JOYCE BANDA WAING’ALURA POYELA LERO KU ZOMBA PA NSOKHANO KUTI IWO NGATI PP ARE NO LONGER IN ALLIANCE

  Рет қаралды 45,999

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 141
@BawulenLuka
@BawulenLuka Ай бұрын
Joyce Banda, saulos chilima, timothy mtambo ndi ma judge komanso ampingo mulungu akakukanthani agalu inu
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Ай бұрын
I like your comment kkkk agalu amenewa ariwika mmavuto kwambiri.
@vitujames53
@vitujames53 Ай бұрын
Anthu ndinuyo..kusowa umunthu ukutu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Iyi ndi comment yabwino yopotsa ma comment onse lero muone zinthu mmene zakwelera + njala ndi Kuba ndalama
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
​@@vitujames53zomwe ankapanga zija zopusitsa anthu zija ndie zinali umunthu? Aaaaaa
@MaggieCement
@MaggieCement Ай бұрын
Pomsooooooo ndiye poti Amalawi ngopusa kumagosatila komwe mbuzi zulowera poti kuli nsipu ubwino wake ayamba kuphana okhaokha mene amanenera chakwera kuti akhesa mwazi pozakhesa wa mphawife atathana kale okhaokha
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo Ай бұрын
Bring back the jet first....otherwise forget.
@BrownNamondwe
@BrownNamondwe 27 күн бұрын
Okuba uyu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Kupeperesa anthu munawapeperesaku mupepesenso coz dziko lero tikulira coz chainu. Lero njala ilipaliponse, Chilima anaphedwa, zinthu zinakwera kwacha ingogwesedwa mmene banja lawo lafunira, misonkho yathu ikubedwa koopsa + nepotism. Malawi waonongeka coz chainuyo, Timothy Mtambo ndi chilima. Mukuyenera mupepese kuntundu wa anthu.
@BrownNamondwe
@BrownNamondwe 27 күн бұрын
Chilombo ichi osachisekelera
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 Ай бұрын
KUTI MVETSELE BWINO ZOMWE ALANKHULA KU MSONKHANO A PP ANENA KUTI ATULUKA KOMA KWA IFE OZIWA NDALE SANATULUKE AYI AKUFUNA AWONE MPHAMVU ZA CHIPANI CHAWO AFTER ABWERERASO KU MCP .
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
😂😂😂😂😂Koma nanunso mnzeru zinakuperewerani bwanji 😂😂
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Akufuna ma vote then azaphakize ku mcp segulan maso amalawi ,sanatuluke awakugwilizano awa
@HappyAutumnTrees-cd9ye
@HappyAutumnTrees-cd9ye Ай бұрын
Anthuwa akuona ngt kusauka ndikupepera et asamatiseweretse ,,
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Amalawi Mai uyu ndi clook ndi wa MCP musamuvotele
@MatthewKanyenda
@MatthewKanyenda Ай бұрын
Akufuna kusokoneza anthu awa, adalikuti pamene dziko lalowa chi vuto chimene talowachi.?
@JaffaliShaibu
@JaffaliShaibu 28 күн бұрын
Alipo ku PP konko ena tinasankha koma samatiyankha mafoni chinzake chinatha. Ndikanamutchula dzina koma basi.
@FredLeman-v5j
@FredLeman-v5j 17 күн бұрын
Munthu watuluka ku Mcp Kom ulibusy kulemekesa M'busa opusayu unyatu Palibe azakuvotere Mai wa cashgate
@FredLeman-v5j
@FredLeman-v5j 17 күн бұрын
Munthu watuluka ku Mcp Kom ulibusy kulemekesa M'busa opusayu unyatu Palibe azakuvotere Mai wa cashgate😂
@sanudiphimba8619
@sanudiphimba8619 Ай бұрын
Kupanda nzeru kwa mai uyu ndikomwe kwaika dziko pamoto, dyera linakula zedi.
