KUWELENGA KALATA YA PUBLIC AFFAIRS COMMITTEE (PAC) YOPITA KWA CHAKWERA

  Рет қаралды 23,653

Malawi Exclusive

Malawi Exclusive

Күн бұрын

Пікірлер: 119
@georgeaiwa8661
@georgeaiwa8661 13 күн бұрын
PAC ndinakwiya moopsa ndimmene inayambira kalatayi as it leaned so much to the president, praising him, but as it flows down, Yooooooo! A PAC mwaitha ndipo mwamuthira madzi oyenera. Kudos🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
@FelixMachika
@FelixMachika 13 күн бұрын
Simunachedwe, nthawi yoyenera ndiyomweyi. Tiyenazoni asamva mkunkhu amenewa. Anthu timakhulupilira atsogoleri a mipingo ndiye sitingabwererenso m'mbuyo, awa a hoke Basi!!!!! 💪💪💪💪💪💪💪👍👍👍👍
@vroemenbanda4883
@vroemenbanda4883 13 күн бұрын
Bravo PAC this is exactly what is happening on the ground. Oooh! God have mercy on us
@JosphineJoshua-gq1rp
@JosphineJoshua-gq1rp 13 күн бұрын
INE SI WA MCP AI KOMA CHAKWERA PA YEKHA AKANATHA KUKHALA WABWINO BWINO KOMA PALI NDUNA ZINGAPO ZIMENE ZILI NDI MPHANVU ZAMBIRI KUPOSA IYEYO.CHAKWERA WANGOKHALA NGAT CHIKWANGWANI KOMA AKULAMULA DZIKO ND NDUNA ZAKE ZINGAPO.EVEN IMFA YA CHILIMA ALI PA FORE FLONT NDI NDUNA ZAKE POFUNA KUT APITILIRE KUKHALA M'BOMA AZIBABE.PALIBE CHILIPO PA BOMA ILI .MULUNGU WAUKANA UFUMU UWU.CHIMWENDO BANDA,KU NKUYU,ZIKHALE NG'OMA NDI NDI ENA.
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 13 күн бұрын
Vuto la chakwera kukula mtima umbava ndi uhule
@Stretor
@Stretor 12 күн бұрын
Pa chiyambi ndimafuna kuyisiya kalatayi koma oooh yes ndili ku mbali yomutchotsa pampando MCP yalephera
@MarySinjirani
@MarySinjirani 13 күн бұрын
Kasongo chakwela chikangawa bonaweooo tula pasi udindowu wa chepa nazo ndale 😎😎😎😎😎😎
@JamesMatupi
@JamesMatupi 13 күн бұрын
CHAKWERA the President MCP boma ndiromweri basi
@patrickkamtambo2533
@patrickkamtambo2533 13 күн бұрын
Very objective criticism, God realized if it were not for this leadership in this troubled period this country could have been down in absolute sense. Corruption really has adversely impacted political sphere of MCP because this is the very problem that compelled Malawians to boot-out Dipwipwi. Therefore, Dipwipwi in all fairness cannot substitute nor take over government, that will be great mistake, and Malawians dare not try venomous Dipwipwi and their cadets you know best what they are capable of doing; and needless to mention their evils deeds
@PETROLJ-n1t
@PETROLJ-n1t 13 күн бұрын
Kuswa kuswa chakwela must go😂😂😂😂😂😂
@WysonChilonga
@WysonChilonga 13 күн бұрын
Ndipo sitikufuna nkumuona komwe,wationetsa mbonaona😢
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 13 күн бұрын
Kkkk uku nde kuswa, kuswadi iyi nde pac timayidziwa ife chifukwa tikumvutikafe ndi a khristu awo. Tsoka ndilo nthawi yoti mcp ikoze zinthu yatha comwe acite ndikupakila wakukasiya cikangawa walephela 0%.
