A speech of hope. Vuto ndikuiwala, chilungamo aliyese amachidziwa, koma akakhala pampando kuiwala dala .
@AliceKapaswicheАй бұрын
We need a brilliant leader like DK All I'll do is to pray for him to do his dreams to help Malawi the warm heart
@MosesBanda-h4x5 ай бұрын
Thumbs up for you Dr Dalitso Kabambe , where were you ?
@AustinMhone-r3s5 ай бұрын
we need young leaders with vision like you but our problem is far beyond that we need to change political system in our country first.
@crosbyphiri17455 ай бұрын
Very good thoughts Dr Kambambe. Qualifying for the top post.
@PhiriChiyambiАй бұрын
Ukungoyenela kukhala tsogoleli u deserve my vote I pray to God for u to win
@lawrencemsonthi61465 ай бұрын
We need people like this Guy
@andreabanda78385 ай бұрын
Yes this is all about federal government system which I strongly support.
@GraceChaweza-b7w5 ай бұрын
Sounds great ideas with the possibilities of developing the country. Oo! God show us the way.
@0wenNkhambule5 ай бұрын
Good Messnge Mr Kabambe❤
@SalamaItimuАй бұрын
More grace Dr K🎉
@RalphZambezi5 ай бұрын
Is sounding good komano corruption dzikoli abale
@retirementtoafrica5 ай бұрын
Interestingly he did not mention it.
@kossamunkhoma41424 ай бұрын
Uyu adzatiwonongera chuma chathu!🤣Each District what?😂😂🤣🙌
@AlickChima5 ай бұрын
Chihana blew the whistle on matters of the federal system of governance. This is exactly what he was referring to. Every city to champion its own resources and be responsible for its growth expansion strategies.
@johnnyirenda58484 ай бұрын
Sure Federal Gvnt can work with not otherwise ,tired of lies
@SymonNamalomba-sh3fu5 ай бұрын
Wachipiku sangayendese Dziko,
@Guttagaard5 ай бұрын
Amwene ndipo inu a Malawi tinalozedwa😂😂😂😂
@mollymasangano4735 ай бұрын
Kikikiikiki 😢😢😢😢😢😢 zoona tidzisakha anthu ama Colin fiction 😅😅
@asahelmachila30265 ай бұрын
He is eyeing the highest office, so his campaign starts with such lectures.
@petroayami025 ай бұрын
When reporting kumatchula date osati dzulo kapena dzana or mawa. All in all keep up the good work.
@MathewKalinkhu5 ай бұрын
A Malawi mumalankhula bwino kwambiri, koma kukuvotelani m'makaiwala mkalowa mu boma. Chakwera ndi malemu ankalankhula zabwino , panopa palibe chilichonse chomwe apanga.
@rexnyalugwe49105 ай бұрын
I totally agree with you. Makhumudwitsa anthu awa
@mercyjubeck59055 ай бұрын
That's the way to go. good Ideas my the God Lord bless you 🙏
@jacquelinecunningham3635 ай бұрын
You are saying the truth we malawian need to change our mind set . A good speech but can it be implemented. 👏👏
@phillipstamaley79015 ай бұрын
Mind set change!! mind set change!! Antill when???
@mosespemba88225 ай бұрын
Just theoretical as such? These public lectures have their interests nanu. You think, they are speakihg sense while their focus dwels on your attention as you listen to them. These are luctural sensions they deliberately plan in political style to cheat a civilised Malawian who thinks is sufficiently literate, listening to them this way. There is no way we can keep child bearing in a family which is already struggling to feed the few they are there. Swallow your own foolishness, understanding these trashes from Kabambe who in the end simply wants to pull more followers to his side for him to win a better position in politics.
@WakisaGodfrey-y8h5 ай бұрын
That's a problem of politicians they can sound good and make us even shake our head then later on you leave us crying
@PeterMKANDAWIRE-v8hАй бұрын
My hope is rising for Kabambe as next president
@umodzi5 ай бұрын
ndiwamzeru koma sitikuziwa ngati mkati mwake muli cilungamo
@williammandhlopa5 ай бұрын
Wabozaa wants to cheat northerners 😂
@victorbanda90395 ай бұрын
Munali m boma momwemo bwanji simunasandutse kukoma paradise zamabodza basi kufuna kumangotipusitsa a malawife
@yassinn56345 ай бұрын
Nganga bulawayo iri patsogolo ungafulukute ku DPP?
@yamikanithomas2314 ай бұрын
You can turn the table. We want intelligence for the development of this country.
@enosmanganda3274 ай бұрын
Very brilliant lecture. Praying for your dreams to come true boss.
