BON KALINDO LERO PA 19 DECEMBER WANG’ALURA MOSANYENGELERA PAZOMWE ZACHITIKA DZULO KU PARLIAMENT

  Рет қаралды 41,474

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 88
@Samson-ve5rs
@Samson-ve5rs Ай бұрын
Chikangawa party must go
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
President Chakwera amandimvetsa chisoni kwambiri, ndipo ndimazifunsa mafunso awiri ndikamva ndi kumuona Chakwera: 1.kulirira u president konsekuja mpaka Ku court, ankafuna azizawadzunza a malawi choncho. 2.Kuyankhula konse ankayankhula kuja Ali leader of opposition, ankangoyankhula koma analibe nzeru zoyendesera dziko? Tikamapanga zinthu a malawi tiziziwa kut kuli Mulungu, ndipo mlingo omwe umamuyesa nawo nzako iwenso umayesedwa ndi omwewo.
@MozyDandawile
@MozyDandawile 7 сағат бұрын
Born kalindo mo fire 🔥
@abgi.doctor.august
@abgi.doctor.august Ай бұрын
The DC Boooon Kalindo president wa aphawi the voice of Malawi 🔥
@kechu289
@kechu289 Ай бұрын
Which Malawi? Weak generalization.
@HendresonNambazo-u4i
@HendresonNambazo-u4i Ай бұрын
Ndiwe Mose Walero
@KondwaniChester
@KondwaniChester Ай бұрын
Bon kalindo my king ❤
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu Ай бұрын
Iweso kalindo ulibe nzeru zolakhula zakozo zimapindula chiani?udayamba kale kale kulakhula koma mpaka lero sitikuonapo chanzeru kuchokera Kwa iweyo,ganyu akupweteka osakalima bwanji alukupatsa ndalama ziti uzilakhula zopusazo ndani?
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u Ай бұрын
Opanda nzeru oyamba nde president wathuyu cz akuyang'anira anthu onse adziko lino koma nzeru alibe mmutu mwadzadza mamina basi, mpaka kuthawa mafunso ku parliament??? Sindinawpneko president mu Afrika opepela ngati uyu, kudana ndi Bon kalindo kuli chabe koma Chakwera aaaaaaaa mavuto tili nawo basi😂😂😂😂
@NicholasKwajama
@NicholasKwajama Ай бұрын
Tiye uko nyima
@AbrahamGaluwapananji-vj7mj
@AbrahamGaluwapananji-vj7mj Ай бұрын
The DC....mumalankhula bwino.... Inunso mukhoza kulankhula m'menemo mungafunire Kwa pulezidenti ....Kaya phunzo.... Koma pamaso pa pulezidenti yemweyo sungachite zimenezo ayi DC....in parliament muli ulemu wake wake....a descent opposition like DPP sali momutukwana....kapena kukangana ndi president....a opposition amafuna kuti president ayankhe mafunso moyenerera....koma taonani a DC....kuti mbali ya boma linatseka nthawi mu parliament.... president sanayankhe mafunso wokhudza foteleza ndi chimanga...m'ma Admarc....
@WilliousNyirongo
@WilliousNyirongo Ай бұрын
Zipanizi palibe chabwino,aliyense.ndiwadyera basi,kaya.tizikometsere bwanji chabwino palibepo apa. Anzeru onse akudzidziwa zimenezi.
@Maxielyies
@Maxielyies Ай бұрын
Powerful!!! ❤❤❤
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri Ай бұрын
The DC woyeeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤
@RoseChimbwefu
@RoseChimbwefu Ай бұрын
The Dc woyeeeeee
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Ай бұрын
The dc moto kuti buuuuuu❤
@GiftBonomali
@GiftBonomali Ай бұрын
The DC number one
@PhillipChisanu-k3r
@PhillipChisanu-k3r Ай бұрын
But on the opposition, don't blame them.kodi mesa ndalama zidapita ku alliance parties,iwenso Kalindo umatikwana ndi ma audio akowo wamva,nanunso amikozi ndi mzanuyunso mwatikwana bwanji,akumangoyankhulatu uyu,2019 to 2020 adalinso pa for front ku ma demotu,pano ife tikuvutika iyeyu akungoyankhula bas,za ziii
@gomezsoko
@gomezsoko Ай бұрын
opposition is sleeping they wont win coz of that
@BeatriceSaulosi
@BeatriceSaulosi Ай бұрын
Ndiye ngati amakukwanani ndi ma audio ake mumavela chifukwa chaa?? 😊
@SandraChibaka
@SandraChibaka Ай бұрын
Umavera chani iwe?😂😂kupusa ukoo
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w Ай бұрын
Achikangawao akanangokhala ku state housi osapita ku nyumba yamalamulo.Athawako buzi yamunthu😮😮😮
@StephanoKaunda
@StephanoKaunda Ай бұрын
More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@KazembeFoster-jw1ww
@KazembeFoster-jw1ww Ай бұрын
DC ma vn akuchedwa kutuluka kaa
@estonmnthali3719
@estonmnthali3719 Ай бұрын
Born kalindo, uku lankhura chilungamo , anthu akufa ndi njala unu kugawana ndalama eish zovesa chisoni
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w Ай бұрын
Zangozazana mbuzi zokhazokha😮😮
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda Ай бұрын
Andale aku malawi makape
