No video

KUBOMAKO NGATI MUKUONERA MUSINTHE Wonder Nsisya Ndi Jonah pamkuku lero pa hot current atokotera boma

  Рет қаралды 31,044

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 37
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 Ай бұрын
Zaululika zoti Chakwera Ndi anzake Ndi amene udamverana Chilima pamodzi ndi Wanthu wena aja Ndipo ada Chita kuwa wombera komanso Mowa maliza Ndi chikwanje, Utsi Ndi amene waphesa Chilima, Ndipo Utsi Ndi Yudasi, panopa nso osamati ndenge idagwa ayi,koma ndenge idagwesedwa Ndi magnet Ndipo m'maiko akunja aulusa Kale koma Ku Malawi ko sada lengeze Chifukwa chiyani? MCP and Chakwera Must go
@JuliusNyirenda-ec1eo
@JuliusNyirenda-ec1eo Ай бұрын
Wonder and Jonah inu ndi machine
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft Ай бұрын
Koma a nsukuluzi muli mwara kwambili keep it up guys
@user-bq8gb7tb1l
@user-bq8gb7tb1l Ай бұрын
No coment
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma Ай бұрын
Utm ikamudalira usi ngat president chipani chifa chifukwa usi akuoneka kuti cholinga chake ndichosokoneza utm pofuna kusapota chakwera alibe vision ngati ya a chilima bola kabambe uja akhoza kuchimanga chipani
@AlexKamowa-u7m
@AlexKamowa-u7m Ай бұрын
Zamaudondo kubanja la chilima awasiye
@ChrissMatchadoeddie
@ChrissMatchadoeddie Ай бұрын
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn Ай бұрын
Amalawi ambirife sitikudziwa komwe tikupita honestly..kubwelera kwa pitala ndi corruption thooooo Chakwera ndi uyuuuu akugona nduna kumangoba ndalama ..we lost our directory
@MuyaoComedies
@MuyaoComedies Ай бұрын
Am following
@AlexKamowa-u7m
@AlexKamowa-u7m Ай бұрын
Maradio akumalawi sanenachilungamo ndima TV omwe ndiamantha
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Ай бұрын
Anyamata aku times mwayamba ku kula mimbatu ngati Ken Zikhale ng'oma. Amenewa mapwevupwevu!
@user-wo2kh4xe8q
@user-wo2kh4xe8q Ай бұрын
ndimati ndifuseko kodi ku America kuribe dothi ngati laku malawi ngati kuridothi ndekuti malawi ndi dziko rochititsa manyazi mulungu amati nseka kuti anthu aku malawi ndi dzinyama wosati athu
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 Ай бұрын
Nkhan ya Mumba iyi chakweraso ankatelo
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Ай бұрын
Mukuyankhula mayikofon ilikutali sitikumva bwnobwno
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q Ай бұрын
Inuyo mumatha 👏👏
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
Ndikuwona amalawi tingokhala ndi DPP Bolani dppp kusiyana ndi izi manyi yeniyeni chakwela 😢
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Ай бұрын
Uwusi ndi chipan cha thiko ,nden akaliyat ndi achipan cha achilima marem ,osat gwenembey
@steeziomfune6611
@steeziomfune6611 Ай бұрын
Dr skc was UTM and he is gone...UTM is finished...ndanena ndanena
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws Ай бұрын
Palibe fundo yeniyeni pamenepo
@ChrisjuZiyaya
@ChrisjuZiyaya Ай бұрын
Takambani za nyasi zomwe zikuchitika m'boma osati kulimbana ndi utm Inu mwatani Kodi???
@LuciusMakupe
@LuciusMakupe Ай бұрын
Jona pamkuku unatsekesa Rainbow Television ndi Aubrey Kusakala ndi chilungamo chakocho
@OSCARBANDAH-x2g
@OSCARBANDAH-x2g Ай бұрын
Ana opanda matha awa ndi mzawo uja B bandah
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Tilibe nayo ntchito kabambe inuso kutuluka kwa utm ku mcp yakuwawani milomo ngati akambuku
@CaristoMatimba
@CaristoMatimba Ай бұрын
Koma Ngati olemekezeka ausiwo anapasidwa u vice President ndi a malemu a achilima.nde mumafuna a usi Akane udindowu or bwanji?
@charlesjimu6054
@charlesjimu6054 Ай бұрын
You said dpp was arrogant why did you not the same word to Kunkuyu's responses to the afrobalometer?
@AlexKamowa-u7m
@AlexKamowa-u7m Ай бұрын
Kwambiliatolankhan
@EstherNgolleka-zs2fj
@EstherNgolleka-zs2fj Ай бұрын
😂😂😂 komatu Jonah
@kadijachilwan967
@kadijachilwan967 Ай бұрын
Kabambe akufuna abe utm apitenayo ku dpp be careful
@henrymwale8994
@henrymwale8994 Ай бұрын
Mukunama mulira
@TonyN.Misoya
@TonyN.Misoya Ай бұрын
Àaaaaaah😅😅😅😢😢😢
@raytavares2256
@raytavares2256 Ай бұрын
Kwanguleka Chipani cha MCP MPAKA wamuyaya ngwazi Dr LAZURUS Macarthy 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉2040 kupitiliza MCP BOMA ILOOO waya waya eeeeetu 😅
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Ай бұрын
Wakhuta chani nanu kapena mwamwa chan
@ernestnyirongo3962
@ernestnyirongo3962 Ай бұрын
@@SamKaposa-i5ciwe zokuti MCP ndi bomaso next year sukudziwa
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 Ай бұрын
Maloto achiumba
@ernestnyirongo3962
@ernestnyirongo3962 Ай бұрын
@@giftmakoyo1441 who do you think will replace chakwera ngati ukuganiza za dpp udzinyenga mwanawe ukanali khanda you don’t know politics
@InnocentKalua
@InnocentKalua Ай бұрын
小丑和白天使的比试。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:51
超人不会飞
Рет қаралды 32 МЛН
He bought this so I can drive too🥹😭 #tiktok #elsarca
00:22
Elsa Arca
Рет қаралды 43 МЛН
BRENDA KOSAMU, LOST & FEARED DEAD
19:12
Rodwell Lumbe
Рет қаралды 10 М.