M’BUSA EMWE WAZUZULA BOMA LA ACHAKWERA UJA NDI UYU NDIPO ANAYANKHULA MOSAPSYATILA MAU CHONCHI

  Рет қаралды 29,908

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 57
@BrightZionga
@BrightZionga 2 ай бұрын
Azibusa opanda mantha keep it up ❤❤❤may the good Lord bless you
@ChimsyUlemu
@ChimsyUlemu 2 ай бұрын
Amen abusa much appreciated for ur message osaopaaaaa osafooka
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Kkkkkk mo fire munthu wamulungu auzeni Zowona afitiwo
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
🔥🔥🔥💪💪💪
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Mau ngati amamwa kachaso chisilu ndi chakwera wakoyo
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 mcp yabalalikadi eishiiii kupha Chilima imene ija ndi Mistake yaikulu heavy
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 2 ай бұрын
Exactly bro
@MasChisi-v4l
@MasChisi-v4l 2 ай бұрын
Ndiye mwati adzudzula chakwera?
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Chisilu ichi ndipo ndiamene amakonza ziwembu zonse zikuchitika mmalawi muno ku mcp
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Tamumveni mau ake osasa ngati amamwa kachaso chisilu cha munthu
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
Ngati boma likulakwitsa kuli bwino kuli zuzula otsaliopa this is democracy,,zachamba aii
@brightcharlie2396
@brightcharlie2396 2 ай бұрын
Vuto la Ife a Malawi kukoka nkhani eeshiii mpaka mufuna a phedwe bas
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Galu ameneyi
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 ziriko
@temwarachaelkhonje3733
@temwarachaelkhonje3733 2 ай бұрын
Boldness at its best
@Mazzy-zu5fo
@Mazzy-zu5fo 2 ай бұрын
Chimwendo Banda anganene chani kudziko lamalawi ndikumva mfiti yachikhalireni abusa munalalika mulungu akudaliseni Chilima anatisiira mau osaopa osafooka tizafera mbendera yamalawi
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 2 ай бұрын
Chimwendo banda machende ake inu simwapha anthu pa 10 june dzausilu
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 2 ай бұрын
Koma iwotu mademo ndi mademo umenewo ndi umodzi akufuna ayakhule kuti chani makamaka kapena zimenezo aziwa liti. Iwo m'mene amanyozela ma speach awo alipotu kodi
@malikoezala
@malikoezala 2 ай бұрын
Upiteso Kwa skc
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Achimwendo mumayankhula ngt munthu wa mzeru koma zimene mukuyankhula pamenepo zo simumadzikwanilitsa inuyo so ndamene mumatsogolera zosankhana mitindu
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 2 ай бұрын
Aliyese watopa mu dziko muno ndi ulamuliro wa Chakwela ndi chipani chake chopusa cha mcp
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 2 ай бұрын
Koma galu uyu wausilu bwanji
@AndrewMagombo
@AndrewMagombo 2 ай бұрын
Boma lopusa molomoti ankhale buxy ndi mabvuto a mlw km ayi kumanga anthu
@hesbaluku7281
@hesbaluku7281 2 ай бұрын
Aaaa mesa anayambisa ndiyeyo zot achewa alipo 14 mita aaaaaa mboli yake😢
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 ай бұрын
MCP ndi chipani cha makape bwanji akuyankhula ngati anthu akuwanyonza pamene anthuwo akuzuzula nkhanza, umbava, kupha anthu,mabodza ndi tsankho lomwe MCP ikupanga.
@retirementtoafrica
@retirementtoafrica 2 ай бұрын
Kudulira ma speech panjira?
@amoschataika7440
@amoschataika7440 2 ай бұрын
Chilungamo chimawawa palibe chomwe walakwitsa m'busayo.
