IYI NDI YA AZIMAYI OKHA | ENANU CHONDE OSAONELA

  Рет қаралды 40,798

Adzukulu

Adzukulu

Күн бұрын

Пікірлер: 102
@AustinStephano-p2v
@AustinStephano-p2v 9 күн бұрын
Kmatu ndi bwino mwina kukhara chete osayankhurapo chifukwa vuto siliyang'ana kt uyu ndi ndan aliyense atha kukumana ndivuto kusiyana ndikumayankhura chipongwe choncho ngt mukuyankhulira enanu dziwan moto umapita kwatsala ntchile nonse mwayankhura chipongwe mumudziwe mulungu ndipo achite nanu nzanuo sanafune kt akumane ndivuto ngt limenelo ngt sinuyo muli ndi ana atha kukumana ndi vutonso
@lolinichitute
@lolinichitute 3 күн бұрын
Azizisukira ndi madzi ozizira kufinyira ndimu ndi soda ,kmaso kudya nthochi daily ,mbali inayo akupemphera mamasulidwe 🙏🙏
@HarryMgabu
@HarryMgabu 8 күн бұрын
Sing'angawakulu ndimulungu chonde pephelani ngatisizisitha salanikudya mulungu sanalephelepo
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 10 күн бұрын
Amuuze mulungu ayankha
@HannahChingana
@HannahChingana 8 күн бұрын
Akumane ndi doctor amumasukile kuti aziwe vuto nchani.. Zikakanika Apemphere plus fasting and prayer
@STELLCHIBALO
@STELLCHIBALO 8 күн бұрын
Mzanga wina wake zmkamuchtikila kmano znathela kwa abusa coz it was not a normal thing
@ZoeChilonga
@ZoeChilonga 3 күн бұрын
Yesani kugwilitsila ntchito soda ndi madzi ozizila basi l hope zisintha
@FatimahMwango
@FatimahMwango 2 күн бұрын
Sory ccta ayetseko yoni pearls amayika kumeneku after 3 days amachotsa fungo ngakhalenso kuteremuka kwakumeneku futsako mmapharmance
@PatrishaKunkhanda-e7v
@PatrishaKunkhanda-e7v 10 күн бұрын
Mutayesako ma clove kugwiritsa ndukumwa end mkutsukilakoso
@VictoriaMlauzie
@VictoriaMlauzie 8 күн бұрын
Akufunika zachikuda coz zimenezo ndizamuwanthu 😭
@nerrcejngulube
@nerrcejngulube 6 күн бұрын
Pofunika kwa prophetic akamuthandiza mulungu satephera
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 9 күн бұрын
Ameneyo apite kwa doctor akamuthandize
@AbusoliswaBuej
@AbusoliswaBuej 8 күн бұрын
😂😂😂😂😅😅😅koma
@ShanetaKalisinje
@ShanetaKalisinje Күн бұрын
Kuchipatala kofunika 8:41
@GraceKing-d2n
@GraceKing-d2n 9 күн бұрын
Aunt dzikoli ndiloipa anthu amapangana chipongwe Zina ndizimenezo Kwambiri tsamirani kwa Ambuye Yekha NDAMENE angathane ndi vuto lanu Koma nzomvetsa chisoni Mmmmmm
@AminnShadiddah-wr1we
@AminnShadiddah-wr1we 8 күн бұрын
poti mwati akufunika ndi azimayi tiyeni nazoni mukatifuna mutiuza
@JessyMunthali-j9u
@JessyMunthali-j9u 6 күн бұрын
Annon wo analozedwa or kupangidwa chipongwe ,,, alowe ku inbox kwanga , Pali zoti ndimufunse then After ndione kuti ndimuthandiza motani
@LindaMwafulirwa-p6s
@LindaMwafulirwa-p6s 8 күн бұрын
Choyamba pitani ku Chipatala mukamve kuti akuti ndi chani'kenako pitani kumapephelo,kutheka ena anakupangani chipongwe asisi,yeselani ndithu ambuye ali nanu sazakusiyani,zisamba ayi chifukwa zikhoza kuwonongaso Banja lanu zikomo
@ELESONCHIKONDI
@ELESONCHIKONDI 8 күн бұрын
Mwina Ali Ndi Matenda Achibadidwe
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 10 күн бұрын
Mmmmm sizofunika chipatara izi km zisamba basi
