KOMA CHIMWENDO BANDA NDI PETER MUTHALIKA ANAMUPUTA CHANI? TAMVANI ZOMWE WAYANKHURA KU NSANJE LERO

  Рет қаралды 10,763

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 178
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 сағат бұрын
Achimwendo mulungu akuona zomwe mukupanga mukulimbana ndi peter 😂😂😂😂😂 inu achimwendo uzachita manyazi 2025
@RafickAlissah
@RafickAlissah 2 сағат бұрын
Awa kumangogawa ndalama eshiii ndalama zathu kuonongeka 🥲🥲🥲🥲
@FortyoneHarwa
@FortyoneHarwa 4 сағат бұрын
Iwe chimwendo banda unapha chilima tsitidzakuvotelani ndipo udzamangidwa
@GiftZuze-ge1ne
@GiftZuze-ge1ne 4 сағат бұрын
Chimwende banda ndiye chisilu kwambere dzako ali manda koma sukabapo kathu
@AusimanKassim
@AusimanKassim 4 сағат бұрын
Panya panu nonse nkhani tizingomva basi yomunyoza peter aaaaaa mulibe mzeru
@adamashrafi5875
@adamashrafi5875 3 сағат бұрын
Tsekula mmimba😂
@AusimanKassim
@AusimanKassim 3 сағат бұрын
@@adamashrafi5875 dikila ndidye kaye
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 4 сағат бұрын
Kodi ndinsonkhano kapena wachiwona ndani? Mmalo mokamba mfundo muli busy kunyoza mumthu woti samakuyankhani😢😢😢😢
@TofficSaid
@TofficSaid 3 сағат бұрын
Chimwendo wamanyi sadickmia Ali Kuti munamupanga chipongwe asenanu amanyinso
@isaackinod1256
@isaackinod1256 3 сағат бұрын
A Malawi don't make mistake kuvotelanso anthu awa!
@GiftKumbweza
@GiftKumbweza Сағат бұрын
Komanso osadzavoteranso DPP
@JacklineNiwahereza-ni3pm
@JacklineNiwahereza-ni3pm 2 сағат бұрын
Achimwendo mukufuna mutchuke koma chilungamo mukuchiziwa kuti boma lanu lalephela
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 4 сағат бұрын
What a stupid government is this??? Chimwendo kodi Muthalika kuima nawo pa u president 2025 walakwa??? Always kumunyoza, koma sumachita manyazi kumatukwana munthu yemwe samakuyankha???
@GiftChilanga-u3c
@GiftChilanga-u3c 2 сағат бұрын
ine busy kuwerenga ma sms komaso ndiri kuseriku kuonera Bakili muluzi tv history is a best teacher mwamusakasaka mwalephera panopa mkuyamba kumuwawaza msekula naye mmimba kkkkk
@dalisoulphiri3094
@dalisoulphiri3094 2 сағат бұрын
Awa anakakhala anzeru sibwenziso akumatchula za infa ya Chilima 😢
@ellenMakoloma
@ellenMakoloma 2 сағат бұрын
Akufuna kuima u president ndi DPP yokha? Mukuwaopa inu hiyaaa
@FelixMapemba
@FelixMapemba 3 сағат бұрын
Achimwendo osamatha mau You never know what comes tomorrow Samalani ndi mulomo wanu
@BlestoneJonas
@BlestoneJonas 3 сағат бұрын
Chimwendo udzakhumudwa kwambiri ukumunamiza chikangawa wakoyo iwe galu kwabasi
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 3 сағат бұрын
MCP muzimuthokoza late SKC, without him ife sitikanakuvoterani.
@ThandiShandu-l6w
@ThandiShandu-l6w 3 сағат бұрын
Zachamba mesa naye amalandila zaboma as wachiwiri or iye akanawina yekha bring another point not that nonsense check 2025 another way of kicking DPP will be there
@SandramKambalame
@SandramKambalame 2 сағат бұрын
Mwalephera kumugwira bakili tv 😂😂😂
@KumbukaniKafatia-cd2hq
@KumbukaniKafatia-cd2hq 2 сағат бұрын
Ndalama tilandira koma forgot our votes!!!!
