Limpopo maplan a UTM ofuna kuthetsa mgwilizana uja MCP yayamba kunjenjemela

  Рет қаралды 14,466

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

28 күн бұрын

Пікірлер: 51
@LeonardMhone-cg1tk
@LeonardMhone-cg1tk 21 күн бұрын
Mayi Patricia kariati, please musalore kutenga unduna timakukondana kwambiri and we don't want to loose you mum,
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 21 күн бұрын
Chikangawa Congress party mgwirizano uthe basi Mphaka sayenda ndi Khoswe
@susantembo2076
@susantembo2076 21 күн бұрын
Mayi Kaliati Chonde stand firm behind UTM. unshaken
@jamessheki4293
@jamessheki4293 21 күн бұрын
Gwirizano uthepo fisi ndi gwape sayendera limodzi😂😂😂
@user-qd7sz1pf1i
@user-qd7sz1pf1i 21 күн бұрын
Mcp ndale zawo akuti amapanga usiku
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 21 күн бұрын
Uthe!!!!!!! Ndatii iyaaaa chipani chakuphaaaaaaaaa
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 21 күн бұрын
inu mukangorora ma udindo amenewo ndinu amfiti komaso simukonda dziko lanu.apapa palibe kunyengererana ayi.Mgwilidzano uthe
@PatrickChirwa-cv5cd
@PatrickChirwa-cv5cd 21 күн бұрын
Mwayamba kunamatu a Ntanyiwa. Ma TV onse asonyeza an Anti-corruption ali ku Immigration.
@DavidJames-uv1jr
@DavidJames-uv1jr 21 күн бұрын
Uthe mgwilizano nthawi yabwino before next year
@yassinn5634
@yassinn5634 21 күн бұрын
Kuthetsa mgwirizano ndi MCP ndi advantage ya DPP
@ShakilahMbwanaa
@ShakilahMbwanaa 21 күн бұрын
Km mayi kaliyati Akane zimenezo aaaa anthu oyipa amenewo zopusa zimenezo
@Hassankazembe-d3o
@Hassankazembe-d3o 21 күн бұрын
Mai kaliat agwa mmayeselo apa koma to my opinion izi asalore ayi .....
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 21 күн бұрын
Chonde a utm musalore asiyeni a MCP akhale nao mai nduna ao kwatsala nthawi yochepa musangalala pompano
@user-hs4bm2yj8r
@user-hs4bm2yj8r 21 күн бұрын
Ndi khumbo langa Kuti a UTM musalolere zimenezo please chonde
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 21 күн бұрын
Musalore akweni maudindo amenewo paja anakuchotsani mwachipongwe agaru amenewo
@user-ht7vs3dp2u
@user-ht7vs3dp2u 21 күн бұрын
Osalora mukalora mwaitanira mtchetche pabara mumezedwano amoyo mutengere chisadzo Kwa chilima osangona chonde a UTM mukavomera mukavomera tiziwa kut chilima simumakonda mumakonda mwachinyengo don't do that please
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 21 күн бұрын
Uthebi basi
@FrankHaruni
@FrankHaruni 21 күн бұрын
Yeah mrs patricia you be follow mind of mr chilima
@user-yg2oi5ln7h
@user-yg2oi5ln7h 21 күн бұрын
Chonde chonde mayi kaliyati musalore unduna tikadari kukondani mama
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 21 күн бұрын
Koma nde uthetsedwedi Mai kaliyat musalore chonde mzimu wa Chilima ukukwiyirani
Zifukwa Zomwe Zingapangitse MCP Kuchoka M'Boma - Concerned Citizen
11:18
KU MCP KUSAMBWAZANA ZAMASEWERA AYI 🔥🔥🔥🔥
24:59
HOT 265
Рет қаралды 3,4 М.
Heartwarming Unity at School Event #shorts
00:19
Fabiosa Stories
Рет қаралды 25 МЛН
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Jimmy
Рет қаралды 39 М.
Olo Anthu A Ku Kasiya MCP Sakuyifuna - Comrade Ntanyiwa
21:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 24 М.
Game Changer akupeleka mau ku MCP mosaopa aliyense or kumangidwa
14:36
NTANYIWA WAPANGIDWA INTERVIEW LERO KUTI MUMUDZIWE IYEYU NDI NDANI
24:05
Kapitan Enteng - August 6, 2024 #KapitanEntengOfficial #IlocanoComedyDrama
16:55
DZWT 540 AM Dramas - Official
Рет қаралды 825
NKHANGA ZAONA ZIGAWENGA 6 ZABWELA MDZIKO MUNO KUDZAPHA KALINDO
12:03
Malawi Trends TV
Рет қаралды 8 М.
Nkhanga zaona Chakwera. Mzimu wa Chilima ukwazuza
31:56
Jay Kawere Mw
Рет қаралды 55 М.