KWACHEMA KUBWEZA MOTO CHAWEZI |

  Рет қаралды 16,426

DZIWE TV

DZIWE TV

Күн бұрын

Пікірлер: 76
@momuumro
@momuumro Ай бұрын
Mbuzi Chawezi Iweyo tangopanga Za MCP yakoyo usalimbane ndi UTM Mesa inu a MCP ndamene mwamupha Chilima Nde chokhalira mu mgwilizanomo ndichani? Chawezi ndiwe mbuzi kwambili
@JustinLipipa
@JustinLipipa Ай бұрын
Ndiwa Mcp uyu, anthu mwawaphera mtsogoleri akhalebe komko
@aaronziyeretsa6420
@aaronziyeretsa6420 Ай бұрын
It's a move by DPP and they have allowed kabambe to be leader in order to redirect all UTM followers back to DPP
@MisheckAselo
@MisheckAselo Ай бұрын
Mgwirizano unatha kale mu 2020 kadasala ndikutulukaku☝️
@user-qz1rp5mh9e
@user-qz1rp5mh9e Ай бұрын
Iwe chawezi president ananena poyera kuti ayima in public mzake ali pomwepo mmmmm ine si wandale koma mzeru mzako ndi zofoka kwambir
@HeinzeVictorMumbai
@HeinzeVictorMumbai Ай бұрын
This chawezii he's MCP member
@martinnyirongo2892
@martinnyirongo2892 Ай бұрын
Achewa alibe respect ndipo ndiwophangira kwambiri, utm yachita bwino
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
The only wise and rational person who leaves a beautiful place where everything is going well and goes to live with the people who are suffering,will find favor in the presence of the almighty God.
@Brihippo
@Brihippo Ай бұрын
Komaso muthu akamwalila pamabeera wina basi
@JohnFrank-cg1yh
@JohnFrank-cg1yh Ай бұрын
Tikuyenela kumapephela tsiku ndi tsiku, nthawi ndi nthawi chifukwa satana ndiwochenjela atha kutigwesa m'mayeseli
@user-sm6pr9cg2q
@user-sm6pr9cg2q Ай бұрын
Zomwe adagwilizana chilima adanena pa press briefing kt ndi 5/5 ndy inu mukut anadziwana awili bwanji
@godfreyamos7452
@godfreyamos7452 Ай бұрын
A Chawezi kunali amzathu , muzatha mosakhala bwino
@MAYAMIKOCHALIRA
@MAYAMIKOCHALIRA Ай бұрын
Palibe Nkhani apa...ngwilizano unatha ...adekhe why?
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 Ай бұрын
Mbuzi iwe chawezi mafuta sangatchipe kuno iwe galu iwe usadandaule ukhala wankulu wa MBC galu iwe
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
Chawezi palibe zodekha MCP is helpless to UTM. What you should focus is MCP agenda
@user-ic1zy4zj1c
@user-ic1zy4zj1c Ай бұрын
Mabwana a chawezi tamuchoseni uyu pa program imeneyi, we need balanced issues, awa ndi achibwana, a Mbuye Mulungu wa zonse mkatheni chawezi yu amen
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Kaliat ndi kathyali nfiti yaikaz
@GiftMathewe-fr3kn
@GiftMathewe-fr3kn Ай бұрын
Sanalakwise chifukwa zomwa adagwilrizana mungwilizano wawo palibe akuziwa
@CathrineBizza
@CathrineBizza Ай бұрын
Nkona anamuxhotsa ntchito ku mbc uyu xhitsiru wamva
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Ай бұрын
Palibe chifukwa cholembela kalata yothela ubalewawo nde asadijile kalata kodi mr chikangawawo atava zimezi anayitanapo a UTM kuti akambilane zakutuluka kwa UTM? Zomatiseka kumaso uwe chawezi uzingodya misokho ya amalawyo osatipusisa mene munkapanga zachipongwe ndichilima ndemumati atani palibeso zodikila myezi mafuna mugule UTM yose nde mwauponda mwakumananazo zanadulila muwona nyekgwe a MCP muwuzeni chimwendo abeleke over muzapenge gwilizano ndi ana achimwendo
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Ndipo monga ngati ine ndikuti anakhonza kwambili kutulukako mcp down
@Brihippo
@Brihippo Ай бұрын
Timafikila kuti chilima atiyakhule poti wamwalira a Patricia watiyakhula
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 Ай бұрын
Ayi choka iwe chawezi utm yachitabwino kutuluka musanga kt akozenyumba yawo even chilima akanavela kalindo bwezi izi kulibe lero winiko amanena zoona kt tulukani mu tose koma sanavele
