Njawala muli busy kubisa mawanga a Usi pa times pamene nkhandweyo ili busy kukuipitsani ku zbs,
@JosephChikoko-to3jiКүн бұрын
Dr Mathews Mtumbuka is my choice of party president.
@thandimagombo1751Күн бұрын
A Usi akudabwatu kuti ma presidential candidates a UTM akumayendera limodzi 😂😂😂😂😂
@ganizanizuze71042 сағат бұрын
I wish SKC were here, tsogolo la Malawi lili mmanja UTM akangosankha president WA mbola Malawi watha basi , ngati kuli convetion yomwe anthu Ali nayo chidwi kwambiri ndi ya UTM
@FranksonKennethChipandeКүн бұрын
A Brian!!!!! You mean kuti aNjawala angayankhe kuti sanawalandire a Usi????? Politics is taking ground
@ThomsonNgomaКүн бұрын
akukanika kuyankha if Usi was there when they made agreement ya K20 million kwa ofuna kupikisana nawo...im beginning to understand Usi now kuti kagulu kena sikakufuna zotsata malamulo....
@bobkatas1974Күн бұрын
The reason is simple and clear,,, Michael is betrayer
@KassimKajosoloКүн бұрын
Njawala wayamba kuyankhula ndale tsopano.
@gideonnkhoma3229Күн бұрын
Brian Banda akunika kufunsa obvious questions like 1.kodi akuti a UTM sapanga za ndeu. Nanga a USI akuti ena mwa azimai a UTM omwe Ali mbali ya USI akumenyedwa pamenepo akuti chiyani a njawala 2.A Njawala akukana kuyankha mafunso ena koma sakuwatengetsa monga amapangira ndi a zipani zina. It clearly shows kuti Banda ndi wa UTM which is unprofessional
@WelingsLongweКүн бұрын
Chipani Cha dpp ndi udf mukuti ndi chabanja amangopasila pachibale pano mukufuna utm ikhaleso chabanja zipani za mu Malawi
@StefanoBinwell-f6xКүн бұрын
takondwa kudziwa kuti kulibepo wanzeru kuposa mai chilima