@PasquaMapemba-my9mw
@PasquaMapemba-my9mw 13 күн бұрын
ZIKOMO ZIKOMO ZIKOMO A PAC. INE MDAKUPATSANI 100% NDIPO CHILUNGAMO KUMWAMBA KUMASANGALALA. AMEN
@AlexanderYovatiKhumalo
@AlexanderYovatiKhumalo 13 күн бұрын
@@PasquaMapemba-my9mw A Malawi tiphunzile pa comment sipophunzilila kunyoza ayi, ku ma khothi tikumva milandu ya corruption , chuma cha Yani chifukwa munthu chake saimbidwa nacho milandu inde titha kuchemelera koma kodi alankhulawo ndi angeloo samalakwitsaa?
@JohnPhiri-t2r
@JohnPhiri-t2r 13 күн бұрын
Pac.ulemuwanu.zichoke izizi zatikwana. Dpp . Nayoso inali ndi makani ukuuzidwa kti anthu akudandaula. Kunjaku . Dausi makani relo.dpp ilikunja. Andale aku maliwi ambiri ndimbuli zo phuzira.😂😂😂 voti yaine inapita ku mcp chifukwa cha chilima. Lero inabwerakoso chifukwa chaifa ya chilima❤❤❤❤❤❤❤ndimamakonda kwambiri😂😂😂😂
@MercyChiwaya-um6us
@MercyChiwaya-um6us 13 күн бұрын
azipembedzo tonse ojiya tiyeni nafe tilembe yathu kkkkkkkkkkkkk
@ManganiStanley
@ManganiStanley 13 күн бұрын
Mwacedwa komanso chidole canucho chilibe nzeru nkomwe
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 13 күн бұрын
Ndipo tisakayike apapa pac yayankhula mawu omaliza mcp chisankho ichichi isavutike mkuima nawo sawina idzidzi nde ndizoona chifukwa olo ana akunkhonde akuti sakuifuna.Pac yanena chilungamo koma tiwakumbuse a pac kuti misewu si ya cikangawa ndi ya APM iyeyi anangosekulira asamacite matama ndi misewu ya APM, mcp palibe yacita dziko muno 0% asakunamizeni koma zina zonse nde ndizoona mmalawi muno muli mavuto a nyooo! Chikangawa must go we dont need him hiz nothing but big fool 💙💙💙💙💙💙 Ana adad ifeo caka cake ncino
@BoswellMitayi
@BoswellMitayi 13 күн бұрын
Bungwe la mpingo anthu olemekezedwa mpaka kutulutsa mawu oti uchitsiru eeee simipingo ayi koma zomvetsa chifundo ndithu
@scoltenroma6240
@scoltenroma6240 13 күн бұрын
Kkkkkkk! A PAC,where wea you for all these elapsing years? Mwandiwaza bwanji,kuswa kuswa anthu amafika potopa,.....Oh Yes!!
@markanthony5402
@markanthony5402 13 күн бұрын
Bendulo waukira, ben longwe waukira a pac awukira kkkkkkk pompano tiona khombe ataukira, the downfall of mwenemutapa kingdom
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 13 күн бұрын
Well done ❤❤❤
@SALIMASSAN-vr8ld
@SALIMASSAN-vr8ld 13 күн бұрын
Palib chifukw chokawelengel chakwer chifukw chan nun apac thaw yosey mubwel pan zanuy palib chomwe akupanga
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 13 күн бұрын
Zoonadi bomali laola ma ministers akuba mopanda mantha chifukwa President ndi wakuba ndi kupha.
@MrGcellrepairsnlaptops
@MrGcellrepairsnlaptops 13 күн бұрын
Children's of Chikangawa you follow everything like mbuzi
@ElizabethMwale-z3s
@ElizabethMwale-z3s 13 күн бұрын
Koma a PAC nthawi yonseyi munali kuti, kapena tinene kuti vinyo wakutherani banzi latha. Koma dziwani kt a pule anuwo akupita nthawi yawathera, ife chisankho tapanga kale mu mtima mwathu.
