LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA 1 JULY 2024

  Рет қаралды 42,634

Club Junta

Club Junta

4 күн бұрын

Пікірлер: 267
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Күн бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time.
@user-wq9ex2sf3b
@user-wq9ex2sf3b Күн бұрын
From Zambia I love bro with bon kalindo my wife came from chitipa MCP yampa athu anzelu,
@MercyNyachi
@MercyNyachi Күн бұрын
Mulungu akulangeni achakwera mwadzuza amalawi ambiri ambuye ngati mukumva pemphelo lathu ife amalawi timenyeleni nkhondo ambuye amen
@FelixKada
@FelixKada 10 сағат бұрын
Big up mr ntanyiwa, ndipo pitilidzani kuigwira ntcito to.🤝🤝🤝🤝🤝🤝🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@LYDIANYAKATU
@LYDIANYAKATU Күн бұрын
Ambuye azikutetezerani a ntanyiwa ,amene akulimbana ndi Inu akulimbana ndi Mulungu kumene amene akulimbana ndi a rwara akulimbana ndi Mulungu kumene anthu a Mcp opanda nzeru mmalo mopangira chitukuko ndarama akupangira kuti achotse mutiti ya anthu heeedee tawaonani eti anthu opanda manyazi ngati awo timakhnyadirani a ntanyiwa may God bless you all the time
@NastonVickta
@NastonVickta Күн бұрын
Tili ngaaaaaa pa Limpopo fm, mpaka agaru oyamwitsa Inu mawere auma
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Күн бұрын
Mumakwana ma Freedom fighters athu athu akumalawi, timakukondani guys❤, MULUNGU azikutetezani ndikukupasani zosowa za pa umoyo wanu, inudi ndima HEROES adziko lamalawi ❤❤❤😢
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o Күн бұрын
I love limpopo fm with Comrade ntanyiwa
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Күн бұрын
Lipopo tiutseni soona shonde lipopo is my favorite shoiss ever from 6pm to 12am osawopha osavowonka ndive amalawi mtanyiwwa osawopha bakili muluzi TV osawopha mulungu adalise inuyyo nosse nkumene mulinko my must brress you orrowyess 💪💪💪💪👀
@jamesmulangalimatemba5351
@jamesmulangalimatemba5351 Күн бұрын
May God protect you my brother tikufuna anthu olimba mtima ngati inu
@BlessigsChabzola
@BlessigsChabzola Күн бұрын
Nanga Iwo a Mcp sakulira nawo nanga bwanji 21days isanathe Iwo akupanga program ya convention. Ndizona zimezi,
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw Күн бұрын
We Love you our junior pangolin no matter what they can't find you chifukwa inuyo Muli mumapapiko a mwini moyo wanu Chauta, Namalenga chisumphi. Ndeno angotaya nthawi azingodya basi
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr Күн бұрын
Andale ndi athu oipa ndizoona ,,koma ndale za tonse alliance ulendo una akutionjeza,,,zinazi this current government akuyenera afufuze nkhope yamulungu,,,azidziwatu pena kuti izi ndizachabechabe Iwo eni adzafasotu!!!
