This program is best of the best programs mostly to those who like this country.Times can make someone to stay in power or out of power unfortunately politicians never know.I like you guys I wish nditazakuonani pamaso mpamaso including Brian Banda mukudziwa anthu osaukafe timamva kuwawa km timaonekabe olimba chfukwa mumatiyankhulira.Long live times,Long live Hot current and times exclusive,Long live Wonder,Jonar,Ochunga and Brian.
@MillieMalakam2 күн бұрын
Ndipo live sukunama
@ShakiraJackson-x8w2 күн бұрын
Guys you have worked very hard this year dare or truthful zonse mwazipanga well done guys pitilizani ndithu kuwasegura mitu amalawi mu 2025 happy new year 🎉🎉🎉🎉🎉
@josephsambo47402 күн бұрын
Work well done indeed ma hot currents
@LimzeySande-b9n2 күн бұрын
Happy happy new year 🎉 APM my vote for next year
@BrightMchoma2 күн бұрын
Zitsiru za zibusa kametedwe ngatii okuba😂
@MathewKalinkhuКүн бұрын
100% guys , no.1 program. Moti George Kasakula adziyamikila azibusa amene aja pa program yake pa MBC .😂😂😂😂.
😂😂😂😂😂 mwanena mwanena basi ndipo ndi za chambadi zeni zeni n no need to withdraw sir😅
@OusmanBen-f4o2 күн бұрын
Zimbani zochuluka zikukana kupanga alliance ndi mcp chifukwa cha fungo lakanyimbi lomwe akununkha nalo mmm ziwavuta ndithu😂😂
@EmmanuelkpPraise2 күн бұрын
Nkhani ya a Bishop mususa unali ulaliki ndipo muulaliki wawo anayikamo maganizo awo pa nkhani ya report ndipo izi zimachitika azibusa amapereka zitsanzo kapena maganizo.Ndipo mboni yomwe akunena kuti anajambula chilichonse ndi MULUNGU.mawu anga omaliza ulaliki sitimayankha kapena kufunsa.
@KellyNyangulu2 күн бұрын
Koma tinakakhala ndi njila yoti tisamadalire zolandila. Why? Tili ndi lake Malawi from chitipa to mangochi and Shire river from mangochi to Nsanje Why chaka chilichonse kulira ndi njala, mkumadalira zolandila. This must end...
@jonathanmaseko60572 күн бұрын
Nkhani imakhala kuti do you have capital to do something better kuti usamadalire?
@AnoldKonde-pd4qt2 күн бұрын
Adakakhala m'busa sadakavotera kut nkhondo ya ku Palestine ipitilire anthu akuphedwa uku pa maiko onse ku Africa kuno malawi yokha bas ikat ipitilire
@Dickies-mk8cd20 сағат бұрын
Chilima adafa kuthupi koma muuzimu tidzakhala naye forevermore.
@RaphaelMaunde2 күн бұрын
Akuti udzikhala nalo nyazi limodzi😂😂😂
@AnnieChimpeni2 күн бұрын
Faka iwee auzeni 😂😂😂 akuti azitsogoleri
@ChristopherKazembe-n6c2 күн бұрын
Nda akuba aja ,anakanika kutchula chipembezo chimene amayimira.
@ChristopherKazembe-n6c2 күн бұрын
Amagwiritsa ntchito anthu kuti apedze umboni koma, koma zinthuuu zina mwa zimene amafufudzazo anazitsiya sanawulutseeeeee chifukwa cha ndalama
Malawi azatheka kukazabwela President okonda dziko lake and akazangoyika lamulo loti oba ndalama za Boma Life imprisonment no any Lawyer allowed to represent him. that alone will transform our Nation.
@ChristopherKazembe-n6c2 күн бұрын
Komaaa Wandor. Kkkkkkk a big up
@wisdom20mkango492 күн бұрын
ubwino wake Times group ndi ya MCP😂😂😂😂 kuphiphilisa chabe uku
@AndrewTarambabkingКүн бұрын
Ine nde sindngavote ndpo sindzavotapo m moyo wanga onse
Watching live from Vitekete Banda village, Euthini, Mzimba, Malawi, Central Africa
@thokojames52312 күн бұрын
for the point of bishop nsusa as ochunga says; he was speacking as who to answer quastion, i would say that ask brian banda to call bishop nsusa on time exclusinve interiew and then you will be able to know the trueth about that. by the wy nothing wrong with what archbishop nsusa say and he was right thats the trueth