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 Ай бұрын
The DC Umakwana. More Firèeeeee❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@MillieMalakam
@MillieMalakam Ай бұрын
The dc God ahead 🙏 my brother
@ChikondiStanford
@ChikondiStanford Ай бұрын
Good speaking
@JulietMunthali-g9b
@JulietMunthali-g9b Ай бұрын
Exactly
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi Ай бұрын
❤❤❤
@md.ruhul-aminmd.ruhul-amin298
@md.ruhul-aminmd.ruhul-amin298 Ай бұрын
The Dc. Fire 😂😂😂😂
@thomasthomson-rn5ch
@thomasthomson-rn5ch Ай бұрын
Sanamusekelere, amamusekelera nda mcp
@GodfreyLumbalo-v9q
@GodfreyLumbalo-v9q Ай бұрын
Kodi Namalomba ndi wa MCP
@BerthaNazombe
@BerthaNazombe Ай бұрын
The voice of truth the dcccccccccc
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron Ай бұрын
Sawona mene amachitira Malema salora zopusa Ramaphosa amasowa Mtendere naye akapita ku parliament
@MichaelHastingsGodfreyMvula
@MichaelHastingsGodfreyMvula Ай бұрын
Politicians are always happy when citizens are suffering so that they can come to power or remain in power. Don't be cheated when they oppose any ruling government, they do that in order to come to power. Work hard for your survival.
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Chakwera pamodzi Ndi MCP akufuna kutichimwitsa ifeyo a Malawi zonse zomwe akupanga Ndi zautsilu zopanda pake ndipo achikhala wamzeru anakapanga resign.
@kechu289
@kechu289 Ай бұрын
A grossly half-empty perception and better described as narcissistic.
@ChisomoYosefe
@ChisomoYosefe Ай бұрын
The DC boooon kalindo
@henrymhango4313
@henrymhango4313 Ай бұрын
Kodi mwati number ya DC ija bwanji❤
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Aaaa MVUTO NDI CHAKWELA MCP ANTHU AMAGADZIDI AWA
@AndrewNdalama-f8h
@AndrewNdalama-f8h Ай бұрын
Don't blame opposition
@gomezsoko
@gomezsoko Ай бұрын
they are sleeping . they have to wake up. i blame them too
@jixonromeo4111
@jixonromeo4111 Ай бұрын
Mmene ine zimandinyasilamo
@TrucidaMacdonald
@TrucidaMacdonald Ай бұрын
Ife kwathu kuno kunchalo tayamba kale kugula 1000
@williamSaka-ep1qz
@williamSaka-ep1qz Ай бұрын
Zoonad bwana karindo
@kechu289
@kechu289 Ай бұрын
Chomwe aphungu a kunyumba yamalamulo anawona kuti amupatse Chakwera ulemu chonchija, ife amene sindife aphungu a nyumba yamalamulo komanso amene tili wotsamwa ndi nsanje ndiponso wasafuna kuyamikira pamene wina wachita bwino, ngakhale titakwera pachulu siingachione. Mukawafunse a phungu anu, akakuuzani choyenera chimene anawona.
@PatrickHalineck
@PatrickHalineck Ай бұрын
Bola ndalamazo akanapasa amalawi osauka
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Ай бұрын
Opusa number ndye Chakwera koz anathawa mafunso ena sanayankhe komas Suraiman ndi mai Jolobala sanapasidwe mpata ofunsa anati nthawi yatha
@BoscoKalua
@BoscoKalua Ай бұрын
Ndarama zampweka kugawana koma ma pensioner akungovutika ndi PEANUTS ngati ndalama boma lilibe eh
@FrancisLunga-l4y
@FrancisLunga-l4y Ай бұрын
Mukamanena anzanu kuti ndiachitsiru ndimbuli inu ndichimwendo sindinu mbuli inunso ndi achitsiru kwambiri mwanva?😂😂😂😂😂
@SilombaJumah
@SilombaJumah Ай бұрын
Zosaenda
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev Ай бұрын
Zongobwebwetaz nde tinatopa nazo
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
The dcccccc❤❤❤
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d Ай бұрын
Boma la mafia😂😂😂
@GraceJackson-s4k
@GraceJackson-s4k Ай бұрын
Don't blame opposition pls
@McanthonyNdau-m4y
@McanthonyNdau-m4y Ай бұрын
Umafuna kuti azilila
@SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON
@SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON Ай бұрын
Zoonadi
@mwayimphundi8254
@mwayimphundi8254 Ай бұрын
😢😢🇲🇼
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani Ай бұрын
💯idzi ndye dzoona zake ndithu Malawi tkusiya pamoto and Makamaka adzisogoleriwa mmmm kunali bwino kuwapasa asilikali alitenge dzikoli alilamulire
@elishabanda1332
@elishabanda1332 Ай бұрын
Nkani za chikangawa everyday don't you have better things to do kodi
@WilliousNyirongo
@WilliousNyirongo Ай бұрын
Ambiri a inu ntchito nkulongolora zinthu zosathandiza,ndiye titengapo chani ife? Asiyireni anthu anzeru atuluse fundo zothandiza a Malawi. Musamayankhule chifukwa chot muli ndi kamwa koma muyankhule ngat pali fundo. Mukamabwebweta chilichonnse, anthu adzolowela kut inu ndinu achoncho.