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga 8 күн бұрын
Apemphere
@JoeChitenje-m7r
@JoeChitenje-m7r 8 күн бұрын
Nkhani asiye kusambra soap kumalo obisikao Bs nkhani yathapo komanso azisukilako madz ozizila ndi soda
@Victoria-s5d5n
@Victoria-s5d5n 9 күн бұрын
Apite kwa abusa achitete ku Zomba akamumasule kapena ngati Ali ku Lilongwe kuno opemphera ena alikonso odziwa
@LinessdorisScot
@LinessdorisScot 9 күн бұрын
Mafungo awa amakhala achibadidwe, si za asing'angazo ayi, zovuta koma
@wadongo
@wadongo 10 күн бұрын
Eish napepe mama pempherani molimbika. Vutoso apa mpa public ena samasuka kukuuza zochita
@FisherAction
@FisherAction 7 күн бұрын
Kumasamba, kumagwiritsanso prefumu ndi kuyamba times daily kunaku kumapemphera
@FisherAction
@FisherAction 7 күн бұрын
2 times
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 10 күн бұрын
Kanyimbo ameneyo Fungo lachibadwidwe olo apange
@gibsonkbanda2771
@gibsonkbanda2771 10 күн бұрын
Doctor akhoza kuchitapo kanthu
@EggretKundembo
@EggretKundembo 10 күн бұрын
Mmmmmmm ai pepani mama
@AustinStephano-p2v
@AustinStephano-p2v 9 күн бұрын
Amai yesetsan mwina kupita ku chipatala ndikomwe angakakuuzen zoyenera kuchita pamenepopo zili bwino chifukwa mwadziwa vuto lanu nde mukawafotokozera adoctor ndamene angakakuthandizen zoona
@GeraldMkandawire-u2v
@GeraldMkandawire-u2v 10 күн бұрын
Ayese kusambira soda mwina
@LeonardButton-e9u
@LeonardButton-e9u 8 күн бұрын
Ayesese kuti akamasamba Malo ake obisikawo asamageilise ntchito soap or kunena kuti thomvu la soap zimenezo zitha,chifukwa adzimayi ambili amagwilisa ntchito soap chifukwa amagona ndikumamva kutsangalatsa koma samaziwa kuti soapoyo samachokako yese ndipamene osalilayo amasanduka acide ndiye akamakumana ndi madzi ena amansungunuka ndikupangaso madzi ochuluka koma akaonesesa samachedwa kuuma kunja kwa Malo awo pomwe kati amakhala kuti adakalipo ndiye amasowaso kutulukila
@LeonardButton-e9u
@LeonardButton-e9u 8 күн бұрын
Ndiye adzimayiwo amasangalasidwa ndi kaumidwe ka kunja pa moyo Wawo watsiku ndi tsiku pomwe kati mukuonongeka chifukwa sizimabwelesa ululu uliwose but when woman to receive privet part yamamuna and mamunayo amakhala kuti wasekula nkhomo
@MwaiJuma
@MwaiJuma 9 күн бұрын
Mulungu amatha mama
@Trynes-p9q
@Trynes-p9q 9 күн бұрын
Mulungu amayakha mama
@OmgaKulemera
@OmgaKulemera 9 күн бұрын
Prayer ya mphamvu..
@MALAWIAN-v2f
@MALAWIAN-v2f 7 күн бұрын
Anakwatiwidwa ndi chiwanda Cha kumidima koma alimbikire mapemphero ,chimakana kugona ndi wina
@WeziKamanga
@WeziKamanga 9 күн бұрын
Prayers
@zuluchifundo7610
@zuluchifundo7610 8 күн бұрын
Nthaw yanu azmai
@Zionechipatso
@Zionechipatso 8 күн бұрын
Pemphero ndiyankho LA China chili chonse
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 10 күн бұрын
Zimakhara tizizozono mwatitayilira mmm
@TalindaMikondo
@TalindaMikondo 3 күн бұрын
Ndi chizonono kumene ndipo sizikufunika nso pephero ai kuchipatala kapena achikuda zitha
@ChrissyScot
@ChrissyScot 10 күн бұрын
U must try to use lemon n salt.. Komaso zikuoneka kt zamwawathu izi ofunika kulimbika kupephera .. palibe Vuto lopanda yankho..