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 28 күн бұрын
Kunama maiwa kufuna mavote aanthu basi ndi wa MCP Joice banda tikukuziwani ife munatipusisa kale
@user-xo8ms5wh2s
@user-xo8ms5wh2s Ай бұрын
Mwakalamba tazisiyana izi zikuchedwetsani zikufunika anthu amuna tipitani mukalape ku Church amai inu 😢
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 28 күн бұрын
Mulungu azikukanthani modzi modzi mpaka mutha phiti ndi ndalama za misonkho yathu ife amalawi
@user-mj4lp9fj4c
@user-mj4lp9fj4c Ай бұрын
Iwe ukuti unamaga sewu wathekerani wake wakuti wasowa zonama kumeneko munthu oipa iwe
@ChristopherNamatika
@ChristopherNamatika 27 күн бұрын
Ndinamanga manyumba ee misewu mamatiresi kkk sabola wakale sawawa masiten ndi mcp yanuyo
@EnerstBanda-m4s
@EnerstBanda-m4s Ай бұрын
Unamangaso Bingu Stadium osaiwala kuyatsaso magazi komaso kubweletsa mafuta omwe kunalibiletu munthawi ya Bingu komaso ndalama za kunja koma sutikukufunani pokhapokha mutaphatikuzana ndi utm
@IqrahSikweya-wm5mn
@IqrahSikweya-wm5mn 28 күн бұрын
Ndi ndale izitu koma iyeyo akunama sanatuluke angofuna kwapusitsa Amalawi
@kekeaufi9834
@kekeaufi9834 Ай бұрын
*Kumvesa chisoni ndi manyazi kwake ,,ambili akusokosa lerowa ndi amene amati mcp ilowe boma,,,lero ali pokopoko 😂😂😂😂tikusowa zotola,,,Atupeletu akhanena zonsezi amatiuza 😢😢*
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Patupere ndi maso mbenya atu amene asala mulungu akudalisene moyo wako tupere alamulire mzikolo rathu la Malawi inshall allah
@ObediMkwala
@ObediMkwala 28 күн бұрын
A JB,mudaitanitsa amayi akunyumba ya malemu Diet Mkwala kuti apite ku state House nthawi imene muli apresident koma palibe thandizo limene mudawapatsa amayi onfedwa,mudawonetsa kulephera kwanu
@ObediMkwala
@ObediMkwala 28 күн бұрын
Amayi aja mudawatsiya ali ndimisonzi m'manso awo muwalondole kunyumba kwawo ,muwafufuze kunthalireko mukawapepese chifukwa amuna awo adafera akutumikira inu,pangani zomwezo
@Blessings31
@Blessings31 Ай бұрын
Amayi ndi deal Yemwe zikumunyansa asanze
@BrownNamondwe
@BrownNamondwe 27 күн бұрын
Mfumu chopi yo ngati wakomedwa ndinsaluzo zake sitifuna nsaru ife
@GoldenIneyo
@GoldenIneyo 21 күн бұрын
Ndine Golden k phiri kukasungu pepani Amayi musawavele Anthu achipongwe ife tilipambuyo panu
@user-qe6wr6wr8p
@user-qe6wr6wr8p 28 күн бұрын
I we about mayi wabodza,Loma dziko limenelo silako,silamakolo ako,koma ndilamulungu ,simunaphunzile koma kuyankhula
@MariaDavison-i6y
@MariaDavison-i6y Ай бұрын
Mseu wa Thekerani anamanga ndi peter osanamiza anthu
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 29 күн бұрын
Kuteroko a MCP akuthamangitsani eti??,
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h Ай бұрын
Mcp siyomapanga nayo alliance akuphani ohoo
@BrownNamondwe
@BrownNamondwe 27 күн бұрын
Zonena pa tv malamba umanga wekha
@Okalekale
@Okalekale 29 күн бұрын
Amayi awa ndiopanda manyazi,dyera ndilalikulu mwa amayi amenewa,m'mene anaonongela dziko? Malawi ali chonchi chifukwa cha UDF,DPP ndi PP ndiye akufunanso kulowa m'boma akatani?,akapitilize kuononga?.Anthu andalewa amatitenga aMalawi ngati opusa kwambiri,akuganiza kuti aMalawi anayiwala za ndalama zimakapezeka ku manda zija?.