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i Ай бұрын
Ndizomwe tikudabwazo kobili zimene amagawanazi zacani? Ndimanena kuti mmalawi muno mulibe presdent ndizimenezi.
@MadyGenuh
@MadyGenuh Ай бұрын
Eeesh
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du Ай бұрын
Zigawenga dzomwa magazi ndi mikodzo
@watsonmhango8794
@watsonmhango8794 Ай бұрын
Worse President ndi Chakwera osanama apa Chakwera watichitisa manyazi kwambiri, corruption is too higher under leadership of Chakwera ndithu😂😂😂😂😂
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du Ай бұрын
Dzikubwelesa chuma kwa. Inu ndi chakwera amalawi asiyeni ndi umphawi wao wachikhalire
@EstherTemwa-j1g
@EstherTemwa-j1g Ай бұрын
The DC boooooon kalindo❤❤❤❤❤
@georgezikabuma9396
@georgezikabuma9396 Ай бұрын
Awa ndi achitsiru Mesa nayenso anali wandali koma school mulibe ndiye ankafuna mpando zidamuvuta opusa kwambiri .
@VincentKachingwe-c6w
@VincentKachingwe-c6w Ай бұрын
Akukumba zakuba ndrama zaku maliro
@MayaChimpokosera
@MayaChimpokosera Ай бұрын
Zopusa zenizenitu
@AleCloset
@AleCloset Ай бұрын
Ati kumachita kumpasa ulemu mfwiiiiti ngat ameneuja... Andale ndafwiiiti
@AngellachifundoMwale
@AngellachifundoMwale Ай бұрын
😢😢😢😢😂😂😂😂😂
@Jaclynwhayo
@Jaclynwhayo Ай бұрын
Iiiiiih koma zomvetsa chisoni kwambiri
@SostenPiyo
@SostenPiyo Ай бұрын
Koma a opposition smartmatic machine ija muichotsadi? Mukwanitsa? Coolness yake imeneyiyi? Uh a Malawi tipemphere kosalekeza ndithu,chenjerani mwa a Ambuye
@NelsonMd-x5h
@NelsonMd-x5h Ай бұрын
Palibe ku chichotsa chi machine chimenechi ngati bwana Muthalika anaka lembetsa kugwilisila chomwecho ndiye kuti ana vomeleza
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni Ай бұрын
Kodi mukudziwa kuti Moz ,Zambia , Tanzania vosewa anachotsa chipepeso, analengeza???? Ndlamazo zinaikidwa kuti
@WilsonMbendela
@WilsonMbendela Ай бұрын
Boma la mcp ndi mbuzi zokhazokha
@AffectionateGeyser-fm7dl
@AffectionateGeyser-fm7dl Ай бұрын
I dont understand did they ask for money?.Its state funeral
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence Ай бұрын
Malawi basi, ambuye ndie akunziwa
@dalitson3558
@dalitson3558 Ай бұрын
Andale onse ndiopa kwambiri
@AustinBornface
@AustinBornface Ай бұрын
Tafika
@NelsonMd-x5h
@NelsonMd-x5h Ай бұрын
Chikaku phonya chi banzi uma lubwa lubwa.
@WaysoLufas
@WaysoLufas Ай бұрын
Ndpo zoonad nd amafia
@EdwinZiwa-x2g
@EdwinZiwa-x2g Ай бұрын
Chakwele ndi mbava tilimbike chabe kulima basi
@McfastonMkhala
@McfastonMkhala Ай бұрын
Get a way iwe umangobwebweta ngati nkhuku aidulamutu.
DPP LILONGWE RALLY WITH ALFRED GANGATA
Malawi Exclusive
Рет қаралды 583
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН
A NAMIWA KUYANKHA MAFUSO ATOLANKHANI 🙌😱
21:23
HOT 265
Рет қаралды 32 М.
NSOKHANO WA DPP KU BLANTYRE __21 December 2024
30:15
HOT 265
Рет қаралды 41 М.
BAYGUYSTAN | 1 СЕРИЯ | bayGUYS
36:55
bayGUYS
Рет қаралды 1,9 МЛН