Ndiye akulu akulu or achikulile Ku chipani kwanuko simukuwafuna
@BrinoKadzakumanjaАй бұрын
Ndinuosokonexa ndan angavotere ref kkkkk
@TamUs-u2hАй бұрын
Za ziiiiiiiii
@RamosfreshАй бұрын
Mmmmmm koma mwati chipani cha LEF kkkkkk. 50+1 inuyo kkkkkk koma maloto ake nde ovutatu. Tazingokhala ma activist . Mbwelera mpakana chipani chanu sichafuko
@Sofi-p1vАй бұрын
Sitikufunanso busa pano tataya chikhulupiliro
@ELLENKANJEREАй бұрын
Kkkk khalani pasi
@ishmaelimani3779Ай бұрын
Muzaziona mukadzakula ana ama 2000 inu
@MathewsJanuaryАй бұрын
Ndikupusa kwaoso Kwa apolisio
@dalitsochibisa2986Ай бұрын
Cheap politics hhhhha! Anthu anazolowera ulesi that's why there is no any appreciation for any achievement. Let God judge us
@Eric-gb9msАй бұрын
Ndi mbewe yekhayo akuziwa za ulimi nfikumuziwa kwambiri
@MustapherLinoАй бұрын
Ma busanso ayi pano ambewenso ndiye ayi
@MussahWilliam-py1ffАй бұрын
Manifesto ,.... Aaaaa ndinatopanawo ine
@thulambale2836Ай бұрын
Na inu nokha mwayesesa pa mfondo zomveka zokhazokha osatukwana ngati zipanazi za DPP
@ChifundoJohn-w3tАй бұрын
Galu iweyo wamva usalimbane ndi DPP chikangawa party iwe
@Sofi-p1vАй бұрын
Not this time around my sister
@AlexKaunda-ny2egАй бұрын
Chakwera his maza faka 😂😂
@mabvutomichaelpanagona1949Ай бұрын
Kodi mukamati David mbewe ndi pastor siakufanana ndi pastor chakwela?kodi zochita zao sizimodzi? chifukwa ndi mapastor.ndiye kuti ambewewa adziwa kuti chuma chiri kundale akufuna ndalama sakufuna moyo wamtsogolo umene ukubwelawo ayi akumvomeleza kusankha moyo wa pansi pano chuma chodyedwa ndi njenjete ayi ndithu pastor mbewe ndithu mwasankha kuti inuyo mudzadyedwe ndi njenjete basi moyo wa mwamba simukuufuna ndithu? Chisankho ndichanu zikomo.