APM put all things to almighty God to pull back Malawian who are now going to Bagamoyo
@RodgersPhiri-ju1eo15 күн бұрын
This is just campaigning issue if fuel is getting up here in South Africa almost every month what about Malawi
@YasinAdam-pn4bhАй бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@atusayeMtalamaАй бұрын
Ndezodabwisa pamenepo poti anakhala pampando ku maliro?
@YusufuUsumaniАй бұрын
adadi❤
@gladysbonongwe1038Ай бұрын
Timakunyadirani dad
@IbrahimSquare27 күн бұрын
Zochitisa manyazi presdent wosasata chikhalidwe cha ziko lache kumanda sitikhala pa mpando shame
@chifundopetro422Ай бұрын
Micaso socasa
@samdiverson9733Ай бұрын
APM machine machine kwamtele out
@williamsalexmbongaАй бұрын
Ndi nthawi yandani ija munkati anthu azidya ziwala ija?
He is going to lose miserably and that's when he will understand that Malawi is not the same
@LuteSynosАй бұрын
Vote andandi❤❤❤❤
@mollymasangano473Ай бұрын
Kikikiikiki koma anakwapulidwadi Brain Banda Hahaha didn't employee his Children he didn't send his children to embassy 😂😂❤
@beinhardkausiwa7107Ай бұрын
My president APM❤
@user-ve4yl1gq8eАй бұрын
Interview inali bwino kwambiri koma bambo Brian muchepetse zizunguzo ambilife ku xool sitinapite 🤔🤔🤔🤔🤔🤔
@user-ph2dw9qt1lАй бұрын
APM was sleeping on his job NEVER vote him again
@user-dd4mn3yk4fАй бұрын
APM my vote❤❤❤❤
@user-ux9ik4zr5xАй бұрын
Apm is just selfish & greedy, he didn't born a politician but because of our stupidity after his brothers death we gim him power,There's no permanent enemy in politics but this man still keeps anger between Joyce Banda.Muluzi is the one who could have be angry with Mutharikas family of what they did with UDF but he shows that he's a real politician.
@user-eh1mg3ww6dАй бұрын
Adad omweo kuti wawaa❤❤❤
@samdiverson9733Ай бұрын
only hope for malawians APM back in 2025
@user-eh1mg3ww6dАй бұрын
@@samdiverson9733 sure
@user-bi6pb5gc8tАй бұрын
Enterview iye kwaine sinandisangalasi chifukwa yakampindwa mchizungu enafe kuaukulu sitinapiteko nkhani ili APA ndiyamalawi vuto ndichani kulankhula cyichewa Kuti nafenso timveko mwina kapena enterview imeneyi mumapangila kuamerika
@patrickmacheso5062Ай бұрын
Mutseke Dambwe mutsekula sukulu.
@GloriousPhiri-tv3rw20 күн бұрын
This gogo will learn the hard way. He thinks he knows everything. Remember in his time he use to tell the hunger-stricken people to go and eat grasshoppers . And also told government workers to go for private sectors or work outside Malawi if they want to prosper
Interview yonse ya chizungu ngati amalawi ndi amzungu izi ndi zausilu ndiye kumamasulila gogo iyiso ngati kwerekwele
@patrickmacheso5062Ай бұрын
Paja mumapita ku Dambwe mmalo mopita ku sukulu that's why.
@SaidiMbawa-st6bjАй бұрын
@@patrickmacheso5062 Uziwuza azako akumangochi osati ine ndilibe nazo ntchito
@patrickmacheso5062Ай бұрын
@@SaidiMbawa-st6bj Anzanga akumangochi??? Ine si Mulawo aise ngati ukufuna kudziwa za ine undipeza ku page house kwa APM.
@user-oe1lg4xo7wАй бұрын
M C P imati APM wakalamba , funso ndirakuti munthu Okalamba angamayankhe mafunso mwamphamvu ndi mwadongosolo moteromu? Adad ndimphaso yochokera kwa Mulungu palibenso angamake pa APM
@kingsleyhopematchaya5184Ай бұрын
Ndi mnyamata apm iwe sudziwa
@eliffagondewe8214Ай бұрын
Mcp ndi olephera ndipo apm akuwapatsa theng'enenge 🔥🔥
@williamsalexmbongaАй бұрын
So this guy is claiming that He will do better the things he failed to do in his 10 years of leadership? What a joke in Malawi 😂😂😂
@samungwira6927Ай бұрын
Imwe mwatuka apa nkhalo mulije God should punish you
@user-nc4vi1jt5gАй бұрын
Boloyako apm kuno sikuamereca
@user-qv4ko6ps4jАй бұрын
Bambo onso yawo
@mashallahleonard2793Ай бұрын
Iweso chitsiru Makolo ako akuvutika ndnjala abale akowo ali president