KANGAUDE part 2...MNYAMATA YEMWE WAKHALA AKUBA | KUVULAZA | KUMPHA | KUTHAWA KUNDENDE on @mibawatv

  Рет қаралды 79,914

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 214
@OwenPhiri-b9n
@OwenPhiri-b9n 14 сағат бұрын
Mulungu alikodi. Mulungu akupatseni moyo wautali bro. You have a living testimony which has changed my life completely ❤
@williechimtaka
@williechimtaka Жыл бұрын
You are the chosen one, born for a purpose. God really has been sending Angels in all your darkness hrs. May the Lords purpose be fulfilled on your life. This is great testimony. Its my prayer to see you one day.
@frankchiwawa4795
@frankchiwawa4795 Жыл бұрын
Eish pliz this story so touching. Kumposa macholowetu
@patience5ndhlovu17
@patience5ndhlovu17 Жыл бұрын
Please it will be best if we can hear from horses mouth e.g police,mortuary assistant, people mentioned and etc
@frankchiwawa4795
@frankchiwawa4795 Жыл бұрын
@@patience5ndhlovu17 kkkkkk I don't they can speak or comment on this.
@smithdolozi
@smithdolozi Жыл бұрын
Kwa ena after kunva nkhaniyi still sakukhulupilira zamphanvu ya Mulungu, koma dziwani Mulungu akafuna kuchita zinthu amachita zomwe iyeyo wafuna, God has power over, Death, Police, Doctors, Mortuary even over Courts. M'baleyu akuyenela apita mmanja mwa azitumiki a Mulungu omwe amuthandizile Kukula kwa moyowake wauzimu kuti cholinga chomwe Mulungu anamubwezela kuyinfa chikakwanilitsidwe.
@clojistix_g
@clojistix_g Жыл бұрын
Cholinga chomwe Yehova wakutetezera ndi kukusungira moyo chikwanilitsidwa ndithu. You have a great purpose ahead, God be with you.
@Gautengstanzo
@Gautengstanzo Жыл бұрын
Mmmm this is amazing have never experienced this kind of salvation before. I salute you lord.
@franceqongwani1970
@franceqongwani1970 Жыл бұрын
Jehovah thank you for showing your power through him and please look after him.
@jamesmakawa-hl6gf
@jamesmakawa-hl6gf Жыл бұрын
Ambuye kumwambako mulemekezeke pa zabwino ndi chifundo mwamuchitila brother wa amen 🙏
@AlexKaunda-x3p
@AlexKaunda-x3p Жыл бұрын
Mulungu Ali ndi cholinga ndi munthu uyu God bless u my brother wrong leave from south africa
@CholapitsaSamson
@CholapitsaSamson Жыл бұрын
GOD is great always This is miracle and unbelievable
@franceqongwani1970
@franceqongwani1970 Жыл бұрын
Why God was keeping this man?? This is mystical 😢
@charlesmpaso2383
@charlesmpaso2383 Жыл бұрын
Ndilibe mawu koma kumwamba kulemekezeke ndithu...mulungu alinawe cholinga never give up
@kettiemnthali9483
@kettiemnthali9483 Жыл бұрын
Yehova alemekeze chifukwa cha chipulumutso chanu brother, sizamasewera ndilibe mau
@mercychiba4007
@mercychiba4007 Жыл бұрын
Mulungu akukusungani ndicholinga kt musithe miyoyo yaanthu ena kt amuziwe yesu
@GraceKing-d2n
@GraceKing-d2n 4 ай бұрын
This is wonderful story Mulungu Ali ndicholinga nawe.Pereka.moyo wako kwa Yesu ndikuyamba kulapa
@henrymkata6001
@henrymkata6001 Жыл бұрын
We have chosen people in this world. They are born as heroes. They win even without a way and if you fight them you lose. If you're around this person trust me you got a big blessing and you can do more with him cuz he don't chase blessings but he's the blessing
@karrassphiri7381
@karrassphiri7381 Жыл бұрын
So touching story. Let us remember the brother in prayer and whatever support he may need.
