I came across this guy when we were doing donations he really cares for the street kids. He is taking care of many young boys and girls. God bless him
@IreneChamanza2 ай бұрын
Mr God knows,you are a living testimony. We thank God for His mercy,love and favour upon your life and family. Eish !! Mwadutsa mumnyengo. May God continu blessing you,your family and the ministry. This is a ministry . You are really a servant of God
@HolinessThindwa-pz5hw2 ай бұрын
ABale MULUNGU apose pa menepa this is really meaning of your GOD knows mmmmh
@ChimwemweZuzeАй бұрын
Ndalira ndalira mokweza!!😢😢😢mulungu ndiwazathekadi bwanji, brother God knows ,mulungu amakukondetsetsani ndipo chikondi chake painu ,nchopanda malire ,ndipo ine ndawona mulungu akusonyeza inuyo kwa aliyese kuti,alape mkutsatira iye yehova
Bambowe wadutsa muzovuta za mbili ndizowawa mulungu akudalitse nakusunge moyo wa utali
@MkandawileLloyd2 ай бұрын
Ziko lapasi 😢😢😢😢😢😢😢😢
@SaidiMbawa-st6bj2 ай бұрын
Inali plan Mwanayo ndi bambo akewo cholinga kusokoneza umboni anthu ama deal ngati amenewo samusiya ndi moyo
@abwinoamatani4921Ай бұрын
Koma bambo inuyo, Mulungu amakukondani koopsya
@SelinaNamagowa2 ай бұрын
Ambuye apitirize kukusungani ndi moyo wanthazi ndi wautali
@Viviennezimpita-fu6fq2 ай бұрын
May l plse have his contact
@ListerMunthali2 ай бұрын
Zina ukamva eeeeh Kumwamba kuli Mulungu guys
@JonathanSokole2 ай бұрын
Hmmmm koma kumwamba kuli mulungu ndipo palibe ofafana naye hmmmm Koma Mulungu hmmmm
@willswills66132 ай бұрын
From brit's to beid buliji ndi wulondo ot utha Kuyenda 3 months or more
@DaudChamba-lr7hr2 ай бұрын
Mmmm I have nothing to say 😢
@rangersonngirazi67412 ай бұрын
Only God Knows
@marjoriefundi2 ай бұрын
To God be the glory
@FrancesPeter-xw3vb2 ай бұрын
Zosezo anali ma plan A Mulungu kuti moyo wanu uphulumuke sizophweka ayi pokuza malile anu
@ThomasJackson-y6u2 ай бұрын
Thanks God
@willswills66132 ай бұрын
Bola lilipo apa pango'ono bwanji osauza athu amene ali mundegemo zomwe zikuchitika bwanji osathawa ku airport kumakhala athu ambili bwanji pokwera ndegepo osakuwa
@MatthewKaliyati2 ай бұрын
You were not following the story that's why u kukhala ngati uli ndinzelu zambili, they were protected and monitored, they can't even talk to anyone also they were in pain according to my understanding.
@ritamaliza34742 ай бұрын
Zandikhudza komanso mantha kuti dziko laipa choncho , how many innocent people who have been victimized and faced untimely deaths just because of , this world is been sodomised , we thank God for rescuing your precious soul , only God knows why He allowed you to come across inhumane acts but a day is coming all these evil people will pay for their evil behavior, I cry for the innocent souls in the hands of these beasts
@vincentmalaulo40462 ай бұрын
God is good
@IvyChithyoka2 ай бұрын
Zonse nkumwamba!!!!
@patriciajangaza6752 ай бұрын
Eeeee Koma kunja kuno anthu akuchitilidwa nkhanza mmmmm
Anthu ndi oipa kudziko lapansi, kumugwiritsa munthu ntchito ulele and planning to kill at the end. Mngelo yemwe adamuyankhula mwana wa Mafia ayankhulenso ndi chigawenga chachikulucho mpaka atalapa ngati akadali moyo