LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA ZAMANYAZI PLAN YOIPA YA MCP YA ULURIDWA PA MBALAMBANDA

  Рет қаралды 10,603

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 35
@SmilingFishingRod-zc4wx
@SmilingFishingRod-zc4wx 27 күн бұрын
Yayayaya a Mthanyiwa kumeneko ndiye kubweraaaaa. Malangizo Anu machenjezo Anu ndi a mphanvu kooopsyaa
@FarooqSwadeeq
@FarooqSwadeeq 27 күн бұрын
Mawo abwino ameneyo Mr big mtayiwa❤
@ChimbaluDaniel-m7l
@ChimbaluDaniel-m7l 26 күн бұрын
Keep it up Amuna
@GifLiche
@GifLiche 23 күн бұрын
This radio yes 😂😂😂😂 osati MBC timabesa nthawi yathu chabe
@DeborahChiwambo
@DeborahChiwambo 27 күн бұрын
I do not know how to figure you Ntanyiwa and your friend wa Bakili and The the DC !!!!!!!!! No words to expound .
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 27 күн бұрын
Mr ntanyiwa kodi mwalimva dzina lina apeleka ma guy akumpoto aja akut Mr chikangawa ndi chimgwilila chifukwa wamaliza kugona ndi azimai aeni ngat mai bida Mia,Collins zamba,gotani hara,plus mai Vera kantukule😅😅😅
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 27 күн бұрын
Ana achepa. Kungomva kuti DPP yili ndi convention, ayamba kale kubowoka mmimba
@MussahWilliam-py1ff
@MussahWilliam-py1ff 27 күн бұрын
Mr mtanyiwa on fireeeee🔥🔥🔥umakwana
@user-st4fh1vf4m
@user-st4fh1vf4m 27 күн бұрын
❤❤❤
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 27 күн бұрын
Kamuna mtanyiwaaa 🎉😢
@user-dn3gp6yi4y
@user-dn3gp6yi4y 26 күн бұрын
Live in Madagascar Limpopo FM timakunyadilani ndi malangizo anu
@DeborahChiwambo
@DeborahChiwambo 27 күн бұрын
Keep keep up
@user-jb5hr4rz2s
@user-jb5hr4rz2s 27 күн бұрын
Manja mwanu a comrade timakunyandilani zambili timamva through u
@robertkabade5011
@robertkabade5011 27 күн бұрын
Kubwera Mr NTANYIWA.
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo 27 күн бұрын
Ana achepa achisale alikoko akaona zonse
@ChristinaNyirenda-zb1if
@ChristinaNyirenda-zb1if 27 күн бұрын
Timakunyadilani❤❤❤
@IlaliJames
@IlaliJames 27 күн бұрын
Mupitilise Kutipazila Zabwin Tikudalila Inu Ndiwabakili Ndikalindo Osaop Zikom Ndilatu
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i 27 күн бұрын
Khaniyaveka Mr ntanyiwa mulungu azikusamalilani thawizose Abale inu muliku BT athuawo akangoyamba zawozo zosokonezazo muthanenawo kumpha kumpha kukhapa kukhapa chifukwa zawo palibe amene anawasokoneza nde asokoneza bwanji a DPP akawone njila yopitila koma zobwelela kwawo asakaiwone athu akumpha a MCP
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 27 күн бұрын
Kkkkkk KK km nde avutikabe mizimu idakwiya
@MalawianMediafm97
@MalawianMediafm97 27 күн бұрын
Nkhanga zaona 📻 with comrade ntanyiwa on Lipompo FM
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 26 күн бұрын
Km MCP sizatheka
@EllinaBitto
@EllinaBitto 27 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 26 күн бұрын
😅😅😅😅Ndakomoka
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 27 күн бұрын
Zoona tikufuna chipani choti Malawi yose ikhale pamozi kumaso azitsogoleri atuluke mumakona ose aziko la Malawi osati achokere mbali yimozi . Komaso a mcp chenjerani ngati mukufuna kusokoneza adzanu mungoziyipisira mbiri poti mbiri yanu yayipa kale mu Malawi.inu munapanga conversation yanu koma palibe chipani kapena munthu anapita kukasokoneza conversation yanu.and moyo wolimbana ndi azanu sizabwino
@enerstmakochera3956
@enerstmakochera3956 27 күн бұрын
💪💪💪💪❤❤❤
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 27 күн бұрын
Palibe sizabwelelaso boma mungobvutika dikilani muziona masiku akubwelawa musiya kulakhula
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 27 күн бұрын
Kumakhala chabe moyo waufiti iwowo zawo anapangitsa bwino bwino anawosokoneza ndindani kamoyo kamagazi manja basi MCP chipani choyipa dairy kumva zoyipa za MCP anthu amenewo atikwana
@Ennlesssodoma
@Ennlesssodoma 27 күн бұрын
Comrade tsopano
@LucyMachine
@LucyMachine 27 күн бұрын
Machenjezo abwino mtanyiwa
@DevisonHala
@DevisonHala 27 күн бұрын
Palibe chingachitike mulungu simunthu
@InnocentKadoma
@InnocentKadoma 27 күн бұрын
Akulimbana ndi dpp
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 27 күн бұрын
❤❤❤
@user-eo2hl9ug1h
@user-eo2hl9ug1h 27 күн бұрын
❤❤❤❤
@AlickJinamu
@AlickJinamu 27 күн бұрын
❤❤❤❤❤
Top U.S. & World Headlines - September 6, 2024
13:19
Democracy Now!
Рет қаралды 216 М.
GTA 5 vs GTA San Andreas Doctors🥼🚑
00:57
Xzit Thamer
Рет қаралды 27 МЛН
He bought this so I can drive too🥹😭 #tiktok #elsarca
00:22
Elsa Arca
Рет қаралды 46 МЛН
У ГОРДЕЯ ПОЖАР в ОФИСЕ!
01:01
Дима Гордей
Рет қаралды 7 МЛН
Moremogolo - Thobalano & Lerato
5:00
Thobela FM
Рет қаралды 19 М.
LIVE: The Latest in Israel
7:56
CBN News
Рет қаралды 111 М.
VHEMBE FM interview NICODERMIC
13:26
Mulata Branded Lifestyle
Рет қаралды 5 М.
WALAVULA MAWU LERO NAMIWA NDIPO UYU SURE ABUDULA NDIWO ZA ZA BOMA ILI
20:41
GTA 5 vs GTA San Andreas Doctors🥼🚑
00:57
Xzit Thamer
Рет қаралды 27 МЛН