@AusimanKassim
@AusimanKassim 4 сағат бұрын
Kd mukapangangisa msonkhano nkhani izikhala yonyozana anthu akupindula chani
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 3 сағат бұрын
Ndalama nzathu mukungogawa ngati zanu machende abambo anu Achimwendo banda
@MartinKawowola
@MartinKawowola 2 сағат бұрын
Panyopako
@musasiyama9423
@musasiyama9423 Сағат бұрын
ndipo iyi ndi mbuzi ya munthu
@ThomuChiwanga
@ThomuChiwanga 2 сағат бұрын
Iwe ndiye chimwendo uzatiwona kuwawa 2025😭😭😭😭
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 2 сағат бұрын
Ndipo palibe cha nzeru chimanena iwe pa nsokhano bola kumvela bakili muluzi tv
@HamidMasamba
@HamidMasamba 3 сағат бұрын
Chimwendo usamayankhule ngati udagwa kuchokera kumwamba, ukumayiwala kuti ndiwe cholengedwa chamulungu udindo mphanvu zonse tsiku lina zidzatha. kapolo wachabe chabe iwe
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy 4 сағат бұрын
Chipan cha anthu opanda mfundo ndondomeko zawo zopoira
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o 3 сағат бұрын
Kkkkkk 😂 chimwendo usasiye kumunyoza muthalika ndi chinsiru kwabasi
@JamesBrown-gx8my
@JamesBrown-gx8my 3 сағат бұрын
Thanks Tatchena ma T_shirt a MCP lero...APM My vote
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 сағат бұрын
Kkkkkkk...adyeleni
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda 2 сағат бұрын
Khani kumangonyoza Peter basi kusowa fundo galu lwe apm my vote❤❤
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 сағат бұрын
Akufunika kuzamugenda miyala pa stage kuti asiye zopusa,,,,iwe Chimwendo uzafela kundende watch out
@EdahAlick-gq2qx
@EdahAlick-gq2qx 3 сағат бұрын
Zomwe ukuyakhula chimwendo ndizamisala ndiwe garu kwabasi
@GabrielThomas-ij1fo
@GabrielThomas-ij1fo 33 минут бұрын
Koma anthu tupembedza madano a Malawi let's work hard nd pray hard KUT Mulungu azitipatsa zosowa zathu otherwise a ndale amangofuna kutipeperetsa!
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 2 сағат бұрын
Ulibe nzeru bambo. Iwe asilamuo siomweo mwapangila upo kuti aziphedwa ndi chikangawa opanda nzeru ukakhala pa nsonkhano usamachulepo galu iwe
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl 2 сағат бұрын
A Banda ma press briefing simunayankhetu pano koma mzayankha chaka chamawa malume cz kukana kufufuza imfa ya chilima it shows munachita kumupha so amalawi Ali maso ndipo akudzimvera okha zoti inuyo mlibe nadzo ntchito
@RafickAlissah
@RafickAlissah 2 сағат бұрын
Awa zomwe anamuphera chilima ndi chani kdi😢😢😢
@MacleansKatungwe
@MacleansKatungwe 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂, Mfundoless, Ndalama zaphwekadi eti? Anthu akufa ndi njala, inu muli busy kugawa Ndalama from our own misonkho. Time will tell tell soon
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 сағат бұрын
Peter sitingafanizire chimwendo 😂😂😂😂. Mwana amalira mturo take... Pelekani mfundo zoti anthu akupaseniso vote
@juniortsegula3847
@juniortsegula3847 3 сағат бұрын
Chimutu ulibe mfundo iwe. Ukapita pa msonkhano ungokhalira Dpp kweni kweni dpp inakulakwira chani iwe. Nzakoyo siakukuyankha AI . tiona 2025 ndi pompano A chikangawa inu
@Martha-m6e
@Martha-m6e Сағат бұрын
Mulungu akukuthani bwana. Pelikan ndaramazo.ineso ndarama ndikuzifuna😂😂😂
@BlanzioAmoss
@BlanzioAmoss 2 сағат бұрын