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 12 күн бұрын
wolo ine vote yanga idapita ku mcp chifukwa cha chilima pano idabwelako pano sindiku dziwa zoti ineyo ndinga votele ndani koma in fact president uyu palibe chimene wapanga miseu ndi zowona koma pazi chakudya palibe chimene akupanga
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 13 күн бұрын
Chidule tiwakumbuse achakwera ku ahebri mawu amanena kuti nkoopsya kugwa manja mwamulungu wa moyo mulungu anawasiya achakwerawo
@MposadaraVizara
@MposadaraVizara 13 күн бұрын
Penapake mukalandira ndalama zakubazo muestsetsekut musamabwere nkumayankhula zozizira ngat zabwerazi. Pac imene yabwerai Siyadziko lamalawi nkutheka ndiyadzikolinalake
@Georgemphamba-to1ik
@Georgemphamba-to1ik 13 күн бұрын
Mavuto achuluka kusiyana ndi zabwino zomwe zachitika muxzaka zinayi chonchi sanzikani mukapume chifukwa simungakwanitse kukonzanso dzikoli. Perekani mpata ena alamulire tisalimbanepo apa
@SurprisedAnacondaSnake-ru1in
@SurprisedAnacondaSnake-ru1in 13 күн бұрын
Apa ndie zamunyela pakamwa papakulupo ngat nvuuu
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni 13 күн бұрын
Kkkkkk😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 13 күн бұрын
Palibe kumbvotera chakwera olo atasintha zinthu
@HenryKatopola
@HenryKatopola 13 күн бұрын
Chakwela paulendo basi
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 13 күн бұрын
Pac yachedwa chakwera anaononga kale inu a pac munali kut mwaona kut chakwera wanuyo wasala ndi masiku ochepa ndichifukwa mukumuzizira
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 13 күн бұрын
Tiwathokoze a PAC, uku ndiye kulankhula. Chakwera ndi boma lake la MCP alephera kale ndipo akuchoka.
@TrasizioMlupwa
@TrasizioMlupwa 13 күн бұрын
Even the president himself doesn't know that he is a president
@ReadsonChisaga
@ReadsonChisaga 13 күн бұрын
Chakwera wanuyo walisaukisa dziko la Malawi.
@RemsyChipani
@RemsyChipani 13 күн бұрын
Pano tikudikira kunkuyu ndi mai wosasamba uja jessy kabwira including chimwendo banda kodi boma ndilomweli kapena ai
@VincentMpulula-h9b
@VincentMpulula-h9b 12 күн бұрын
Eeee kuswakuswa
@marryphili5419
@marryphili5419 13 күн бұрын
Well done panopa chilungamo chayamba kuyenda ngati madzi ine siwschipani china chilichose Koma ngati kuli wuramulilo wowononga ndi wumenewu WA achakwera zomwe akuziwa ndi kupha, kuwononga, kubweresa njara mu dziko,kunama ndi kumanga anthu Kuti asamawazuzure Koma ndiye ziliko ndi mwana yemwe akuziwa Kuti chakwera watiwonongera dziko la Malawi 😢😢
@gracekamzati
@gracekamzati 13 күн бұрын
Takunyadilani apapa APAC mwalankhula zoona
@MosesNyasulu-c3x
@MosesNyasulu-c3x 13 күн бұрын
Sopano muwona ambiri amuwukila chakwera ambiri atulukamo mchipani apa basi chakwera vavuta
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 10 күн бұрын
Awa tatopa nawo mcp ndi panja basi. Achokeeeeee!!!!!!
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 13 күн бұрын
Ujayu amati oyankhulira boma ujatu azimva chifukwa Pena akati ayankhule amakhala ngati akuyankhulira kuujeniiii
@ManganiStanley
@ManganiStanley 13 күн бұрын
Eee apac apa mwayankhula chilungamo
@ConnexKhomba
@ConnexKhomba 13 күн бұрын
Muthu ofuna kugwila tchito sangagwile tchito ndi zikhale chimwendo kabwila nkumat ziko lingasithe athu akukanika kuzisambisa okha
@SamsonChavula
@SamsonChavula 13 күн бұрын
A PAC mwayesesa ngati Ali ndi makutu wamva
@GraciousMkyelu
@GraciousMkyelu 13 күн бұрын
Only truth 🎉🎉
@jabinmwamlowe
@jabinmwamlowe 13 күн бұрын
This is 🔥
@McfordKaunda
@McfordKaunda 13 күн бұрын
Pac iyi ndi ya athu amulungudi ndangokhara osauka km mulungu akuonen
@CharlesNangomah-x8e
@CharlesNangomah-x8e 13 күн бұрын
This guy does not deserve to called president😂
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 13 күн бұрын
Anthu awa ayionera patari kut uyu zake zada, ndipo, afune asafune, ndiwautali
@MariaJaya-s9b
@MariaJaya-s9b 13 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@HawaHussein-o5k
@HawaHussein-o5k 13 күн бұрын
Ameen ameen ambuye alandile ulemu chilungamo chalankhulidwa mooneka
@BigsonIliyasa
@BigsonIliyasa 13 күн бұрын
Mwawachita bwino achikangawa powauza chilungamo
@Martha-m6e
@Martha-m6e 13 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂Ana aboma ndi lomweli mukuva bwanji?😂😂😂😂.