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi Ай бұрын
Ambuye yesu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Chakwera wakupha garu nyani mbuzi mfiti tombolombolo okumwa madzi ndikuthako
@ClementsKamanga
@ClementsKamanga Ай бұрын
Inuyo fundo zanu zilibwino koma anthu opanganawo mgwilizanowo mbola amai anthu akuopan chifukwa cha awowo
@JhdaLifi-vu9sd
@JhdaLifi-vu9sd 29 күн бұрын
Hule lamunthu ili zopepelesana tinasiya kugwadila mafano ife tinatopatu
@JevinTeller-en9rh
@JevinTeller-en9rh 29 күн бұрын
Bola JB yu osati Lazaro wa umphawiyu
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Amai kuganidza watsanje lelo malawi ali pamoto pomwe munat anyamata alipula.pamoto dziko lelo nthawi MUTHALIKA ndi CHAKWELA mamvuto ali pati inu mwawononga nawo malawi kumatso mwaphetsa chilima chifukwa chodana ndi MUTHALIKA nde mwatidzudzitsa amai ndi MCP yanuyi yankhaza yakupha
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Anapepelesa Amalawi kuti avotere chakwera,mavuto omwe ali lerowanso ali pat of it sangazembe,amati chakwera ndi m'busa sanganame.
@MahallaMinistries-fv1hw
@MahallaMinistries-fv1hw Ай бұрын
Baby politics in Malawi. Lord have mercy.
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x Ай бұрын
Chilungamo koopsa zedi brother anthu opepera awaa
@FredLeman-v5j
@FredLeman-v5j 17 күн бұрын
Mmai wabodza iwe shut up..... Sunatulukeso ku mcp
@FortuneAndrew-nb2im
@FortuneAndrew-nb2im Ай бұрын
Anthu opepera ngat inu ndiomwe mwapangisa malawi kukhala ovuta kwambiri mabvuto azaonen
@VincentMtambo
@VincentMtambo 29 күн бұрын
Chilungamo akuchidziwa
@BoscoWilliams-zl5sl
@BoscoWilliams-zl5sl Ай бұрын
Ayi zikomo mayi joyce banda pozindikira lero kuti tonse alliance kulibe. Mangani malamba and i quote
@VirginiaMafenda
@VirginiaMafenda Ай бұрын
Ngati atuluka bwanji akulimbana ndi peter munthalika pa mfundo yoti sanatuluke munyengo ya cyclone moti alunjike za sogolo lawo landale pamene atulukamu
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Division of southern votes that is great strategy
@user-ov7yw4bq7y
@user-ov7yw4bq7y Ай бұрын
Nsalu zithandiza chani koma kumalawi tili mubotolo ndithu
@MatthewKanyenda
@MatthewKanyenda Ай бұрын
Eish akulu inu Mmmm anthu timaganiza mofoila kwambiri et nsalu zoona anthu mkumaombera mmanja?
@user-uk3bz1hr5t
@user-uk3bz1hr5t Ай бұрын
Enawa nde akugawa chani?
@ObediMkwala
@ObediMkwala 28 күн бұрын
A JB adalojeza kuti amangira amayi omwe amuna awo adamwalira pangozi yagalimoto museu wachitipa jembia,koma ny'umbayo sadamange m'paka pano kuchoka chichitikireni changozi 2012,tikunena lero ndi 2024,atiuza chani ife?apite kuchitipa south akamangire kaye amaio aferedwa kaye ny'umba imene adalonjeza
@jamesmuyaya1158
@jamesmuyaya1158 29 күн бұрын
Kodi when will the issue of politicizing maize end,??
@AbuZubeir-x4c
@AbuZubeir-x4c Ай бұрын
I support you amayi zinthu izi munaononga nokha nde bwerani mudzakonze zomwe munaononga
@ChristopherNamatika
@ChristopherNamatika 27 күн бұрын
Sabola wakale anzanga sawawa
@PaulOSBjaulen
@PaulOSBjaulen Ай бұрын
❤❤❤❤❤
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 Ай бұрын
Mayi, kaphikileni ana kunyumba ,ana akufa ndinjala
@user-io2uw2me9f
@user-io2uw2me9f Ай бұрын
Kunenatu chilungamo sck Joyce banda ndi mtambo sikut ndi anthu oipa koma chakwera nde mfiti theretu sanapange malonjezano ndi azake
@user-mx5cx3gl4h
@user-mx5cx3gl4h 29 күн бұрын
Mesa munatitulusa mu mboma mwa khaza,,,muwonadi nyengwe
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p Ай бұрын
Ndale zama handouts siti tandiza amalawi.