@saukophiri4535
@saukophiri4535 Жыл бұрын
Have been waiting for this part Thank you kangaude
@godfreychiotcha4503
@godfreychiotcha4503 Жыл бұрын
Tchimo lingakule bwanji amakhuluka ngati wapempha chikhulukilo,ndi ntchito ya mwazi wa ambuye yesu kusuka tchimo, ambuye akutetezeleni m'bale
@FickrahJali-qf4lh
@FickrahJali-qf4lh 6 ай бұрын
👏
@Cosmas-c9v
@Cosmas-c9v 4 ай бұрын
Thanks dude!! For yur confessing...no matter hw big sin is....God will washed away...nothing but blood of jesus...
@afritouch4660
@afritouch4660 Жыл бұрын
This is unbelievable story.. WIW..!!😮
@charlesbanda3498
@charlesbanda3498 Жыл бұрын
Komatu a Seventh day samapemphera sunday ngati momwe akufotokozeramu.
@kephasmseteka3462
@kephasmseteka3462 Жыл бұрын
the story has abit of a happy ending :) , if he really mean zomwe akukambazi nde kuti the guy wasinthadi. So touching kumapetoku
@hafeezismailnsamala8812
@hafeezismailnsamala8812 Жыл бұрын
BROTHER ATHUWA CHONDE AKANATIPANSIRA NUMBER YA AIRTEL MONEY NDI MPAMBA PLEASE PLEASE. MULUNGU AMABVA KUKHULULUKA AKUKHULULUKIRA.
@JamesKeneth-c8c
@JamesKeneth-c8c Жыл бұрын
Mmmmmm mulungu ndiwabwino kwambir mulungu yemweyo amuteteze ndipo khumbo la mulungu likwanilisidwe pa moyo wake
@weisheit8037
@weisheit8037 9 ай бұрын
wow...good job from the interviewer n the guest too, osaiwala english subtitles....much respect
@Maxielyies
@Maxielyies Жыл бұрын
This is too impressive, may God fulfills His will upon him
@tingamasi106
@tingamasi106 Жыл бұрын
Abel pliz this story should not end here. Meet ena atchulidwawo alongosolepo
@MittonMwandira
@MittonMwandira Жыл бұрын
Mmmm this is so much amazing, my brother God have got a big purpose with your life and a big reason to other people you must praise and worship God the lest of the whole of your life please. God is good all the time
@MoboGobo-zg4xm
@MoboGobo-zg4xm Жыл бұрын
Yes God is wonderful 🤗🤗
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef Жыл бұрын
is amazing sure take step to pray dipiry
@MaryChimowa-f8u
@MaryChimowa-f8u 6 ай бұрын
Mulungu ali nanu cholinga osachimwaso Mulungu ndiopsa kwambiri aposa zolankhulidwa ❤grory to God powerful
@McDonaldChayaka-hd9tv
@McDonaldChayaka-hd9tv 2 ай бұрын
My God is able and he will never fail
@peterbakuwo1249
@peterbakuwo1249 Жыл бұрын
Got you straight,....was waiting this part 2. Thanks kangaude.
