KOMA MANGANYA NDI MACHINE ~ WAKANA KUPITA KU UTM KOKAFUNSIDWE MAFUNSO NDI ANA KU UTM

  Рет қаралды 8,283

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 96
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 17 күн бұрын
Madolo alero ndimakape amawa by Sir solder Malemu Lucius Banda
@MosesTangwe
@MosesTangwe 18 күн бұрын
Ndi tissue ya MCP uyu
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor 17 күн бұрын
Mmmmm koma Munthu kukakhala pa bwino poipa pakukudikira this is a promise iweyo usi anthu womwemo ukuwauza pano this are same people there will Laugh at you samala lino dziko lapatsi 😂😂😂🙌🙌🙌
@AubreySkeffah
@AubreySkeffah 18 күн бұрын
Enaso ndinuosaganizabwino usi akulankhulazazeru❤
@ThabaniZuma-d7u
@ThabaniZuma-d7u 18 күн бұрын
MICHEAL USI TAMVA IZI.. INEYO NDIM'MODZI MWA ANTHU WOMWE TINALI PA NSOKHANO WAKOWU NDIPO NDINALINSO MUGULU LA ANTHU WOKWEZA MIKONOWO " NDIYENO LET ME TELL THE FACT.. WAFUNSA KUTI KODI IFEYO TINGAKAVOTELE ZOSEMPHANA NDI IWEYO.?. NDIYENO ndafuna ndikuyankheno motere". IFEYO sitingavoteledi ZOSEMPHANA ndi iweyo, IFE TILI READY KUPITA KUKAVOTELA CHIPANI CHOMWE IWEYO UNGATIWUZECHO, Komano kupatula MCP Yokha apo pokhapo ndiye uyiware kuti vote yanga uzayiwona
@MikeGomani-tb9np
@MikeGomani-tb9np 18 күн бұрын
Akanakhala dolo akanakamusaka Chilima mpaka mmamawa monga Chilimayo akanapangira kukanakhala kt wagwa ndi Usiyo
@henryphiri6100
@henryphiri6100 18 күн бұрын
Oipa uyu, yakoma lero utm
@StellaMicheal-q1j
@StellaMicheal-q1j 18 күн бұрын
Usi Moto buuu
@EMMARKKALIAPA
@EMMARKKALIAPA 18 күн бұрын
Usi si wa nzeru uyu mphuno yophwayikayo ukanakhala kt umakhala limodz bwez mutafa limodzi.....😢😢😢😢😢😢
@JamesNkota
@JamesNkota 18 күн бұрын
Yangomuunaninso kuti pokhalira pake iyeyu asaaaah😅😅😅
@giftkanjuchi-qm8hf
@giftkanjuchi-qm8hf 18 күн бұрын
Manganya ndimakuyesa wa nzeru koma mmmm mamina okha okha
@YobuKamanga-d2k
@YobuKamanga-d2k 18 күн бұрын
Kopita walibe mangaya wanuyo osati ndi machine ayi
@JasonMailos
@JasonMailos 18 күн бұрын
Manganya ndichisi pamodzi NDI Bsmalawi
@GroliaMwanyongo
@GroliaMwanyongo 18 күн бұрын
Awa ndiye akuti chani asachenjere
@juruEzra
@juruEzra 18 күн бұрын
Onsewa ndi alimi , tangowapatsa wina aliyense tumba lafeteleza ndipomwe ukhale dolo
@edfrenkampala7342
@edfrenkampala7342 18 күн бұрын
Yapamaliro ndalama ifagwira ntchito yoyatsa ma candle muzigawi zonse za Malawi 😢
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 18 күн бұрын
Does he think that MCP will take him as a Running Mate wa Chakwera?????? I don’t think so. Atupele is eying that same post 😂😂😂😂
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 18 күн бұрын
Patricha akuti bwanji my anga
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
manganya,chiza,anthu,enawo,uwasiye
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 18 күн бұрын
Anthu amenewa alibe chochita kuposa kukhala ndi kumvetsera zachabechabezi. Anthu akudandaula njala.