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq Ай бұрын
Mayi wanga contact yanu ndilibe koma ndikufuna nditalankhula nanu pofuna kuti ndithandizane nanu ku manga ma structures
@mcsydenynsinga7610
@mcsydenynsinga7610 Ай бұрын
Mujuaputa nokhatu anzanuwo mayi!! Kkkkk akakubwezelani basi muzinena kuti ndioipa akutukwana amayi kkkkkk inutu ndi a phokosodi ndithu😂😂😂😂
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh 29 күн бұрын
Aaaaa inu munasokoneza amalawi musazivutepo apa
@SheriffNseula
@SheriffNseula Ай бұрын
Kodi fundo zonsezi mwayenda nazo ku tonse alliance osadzichita bwanji kumenekuja?zauhule basi Kodi kupanga alliance kuja mesa kuti nonse muyendetse dziko?ndiye lelo mudzinama zamfundozinso???mwaipa basi
@Edson-sj8vn
@Edson-sj8vn Ай бұрын
Alephera kubamo pano MCP ndiyoipa kkkk andalewa anakonzaa
@ThomasMwandila-tn7cf
@ThomasMwandila-tn7cf 29 күн бұрын
Amama mukutani nthawi yanu chakudya chinariposepose
@FatimaSande-lb1hd
@FatimaSande-lb1hd 26 күн бұрын
Koma amai ali pompano? 🤭 Nzibambo kudikila kkkkkkk.....
@vitujames53
@vitujames53 Ай бұрын
Nkhani ndi imeneyo...okumva wamva
@HappyAutumnTrees-cd9ye
@HappyAutumnTrees-cd9ye Ай бұрын
Anthu lero akuvutika ndinjara ndie muzit tatuluka mukutanthauza chani muwasiya anthuwa akuvutika Chonchi mulungu akuyendeleni anthu inuyo ndithu😭😭😭😭
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu Ай бұрын
Amayi anthu asakupusiseni, panokha simungawine, even itakhala kuti si 50+1.
@PaulDaka-dc3re
@PaulDaka-dc3re Ай бұрын
Mayiwa achedwa nazo it's too late
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq Ай бұрын
Mayi Banda tili nanu limodzi ndipo titipulira limodzi ngati mutafuna kutero
@simonmakamba9539
@simonmakamba9539 Ай бұрын
Mayi wanga uyu ndilibe naye vuto konse
@thomasmcbanda9794
@thomasmcbanda9794 Ай бұрын
Kuzavotera pp wavotera MCP samalani
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o Ай бұрын
Mai woipa iwe kachipani Kako kam'manjako
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 29 күн бұрын
Tangopitani denfen jbk inu Mai, za ndalezi ai siyani😂😂
@user-lc3sw8iz2g
@user-lc3sw8iz2g Ай бұрын
ATUMIDWA NDI MCP KUTI AGAWE MA VOTE A DPP KUMMWERA
@HajjAmadu-e1u
@HajjAmadu-e1u Ай бұрын
Maiwa ndiopa inde tikamva imfa ya chilima ati akukhuzidwa koma Pena tiziyamikira ku zomba amangra nyumba anthu akulu akulu apa ai anayesetsa mai
@swadikimbwana7680
@swadikimbwana7680 Ай бұрын
Mai ndithudi munapanga chithukoko kwabasi Apa ndikuchita maDua kuti Insha Allah mukakalenso pa mpando wa Pulesideti 2025
@MirajiYusuf-u9r
@MirajiYusuf-u9r 29 күн бұрын
Push us mom nganganga pambuyo panu
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v Ай бұрын
Cash get back
@mosesdevwe4267
@mosesdevwe4267 Ай бұрын
After utagulitsa ndege,,, mayi awanso nde ayitu
@user-chimenyaMTV
@user-chimenyaMTV Ай бұрын