@clairelewis5309
@clairelewis5309 Күн бұрын
Mwadzuka bwa Comrade Ntanyiwa from Nottingham.ndakunvani ,very clear
@harrisonkalimbakatha5339
@harrisonkalimbakatha5339 Күн бұрын
Comrade ntanyiwa umatiyimirira MCP ndi chipani chakupha ndipo sichizasintha mpaka kalekale ndipo atikwana anthu amenewa tikuona kuchedwa 2025
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Күн бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@MadalitsoTamayenda-ez5pj
@MadalitsoTamayenda-ez5pj Күн бұрын
Stay safe doctor ntayiwa ,, God protect yu whereever yu go kept up💯🔥💥
@YohaneChibweya
@YohaneChibweya Күн бұрын
Mwadzuka bwanji Ntanyiwa musaope mulungu amapanga njira popanda njira masalimo 35 komanso masalimo 91 Pali mmawu a chilimbikitso
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft Күн бұрын
MCP yonse ikupenga pano ?? Keep Resting well Klaus Chilima
@user-dq9oe8sp8k
@user-dq9oe8sp8k Күн бұрын
Long live bwana Ntanyiwa
@MerryWayson
@MerryWayson Күн бұрын
Mr Mtanyiwa End Mr Kalindo , mulungu sakutayani tikukuikizani m,mmanja mwa mulungu azikutetezani nthawi ndinthawi mukutiimilira ambuye akusungeni maka kukutetezani Kwa adani a MSP
@VirginiaPaulino-xc8ph
@VirginiaPaulino-xc8ph Күн бұрын
What either like or not ife nganganga pa Limpopo aziona agalu amenewa
@RuiJemusse-om7po
@RuiJemusse-om7po 20 сағат бұрын
Mulungu akhale Nanu amina Inu, wina asakutsekeni pakamaa, Mr Ntanyiwa and Mr Kalido go ahead
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Күн бұрын
Nawoso amanganya ali kwangwalala njekate kuno olo ndimantha omwe alibe adzikale ng'oma mudzazafe mukale amuyaya ku MCP pamosi ndichimimba chanucho pamosi ndi chakwela chigawenga chakumpa chilombo chigawenga chakumpa
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 Күн бұрын
Mungoti pheeee muone !!!! 🎉🎉
@SymonZemben-gd3ne
@SymonZemben-gd3ne Күн бұрын
Much love to you Limpopo FM with your team,Mr Born kalindo and Bakili TV we love you all keep it up leave long with 🐐🐐🐐
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Күн бұрын
Ndipo tikuziwa zinthu ndi BAKILI MULUZI TV bg up brothers
@frankdiyele7467
@frankdiyele7467 Күн бұрын
Truth shall prevail we have suffered enough abale
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js Күн бұрын
People are sleeping literally without food yet they can spend all this huge amounts of monies just to protect themselves.May God honestly judge them.God bless you in and may he always protect you
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu Күн бұрын
Manganya fiti yudasi chakwera pilato mwampha chilima wanthu tsogoro lathu tikulira lfe chakwera please usogoreri amatero manganya galu wanthu
@LunnahMtambo
@LunnahMtambo Күн бұрын
Comred munthanyiwa ndipo tili limodzi ,ndipo timakunyadirani chilungamo tichiziwa kudzera ku lompopo fm ndipo angero amulungu akutetezere
@user-ve4zn2ne1k
@user-ve4zn2ne1k Күн бұрын
😂😂😂morning Mr Ntaaaaaaaaanyiwaaaaaaaa we love you
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Күн бұрын
Mchewa watichitisa manyazi kwambiri zaonesa ngati achewa tonse ndi mbuli. Zandinyasa zedi.
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x Күн бұрын
Buddy Ntanyiwa 🖤💣 Keep doing the needful ♥️🙏
@HaliJana
@HaliJana 6 сағат бұрын
Zakhali n'goma panyopako wava ukuwasakilanji azako galu iwe osongomadya ndalamazo bwanji mimbayo ngati nyini yamako zakhali n'goma
@user-xk9vs9qc2s
@user-xk9vs9qc2s Күн бұрын
Fighting for the nation god never leave you like that freedom fighter mtanyiwa God protect you
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa Күн бұрын
Kodi a zikhale ng'ona mvuto lawo ndi chani?
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Күн бұрын
Mumuwuze Cilil Ramaphosa President wa South Africa kuti chakwela and his useless government ndi zigawenga
@LeonardMhone-cg1tk
@LeonardMhone-cg1tk Күн бұрын
May God protect you 2 Bakili tv and MR Ntanyiwa 🙏🙏
@memoryedwin
@memoryedwin 19 сағат бұрын
Mulungi azikudalitsani mr mtanyiwa
@user-xf8xb2iq9i
@user-xf8xb2iq9i Күн бұрын
Usi ndamuda bas tilire bwanji ifa ya chilima😢😢😢😢
@aligrayjeo1071
@aligrayjeo1071 Күн бұрын
Kodi nzotheka kuti tikhale ndi silent special forces Ku Malawi kuno tingopanga za MCP iyi basi chifukwa campaign nde sapangatu akapangila ground yake iti yoti akhale ndi chikhulupiliro kuti a Malawi akawamvetsera nyasi zawo mapeto Ake akachoka ataphwanyidwa ndi miyala ngati sakudziwa savage people
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki Күн бұрын
M'busa wa ntundu wanji opanda chifundo,opanda chisoni,, kukanika ku khululukila Chilima ngati adawalakwira
@jafalimussa5146
@jafalimussa5146 Күн бұрын
Wawa ma boss muwuze avesese azazolowela
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 Күн бұрын
Malawi army and police will side with the civilians on 10th July. You will see.
