Tsiku lina mulungu adzatsanjika dzanja lake lamukwiyo pamutu pa Lazalo Chakwera
@user-nf3ik3ff6y13 күн бұрын
Lipopo FM number one ❤
@victormunthali192412 күн бұрын
2 one bkmtv
@ImanRashidi-so4oo13 күн бұрын
Sangamakambilane zamzeru koma zompha anthu stupid mtanyiwa osaopa wanyamula ndembela pa Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 palibe amene angakumphe
@DorrahBanda13 күн бұрын
La 40 chakwela lizamukwanira
@MadalitsoTamayenda-ez5pj13 күн бұрын
😂😂😂 awuzen Ana Arira awa
@MosesKalenge13 күн бұрын
Atimaliza 💔🙌🙌🙌🙌
@KennedyKanyama-ce8lb13 күн бұрын
Always with u ntanyiwa. U r number 1❤❤❤❤
@zimmekapachika678413 күн бұрын
Boma lanji longopha anthu,tipheni dzikoli mutsale naro...munthu opanga zoipa amafa ngati galu nthawi yako ifika mr Chikangawa C
@inessmsiyambiri851712 күн бұрын
Mr chifunga chakwera
@MabvutoMichaelPanagona13 күн бұрын
Ndi boma lanji lopha anthu
@user-sm8gx4vf1v12 күн бұрын
Mfiti yamunthu chakwela chikangawa from ntcheu kwawo kwa skc
@FloridaMakwinja-eq2ek12 күн бұрын
Chakwera chikangawa ulibwanji ndi dziko lakolo Munthu wankhanza iwe
@MandalaChaona12 күн бұрын
Ayikeni poyera Brother Mtanyiwa Anthu oyipawa . God is watching
@JaneChimasula12 күн бұрын
A Malawi maso athu ayang'ane kwa mulungu basi chifukwa die amene azatimenyera nkhondo tili chete 😢
@RitaKainga13 күн бұрын
Mulungu wathu ndi wamoyo,khutu lake silogontha,mado ake samazinza,with sure awa etetezera ana ake
@PreciousHalias13 күн бұрын
Roud n clear from Sandton... Ntanyiwa 💪
@user-oc9vl9xz8e12 күн бұрын
Koma kaliyati ndi mzimayi osagwedezeka sangapange zopusazo kulandila ndalama ku MCP..ngati ndalamazo mai angakupaseni landilani after nguzangolengeza kuti mwatukuka my ngwilizanowo tizaone ngati azaime poyela kuzaitanisa ndalamazo
@KnowledgecGodwin-xo4pw13 күн бұрын
Big up me Mr Ntanyiwa
@RobertChimenya12 күн бұрын
Asilikali akumalawi amalandira ndalama zaulere ndiadyera kwambiri nchifukwa chake Ali mbali ya chipani osat kuteteza nzika tiyeni tizaona ukazatha udindowo
@user-wb3us4pg4b13 күн бұрын
❤❤❤ comrade ntanyiwa
@PaulDaka-dc3re12 күн бұрын
Ndi moto wawa👏👏👏
@PeterMphanza11 күн бұрын
Nice job comred kp it up
@FrankWaresi13 күн бұрын
Tiyamika mulungu osaopa kulibe wamuyaya
@MandalaChaona12 күн бұрын
Koma Mr Lazarus Chikangawa mwaonjeza,muphe anthu onsewo muwaphe akulakwirani Chani, kukana kudzudzulidwa pa kupha anthu 9 eeeeee Koma ndinu Mulungu wachiwiri,mwafikapo 🔨⚒️⛏️
@doreenkaliati316613 күн бұрын
Ambuye sakhala chete pa nyengo zathu Mulungu wathu ndi wakumva ndithu sagona turo ai
@DorrahBanda13 күн бұрын
Zoonadi ndipo kwambili
@CHIWSABINYAMBOSE13 күн бұрын
Izi ndizoona amuhone anatengedwa last week kuchoka kuno kumzimba boma nkupita nawo ku Lilongwe kuja kunali born kalindo 😢😢koma ngati atamuphe mutiva ife kuno achina mzimba
@chrissyamanda551012 күн бұрын
Mmmmmm koma anthuwa ndi asatana eti Nde amawatenga amhone kuti alakwanji mmmmmm ayayayaa atasatu atasa anthuwa
Upo wawo sungapindule chifukwa imfa amaivomeleza ndi Mulungu..I can tell you kut Chakwela mtendele alibe ngakhale kadontho mkat mwa moyo wake..mwadzi wa Munthu ndi ovuta😢😢...dekhani muone zomwe zichitike
@KunyengaMoyo13 күн бұрын
We're ready tiyeni pamseu
@NijomanSimarose12 күн бұрын
U are doing good job bra
@ConfusedAstronaut-qv6wq13 күн бұрын
Zoonadi awulureni ,escipeciaally, yudas ameneyu,chigawenga chowopsachi.ndipo osawopa mpaka chilungamo chitawoneka basi. From ndauza village.