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Utm yagulisa chipani ku dpp
@MaryMlongoti
@MaryMlongoti Ай бұрын
Chawezi umatha
@rabsonswathera738
@rabsonswathera738 Ай бұрын
Kuchoka mungwilizano kwachitika munthawi yake
@peterdanie4684
@peterdanie4684 Ай бұрын
Chawezi great analysis
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s Ай бұрын
Ndipo achawezi sawlekeze kuonesa mutu ukakwela galimoto yako tikukhazula tionana aise manyi ako wanva
@user-qk2hw4ex3c
@user-qk2hw4ex3c Ай бұрын
Chisilu iweyo simadziwa Kuti Pali ndale kupha chilima
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Ай бұрын
Satana akalowa mpovuta kumutulusa, Chawezi amlowa satana.
@DamianoGabriel-sh2mf
@DamianoGabriel-sh2mf Ай бұрын
Chawezi capaign director wa mcp banja likatha palibe za ulemu
@jameshuwanzulu
@jameshuwanzulu Ай бұрын
Or ndi dzina lomwelo likungosonyeza kut ndi wa MCP
@estonmnthali3719
@estonmnthali3719 Ай бұрын
Chawezi ndi wa MCP
@idilissmuyer2914
@idilissmuyer2914 Ай бұрын
Pamtumbo panu inuyo mwasowa zokamba mamwapwala anu
@leonardmalirana7423
@leonardmalirana7423 Ай бұрын
Ngati, mgwirizano unali wa anthu awiri basi uthepo winayo anatisiya ndiye UTM isiyeni
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Chawezi ndiwe Galu
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
Whether the votes will be minus 20% we don't care . USI and the cabinet ministers can remain at MCP we don't care .The best Usi can do is to start his party and do the alliance with MCP . That will be his correct decision. He must not use UTM emblem because at UTM I don't see his impact achedwa kwambiri.
@user-qk2hw4ex3c
@user-qk2hw4ex3c Ай бұрын
Chawedzi ndiwe osokonedza
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 Ай бұрын
Kod iweyo why ukukamira zimenezo ndiwe mbuzi et ?
@user-ck7eb7tb7v
@user-ck7eb7tb7v Ай бұрын
Iwe apanga nthawi yoyenera, afufuza bwanji za ifa ali ku tonse komweko? Aasa!
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl Ай бұрын
Chawezi zinarakoro ndiramunthu wamukazi anakupasayo anakuwononga ndiye utisamare uzapezeka mumavuto mumene umamwera mowa iweyo🆗
@patrickmwakilasa7198
@patrickmwakilasa7198 Ай бұрын
Agalu inu
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 Ай бұрын
Programe iyi kulibwino angoyithetsa chifukwa zimene zimakambidwa akumapanga back up mcp so palibe Amalawi yingatithandize Programe yanuyi ayi just suspend it
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr Ай бұрын
Kodi chawezi yu mumamutengelanji? Uyuyu adzandilakwitsa one day. Victor or abel, banda are the bes uyu ndiwa mcp. Sadzatheka Chawezi akupeza zabwino ku bomaku ndipo ativuta kulera 😅
@Chrissyluwe
@Chrissyluwe Ай бұрын
Chawez u hv no timing
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g Ай бұрын
Chawezi samalira ayise we know ukulimbana ndi azipani zotsutsa samalira ayise I know you are there for mcp
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
Chaweza what you should know is we didn't do a hasty decision . It a fine a decision and you can't change it. We are not desperate rather and we as voters cannot take it Chawezi you are MCP and no body can listen to your views . Member wa nzeru cannot proceed to be in alliance with MCP .
@petroszgambo9949
@petroszgambo9949 Ай бұрын
Useless program
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Achilima anali odekha mtima, koma ku bwela kwawo ulendo wakunja uja koria,anali ndicholinga chotuluka mu tonse kale, koma tsoka asanaphume kubwela kwaku koria ,ndimene amapita kumarilo akusambala posadziwa kuti awusi chisisi anakamuuza kale chakwela, kodi zonsetu tikuzidziwa koma ndalama ndalama, koma mulungu simuthu