❤manyazi alibe ameneyi mbava galu
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 сағат бұрын
I think athu mukukanika kugona naye Tulo apma ndie simunati Mumva nae mteza akuchosan Ku state house 😅😅
@PraiseKawerama
@PraiseKawerama 3 сағат бұрын
Kugula anthu kumeneko 😂😂
@lovenesskampira
@lovenesskampira 3 сағат бұрын
Achimwene ndi anzanuwo Peter mwammwalilisa kangaroo lero zakudinyani poti amwalira chakwera?anthu mumakhala nsanga History is the best teacher
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 3 сағат бұрын
Zautsilu ife ayi wamva iwe chimwendo banda usatiputsitse ife wamva ,
@musasiyama9423
@musasiyama9423 Сағат бұрын
Inu akamwendo banda ,,Malawi inachangamuka,,,mukungotaya nthawi yanu
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u Сағат бұрын
Iwe chimwendo ndiwe galu cz BMTV sanayambe lero even nthawi ya DPP analipo and ulibe manyazi ndi bodza galu
@MakabaBauleni-c2i
@MakabaBauleni-c2i Сағат бұрын
Pantumbo pako chimwendo umatinyozera bambo wathu peter Muthalika,iweyo Muthalika anakulakwira chani kd kapena kulibe zipani zina zoti utha kumanena chomwe namachende iwe unaona ndi peter Muthalika bx panyelo pako
@EliasTime-n1n
@EliasTime-n1n 3 сағат бұрын
Alibe nzelu uyu
@musasiyama9423
@musasiyama9423 Сағат бұрын
mbuzi yamunthu iyi
@babranzima8120
@babranzima8120 Сағат бұрын
Ndiye tizithu palizeru apa sakuganizila amalawi chimwendo bolaiye wakhuta mchimimbq mwake
@JoãoChirwa-n3l
@JoãoChirwa-n3l 9 минут бұрын
Bakili mulizi tv amatiwaza ase iye samanwna maboza km inu akanganya inu mwatikwana
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya Сағат бұрын
Chimkhwimbi chonsecho okuyankha okhala ana okha okha....sungazifunse? Tamayankhulani mfundo zoti mwina mungazapeze mavoti panthawiyo
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 2 сағат бұрын
ALOMWE MWAGUNDIKA KUSUTSA AA MLI KUNO KU JOHN KUVOTA PA FB.
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 сағат бұрын
Za ziiii
@NoreenNaituri
@NoreenNaituri 3 сағат бұрын
Koma nde kuikhadzulakhadzula DPP kkk
@IsmailTambula-g1k
@IsmailTambula-g1k 3 сағат бұрын
Zakuziwa zimene akuangula awa jela mdilime lakula awa mulungu anamuika chakwela phapando affine azafune mulungu amuchoza DPP iwina tikufuna kugula zithu mochipa
@AllanWyson
@AllanWyson Сағат бұрын
Zisiru izi osazivoteranso ,,, agalu amenewa asokoneza dziko lathuli
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 сағат бұрын
Chimwendo Banda ndi mbuzi galu chimutu chakocho ndizachiocha kuchipanga Kanye nya wamva iwe crocodile
@NickNyilendachisengah-p4u
@NickNyilendachisengah-p4u Сағат бұрын
Mwawanzunza zaka zosezi lelo mukutichani msanje mulibe mzelu mwapangachani
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 2 сағат бұрын
Achitsilu inu Chibvumbulutso 3 vs 17 bible lake ndi la Mulungu kapena la Satana?😢😢
@GiftMeatine
@GiftMeatine 3 сағат бұрын
Kandalama muperekako tapita naoni ku machinga anthu akudya chitedze mwatani achimwendo banda mtima wanji uwu opanda chison a Richard eeeee koma tkapuma kumwambaaa eeeee ai
@AndrewAsanChipangaya
@AndrewAsanChipangaya 2 сағат бұрын
kma apo ndizonad mulungu anangomutenga chakwera ndi chimwendoyi kma nanga achimwendo aba ndalama za mbili za boma kma tamuoneni sakuoneka ngati ali ndi ndalama kukhwima ngati maungu ana amenewa kmaso utsazinamize ife sitingavotele agalu awa ayi