@LouisKanje
@LouisKanje 18 күн бұрын
Chawonanzako Moto umapita kwatsala tchile
@francisvisage2705
@francisvisage2705 18 күн бұрын
Iwe manganya Yamba kuyowoya Za chakwera wakalekelachi church na kunyumba ndyale pala ukuti mu church kuyowoya Za ndyale mu church 😅
@GroliaMwanyongo
@GroliaMwanyongo 18 күн бұрын
Ndiye akufuna kuti adziwe kuti atani
@rosszalira4035
@rosszalira4035 18 күн бұрын
Ndikape akumaziona ngati dolo
@KondwaniChikopa-hu3qg
@KondwaniChikopa-hu3qg 18 күн бұрын
Achitabwino kukana kupitako a a utm ndi dpp ndi osowa zonena
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
wakhoza,osapitako,akadatsika,maweti,manganya,siomusetela,dpp,ndi,utm,ikudana,ndimanganya,km,uyu,ndi,dolo
@EvansEgra
@EvansEgra 18 күн бұрын
Bs Malawi, wokondera inu
@MartinRajab-w5e
@MartinRajab-w5e 17 күн бұрын
Aphwanya malamulo unawayika ndiiwe chimanga chopephacho
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba 18 күн бұрын
Koma USI athanananu
@AubreySkeffah
@AubreySkeffah 18 күн бұрын
Àusi amalankhula chilungamo ndale sakudya enamafunakungodzilemeretsa basi
@LemsonManyowa-z1y
@LemsonManyowa-z1y 18 күн бұрын
Ausi musanyengeke muli kutali kwambiri komaso zikuonesa kuti mutu mwanu mwasiya kugwira
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
komaso,msonkhano,wa,kabambe,,ndi,wa,ausi,ungakhale,ndi,anthu,ochuluka,ndiiwabwana,usi,chifukwa,alindifundo,zoveka,
@GiftMitochi
@GiftMitochi 18 күн бұрын
Tikumvera sewelo la tikuferanji.
@fosterkatemba1269
@fosterkatemba1269 18 күн бұрын
Bwanji osafunsa ngozi yandege
@BlestoneJonas
@BlestoneJonas 18 күн бұрын
Kamanganya alibe mfundo uzatha ngati ma katani siukuona patali full vice president kumakagawa chimanga fertilizer ukumupangola kampeni Chikangawa
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
kd,usi,ndikabambe,wanzelu,nindani,nanga,alindifundo,nindani,mutha,kuona,kuti,usi,ndodolo
@LonexWataya
@LonexWataya 18 күн бұрын
Nkachitsilu aka
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
usi,siosokoneza,usi,alindi,gulu
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
emwe,akufuna,kuti,usi,asamagawe,chimanga,ndamene,sakufunila,zabwino,anthu,,usi,alindi,anthu,ake,okwanaso,kwambili,
@EthelKubalasa
@EthelKubalasa 18 күн бұрын
AMalawi uyu asatipusitse, ndi amene anamupereka malemu SKC ku MCP, uyu ndi yudasi.
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
amene,akudana,ndi,usi,chifukwa,chothandiza,anthu,,iwowo,asalimbane,ndi,usi,awauze,amene,akulandila,chimangawo,kt,akalandila,asamadye,,ndikwapititsila,chawo,
@ChidaPhiri
@ChidaPhiri 18 күн бұрын
Kodi Usi kweni kweni ali mbali iti? Akuziika mmavuto zedi zimuthela posachedwapa ndithu
@AlephaManganjira
@AlephaManganjira 18 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@HenryTruwa
@HenryTruwa 18 күн бұрын
Inu mufuna kudziwa za ndalama ya pa maliro , koma amalawi akufu kudziwa chinachitisa ngoziyo mutifunsire ku bomako
@EvansEgra
@EvansEgra 18 күн бұрын
Iwe ngozi sumayidziwa?