@leonardmalirana7423
@leonardmalirana7423 Ай бұрын
UTM IS NOT THE FIRST PARTY TO MOVE OUT OF THIS ALLIANCE , PEOPLE ARE TALKING ALOT BECAUSE IT HAS MANY YOUTH FOLLOWERS SO ZIKUBAYA ANTHU AMBIRI.
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Ай бұрын
Where is victor
@Raph-kayRaph-kay-g5v
@Raph-kayRaph-kay-g5v Ай бұрын
Chawezi uzafa ngati garu
@vincentkamangamr9062
@vincentkamangamr9062 Ай бұрын
Chawezi umawoneselatu kuti ndiwe wa MCP all times on this program
@DysonUmali
@DysonUmali Ай бұрын
In life ngati mkazi wakukana olo mutalankhula motani it's helpless to the man. UTM is done with MCP
@WilfredChinkono
@WilfredChinkono Ай бұрын
DK simunthu wamba UTM ikutenga boma 2025
@UsumanLuwayo
@UsumanLuwayo Ай бұрын
Ngati Dewesi ali pa banja njofunika kumunyengera mkadzi wake nde kupanga dzoti anthu adzamugwire mkadziyo akuchita chigololo nde iyeyo adzamve, then tidzaone ngati adzadekhe osathetsa banja antil 3 months
@PaulChaleka-lb4vx
@PaulChaleka-lb4vx Ай бұрын
Chawezi ndi wa chakwera
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb Ай бұрын
Chawezi chawezi chawezi
@ChikuMatemba
@ChikuMatemba Ай бұрын
we don't like Chawezi on this Program
@BehindThecamera-xo1qg
@BehindThecamera-xo1qg Ай бұрын
Ulemu wa chani galu iwe chawezi, umamupasa ulemu munthu oipa
@BehindThecamera-xo1qg
@BehindThecamera-xo1qg Ай бұрын
Miyezi 4 inachuluka anthu ambiri akanasala ku mcp , achita bwino kutuluka fumbi la kuchikangawa lisanathe .
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl Ай бұрын
Komatu chawedzi pena amayankhula ngati mbuli zedi kodi amene samadziwa kuti alliance ya utm ndi mcp inali yoti five yrs wina akhala president kenako wina azaimeso, ndi chifukwa ichi ndi chomwe chinabwelesa kusagwilizana cz ingakhale Dr late SKC ananena poyera kuti ngati Dr chakwera sakufuna kutula pansi udindo ndiye tiyenera tikavote. Utm kutuluka siinalakwise aii cz mcp siinalemekedze ingakhale imfa ya chilima mzinthu zambiri kumapanga msonkhano anthu akulilabe kenako uziti afulumira kutuluka ukhalike ndithu ngati akukunyemera tazingodya makobidiwo komano usaganize mombwambwana aiii
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z Ай бұрын
Ine anthu awa amandionekera mwa mcp cp eeee ndiye aaaa sinkonda kunvera zamenewa
@user-cs6zy3ix8d
@user-cs6zy3ix8d Ай бұрын
Chawez ndi iwe mbuzi
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Ай бұрын
Chawezi wabodza iwe, sukuyenera kukhara analysis poti zuonekeratu ndiwe wa MCP
@PatrickDisple
@PatrickDisple Ай бұрын
He knows only how to speak but not to understand what he is speaking. Mr Chawezi 😅
@user-oc8nj3or6y
@user-oc8nj3or6y Ай бұрын
Ndi ntchito yawo,,,anali kuti? Nthawi yonseyi
@chimwemwechiundira6002
@chimwemwechiundira6002 Ай бұрын
Halayansi yabayatu
@tonnychimbiro
@tonnychimbiro Ай бұрын
Zinthu zake
@PiusChawinga
@PiusChawinga Ай бұрын
Wabweza bwanji?
@user-my5jj5we5j
@user-my5jj5we5j Ай бұрын
Unuso mukuziwa mugwilizano panalibe
@KestonNGUBO
@KestonNGUBO Ай бұрын
Zoonad iwe
@user-gy8yn6qw2k
@user-gy8yn6qw2k Ай бұрын
Ineyo i don't like this guy is not the best for me ........
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Ай бұрын
Chawezi ma comments ako ngooneseratu uli mbali yinayo uli against UTM
When you discover a family secret
00:59
im_siowei
Рет қаралды 33 МЛН
KUYANKHULA KWA JOYCE BANDA
21:25
HOT 265
Рет қаралды 18 М.
BON KALINDO WABWERANSO NDIIZI TAMVERANI 05/09/2024
16:42
LIKI-LIKI Ladies
Рет қаралды 24 М.
Record Label Ya Ku Malawi, ipindula?
13:59
Sam Malvitha
Рет қаралды 7 М.