@MarthaChigonero
@MarthaChigonero 13 күн бұрын
Kutopa ndiye tinatopa kale tingodikila pa 16cept
@MarthaMtenje-r6o
@MarthaMtenje-r6o 13 күн бұрын
Ndakomoka ineeedee😂😂
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 13 күн бұрын
Nyanja ilikuti?Mnzathu wanuyotu zinthu sizikuyenda,kusoweka laola,kusowa mphamvu,mwalephera kuthetsa katangale,kuimira kolephera,ever since.Chuma cakanika,maunduna,maulendo musiye,njira mumasakaza.Ntchito za boma zangwa,mukuchita zakatangale OPC,Chisankho muchiyendetse bwino,ziwawa kuziretsa ndi uchitsiru,amenewa akalephera zidzavuta,kumangana maka otsutsa zisokoneza,otsutsa atsutsa ngakhale tayamikira palibe chomwe mwachita,zikuoneka kuti mwalephera mochuluka,Pomaliza mwalephera.
@MeruMitha
@MeruMitha 13 күн бұрын
a pac anyoza kwambiri.
@OwenMindozo
@OwenMindozo 13 күн бұрын
Pamene palibe masomphenya ndi ngozi yaikulu zedi imachitika pakati pa m'mabunge, mu mzinda, m'mdziko, pakhala kuti mtsogoleri akapanda masomphenya.
@ManganiStanley
@ManganiStanley 13 күн бұрын
Eee zibusa akwiya mpaka uchitsilu
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 13 күн бұрын
Amung'amba wapita basi galu ameneyi .
@LakwanjiMlambala
@LakwanjiMlambala 13 күн бұрын
Anena chilungamo central region ndiyokwiya
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 13 күн бұрын
Musawasisite okhuzidwa ndi kuchitisa chisankhowo alephera kale ntchito yawo Madera ambiri sanalembeko anthu
@GladysBonongwe-p6b
@GladysBonongwe-p6b 13 күн бұрын
Auzeni mwina amva
@IzekiPonyani-n1s
@IzekiPonyani-n1s 13 күн бұрын
Pankhan ya zisankhopo alankhulspo monyengerera kwambiri I'fe sitikufuna sisimatiki machine, sitikufunaso Anabelo mtalimanja, sitikufunaso my amkulu wa Nrb
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 13 күн бұрын
Nkhutukumve samamva muuzeni
@sostenBenardmanyozojunior
@sostenBenardmanyozojunior 13 күн бұрын
Koma kalatayo yalembedwad motelomo? Ndikukaikila ndithu coz enafe tinataya chikhulupililo mu bungwe la PAC
@Mtchujuku
@Mtchujuku 12 күн бұрын
Nane funso langa ndi lomwelo. Mau ena akutchulidwawo akukaikitsa mwee. I hope we will get a copy and see the verbatim
@GeorgePatels-go7wj
@GeorgePatels-go7wj 13 күн бұрын
Ati chakwera mmbusa nzawo kkkkkk
@PeterKainga-e3h
@PeterKainga-e3h 13 күн бұрын
PAC yachedwa komaso mtsogoleri uyu alibe kuthekera kulikose chifukwa ndisozikonda
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 13 күн бұрын
Nthawi yabwn PAC ouma mutuyi alibe nzelu
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 13 күн бұрын
Achina boma ndilomweli, alipompatu koma? Koma izizi zachitikadi?? Anthuwa atuluka bwino bwino mu palace?😂😂 Wow zokongora bwanji
@liliantamaona1669
@liliantamaona1669 13 күн бұрын
A Thawala alemba nawo, okay.