@user-yc3ik9dq3x
@user-yc3ik9dq3x Күн бұрын
Hopefully 🤞
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 Күн бұрын
Sizayiwalika ifa ya Chilima mpakana kale kale tizakhala tikukumbukira misozi yosantha
@leviouslongwe2950
@leviouslongwe2950 Күн бұрын
Angoni akulira zoona a Malawi, averwni zadutsa malire. Kunaphedwa ANTHU odziwika ndiponso amene amafunira Boma lathu zoyenerara. Kuphedwa Kwa: Mr.Albert Muwalo Mr. Focus Gwede Mr. Dick Matenje Mr. Sam Mpasu Mr..Saulosi Chilima ANTHU asanuwa anafa imfa zowawa a Malawi muli apa. Zowawa kwambiri.
@hudycorex1893
@hudycorex1893 Күн бұрын
More moto Ntanyiwa!!!
@Yungjoe786
@Yungjoe786 Күн бұрын
142 million for what?they're very stupidity instead of helping the needy with that cash.....mitu ngati zidebe
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Күн бұрын
Apa palibe kusunga chilungamo chakwela wapha chilima ndiathu 8 opanga cholakwa dyela
@africahasani-gl2nq
@africahasani-gl2nq Күн бұрын
Manganya kumupeleka chilima kwa pilato mmmmm wandikumudwitsa kwambili manganya
@ZionekaMember
@ZionekaMember Күн бұрын
@@africahasani-gl2nq kamba ka udindo
@user-rl8xs2kf1o
@user-rl8xs2kf1o Күн бұрын
Ndamuda manganya
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Күн бұрын
Limpopo ndiyakatundu
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z Күн бұрын
Tiyen tiyen ntanyiwa umandisangalatsa kwambili❤❤❤❤❤❤❤
@MisheckBandah
@MisheckBandah Күн бұрын
I love and I'll ❤ chilima for ever
@SangwaniKawawa
@SangwaniKawawa Күн бұрын
Keep us posted boss💯
@GeorgeChakuamba
@GeorgeChakuamba Күн бұрын
kkkkkkk😂😂😂😂Ntanyiwa yemweyo auzeni aMalawi chilungamo
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Күн бұрын
Iwe Zikhale ng'oma udzathera mmanja tsiku lina😂😂😂😂😅😅😅😅mimba yako
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Күн бұрын
Ndipo ndewalasa mtantiwa, fans yonse yokonda limpopo FM and bakili muluzi tv alongside Bon Kalindo, sitimagona and daily timakhala tikusakasaka ma audio anu and popanda kutulusa ma audio anu, amalawi sitimamva bwino mmitima mwathu . Tinasiya kumvera times , zodiac , mbc, mtv, luntha, nzeru, too many to mention
@StiveKantiki
@StiveKantiki Күн бұрын
Timakunyadilani bigy🎉🎉 km ndipemphe Nyimbo mwaika kumapetoyi yemwe anaimba tikuifuna ikuti matembelelo agwele pamutu pako kkk
@sarahlukongolo4901
@sarahlukongolo4901 Күн бұрын
Tinaona kale ife a usi kuti aliku mcp mmene amkayankhira pa Times nawo akolola akuona ngati chilima anali opusa eti
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn Күн бұрын
Zoonadi penapake Chilima anali osamva komanso osakhwima pa ndale chifukwa Michael Usi ankaonekeratu kuti ndiwa MCP and why Chilima bravery told Usi kuti akufuna kuthetsa m'gwilidzano, that's why he's died
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg Күн бұрын
Nkhan nd pa 10 July tikalile malilo achilima ku Lilongwe 🥺🥺
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 Күн бұрын
May God bless and protect you wherever you are comred
@cynthiataulo5211
@cynthiataulo5211 Күн бұрын
Usi amaoneka maso mwa mwa mwa kuchenjelesa. Ka snake kenikeni. Blood in their hands, angobwelesa matemberero to their generations to come. Anawo zizukulu zawo mapemphero awo azakhala abomination before God. Peace will be their enemy.
