U are right zimene wanena.....anakakhala kuti ndi iweoyo chimwendo unali mu ✈️ ndi anthu ena Chilima anakakhala okathandiza anakakhala SKC.....why coz anali ndi umunthu....ndeeee who did ever did tha to Chilima ili ndi dziko ndipo limatembenuka
@HalimaMussa-j6t2 ай бұрын
Mulungu sachedwa azawaika poyela dziko lizadziwa
@jameslifah79094 ай бұрын
Strong woman ever,you stand by the truth. Let love lead❤
Well spoken mama and we understand every single point of ur message and keep it up you're opening our brains
@Yungjoe7864 ай бұрын
I salute you aunt The TRUTH eish
@LukasBamus4 ай бұрын
Always on my mind uncle God bless you wisely and continue to reviled more sicrets in this world
@WelemuSayizi4 ай бұрын
Koma azimayi ngati amenewa ndi mwana wathu koma Malawi ndi yodala mayi uyu ngakhale azibambo 10 muli mu mcp simungafanane naye iron lady more fire!!!
@ROSELIKHWAKHWA-y7e4 ай бұрын
More 🔥❤
@SadrackTseka22 күн бұрын
Abusa okhumudwitsa okhumudwitsa dziko lonse lapansi ndiye ndi achakwera dyera khwidzi kuzikonda Dumbo zadzadza mwaiwowa kd ndikufuna udindo kokhakokhako mpaka pa menepo speech on mama God protect you
@AllanTamula4 ай бұрын
Your comments towards Malawi politics is just great.
Chimwendo banda chakwera kunkuyu namajekete wankulu wa army manganya athu amenewa ndi amene anapha athu onse 9 aja koma thawi yawo yatha sopano mcp yamagazi crocodile 🐊
People like this woman must be abandant, keep it up mama
@giftkanjuchi-qm8hf4 ай бұрын
It is making sense mama ndinu di achipatala
@FelistasNkasalaMakumbo4 ай бұрын
Love you mama mumatiyimirira❤❤❤❤❤
@atupelemposa47864 ай бұрын
Sanamukondepo chilima ,they just use him to remove DPP, Munthu woti ukumukonda or atadwala umathamangila nayo ku chipatala .
@GlynLumbe3 ай бұрын
Muti ineyo Ku Namwera Ndiye kwathu kumudzi kumachemba MOTi timatsikila galimoto pa chesailesi kumapita ku machemba tiyakhulileni Kwa Anthu wathu osowa chikondi wa kuno
@ErnestChansa4 ай бұрын
Point point anamumpha chakwela ndi fit anthuwa a MCP
@yassinn56343 ай бұрын
Point of Correction Sisy Mtambo sanachite kuchoka yekha mboma anachita kumuchotsa.
Big up mama, please tayakhuleni madam Mary ngati nkotheka achitsogolere chipan i
@EliasManthenga4 ай бұрын
Mummy mukazafika ku South Africa zandizwsen tizadye kota limozi, kuima pa chilungamo amalawi aziwe ❤
@MchachaGoodson4 ай бұрын
Keep doing good work yourselfless be blessed.
@ThomasNChinseu4 ай бұрын
Nice touching to u nurse in USA keep it up
@IvanRoux-vl8gu3 ай бұрын
That's true negligence
@danielswaleyi97763 ай бұрын
Well articulated, I have learned slot from you sis.
@Halima-i4x4 ай бұрын
MCP ndichiman chakupha chifukwa chilowelen MCP boma onan Malawi anthu mene akumwalilila eeeee chakwela akuononga dziko labwino bwino ndi 2 😢😢😢 koma one day is one day
🤣🤣🤣🤣 Koma ndi osekesa kwambiri apa Pali cha nzeru chilichonse chomwe munthuyu wayankhula, even izizi sizikupeleka evidence or proof yoti munthu anaphedwa kapena Kuti inali movie
@YammsyZebron4 ай бұрын
Ndipo onse anapanga izi apenge
@AdizzMadizo4 ай бұрын
MCP ndi anthu akupha zigawenga zakupha palibe kuchosera ayi
@FebbieNjewa-g3k4 ай бұрын
Sure sure Abiti tell them ,,God bless yu more
@MussaChilembwe4 ай бұрын
Komaso anachita kuphedwa athu onse aja ndege sinagwe ayi koma anachita kuphedwa basi straight point basi chakwera anachita kukonza kuti afe athu onse aja anapha basi chakwerayo
@RobertLuka-wy9cl4 ай бұрын
Auzeni mayi achimwendo ndi chitsilu chopusa
@jameswajumpha67904 ай бұрын
Dan Lu naye imukhuze nkhani iyi kulondola kosekose athu osakhazikika😂😂😂😂
I rember 2012 mwana wanga anali Al ndi 1year.anasowa koma mizionse unatuluka kufunafuna mwana ena kumalowela kupolisi ena kwa chairman.ena kulengeza ma video show mpaka mwana anapezeka ndiye vp akalekeze kufufuza Ati ayi kwada nyelo zamawo
@RidgieGondwe2 ай бұрын
Well done mamie
@AlihIbrahim-s7v4 ай бұрын
Athileni fire,,,,,,,,zitsilu za mcp plan yawo sanayitenge bwino amawona ngati nthawi ya kamuzu ino,,,,,this is new generation yopita ku school,,,,komaso Dr Muluzi anatimenyela nkhondo yolankhula pazomwe zikuchitika,,,,,,,,,,,,
Yes timukamba kumene anafa imfa yowawa SKC ndi ena wonse aja ulemu wanu mama
@IvanRoux-vl8gu4 ай бұрын
Thats true Mam
@JonathanMtambo-w6e4 ай бұрын
Nkhani ya chilima sii, zatha pokapoka chilungamo chitabwera poyera
@AnniePetro4 ай бұрын
Chilungamo mama
@KhumboNyerenda3 ай бұрын
Good message mum
@wonganimwase98813 ай бұрын
Even if a child is late coming from school, the parents don't wait for an hour to atart searching,, talk less of saying that the search will resume the next day. Every flight has a manifest and a whole pesident couldn't didnt have the correct list of passengers on the plane.
@NickUpoche4 ай бұрын
Keep it up mm,proud of u
@dewasicmalunga33744 ай бұрын
I salute you kusyeto wakumangwetu
@PercyRoos3 ай бұрын
That is true mamma
@QueenMoses-c1n4 ай бұрын
Big up mama u really encourage us
@gladysmanthimba78514 ай бұрын
Abiti ndinu fire. Mau opanda chigamba. Zikomo kwambiri tili nanu limodzi
Eeeeeeeeeeeeh Koma yaaaaa ine ndili pheeeeee ena kuseliku akungosegura mmimba
@TITANIMATOLA3 ай бұрын
True mama osaopa osafooka
@ÑaloWemba2 ай бұрын
Wow 😮 chilungamo ichi
@HolmanDazah4 ай бұрын
Anyani a MCP a mfiti, sanankonde spirit yao ndiyakupha basi ndipo ife a Ntcheu zikutiwawatu, DPP inamusula Bhiyeni mundale ndipo, you didn't know kuti end of the day 2025, chilima internally amaganiza alliance ndi DPP.