@HappyKanyangala-oq1kk
@HappyKanyangala-oq1kk 13 күн бұрын
Koma a pak awa ndiwabodza komaso mitiyawo sigwila milili yoseyi samaiona?
@marryphili5419
@marryphili5419 13 күн бұрын
Milili yinagwa kumalawi kokha za ziiiii ngati amakugawira akapakura muziwona sitingalole Kuti tizivutika chifukwa cha galu ameneyu
@Emelzelie
@Emelzelie 13 күн бұрын
Nthaw ya COVID I remember mukunena KT a DPP akunamizira COVID kulibe matenda nde inu mufuna ziveke bwanji, mmanamizira nkhondo ya Ukrain , Ku Ukraine komwek anakupasan chimanga amene akumenya nkhondowo . Kuvomereza ndikwanwino , awa angodziwa kupakula ndalama mkuzilemelesa okha pano ndalama zikusowa
@EsetaGerate
@EsetaGerate 12 күн бұрын
Koma lnuyo a pac munari kut nthawi yoseyi zotipusitsa lfe ayi mwaona kut MCP lkutuluka nde mufuna muoneke abwino asatana lnu
@SidreckRashid
@SidreckRashid 13 күн бұрын
Sangamve galu ayu ndipo sangasinthe.....president wa tsankho
@StellaSankhulani-w2m
@StellaSankhulani-w2m 13 күн бұрын
Hehede koma ndie
@AbdulNyambi
@AbdulNyambi 13 күн бұрын
Mumuwuze chakwera wanuyo machendake
@ManganiStanley
@ManganiStanley 13 күн бұрын
Koma tathokoza Poti mwamuuza chilungamo na macende ameneyi ndipo watikwana
@henryTembo-n7u
@henryTembo-n7u 13 күн бұрын
Anthu amafikapotopa kungotopakuti basi tatopabasi 😅😅😅😅😅
@IshmaelNgeyani
@IshmaelNgeyani 13 күн бұрын
Pac iyi siyojiya ija
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 13 күн бұрын
Komatu kuyankhula eeeeish
@NEDGIFT-p5t
@NEDGIFT-p5t 13 күн бұрын
Bola amuuza chilungamo izi zikusimikidzira kuti boma lagwa ndipo saona vote yona ameneyu
@EmmanuelJoseph-lj5eu
@EmmanuelJoseph-lj5eu 13 күн бұрын
Zoona
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 13 күн бұрын
Zavuta kupanda
@ChikondiDayce-sl9bu
@ChikondiDayce-sl9bu 13 күн бұрын
Amaremba mumuuze kuti mutuwake😂....... Wapanga Chan kapeyi
@OretarbadrBwanali
@OretarbadrBwanali 13 күн бұрын
😂😂😂😂
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h 13 күн бұрын
Too late for tears 😂😂
@WhyteSmart
@WhyteSmart 13 күн бұрын
Achakwera palibe chomwe angasinthe ay nthawi yatha bc
@AlexanderYovatiKhumalo
@AlexanderYovatiKhumalo 13 күн бұрын
Kalata yamveka kuchokela ku PAC sikulakwitsa ayi, ine langa ndi funso Kwa PAC Kodi ma president amene timasankhawa amabwela ndi thumba lawolawo loyendetsela dzikooo? Kapena limakhala thumba limene amasiya ochokayoo? Chifukwa kukalowa kwa mkazi amene mu nyumba yake mulibe ziwiya zophikila limavuta banjalo.
