No video

Limpopo Ntanyiwa watulukila ndi zomwe wasokola lero pa 18 July 2024

  Рет қаралды 31,398

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 137
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 Ай бұрын
Inetu m'mene ndayambira kusaka ya lero 😂😂😂😂😂,, ndie apa ndangoti gululu ndi limpopo fm ya fresh 😜😜😜😜
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Limpopo FM ndi Comrade Ntanyiwa program yake ya Nkhanga Zawona ndi FIRE🔥 🔥🔥🔥🔥❤
@SumanJames
@SumanJames Ай бұрын
Ulemu amtanyiwa
@SumanJames
@SumanJames Ай бұрын
Chisankho chikuchedwa
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
@@SumanJames Ndipo kwambiri brother chisankho chikuchedwa ife tikufuna kuwona Zina
@SydneySibande-z6k
@SydneySibande-z6k Ай бұрын
Kkkkkkl aNtanyiwa u àre aLinguistic Talker now, I salute u
@DanielChisaka-tg1il
@DanielChisaka-tg1il Ай бұрын
Ndimakunyadilani Anyamata a Limpopo FM mumakamba zowonadi
@CHIWSABINYAMBOSE
@CHIWSABINYAMBOSE Ай бұрын
O my vote is still waiting for you UTM🎉
@AdidasPuma-lu8sz
@AdidasPuma-lu8sz Ай бұрын
Utm yake iti yamakanduro kapena yamithiko😂😂😂😂😂
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Nyimboyi imatalika kwambiri,,timafuna tinve zomwe mwabweretsa osati nyimbo
@AchinaKellz
@AchinaKellz Ай бұрын
Akainde ndiopusa why you allowed evildoers to enter your country while innocent human spirit are crying in the grave yard Malawian are crying and people are dead don't forget Malawi Zambia Zimbabwe is one country 😢
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Ай бұрын
Mtanyiwwa osawopha osavowonka ndive amalawi mtanyiwwa ulemu wanuw you welcome by lipopo 😅
@ThandiMbewe
@ThandiMbewe Ай бұрын
Momred ntanyiwa umakwana❤❤🎉
@MandalaChaona
@MandalaChaona Ай бұрын
Tiye nawo Mchimwene NTANYIWA. Kuziyika poyera Amalawi aziziona. Keep it up Brother from Limpopo FM
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf Ай бұрын
Zoonadi Achimunthuwo apume asiile enawo apikisane iwowo anatsazika kupita ku TONSE
@JahmielIshumael
@JahmielIshumael Ай бұрын
Ulemu wanu mntanyiwa
@AnussaAlli
@AnussaAlli Ай бұрын
Ndmakunyadlani Anyamata a limpopo FM mumakamba zoona zokhazokha❤❤❤❤❤
@AjibuTwalibu
@AjibuTwalibu Ай бұрын
You are welcome Mtanyiwa
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope Ай бұрын
1 billion US dollars ife tikuvuti Kugula zinthu modula ayi ndithu mulungu amukathe ndi chimphaliwali Wali chakwera ndi banja lake lonse
@MervisYobe
@MervisYobe Ай бұрын
Eti Inu munthu woyipa uyu mmmmh
@MikeMapemba
@MikeMapemba Ай бұрын
Mumakwana aise umatiuza zobisika ndipo ukutitsekula m'mutu big up tilinawe limodzi
@UsenLashid
@UsenLashid Ай бұрын
Madem amenewa achotse onse athu akuba awa president ndi nduna zawo
@MphatsoChangata-ti9ru
@MphatsoChangata-ti9ru Ай бұрын
Timayambira kudzimva pano kenako kwinako
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri ditu esh
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc Ай бұрын
Wise man
@AnockyDavidd
@AnockyDavidd Ай бұрын
Congratulations Limpopo FM were looking forward malipoti andege from there.