@SelinaDeniasKalemboni
@SelinaDeniasKalemboni 10 күн бұрын
mulungu nde yakho la zonse mama
@agnesskasambala4789
@agnesskasambala4789 4 күн бұрын
Ndi infection yimadana ndi umuna zofunika doctor ndithu zitha ndithu sikulodzedwaso
@Masi-e9f
@Masi-e9f 2 күн бұрын
mmmmmm ndizamuwanthu munthu amakuthira madzi amaliro munthu osadziwa ineyo munthu anandiuuzapo kupanjira Kuti ukunokha bwanji
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 10 күн бұрын
Choka ine ndavela😂
@VioletDambolachepa
@VioletDambolachepa 8 күн бұрын
Mupita kwa Doctor akakuthandizana Pali mvuto ndithu
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 10 күн бұрын
Kodi bhonya akazi ambilitu amavka bhonya km sitigawqwuze cnanga timawopa kukhumudwisana kapena kukhala ndi stress ka ndie timangomutuluka basi enanu musazitenge udolo asikana enanu ndi afungoso 😂😂😂
@Shupe-z7q
@Shupe-z7q 9 күн бұрын
Muwauze akazi anu adzisambira soda komanso lemon ndi mchele mudzandiyamike. Mkazi amakhala ndikafungo kachikazi ngati akuchoka mu period basi mumvelenso nkhaniyo munthuyo wagonapo ndi akazi angapo uyuyu anali wafungo ngati akazi mukuwanena kuti akazi amanunkhadiwo. Zikomo
@FagessieMakhuludzo
@FagessieMakhuludzo 8 күн бұрын
Pemphero ndilofunika chemwali
@wisdomkadodanyoni1190
@wisdomkadodanyoni1190 10 күн бұрын
Sorry mama
@OliverChaxy-gy3ss
@OliverChaxy-gy3ss 8 күн бұрын
Zoon
@KelvinKaphiri-l2n
@KelvinKaphiri-l2n 10 күн бұрын
Mmm zosaenda
@ANGANILEMwenefumbo
@ANGANILEMwenefumbo 10 күн бұрын
Azidya thochi imodzi patsiku mamawa uli wonse asanadye kanthu
@RhodiWhite
@RhodiWhite 10 күн бұрын
Sono ukati yazimai ndiye umaponyelanji pano sono akufotokozayo ndi zimai
@FaidaAdimu
@FaidaAdimu 9 күн бұрын
Apite kuchipatala akamuone ngati alibe fistula
@EnockSankhylani
@EnockSankhylani 10 күн бұрын
Chizonono chimenechi akuyenera kupeza achikuda ndilowerer inbox
@blessingsNyirenda-pj3rs
@blessingsNyirenda-pj3rs 10 күн бұрын
Come to my box although za azimayi sorry for that.
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga 8 күн бұрын
U have to believe and pray extra harder palibe vuto losatha padziko pamaso pa mulungu, u have a good man he is your real saulmate
@TadalaBrown
@TadalaBrown 5 күн бұрын
Apeze adyo ND kasalu ka cotton adyoyo kumusija ndkumuika pansalu ka cotton ndkumavala ngati pad mawa, masana nd madzulo adyo amayamwa madzi oipa amene amapezika Malo obesika pakutha Kwa mwezi adzawona kusitha 4:55 4:57
@VeloLibawe
@VeloLibawe 10 күн бұрын
Choyamba apite kucipatala akaonedwe
@HameedaStambuli-fx5vt
@HameedaStambuli-fx5vt 10 күн бұрын
Mmmmm
@yunusibnsallamaitim6924
@yunusibnsallamaitim6924 10 күн бұрын
Koma yeah mwina tu kumagwiritsa Doom spray b4 kugonana
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 10 күн бұрын
Atafune neem kwanuko ilipo fungo lonse kuchoka
@EdinaMwase-f8f
@EdinaMwase-f8f 10 күн бұрын
Zofunika kuchipatala akakuyeze zikakanika kuchikundako
@ConeyMbota
@ConeyMbota 9 күн бұрын
Ndzotheka kuchiza vutoli
@ConeyMbota
@ConeyMbota 9 күн бұрын
Ndkhoza kuthesa vuto la kanyimbili
@LinlyMathewe
@LinlyMathewe 10 күн бұрын
Izitu koma iyeyo siwoyambadi alipo ndithu anthu oterowo koma zimangifunika kulimba mtima kusaka achikuda basi
@ChisomoTrevor
@ChisomoTrevor 10 күн бұрын