@KefasiKatayila
@KefasiKatayila Жыл бұрын
Ambuye ndinu wamkulu ndinthu❤❤❤❤❤
@thoccoleman9783
@thoccoleman9783 Жыл бұрын
Ambuye ndilibe nanu mawu
@BesterSengeledo
@BesterSengeledo 6 ай бұрын
For sure Mulungu akufuna Akuluwa alape monga akuchitilamu
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 Жыл бұрын
Have been patiently waiting for part 2 thanks kangaude
@gracekandodo6162
@gracekandodo6162 7 ай бұрын
Ambuye mulandire Ulemu chifukwa cha Chifundo chokwanira . Amen
@fanniekamanga7760
@fanniekamanga7760 6 ай бұрын
What God cannot do does not exist. Amazing Testimony
@StanfordPhiri
@StanfordPhiri 7 ай бұрын
Mulungu ndi wabwino nthawi zonse
@sarahgalleta9240
@sarahgalleta9240 Жыл бұрын
This guy is loved by the most high ...what a testmony
@RobertJosephy
@RobertJosephy 4 ай бұрын
Ambuye apitilize kukutetrzelan. Amen
@dronlambert8796
@dronlambert8796 Жыл бұрын
Your blessed brother God is keeping you for his work
@lame8
@lame8 Жыл бұрын
Likufunika thandizo lachangu anthu amuthandize😢 koma akanasiya number kuti anthu akoza kuponyako kenakake kuti athandizike mwachangu ife tili kutali ndikanakonda akanasiya number ya wina aliyese amakala naye pafupi. Mulungu ali ndi plan yayikulu kwa ameneyu osamayika❤
@kondwanichimbayo5409
@kondwanichimbayo5409 6 ай бұрын
Anthu owathandiza siawa. Uyu akagwere
@mrsoko.catholicsongs
@mrsoko.catholicsongs Жыл бұрын
It's a touching story. Glory be to God! 😥
@AngelaBanda-r6b
@AngelaBanda-r6b Жыл бұрын
Lord have mercy the story is so touching 😢
@KennedyKutembo
@KennedyKutembo Жыл бұрын
Nkuluyu palizina zomwe akubisa ngati mu part one muja anamufusa zamakwala wakana akuti ayisamagwilisa ncthito makwala matulukidwe Ake akupolisi sakuoneka bwino zomwe zikuoneka kuti chiwanda sichinamuthele kukumana naye usiku usinthe njila
@mailos.laisoni7001
@mailos.laisoni7001 4 ай бұрын
Ya Allah 🥰
@EmilyNhlema
@EmilyNhlema 6 ай бұрын
Ambuye mukule ine ndichepe🙏🙏🙏
@THOSISTUDIOS
@THOSISTUDIOS Жыл бұрын
111 years imprisonment with hard labour ehhh 😅😅😅
@YoungMwacho
@YoungMwacho Жыл бұрын
Abel follow up this story with Police, Hospital, Prison, and Judiciary/Court. We have heard his side of the story and let us hear from the other sides. It is very difficult for some of us to believe such a story from the person involved himself. Like mortuary experience was supposed to be told by someone else. Hope you will follow up.
@tingamasi106
@tingamasi106 Жыл бұрын
Very true
@AckimSaka-n7x
@AckimSaka-n7x Жыл бұрын
Exactly being in mortuary for 3 days as dead person and back to life is something no human will easily believe unless the hospital personnel tells their side
@GibsonPatrick-t4g
@GibsonPatrick-t4g Жыл бұрын
Poyamba zinali bwino koma pano 😂😢😢😢 aaaaaaa zikungo kala ngati ana achishepele ngati mwatopa kuli bwino kungo siya chimfukwa palibe chomwe mukuchita mungo tayisa nthawi yanu pachabe malo moti muzikalima maganyu m'minda mwa anthu 🏒🏒🏒
@BaxterChipofya
@BaxterChipofya 6 ай бұрын
Msamale mkango umenewo wukadzuka wuzakuvulazani seventh day imapemphera Sunday ?akuzingani ngan mlonda wakulilongwe kapena kukuluman ngati momwe anaphera m'bunu uja
@Eunbabiecavalo
@Eunbabiecavalo 2 ай бұрын
Achina sam anaphedwa nawo nthawi imeneyo iiiii😢😢
@austinmpahuwa6552
@austinmpahuwa6552 Жыл бұрын
My brother God love 💝 you,,, you must pray hard 💗 there' something
@jimmymanda2081
@jimmymanda2081 8 ай бұрын
Ambuye akukhululukire bro komanso akuyendere mwapaderadera
@lekanikhobamwale
@lekanikhobamwale Жыл бұрын
Its touching story indeed
@raytavares2256
@raytavares2256 Жыл бұрын
Greetings from North London UK 🇬🇧. Please I want to meet up with the brother this man is either a prophet or an apostle and the Lord must keep him safe. I want him to come and live with us in Rumphi we will give him a good job.