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ntanyiwa katundu uyu MBAMBANDE ndi BAKILI MULUZI tv, tikuziwa zisisi zambiri pamalawi pano
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d Ай бұрын
Limpopo fm number one oyipa apye mtima
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Lipopo FM number one
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp Ай бұрын
Ndalamazo zilikuti Abale Ife tikatape nawo
@benjaminjobo3525
@benjaminjobo3525 Ай бұрын
Big up Mr Ntanyiwa🔥🔥🔥
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp Ай бұрын
Ndipo zoona apite akayndele anthuwo DPP boma
@MariaWilson-gq8st
@MariaWilson-gq8st Ай бұрын
Mumakwana musasiye ziyakhuoan tizizziwa Ife zomwe zikucitikazi
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana Ай бұрын
Koma a ntanyiwa ayi zikomo ❤❤❤❤
@braveglorymwanzagolah4899
@braveglorymwanzagolah4899 Ай бұрын
Best TV
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb Ай бұрын
Limpopo FM radio station Inu mukunenadi zoona kuti anthu tisamvomele kuchotsa lamuro loti 50+1 isachotsedwe ndipo izachotsedwe 2025 TIka voter 🤣🤣🤣🤣🤣👏👏👏👏kuchoka kuno ku South Africa port Elizabeth
@Donvaga
@Donvaga Ай бұрын
Limpopo FM with comrade ntanyiwa 😊
@Chrissyluwe
@Chrissyluwe Ай бұрын
Limpopo more 🔥🔥🔥
@MaggieChiomba
@MaggieChiomba Ай бұрын
Bwana
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Ай бұрын
Iphembelele Limpopo ipase moto😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@AllieFunaya
@AllieFunaya Ай бұрын
Katundu wa boma watulukira
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x Ай бұрын
Limpopo FM ♥️🔥🔥
@MarthaJulianaKachingwe
@MarthaJulianaKachingwe Ай бұрын
Limpompo FM Woyeeeeee
@aubreymagombo5907
@aubreymagombo5907 Ай бұрын
Keep fire burning comred ntanyiwa mumatha inuyo
@FatimaHanifu
@FatimaHanifu Ай бұрын
Following you ntanyiwa ❤
@TressLuka
@TressLuka Ай бұрын
Mtanyiwa ndi 1. Tiuzeee 😅😅😅 Chikangawa Party 😢😢😢
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Chakangawa party yatchukatu kkk
@ChisomoJinard
@ChisomoJinard Ай бұрын
Amtanyiwa kod ndinu akwathu ku nkhotakota 😂😂😂😂😂😂
@MalawianMediafm97
@MalawianMediafm97 Ай бұрын
This is comred ntanyiwa on Lipompo FM kuzangoturikira ndi nkhanga zaona chaka chake ndichino
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Kwavuta kwambili kkkkk
@BrilliantNyirenda
@BrilliantNyirenda Ай бұрын
Tili makola a Ntanyiwa 🤸
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi Ай бұрын
Wellcom Ntanyiwa.