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 3 сағат бұрын
Kodi a Chimwendo mukudziwa kuti mphavu zimatha ? Kapena mwina muzadziwa mukazaluza😢
@HamidMasamba
@HamidMasamba 2 сағат бұрын
Please tanenani fundo zoti anthu azakuvotereniso not kunyoza Peter, nsonkhano uliwonse tisamangonva za Dpp and Peter, uwuzeni anthu muzawapangira chani popeza 4 years zakukanikani what is your dream for next term mbuzi inu
@FaysonChimbalanga
@FaysonChimbalanga 2 сағат бұрын
Kkkkk makadeti mukufuna kutiuza kuti chomwe mumadziwa mkutukwana basi nde mwagwa nayo, yotukwanayo sikuthandizani mwina kapena mchilakhulo chanu (sanje basi ndinu buzi zamano kusi
@hassanfaizadaffer2421
@hassanfaizadaffer2421 46 минут бұрын
Kaya chinapangisa ndichani osakwera dege ija eshhhh bola ukanafa iweyo
@LastonChamila
@LastonChamila 3 сағат бұрын
Komaso mukuyankhula zano zomwe osat za Dpp
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo 4 сағат бұрын
Kodi simunagawe ndalama chifukwa zikuwoneka kangti athu awa sakukondwa😅😅😅😅😅
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 3 сағат бұрын
Umutenge nkazako ayimile dpp kuti usiye kunyoza peter mwina mutu wakowo umakulemela usakanyoze peter
@EllenChimera
@EllenChimera 3 сағат бұрын
Achite mutu ngati phwara😂😂😂😂😂😂
@ellenMakoloma
@ellenMakoloma 2 сағат бұрын
Tikudyerani ndalama zanu zokubazo koma sitizakuvoterani azitsilu inu
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 3 сағат бұрын
Chipani Cha maganzi maganzi nkhani kunyonza anzawo Peter yo amukulakwirani chani kupanda mfundo kunamakooo njanjiyo akuti yayamba MCP panyapako Saadic Miyayo munamupha lero anthu aku Nsanje akukumbutsani chiphinjo chomwe anachipanga okha Maso patsogolo anthu aku nsanje
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he Сағат бұрын
Ma cadet chonena chidagwera mkati ataona push ups apule
@SteynMaduka
@SteynMaduka 2 сағат бұрын
Or munthu angakuyipise motani koma iwe sukupanga zimenezo choti uzilimbana nazo ndi chiyani
@MathewsJanuary
@MathewsJanuary 2 сағат бұрын
Uzazipha chimwendo wekha.
@JulietKapata
@JulietKapata 3 сағат бұрын
Zazi mesa muliapa because of chilima mwaphayu
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley 2 сағат бұрын
Mukawina 2025 mutinamiza chani kuti tizakuvoteleni
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 3 сағат бұрын
Ndalama musiranfira kom wo sa votera chakwera akumvunika UDF and dpp utm aford
@MbeedaJames
@MbeedaJames 3 сағат бұрын
I hate this chimwendo alot than chakwera himself chimutu kukula🙄
@MisheckAselo
@MisheckAselo 3 сағат бұрын
Chimwendo ndale za chimidzi zonyozanazi talekani
@ChingaChibamba
@ChingaChibamba Сағат бұрын
Koma tiva ziti lelo kuyankhula zina mawa kuyankhara zina eich koma ziko lathu zochitika kuchuluka
@swadikimbwana7680
@swadikimbwana7680 3 сағат бұрын
Pls don't use money distribution as campaign
@GoodsonLevison-r1r
@GoodsonLevison-r1r 41 минут бұрын
Ukulimbana ndi dpp iwe chimwendo uzafa ndi mwala umox kut thiiii
@LastonChamila
@LastonChamila 3 сағат бұрын
Zose tisiye mmanja mwamulungu a M CP muziwe kut de sky is limit mukamaika achipan ku MEC transparency and acounterbility tiwona bwanji koma muziwe kut msembe iliyose ilindimalile mulungu akuona
@patricksamson4852
@patricksamson4852 3 сағат бұрын