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 Жыл бұрын
Dont make him to return to sin as a prophet aaaaaaa
@Mpungwe123
@Mpungwe123 Жыл бұрын
Link up with mibawa TV team
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 Жыл бұрын
Ndiokhwima uyu guys. Uwu si mwayi ayi
@PeacePhalira
@PeacePhalira 2 ай бұрын
Koma inu muthu angazike ku motoury ndikuyamba kumenya ice uja umakhala wazizidwa, sindikukhukhulupilira
@MacfallenMoses
@MacfallenMoses 6 ай бұрын
Zikomo Ambuye chifukwa munalola kuti ndikhale modzi mwa anthu amwai omwe amvetsela bwino zazikulu mwazichita pa mmbaleyu moyo mwambwezela kale tsopano dalitsani tsogolo lake.
@CHANCYJERE
@CHANCYJERE Жыл бұрын
ndiribe mau mr jere mulungu ari nanu choringa
@ShadrekMofat
@ShadrekMofat Жыл бұрын
Ndizowona iiiiiiiiiiiiiii brother muzipephera
@FauzaTabu
@FauzaTabu 2 ай бұрын
Kumotchale musamatelo muzitisiya enafe timakhala tangokomoka
@chiccongalande842
@chiccongalande842 Жыл бұрын
Greater Grace
@GracePhiri-z3p
@GracePhiri-z3p 2 ай бұрын
Am speechless
@Yabwata
@Yabwata Жыл бұрын
Number yakuti uyo wakhumba kuwikapo thandizo yilikhu, tumaniko apa..
@slimcharlesjnr1882
@slimcharlesjnr1882 Жыл бұрын
I have been waiting for this part 2
@AlexKaunda-x3p
@AlexKaunda-x3p Жыл бұрын
Apolice akumalawi ndi afiti komaso amphawi kusowa nindalama yogula sugar shame mulungu anamupulumusa manyazi bwa God his great
@AlickZidana-cb1jx
@AlickZidana-cb1jx Жыл бұрын
Sauli ndipo adasitha nkukhala saulo Kaya tankhoza Koma zodabwitsa izi
@muhammadwinesi7737
@muhammadwinesi7737 10 ай бұрын
Saul to paul😊
@Patrick-br1fy
@Patrick-br1fy Жыл бұрын
Good is good
@nelsonbanda4077
@nelsonbanda4077 Жыл бұрын
Pena zikunveka ngati zopeka.....kudzuka ku motuary kukutidwa ice 3dsys magazi osauma aaa
@hamiltonalbertoleuanecatet4087
@hamiltonalbertoleuanecatet4087 Жыл бұрын
Interessante
@daviechapweteka4759
@daviechapweteka4759 2 ай бұрын
Munthuyu ndiwaboza ndikale ndiye tizivela zimenezoso
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Жыл бұрын
Kod mumabisilanji mayinawo,Mesa timafuna tiziziwa ntchito yotamandika ya apolice akugwila pothesa umbamvawu,koma ngati unasiyadi uzipephera m'bale, unali wachabechabe utame mwayi osakukhiya,111 year kkkk kunali kofera komko,sono ma datewo amawakumbikira bwanji poti anali atafa, anyway Alinawe cholinga Mulungu
@afritouch4660
@afritouch4660 Жыл бұрын
Kamoyo kanga kanaduka kuti duuu..!!😢
@djmakedzana9917
@djmakedzana9917 28 күн бұрын
😅😅😅😅😅
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 Жыл бұрын
Mulungu amukhululukire pa zonse kwa amene analuza achibale khululukani uyu ndi munthu
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 Жыл бұрын
Kodi program imeneyi imaonetsedwa lachingati? & nthawi yanji?
@BettinaMadise
@BettinaMadise 9 ай бұрын
Sunday 9 PM
@lossakaonga736
@lossakaonga736 Жыл бұрын
Eeeh grory to God ❤
@DroliiDongowa
@DroliiDongowa Жыл бұрын
Mulungu amapanga zodabwitsa pa moyo wamunthu.
@LuckyChimangeni
@LuckyChimangeni 8 ай бұрын
Mulungu akufuna kutiphuzitsa kudzera kwa munthu ameneyu. Komaso akufuna kuti a.umudxiwe Mulungu komaso apeleke umboni ngati uwu
@VictorMalola
@VictorMalola 4 ай бұрын
Ndimangomva za Sibweni mu limbe umu
@phirieveristo4448
@phirieveristo4448 Жыл бұрын
His grace served him
@jacobchimtaka3057
@jacobchimtaka3057 Жыл бұрын
izi ndizodabwisa kwambi langizo mulungu amuziwedi ndipamavuto kaya pantendele alalikile kwambili mawu komaso ife tikadali kuba titengelepo phuzilo amalawi.