@lottiempata2487
@lottiempata2487 Күн бұрын
Don't be afraid 😨 for anyone else
@ElasonAimon
@ElasonAimon Күн бұрын
Mukuti imilira a Limpopo mulungu azikusamalirani nthawi zose
@dedzafranchise
@dedzafranchise Күн бұрын
much love to you comrade musadzamwalire
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed Күн бұрын
Mmmmm ay koma mcp yaonjeza nkhanza ndipo sitikuifuna.
@Jamesmwale-iz4ri
@Jamesmwale-iz4ri Күн бұрын
Ntanyiwa mukumatimvetsa kukoma za IFA chilima
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula Күн бұрын
Ine ntanyiwa tikungodikila 10 July kuti zalire bwino marilo achilima from kalonga
@user-wq9ex2sf3b
@user-wq9ex2sf3b Күн бұрын
God bless you
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Күн бұрын
Mmmmmm koma ndalamazi zimenrzi zokumachokera kuti? Chifukwa nde zikumadabwitsatu
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Күн бұрын
Amenewo tikumana pa 10 pano
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo Күн бұрын
Dziko lanthu la Malawi likamati lizilakhula chilungamo ngat Limpopo FM tikadalemela kwambiri koma eeeeeh
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Күн бұрын
Dziko lija azaza ndi afiti adyera, magazi mmanja
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Күн бұрын
Oyimba anayimba kuti amene udyanaye ndiamene azakupeleke. Manganya unapangilanji zimezi ndalama sizitha koma moyo wamuthu ukatayika kulibe kwina kokautenga muzivele chisoni ambuye achitenanu ndiye tikuwonelali 2025 ngati muzapitilize nawo azanuwo kuyendesa boma kupepela kwake kwantunduwanji munampeleka zanu chifukwa cha udindo kapena kungongola kwake poti anabadwa ndizose zomuyenela zelu chifundo kukongola komaso kuzichepesa nfikusasakha ntundu mulungu simuthu amatulusa zobisika lino ndiziko
@user-jy5ez2vq7k
@user-jy5ez2vq7k Күн бұрын
,ooooooo
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi Күн бұрын
comrad mungulu akuonjezele moyo
@ventonngwira
@ventonngwira Күн бұрын
BV
@MercyNyachi
@MercyNyachi Күн бұрын
Kodi ziko Lathuli lilindindala eti ife amalawi koma nkumwamwa tea sugar wake wa baks juice zoona achakwera inu😢
@mathewssiliya574
@mathewssiliya574 Күн бұрын
nkhani yofuta kuvesa kulingalila ndimalila 2024 zindizaiwala
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 Күн бұрын
Nsiku lina mlungu azakwiya nanu ndipo muzayaluka masana sanaa
@Nelliekaiya
@Nelliekaiya Күн бұрын
Ingoing'alulani azidzakugwilani atayaluka kale
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js Күн бұрын
God fights the battles
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ mtanyiwa iweyo usazafeyi😂😂😂😂 kusiteti hausiko wina akungonyeratu magazi uku 😂😂 mwazi wanthu amene aja ena akungosanza gamazi kkk
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki Күн бұрын
Mayi Yolamu Mulungu akudalitseni,akuyang'anileni,,akusunge moyo wanu,, chonnde chonde musavomele kuti a MCP akupakeni magazi a chilima chonde mayi, a MCP panopa ali so desperate thay can do anything as long as it can keep them from being exposed,, may yolamu a MCP akufuna opita naye,,akufuna akupakeni manyi,,,zikomo mayi inu ndi nakubaladi osati joyce Banda
@EllahEllah-hu7hi
@EllahEllah-hu7hi Күн бұрын
God have mercy
@SteveMamani-nv3mo
@SteveMamani-nv3mo 19 сағат бұрын
Nice work brother
@Uncle_B265
@Uncle_B265 Күн бұрын
Ndalama mmalao mothandiza a malawi Ali buzy kupanga hayala kuti azipha anthu osalakwa why koma