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 Ай бұрын
Limpopo ndiwedolo umangalula chulungamo
@EllinaBitto
@EllinaBitto Ай бұрын
Mtanyiwa ukamayankhula penapake ka relief kakumakhalamo mumtimamu pa imfa ya A Chilima😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@user-sx7mr7gr7n
@user-sx7mr7gr7n Ай бұрын
Ife kunoso ku Qatar muzitipasa moni kukhala osamvela Limpopo FM sitimva bwino
@CathrineBizza
@CathrineBizza Ай бұрын
Utm my vote
@EnockPhiri-ho7zb
@EnockPhiri-ho7zb Ай бұрын
Limpopo
@FaheemChipojola
@FaheemChipojola Ай бұрын
Angoona kuononga ndalama koma mangochi sangavoteledwe amta mangochi ndi ya DPP ndipo ndlinganga ndi dpp❤
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri tu adyeledwa amenewa kkk
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg Ай бұрын
Yomweyo chikangawa
@lovenesskampira
@lovenesskampira Ай бұрын
Musamasowe a mtanyiwa mukamasowa tsiku langa limada
@CharlotteMushimiyimana-g6b
@CharlotteMushimiyimana-g6b Ай бұрын
Yomweyo abon kalindo auze amalawi 3:52
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb Ай бұрын
DPP 2025 must be back to government 😂😂😂😂😂
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri tu kkk
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
boma la zigawenga ili kuyaluka kulipo sathawa chakwera watenga mbiri yokupha wayaluka ndikupha
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm mavuto kwabas
@RaymondManda
@RaymondManda Ай бұрын
Ndikufuna contact ya comrade Mutanyiwa ndili ndi uthenga oti ndipereke kwa iwo
@BlessingsBanda-ol2pg
@BlessingsBanda-ol2pg Ай бұрын
Mumatipanga alipopo
@FrancisDominic-w1s
@FrancisDominic-w1s Ай бұрын
Mwasowa ife tulo silimabwera kusasaka Limpopo kuno ku cz
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 Ай бұрын
Ndipo kusaka simuzaoneka kkkk ndakupezani koma smiling All the way,,its nkhanga zatong'ola for me😅
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri kkk
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 Ай бұрын
Palibe zochotsa munthu ku utm tibulanapo
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Ndi zitsiru aziwachosa anthu mu UTM ngati chipani anayamba ndiwo?? Zianthu zoyipa izo
@TroubleMuthala
@TroubleMuthala Ай бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@RitaKainga
@RitaKainga Ай бұрын
You are the concollars guys
@MandalaChaona
@MandalaChaona Ай бұрын
Koma Achimunthu Banda mukhalike nokha munasanzika kupita kuli mphika wa makobili lero mukubwereranso hmmmm koma dyera linali 😂😂
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 Ай бұрын
Chimunthu Banda asalowe through DPP ticket. Anathawa kuDPP kale.
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Ай бұрын
UTM yamithiko 🤣🤣🤣🤣🤣
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Kkk
@user-st1sn7cr7d
@user-st1sn7cr7d Ай бұрын
Bambo asikono 😂😂😂😂😂😂 munyatu takutulukan
@Martha-m6e
@Martha-m6e Ай бұрын
Usi ndi enawo apenga basi.muwona mwazi ndiovuta.
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri
@RhodaBandah-sh1ir
@RhodaBandah-sh1ir Ай бұрын
Mizimu yochuluka ikudandaula ....mcp muzafa imfa yowawa
@user-gp2zp2dj1w
@user-gp2zp2dj1w Ай бұрын
UTM u have my vote
@beatricenkhoma1109
@beatricenkhoma1109 Ай бұрын
❤❤
@AdidasPuma-lu8sz
@AdidasPuma-lu8sz Ай бұрын
😂😂😂 akuti yomweyo galu iwe 😅😅😅 koma akulu inu 😂😂😂😂
@RashidSaid-lk6bb
@RashidSaid-lk6bb Ай бұрын
Achimunthu Banda asazimvutitse kubwelera ku DPP and sitikuwafuna ai yemwe adatuluka adatuluka basi Mr ur not welcome to DPP 😂😂😂😂😂
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Wakhaula ameneyu kkk
@CatherineKamsare-cy3yo
@CatherineKamsare-cy3yo Ай бұрын
Adzafa imfa yowawa agaru amenewa
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o Ай бұрын
Ok bwana
@user-nz5jh1yk1g
@user-nz5jh1yk1g Ай бұрын
Malawi wayaka motooo
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Ай бұрын
Chakwera ndichimuthu choipa kwambiri anapha Chilima ndi Kasambara zisakho sangawine zosatheka 💔💔💔💔 kumachende kwake
@MervisYobe
@MervisYobe Ай бұрын
Kkkkk
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri
@ChisomoBanda-g5s
@ChisomoBanda-g5s Ай бұрын
👍👍👍👍👍👍🙆🙆🙆🙆🙆🌹🌹🌹
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o Ай бұрын
Yomweyo pumbwa iwee 😂😂😂😂😂
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda Ай бұрын
Anya a mcp awa azinyera ayaplmbankupanga zosaziwika
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Ай бұрын
Pafikilapa kungowauza achakwela kuti comryde akukhala uku mundipase 100 million atha kukupasa chifukwa sakugona Nanu tulo
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo Ай бұрын
Chimunthu Banda akuthawa😂😂😂
@IssahAluba
@IssahAluba Ай бұрын
Khanga zaona chakwera akuba anaake
@user-oj2jr6kf9c
@user-oj2jr6kf9c Ай бұрын
Lelo kuchedwa kumeneku bwanji????