Mwendo ndinu ovesa chisoni manyazi mulibe ndale zopanga kunyoza anzanu achitsiru inu anthu sakukondwa mukuchita kuwakakamiza zazi
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe Сағат бұрын
Nanga njala bwanji galuwe zabodza izo mwanambwa
@andrewmbilinte4589
@andrewmbilinte4589 3 сағат бұрын
Kodi ndalamazo akugawira ndani ,mesa ndi a Malawi.Ganizani guys polankhula
@Lushaka
@Lushaka 2 сағат бұрын
Guys Malawi people we lost way this is not politics bt talking shirt without plans just think 🤔 what kind of this people always busy about Peter Peter problem our people who like to follow every way why Malawi people u don't teach how to respect one another every day Peter just build our country we tried kind of this things amalawi we must wake up this people taking advantage with our youth why Guys check South Africa youth or Kenya youth never allow kind of this readers no respect nothing we can see ourself 😢
@TedzaniIVPowerStation
@TedzaniIVPowerStation 2 сағат бұрын
😂😂😂😂nde za maudindo ansenawo chikuwakhudza mchan?😂
@keeganvanloggerenberg3029
@keeganvanloggerenberg3029 3 сағат бұрын
Achimwendo ndalamazo osango gawa chimanga bwanji ??? Anthu kunjaku akudya chiteze osati wachiona ndani izii
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o Сағат бұрын
Kkkkkkk tirandile ndaramazo chonde osana ndarama ndi mistake yayikulu
@GiftMeatine
@GiftMeatine 3 сағат бұрын
MwaNduna zonse opepera nd Richard
@JamesMachunga
@JamesMachunga Сағат бұрын
Chimwendo masiku akunthela uzafa ngati galu
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley 2 сағат бұрын
Tiyeni tiwadyele basi koma osakawavotela akanganya amenewa
@kingzack8999
@kingzack8999 47 минут бұрын
Kodi chipani ndi dpp yokha Malawi yonse
@MchengaAssama
@MchengaAssama Сағат бұрын
Iwe munthu onvesa chisoni kwambiri anthu mene akuvutikilamu mulungu akuone iweyo
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 3 сағат бұрын
Iwe njanji unyadila ya ku Mozambique pajaso umanyadila magreda a ku India chimanga chikunena iwecho ndalama wagulila iwe chimangacho wazitenga kwa amako
@JoãoChirwa-n3l
@JoãoChirwa-n3l 17 минут бұрын
Mcp likuopa dpp bas mbona khumbai ali busy ndi dpp pakunya pamako ndithu
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe Сағат бұрын
Chipani chokupha nizomwe amaziwa
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera Сағат бұрын
Kukula mutu koma fundo mulibe.
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 сағат бұрын
Usalimbane ndi Sameer suleman..
@simonpaul6567
@simonpaul6567 3 сағат бұрын
Chitsilu owe zomwe ukudziwa ndizimenozo just answer the question who told you that plan is full?
@BrianMuleke
@BrianMuleke 3 сағат бұрын
Ma president onsewa kma peter bas kkkkk kupanda mfundo
@MartinKapito
@MartinKapito Сағат бұрын
Mfiti ndi iwe ndi ladzaro munapha chilima
@MussaZimba
@MussaZimba 3 сағат бұрын
Kuchikwawa munangokamupha mwana uja agalu inu
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 3 сағат бұрын
Ma late onsewo munadya mesaa😢😢
когда не обедаешь в школе // EVA mash
00:51
EVA mash
Рет қаралды 4,3 МЛН
VAMPIRE DESTROYED GIRL???? 😱
00:56
INO
Рет қаралды 6 МЛН
Kell Kay - Ndabwera Ndi Nkhani ( Ndabwera Ndi Nkhani )
6:07
kell kay
Рет қаралды 42 М.
когда не обедаешь в школе // EVA mash
00:51
EVA mash
Рет қаралды 4,3 МЛН