@HARRYSABBATEEN
@HARRYSABBATEEN 18 күн бұрын
umphawi sizinthu umangoti ukuwalowela uku walowela amalawi tiyeni tizigwilisa ntchito mnzeru guyz awawa awa mupusa nawo awa
@MkwalaFrank
@MkwalaFrank 18 күн бұрын
Mukudya ndalama za njanya mwagulisa
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo 18 күн бұрын
Kdtu oyamba siinu kugawa chimanga kmno ndikoyamba kt VP azigawa chimanga kmso anthu sakukufuna ku UTM ko km zomakakamilazo bambo inu nsalu yanu ikukuvutan mpat
@KondwaniChikopa-hu3qg
@KondwaniChikopa-hu3qg 18 күн бұрын
Akuzuzula a wusi ndiopanda nzelu
@ThabaniZuma-d7u
@ThabaniZuma-d7u 18 күн бұрын
Siwungawapusise anthu iweyo Michael Usi" Pajatu angelezi adati.. ACTION SPEAKS LOUDER THAN WORD'S. Iweyo ndiwe WA MCP ndipo chilichonse chomwe ukumapanga" Ukumapanga mofuna kuti anthu ayikonde MCP kudzera mwa iweyo. Ndiwe Tissue ya MCP, Ndiye usamazivute nkumawawuza anthu kuti sindiwe WA MCP wamva. MCP naa ngati yili ndi anthu wokwana 1 million .' Ndiye kuti wachi 1million yo ndiyiweyo.. Mphaka iwe anthu panopa anadana nawe Kwanthunthu..
@StellaMicheal-q1j
@StellaMicheal-q1j 18 күн бұрын
Usi ndi bwana wanga ulemu wanu bwana
@petergoba4224
@petergoba4224 18 күн бұрын
Ndichitsiru
@happybinali4673
@happybinali4673 18 күн бұрын
Anagulisa chilima ndigalu
@EvansEgra
@EvansEgra 18 күн бұрын
Anafa nthawi yake
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
utm,ikudana,ndi,manganya,ayi,letsani,anthu,anuwo,asalandilenawo,,ife,tikuti,usi,akukhoza,kuchilitsa,anthu,
@TonyBanda-y4i
@TonyBanda-y4i 12 күн бұрын
Nyimbo yamalawuloyo anthu akuyimba mokayikira big boma ili basi zathapo
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
kabambe,sakhoza,ndale,alibe,kuthekela,kukopa,anthu,
@giftkanjuchi-qm8hf
@giftkanjuchi-qm8hf 18 күн бұрын
Malo moti ufotokoze mmene munaphera chilima uli bizy akufusa za ndalama za maliro. Zopusa
@Thembokatuli
@Thembokatuli 18 күн бұрын
Ufiti umenewo
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 18 күн бұрын
Anthu anali mu ndege muwazuse muwafutse nokha usi was not part of flying in the plane
@LouisKanje
@LouisKanje 18 күн бұрын
Ausi ikakondwa Amazonia alipafu Kudzaingura
@EvansEgra
@EvansEgra 18 күн бұрын
Usapiteko iwe, iweyo ndi boma, asakupute dala. Iweyo boma basi
@NyuwaniMkwela
@NyuwaniMkwela 18 күн бұрын
Mwana oyipa kwambili uyu
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 18 күн бұрын
Palibepo chomwe usi akuchita ndipo ndi mbuli ngat president wa mcp onyamula sugar ku chipoku uja,
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
indedi,asasiye,kugawa,chakudya,,dpp, ndi,utm,ipititse,chake,chakudya,anthu,achile,kunjala,osamangodananaye,usi,pititsani,chakudya,chanu,anthu,akuveni,kukoma,ngati,simutelo,usi,atenga,masapota,onse,
@GraysonZongonongo
@GraysonZongonongo 18 күн бұрын
Usi chindeli chomeni wuli kugulisha chilima iwe
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
usi,olo,atayamba,chipani,chake,usi,alindi,anthu,ake,
@RabiBanda
@RabiBanda 18 күн бұрын
Kubalalika basi
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
munthu,ogawa,chakudya,komaso,feteleza,ndimunthu,omango,lankhula,ndidzapanga,wabwino,nindani,,sinthawi,yomangolakhula,ayi,km,,anthu,azilandila,basi
@juruEzra
@juruEzra 18 күн бұрын
Nthawi nkhachitsiru
@juruEzra
@juruEzra 18 күн бұрын