@PetroMatias
@PetroMatias Ай бұрын
50+1 ilipobe itha 2025
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Thiko. Komweyo
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope Ай бұрын
Utm ya thiko yomweyo😂
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Kkk
@JoelKananji-f2o
@JoelKananji-f2o Ай бұрын
Umakwana
@JohnAsendi
@JohnAsendi Ай бұрын
Achithu banda dyera timakuuzani musasatire ndalama sikutikumbukira uku tsopano🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌
@user-rl8xs2kf1o
@user-rl8xs2kf1o Ай бұрын
Palibe zosintha malamulo 50 +1 m ' bwalo chikangawa wagwa nayo basi 😂😂
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Ndipo kwambiri tu kkk
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Ife anyamata support yathu ndiya ma candles ikunena chilungamo, za usi zama drama ife ayi azikapanga ku mcp
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko Ай бұрын
Komaso olimbana ndi ntanyiwa awona nyekhwe 😮😮
@EnthusiasticMountain-xd7vn
@EnthusiasticMountain-xd7vn Ай бұрын
Zovuta kobasi
@PaulMwachande
@PaulMwachande Ай бұрын
Comred ing'aluleni bas makwacha apezeka bwanji??pazambia anthu oyipa awa mmmmmmm ayi 2025 ikuchedwa kukwana bwanji tichose nyasi zimenezizi bas
@TimvenjiMpoma
@TimvenjiMpoma Ай бұрын
Tili Mano kuvela mwachidwi
@HaliJana
@HaliJana Ай бұрын
TAMALANDILANI NDALAMA ZO MUZIWAUZA KUTI TIONANA 2025 OKAY
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr Ай бұрын
Malipilo okumpha a chilima. 😮.ndalama zikungoonongedwa koma ife tikugula zinthu mo dula ferteleza odula koma mulungu akuoneni achakwela
@MervisYobe
@MervisYobe Ай бұрын
Madandaulo anthu sapita padera sure
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Ай бұрын
​@@MervisYobendipo zowonadi chilichose tikugula modula koma ndrama kumangomwaza ife tikumvutika
@BwanaGD
@BwanaGD Ай бұрын
Chitani machawi a dpp mukawone ku nkhotakota chikagawa wavuta uku koditu akupaga zokanika zonkhazonkha akugoti akatele agwidwa hiiii makendulo tiyeni nawoni zipalapasika zonkha
@user-ky8eq5ek1p
@user-ky8eq5ek1p Ай бұрын
Akamapasidwa ndalamozo Feteraizer Akugulidwa k4000:
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
Zomvesa chisoni kwambiri mmm kumalawi amwene mmm
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi Ай бұрын
asakhe wina oyimila
@EnthusiasticMountain-xd7vn
@EnthusiasticMountain-xd7vn Ай бұрын
Malawi okomela tonse uja🤒
@MonicaSembo
@MonicaSembo Ай бұрын
Eshi
Touching Act of Kindness Brings Hope to the Homeless #shorts
00:18
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 17 МЛН
1ОШБ Да Вінчі навчання
00:14
AIRSOFT BALAN
Рет қаралды 4,4 МЛН
Секрет фокусника! #shorts
00:15
Роман Magic
Рет қаралды 60 МЛН
Moroadi Cholota's urgent application challenging her arrest
2:04:15
NRF Awards Sun City
2:19:01
National Research Foundation (South Africa)
Рет қаралды 14 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
Touching Act of Kindness Brings Hope to the Homeless #shorts
00:18
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 17 МЛН