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp Күн бұрын
Power message
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Күн бұрын
Morning Mr Ntanyiwa
@OweniMalokooweni-es9qx
@OweniMalokooweni-es9qx Күн бұрын
Kwacha bwenji if kuno ku khonjeni kwa bhobho 🎉🎉🎉🎉
@StanzioDymon
@StanzioDymon Күн бұрын
Alekeni ana a agaluwa
@AbdulsartalSartal
@AbdulsartalSartal Күн бұрын
Khani imeneyo mumuuzenso Leyton mangochi chifukwa ndi kangaude amagothengeka ndindalama
@DevisonHala
@DevisonHala Күн бұрын
Mumajambula bwanji mtima umawawa nimafunitsitsa kukambako bos
@HaliJana
@HaliJana 6 сағат бұрын
A MCP NDIKUUZENI SIMUNGAWAGWILI ANTHU AWA KUFIKILA MUTACHOKA MBOMA ,
@BeatrizUlanda-ht2th
@BeatrizUlanda-ht2th Күн бұрын
Asirikari aja ayamba kuurura kuti anapasidwa ndarama zokwana 14mirioni
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Күн бұрын
Keep it up bro, ineso mkuona kut aUtm ayambe aziyimire paokha asakakamire kugwilizanoku ,mukakamira kumeneko ambiri akusikani
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Күн бұрын
Good Messnge Lipopo FM number one good
@wittinessnkhokwe
@wittinessnkhokwe Күн бұрын
Iwe Monica chakwela usatitukwanise ,mpaka tikutchule phunzo?khope yonyatsayo
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Күн бұрын
Km anthu kusankha akazi kunawadutsa kumanzere ...nkhope yopyelera.
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn Күн бұрын
Michael Usi wanted that position of vice president of Malawi than Chilima who helped MCP to come back to power after a lot of years
@vengesoko
@vengesoko Күн бұрын
Manganya ndi mthira kuwiri iiiih ,ndiye tawonani waphetsa mzake iiiihh😢
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Күн бұрын
NDIPO MADEMO AMENEWA AMVE NAWO KUWAWA MPAKA ACHOKE A MCP SITIKUFUNA KUTI AFIKE MU 2025 AYI USI NAYE NDI CHIWANDA
@marryphili5419
@marryphili5419 Күн бұрын
Ndipo imfa ya chilima yizakhara history mupaka kalekale ndipo ndi ana womwe sanabadwe azayiziwa history imeneyi
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Күн бұрын
Basi nkhani ndi pa 10 sitikuopa police tikaponda zimenezo pa 10 sikale tasala ndi 8 days so soon
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Күн бұрын
Ndipo kwambiri tu
БОЛЬШОЙ ПЕТУШОК #shorts
00:21
Паша Осадчий
Рет қаралды 7 МЛН
Please be kind🙏
00:34
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 188 МЛН
Deal mit US-Justiz - Warum Assange gerade jetzt freikommt | ZDFheute live
20:38
We need more Moor! | Kemferts Klima-Podcast | MDR
41:24
MDR Mitteldeutscher Rundfunk
Рет қаралды 2,8 М.
MUNTHU WAMULUNGU kuling'alura boma la CHAKWERA...lalephera
4:43
LIKI-LIKI TELEVISION
Рет қаралды 2 М.
The History of University of Limpopo
6:51
University of Limpopo
Рет қаралды 2,5 М.
#222 Neue russische Angriffsschwerpunkte | Podcast Was tun, Herr General? | MDR
1:08:16
MDR Mitteldeutscher Rundfunk
Рет қаралды 65 М.
Prepared Or Not - This Is Coming In JULY - Prophetic Message
21:08
Great Miracles Avenue
Рет қаралды 128 М.
ZOCHITIKA KU DPP🙌🙌🙌🙌
23:16
HOT 265
Рет қаралды 9 М.
Все мы немного НИКА!
0:17
Привет, Я Ника!
Рет қаралды 2,6 МЛН
Funny cat woke up early 😂👻🥳
0:38
Ben Meryem
Рет қаралды 12 МЛН
Все мы немного НИКА!
0:17
Привет, Я Ника!
Рет қаралды 2,6 МЛН
Достали существо из под земли
0:29
RICARDO
Рет қаралды 1,5 МЛН
Идеальный день ребёнка😂
0:11
МишАня
Рет қаралды 4,1 МЛН
Яйца мою 🥚🤣
0:37
Dragon Нургелды 🐉
Рет қаралды 1,6 МЛН