Kodi a utsi will you be vp all the time? wina analipompo koma pano alimu grave
@overtonekanyenda9400
@overtonekanyenda9400 18 күн бұрын
Kabambe mwa Usi akulowamo ka 10
@Hdsagdf-t1n
@Hdsagdf-t1n 18 күн бұрын
Ungopitani komwe mukulowelako osati kusokoneza azako coz ndiufulu wamunthu kuti akhoza kusapota chipani chilichose
@AbuZunairaHanafie
@AbuZunairaHanafie 18 күн бұрын
Ndikungoona kuchedwa kt Tika vote manganya ndi oipa anapha nao chilima akumutuma a mcp
@princesskambalikena
@princesskambalikena 18 күн бұрын
Ndipo ndiokuladi mtima mmm wagawila nsalu ndi matishet za utm kufuna kulimbana ndi nzake koma kabambe salimbana ndi usi. Ndungolakalaka kuti masiku athamange tivote tiiwaleko zamanganya akuchita kubowa. Angakwanise kugawila aliyense chimangacho manganya ndiovesa chisoni
@LouisKanje
@LouisKanje 18 күн бұрын
Mau nsamatha
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
chipani,cha,utm,chimafuna,kumuona,ngati,usi,nimbuli,usi,siopusa,
@LouisKanje
@LouisKanje 18 күн бұрын
Ukakwera muntengo usamatukwapansi Osaiwala mau oti nyansi saphimbira Polina sakwilira ziputu Zimamera mama umapusa akulu adatero Akoma akagonera akulu mau
@francisvisage2705
@francisvisage2705 18 күн бұрын
Manganya, shame on you 😢, Your master Chilima is gone, ukawanku dazi ilo denge yikasowa Ku chikangawa? I don't like this dude called manganya ...I 🤔 he's wise
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
olofeteleza,akugawayo,amene,akudana,nazo,,apititse,wawo,uko,ndiye,kukopa,kwabwino,osamango,lankhula,,km,kupeleka,thandizo,,manga.nya,woyeeeeeee,my,voti
@FrankLampard-m1w
@FrankLampard-m1w 18 күн бұрын
Koma mpwampini uyu😂😂😂😂
@Hdsagdf-t1n
@Hdsagdf-t1n 18 күн бұрын
Iiiiii manganya akanakhala dolo akanangoyambitsa chake chipani kukakamila udindo hahaha mfundo ulibe unalekelanji kukasunga ngati umadziwa kuti sadatsate malamulo
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
utm,ndi,dpp,ikufuna,izapeze,polankhula,zanjala,tikuti,usi,apitilize,enawa,fundo,alibe,anthu,sangalephele,kukalandila,chi,fukwa,cha,utm
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo 18 күн бұрын
Kd inu muzaima paballot yachipan chit
@ChristopherJumu
@ChristopherJumu 18 күн бұрын
Kod iwe manganya ndale unapangila kut namapwala iwe??
@EvansEgra
@EvansEgra 18 күн бұрын
Iweyo unapangira kuti ndale?
@GertrudeMayuni
@GertrudeMayuni 16 күн бұрын
😂😂😂😂
@MphatsoMaguba
@MphatsoMaguba 18 күн бұрын
Drama
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 17 күн бұрын
ose,mukudana,ndimanganya,mulandilitse,chimanga,chanu,mulandilitseso,feteleza,wanu,kt,anthu,adziwe,kt,mumawakonda,osamangodana,ndi,munthu,ochita,zabwino,ngati,usi,
@FlorenceKatunga-d9o
@FlorenceKatunga-d9o 18 күн бұрын
Tangomusiyani ndi wamisala uyu mutu wake sumagwira akazatopa azatsiya yekha
@BenardPeter-pd5mh
@BenardPeter-pd5mh 18 күн бұрын
Kkkkkkk
@happybinali4673
@happybinali4673 18 күн бұрын
Anagulisa chilima ndigalu
UNTV: C-NEWS | January 17, 2025
54:54
UNTV News and Rescue
Рет қаралды 103 М.
BBC Hausa Labaran Duniya na Safe Yau /17-01-2025 #bbc #bbcnews #bbc
30:04
Michael Usi - Akanaziwa sakananena izi
5:36
Malawi Top Talent
Рет қаралды 63 М.
EXCLUSIVE WITH PATRICIA KALIATI | 04 JANUARY 2025
1:13:01
Malawi News Update
Рет қаралды 94 М.
Nkhani ya Blackbox si yokambirana; Anthu atopa ndi mabodza a kongeresi
12:07