Nzanga wina wake akamvekaso fungo koma linantha akanthilako soda ndi mandimu pano alibwino akuti yesani kunthilako soda
@MartinNgoma-tp2jk
@MartinNgoma-tp2jk 10 күн бұрын
Alikoma nkhwala achiboyi nimatenda awo
@MosesNyasulu-c3x
@MosesNyasulu-c3x 10 күн бұрын
Apite ku chipatala.chituzilo mabuleki amamasuka mazi angotuluka
@WilsonNedi-s6t
@WilsonNedi-s6t 10 күн бұрын
Anamupanga chipongwe ena
@LovenessMphukiwa
@LovenessMphukiwa 10 күн бұрын
Ayambe wapita kuchipatala zikukanika ayese zachikuda
@ShackreenSINSAMALA
@ShackreenSINSAMALA 10 күн бұрын
Kumakhala kuti wina anatengapo gawo adamupaka mtudzitudzi ameneyu ndithu angopita ku chikuda
@ReginaStaliko
@ReginaStaliko 10 күн бұрын
Iiiiiiih sorry zosayenda azipephera kwambiri
@SammuelThawani
@SammuelThawani 10 күн бұрын
Very sorry
@AlexanderTraffick
@AlexanderTraffick 10 күн бұрын
I think anarodzedwa
@JabulanMussa
@JabulanMussa 10 күн бұрын
Aziphembela kwambili
@catherineMalisawa-z7z
@catherineMalisawa-z7z 10 күн бұрын
Samban minzi za ntote kapena casava twice a day for 3
@IssahBwanali-i8w
@IssahBwanali-i8w 10 күн бұрын
Zamu wanthu apite kwa sin'hanga
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 9 күн бұрын
Ma vaginal yeasts amenewo ma fungus disease amwe mankhwala a chikuda .
@mercygongolo8431
@mercygongolo8431 8 күн бұрын
Pempelo basi
@MissyThobve
@MissyThobve 10 күн бұрын
Zovuta kobasi
@VeroMaster-lo1mu
@VeroMaster-lo1mu 10 күн бұрын
Tayesani kuchipatala
@AlexanderTraffick
@AlexanderTraffick 10 күн бұрын
Azipakako chitedze akazati mayoo kuchira ndikomweko
@FrancisShumba
@FrancisShumba 10 күн бұрын
Kķķķkkk
@Unknown-n9w4y
@Unknown-n9w4y 9 күн бұрын
Kumakhala ndiumuthu pena
@AlexanderTraffick
@AlexanderTraffick 9 күн бұрын
@Unknown-n9w4y Alibe umunthu mwiniwake wankhani ayibweretsa bwanji pa Media nkhani yonyatsa ngati imeneyi
@TharcilleNyampunda
@TharcilleNyampunda 9 күн бұрын
Koma abale!!chitedze ndi mankhwala? Ulandile Yesu ndithu
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 10 күн бұрын
Bwanji wosaponyela azimayi muzikhala serius
@NoahNjati-ee4dp
@NoahNjati-ee4dp 10 күн бұрын
I have solution for that kungoti mwanena kuti aonere ndi akazi okha
@WeziKamanga
@WeziKamanga 9 күн бұрын
😂😂😂😂
@NoahNjati-ee4dp
@NoahNjati-ee4dp 9 күн бұрын
@@WeziKamanga 🤣🤣🤣
@Jamesmadeya-t7f
@Jamesmadeya-t7f 10 күн бұрын
Azipephela kwambili mulungu amayankha
@Aishajuliusjekapu-u6z
@Aishajuliusjekapu-u6z 10 күн бұрын
She should try water therapy and prayers
@WilliamBauren
@WilliamBauren 10 күн бұрын
Not every thing needs God,bt try our best
@FaidaAdimu
@FaidaAdimu 9 күн бұрын
Apite kuchipatala akamuone ngati alibe fistula
Zina UKAMVA kamba anga KHWESI🥵
24:13
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 17 М.
When you have a very capricious child 😂😘👍
00:16
Like Asiya
Рет қаралды 18 МЛН
So Cute 🥰 who is better?
00:15
dednahype
Рет қаралды 19 МЛН
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 108 МЛН
MALO AMIZIMU AMENE AKAZI SALOLEDWA KUFIKAKO MDZIKO LA MALAWI
12:49
Factory265 Media
Рет қаралды 158 М.
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
40 Qiso┇40 Qiso Ee Ygu Saameynta Badan 2023ᴴᴰ┇► Sheekh Musdhafa Xaji Ismaciil
3:26:03
ANTHU OTCHUKA OMWE ANANYOZA MULUNGU | NKUMWALIRA
6:04
Adzukulu
Рет қаралды 25 М.
When you have a very capricious child 😂😘👍
00:16
Like Asiya
Рет қаралды 18 МЛН