Koma nyimbo YOMWE mumaika pansi simagwilizana abwana sithani beat
@FatimaSande-lb1hd
@FatimaSande-lb1hd 26 күн бұрын
Eya inenso sindimvekera bwino imasokoneza
@arthurmakuluni6676
@arthurmakuluni6676 29 күн бұрын
Inde mayi
@BrownMainje-sh7hj
@BrownMainje-sh7hj Ай бұрын
Joyce Banda iwe sukufunachani iwe sukufunachani iwe Joyce
@TomasKalizga
@TomasKalizga 29 күн бұрын
Bro kungokupemphani kuti mkamapanga posit ma videos muleke kuyamba kulakhulapo komaso musiye kuikapo nyimbo coz overafe zikuti sokoneza
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 29 күн бұрын
Mamaawa dyera
@FrankFrancis-ch3xv
@FrankFrancis-ch3xv Ай бұрын
Nzibambo kudikula kumeneko koma mayi alipompano?joyce banda funso?😅😅
@dianachabs
@dianachabs Ай бұрын
Tipatseni signal 🚦 mama tilowele kuti?
@user-fh3dn8kt2j
@user-fh3dn8kt2j Ай бұрын
Akuima chifukwa anthu akuti awauza, kuti aime aati,,koma maiwa nde mphanvu zikupita ndithu koma dyera silabwino ataa
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev Ай бұрын
Ndale zoyipa mwapangana zoti mugawe ma vote akumwela kuno....mmmmmmm
@chisomokalinda6666
@chisomokalinda6666 Ай бұрын
Tipaseni number yawo mayiwa
@user-dg5pc6rz1b
@user-dg5pc6rz1b Ай бұрын
Kkkkk mcp siyingayanjaneso ndi utm anthuwa akudziwa
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o Ай бұрын
Tikumenyan ana mwachepa nazo😂😂
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 29 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 atulukamo
@MphatsoMkanda-g1o
@MphatsoMkanda-g1o Ай бұрын
Anali kale uyu
@sanudiphimba8619
@sanudiphimba8619 Ай бұрын
Mai wachinyengo uyu,
@kennedychinguwo1640
@kennedychinguwo1640 Ай бұрын
Kodi PP ndi chani??
@dianachabs
@dianachabs Ай бұрын
Amayi woyeeeeeee
@chimwemweshadrick5972
@chimwemweshadrick5972 Ай бұрын
Amaiwa amabhebhetsa
@williammandhlopa
@williammandhlopa Ай бұрын
A usi akutani ngati alliance yathaa
@KateMunthali
@KateMunthali Ай бұрын
Kayatu🤗
@user-gm9xj1wc2m
@user-gm9xj1wc2m Ай бұрын
Muli mbuli mbuli
@tobiousmtenje139
@tobiousmtenje139 Ай бұрын
Inatha kale kale,anthuni mumangokakamila
@ADHASAPONYILENDA
@ADHASAPONYILENDA Ай бұрын
Kusowa chochita manyazi awo
@dalitson3558
@dalitson3558 Ай бұрын
Uchose nyimbo ikumveka pansiyo
@jahmanmakwinja-ef7zn
@jahmanmakwinja-ef7zn Ай бұрын
Kung'alura mai more fire
@duncanKingsly
@duncanKingsly Ай бұрын
Palibepo ndikunva
The FASTEST way to PASS SNACKS! #shorts #mingweirocks
00:36
mingweirocks
Рет қаралды 14 МЛН
Angry Sigma Dog 🤣🤣 Aayush #momson #memes #funny #comedy
00:16
ASquare Crew
Рет қаралды 49 МЛН
Electric Flying Bird with Hanging Wire Automatic for Ceiling Parrot
00:15
MFUMUKAZI..28/06/23..FLORA SUYA'S👉+265883106798
27:54
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 18 М.
The FASTEST way to PASS SNACKS! #shorts #mingweirocks
00:36
mingweirocks
Рет қаралды 14 МЛН