@PasquaMapemba-my9mw
@PasquaMapemba-my9mw 13 күн бұрын
Kafusaneni ku banja kwanuko zimenezo, mukuona ngat ndife ana?? TIBWEREZENSO ANTHU AKATI ATOPE AMATOPA AMALAWI CHETEYU SIKUTI TANGOFUNA KOMA TIKUDYA MITU KAYE, APAPA TAYAMBA TAYAMBA BASI NDIPO KAYA NDIKUFA TIPHENI TONSE
@DicksonTembo-b1k
@DicksonTembo-b1k 13 күн бұрын
Fuso lopusa mbuzi
@innocentkamanga2043
@innocentkamanga2043 13 күн бұрын
Kugagada
@IsabelMmamiwa
@IsabelMmamiwa 13 күн бұрын
Kkkkkkk ndikhare mbuli
@FestonManuel
@FestonManuel 13 күн бұрын
Zoputsa nthawi yonseyi mudali Kuti kapena buns yakutheran
@KondwaniPhiri-l2z
@KondwaniPhiri-l2z 13 күн бұрын
Galu iwe
@ernestphiri5507
@ernestphiri5507 13 күн бұрын
Muuzeni samamva ameneyo
@IdressaMussa
@IdressaMussa 13 күн бұрын
Chakwera wandikwîsa patumbopak nyini yako
@CarolineLiabunya-j8k
@CarolineLiabunya-j8k 13 күн бұрын
Muzinvatu inu achina Boma ndilomweli mitu
@JosphineJoshua-gq1rp
@JosphineJoshua-gq1rp 13 күн бұрын
Chakwera wayesetsa pat??? ??
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 13 күн бұрын
😂
@McDonardMapala
@McDonardMapala 13 күн бұрын
Nkhan ndi chuma chazikolanthu aopo alasa
@MussaRafael-d4q
@MussaRafael-d4q 13 күн бұрын
Zoonadi MCP ikununkha ndipo yawola
@EstherSamuel-e7x
@EstherSamuel-e7x 13 күн бұрын
😅
@ChibakuliKaisi-cm3hn
@ChibakuliKaisi-cm3hn 13 күн бұрын
Bolozani
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 13 күн бұрын
PAC mwachedwa, mmayenera kupanga advisory role osati criticism...inuyo mwina mmafuna mupatsidwe dipo ndiye mwaona palibepo za tipping.... Inuyo ndiye nanuso mwalepheraso role yanu....kodi Chakwera angalowe mma ofesi onse nkumagwira ntchito yekha??? Tiyeni aliyese apange mbali yake otherwise Malawi azikhala chonchobe...Laz wayesetsa🎉
@ndalamaandrew
@ndalamaandrew 13 күн бұрын
Death is real, kuvomeleza Umasiye kukuvutani. He must go
@ndalamaandrew
@ndalamaandrew 13 күн бұрын
He is fool and manipulative.
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 13 күн бұрын
Mwana wang'ona iwe just zip up . Advisory role yambuyako?
@markanthony5402
@markanthony5402 13 күн бұрын
Ampatse advisory lore ndani, mesa iye ndi president chalephera basi chimunthu chanucho
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 13 күн бұрын
Apac anali kuti nthawi yonseyi akufuna ndalama agalu amenewa awona kuti boma likusintha mbuzi za chinyengo
@FelixMachika
@FelixMachika 13 күн бұрын
Kiss :mpsopsono
Ku Malawi Kuli Mitundu Inayi Pa Ndale - Richard C Mphepo
33:40
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 450
🎈🎈🎈😲 #tiktok #shorts
0:28
Byungari 병아리언니
Рет қаралды 4,5 МЛН
Ful Video ☝🏻☝🏻☝🏻
1:01
Arkeolog
Рет қаралды 14 МЛН
ССЫЛКА НА ИГРУ В КОММЕНТАХ #shorts
0:36
Паша Осадчий
Рет қаралды 8 МЛН
Caleb Pressley Shows TSA How It’s Done
0:28
Barstool Sports
Рет қаралды 60 МЛН
Afe Babalola Drops Charges Against Dele Farotimi
4:07
Channels Television
Рет қаралды 10 М.
Sharman: 'VHP is een consistente partij die het meent met het land, - Tbn Prime Alert 24 Jan 2025
12:37
Trishul Broadcasting Network (TBN PRIME ALERT)
Рет қаралды 2,2 М.
В Швеции ищут, кто разорвал подводный кабель
1:01
Euronews по-русски
Рет қаралды 20 М.
🎈🎈🎈😲 #tiktok #shorts
0:28
Byungari 병아리언니
Рет қаралды 4,5 МЛН