@KennedyChirwa-v4g
@KennedyChirwa-v4g Жыл бұрын
God is great
@ChisomoMsiska-oi2vg
@ChisomoMsiska-oi2vg Жыл бұрын
Koma ndizoona izi😮
@foleialamassauco
@foleialamassauco Жыл бұрын
Tifuse, kwanwo amakudziwa koma?
@chimwemwemorris6827
@chimwemwemorris6827 Жыл бұрын
Mulungu ndiwabwino
@JamesKeneth-c8c
@JamesKeneth-c8c Жыл бұрын
Komanso number simunasiye bwanji ndimafuna nditalankhula nae please number yake tipaseni ndithu
@jamesjumbe1102
@jamesjumbe1102 Жыл бұрын
Anali ice thupi lonse koma osafa? 😂Joke
@jamesjumbe1102
@jamesjumbe1102 Жыл бұрын
Amadziwa bwanji zonsezi munthu ati anali ngati wafa, ndipo anamuuza mndani munthu anali ku mortuary
@mzatimw7426
@mzatimw7426 7 ай бұрын
This is a movie in reality this can never happen....Uyuyu akunama.
@louisbonongwe8537
@louisbonongwe8537 10 ай бұрын
Lazaro anakwililidwa mkukhalaso ndi moyo,do u hv any idea mmene zimenezi zinachitikira or its a joke too?
@jameschiziwa
@jameschiziwa Жыл бұрын
Mkulu mungayezganga kubwerera ku moyo wakale. Mudziweni Yesu chifukwa ndiye yekha angakuthandizeni mu umoyo watsopanu umene udzikubvutani chifukwa anthu atenga nthawi to trust u. Koma osafoka mulungu wa kuchitilani zazikuku
@user206
@user206 Жыл бұрын
So touching
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 Жыл бұрын
Koma nkhani zina😂😂😂😂
@marichiyotamu7208
@marichiyotamu7208 Жыл бұрын
He surely has the nine lives of a cat. 😂 However, it's confusing and amazing how he was always able to escape death at the last moment all the time! Scary story, indeed .
@tadalamuwa-dh7pu
@tadalamuwa-dh7pu 8 ай бұрын
Eeee lord muliko ndithu kumwambako
@RudoWarren
@RudoWarren Жыл бұрын
Uli ndi manja usaka wekha, munthu okupha uyu😢😢
@limbiechisaka1027
@limbiechisaka1027 6 ай бұрын
Ichi mchabodza 😂
Kangaude Kucheza ndi Mr god know Part 2
59:17
MALAWI 265
Рет қаралды 38 М.
SANKANDILORA KUTULUKA PANJA - KANGAUDE PART2 WITH GOD KNOWS
55:02
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 39 М.
번쩍번쩍 거리는 입
0:32
승비니 Seungbini
Рет қаралды 182 МЛН
Who is More Stupid? #tiktok #sigmagirl #funny
0:27
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 10 МЛН
UFITI ULIPO NDITHU...zambiri mukanema uyu
51:32
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 70 М.
CRUISE 5 WITH ROSSANA STELLA TURNER
1:18:43
Zodiak Malawi
Рет қаралды 46 М.
Omwalira apezeka wa moyo
48:05
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 83 М.
MAI WINA ANABELEKA MWALA atayembekezera kwa miyezi yochuluka
56:43
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 30 М.
The Last Fishing Boat - a film by Shemu Joyah
1:49:51
C. Shemu Joyah
Рет қаралды 213 М.
UMFAZI WAMI WALALA NENDODA NGIBUKA
1:09:07
THULELENI TV
Рет қаралды 776 М.
CRUISE 5   ELIYA NZERU WILLIAM
1:20:13
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 425 М.
번쩍번쩍 거리는 입
0:32
승비니 Seungbini
Рет қаралды 182 МЛН