@ModicaiChirwa
@ModicaiChirwa 2 ай бұрын
Chimwendo Komanso MCP yonse ndiyoipa kwambiri ,chifukwa ndiichi MCP yagula mifuti 400 yophera Malawi chifukwa cholidzudzula bomalawo lomwe laononga Komanso kupha Komanso akulamula dziko kamba Koti anagwiritsa ntchito anyamata omweo kupanga ziwawa ndikunyoza atsolleri azipani Zina lero akuononga ndiwo ndiye zawaophya anthu opanda umunthu awa amcp muchoke basi mukuyambitsa nkhondo mdziko inuyo mukumayankhula Kuti mupha wanthu inuyo pomwe anzanusaanayankhuleko choncho
@EdisonNakulenga
@EdisonNakulenga 2 ай бұрын
Auzeni asatanawo
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 ай бұрын
Iwe Chimwendo Banda pamtumbo pako ndithu zoti munapha Chilima aliyese akudziwa
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 ай бұрын
Ndichitsiru chimwendo..mutu ngat bans
@WedsonVinkhumbo-q9l
@WedsonVinkhumbo-q9l 2 ай бұрын
Mmmmm sititopa
@christopherbanda4698
@christopherbanda4698 2 ай бұрын
Iwe chimwendo get out
@Cathy-oc7vd
@Cathy-oc7vd 2 ай бұрын
Akufuna kutamidwa
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Chimwendo iwe ndi galu kwabasi ngati mukuchita zoipa athu asazuzule pakanwa ngati pa toilet
@MasterMwandira-q8v
@MasterMwandira-q8v 2 ай бұрын
Chimwendo kazidyelanithu ndalama za mcp, chaka chamawa mkakhale pansi
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
@@MasterMwandira-q8v muziti ndi eakundende
@SammyKasolota
@SammyKasolota 2 ай бұрын
Kwachemeratu
@inamrigala
@inamrigala 2 ай бұрын
Olo amusake km wa wakamba zowona chimwendo ndi nkumba
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 2 ай бұрын
Azibusa ngati atopa asiye ubusa akalowendale, maka azibusa a ccap mumaonjeza dyela.
@VenançioZocueza
@VenançioZocueza 2 ай бұрын
Ngakhale nthawi ya David anadzudzulidwa ndi mneneri atagona ndi mkazi wa uliya muhitu
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 2 ай бұрын
Uchitsiru si Ndiwe uja dzana umanena ku achewa mulipo ambiri
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 ай бұрын
Inu ndinu achitsiru palibe chamzeru mmayakhula pamtumbo pako ndi Chanyera wakoyo anthu amagazi inu
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Kkkk awudze munthu wa. mulungu
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf 2 ай бұрын
Chimwendo kungokula kukamwa koma palibe chanzeru chomwe anganene iyeyu akuti umodzi pomwe akupha anzawo
@HarriePearson
@HarriePearson 2 ай бұрын
Iwe wopusa kwambiri chimwendo
@BrightZionga
@BrightZionga 2 ай бұрын
Chimwendo ndiwe kape
@SammyKasolota
@SammyKasolota 2 ай бұрын
Kkkkkkkkkkkkkkk
@RomeoLapken
@RomeoLapken 2 ай бұрын
A malitili amakhala okuba?
@ChizymanJason
@ChizymanJason 2 ай бұрын
Kma ya
@YoungMwacho
@YoungMwacho 2 ай бұрын
The whole synod attending such stupid gatherings which are pure political. A matili anakhala akuba, these people were thieves. Waste of time and resources.
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Chimwendo banda chisilu cha munthu
@YoungMwacho
@YoungMwacho 2 ай бұрын
Buzi zokhazokha
@KulinjiGoodsonnkhoma
@KulinjiGoodsonnkhoma 2 ай бұрын
😂😂😂😂 zavuta basi
@JamesMopiha
@JamesMopiha 2 ай бұрын
Ey
@ChizymanJason
@ChizymanJason 2 ай бұрын
Umodzi ndikupha anthu 9?
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 2 ай бұрын
Chimwendo banda zimachende zako
Inside Out 2: ENVY & DISGUST STOLE JOY's DRINKS!!
00:32
AnythingAlexia
Рет қаралды 18 МЛН
ДЕНЬ УЧИТЕЛЯ В ШКОЛЕ
01:00
SIDELNIKOVVV
Рет қаралды 3,9 МЛН
😜 #aminkavitaminka #aminokka #аминкавитаминка
00:14
Аминка Витаминка
Рет қаралды 491 М.
Миллионер | 1 - серия
34:31
Million Show
Рет қаралды 2,8 МЛН
MFUMUKAZI 9 OCTOBER 2024 PA TIMES TV
28:46
MALAWI 265
Рет қаралды 4,2 М.
Akweza cement ndi mafuta ophikira kuti apeze ndalama za campaign
9:31
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 42 М.
Inside Out 2: ENVY & DISGUST STOLE JOY's DRINKS!!
00:32
AnythingAlexia
Рет қаралды 18 МЛН