I like him so far, Koma Kodi izizi mukunenazi sir tikakuvoterani mudzapanga? So sad kuti mumazayamba zina kusiya zimene inu munapanga promise, Kodi ndiye kuti mwina their is a demon in that sit makes you guys to forget this beautiful vision mukalowa Boma. Poor Malawian tipephere kwambiri for our nation we need God to intervene to get rid off the demon that makes our leaders go mad and become the selfish leaders. Dear God please give us a good leader and protect him from evil, we are tired. Enough is enough. We need you for real now, we have surrendered. Please???
Ku Malawi palimbe msogoleli ologotsoka onse ndi akuba
@JonasKondowe5 ай бұрын
Ndiye mukamaliza kuyankhula zithera pompo basi kwanu nkuyankhula
@AbdulJohn-t7lАй бұрын
Ndawonapo muli Mr Mahata munthu yemwe ndi mamukonda ndi ma ideas ake pa politics
@JuvenileDebwe-bv8ow5 ай бұрын
This guys knows what is talking about coz he's been in the financial sector
@MikeMwale-bw1xw5 ай бұрын
Yes and he knows where to start,becoz those young pple in the universities needs to be well equiped,hence the future of this country depend on them.
@YellowmanMalawi-qe8zh5 ай бұрын
Okubaso uyu akutero
@BillyMhone-jp3kn5 ай бұрын
Good Ideas
@williammandhlopa5 ай бұрын
Aaaaaa what rethinking. You were in the government and north was forgotten.
@mcsydenynsinga76105 ай бұрын
It really needs a strong prayer for your dream to come true Mr ,problem are the people who are in the top offices. You can write your business proposal today a nice one but to gate ngongole for that kkkkk ndie olemela kale , because of the terms and conditions you can be asked from the banks to grant you a loan
@LamieTiger5 ай бұрын
Adawa mfundo dzawo dza mphavu Koma zochitika dzawo muntimamo zilingat president waku Kenya
@martinmoyo42115 ай бұрын
Mwakulankhula mfundo zabwino koma inuyo munali kumphika wandalama bwanji simunatulutse ma plan awa? DPP mumangoiyang'ana kuti igwe.
@WilliamNhlane-fd9hi5 ай бұрын
Problem with Malawi they don't like educated people like this one, they clap hands to ignorant people.
@retirementtoafrica5 ай бұрын
Amen, the hatred is real. Kuzolowera kusauka, katangale ndi bodza!
@EmmanuelNkosi-ts8bn5 ай бұрын
The only problem is that they are just good at speeches but can't impliment it
@EmmanuelNkosi-ts8bn5 ай бұрын
The only problem is that they are just good at speeches but can't impliment it
@FATIMABWANA-b3dАй бұрын
Akuyankhula zomveka zot atapanga zimene akuyankhula atalowa boma Malawi kusintha koma atsogoleri ake akalowamo bs amasankha kiwononga dala
@prestonkasito18155 ай бұрын
Good theory. Malawi is good in theory. If he happens to be a leader of this nation all these said not even one will be implemented.
@williammandhlopa5 ай бұрын
Implementation is difficult
@williammandhlopa5 ай бұрын
Trying chilima formula. Will you fit in that
@InnocentNgulube-f5cАй бұрын
Mau a mphamvu kwambiri kuchoka kwa Mr Kabambe
@FATIMABWANA-b3dАй бұрын
Vuto kuiwala Dala bs koma zochita amadziwa koma bs kusankha Dala kiwononga mfundo imeneyo tachitani mukalowa boma plz
@ChrisChitsulo4 ай бұрын
This guy was once the governor of Malawi, when has he realized this?, ma vote awa
Chinsinsi: Kabambe, Namkhumwa, Mutharika, Saulosi Chilima, Chimulirenji. Onsewa ndi ma cousins. But I wonder why they are never united. This shows that DPP is the only democratic party in Malawi. When Chilima planned to leave Tonse alliance, Chakwera killed them. Yet people leave DPP and live. DPP my vote💙💙💙
@retirementtoafrica5 ай бұрын
Amen, Peter is a true educator, amangoti go and multiply!
@ancientnkhata11375 ай бұрын
Osapanga mix late SKC ndi mbwerera zanuzo. APM ndi tribalist
@edsonnyasulu53945 ай бұрын
Onse akufuna kutchuka basi alibe mutima wothandiza nkhani ndi kuba ndalama za amphawi
@actuarialscience22835 ай бұрын
@@ancientnkhata1137Chakwera bwanji mbuzi iwe Mac-Hendie-son? Afford Bwanji. To be honest chomwe chinapha Chilima ndi dyera. Bon Kalindo pa 6 June anmuuza Chilima kuti asakwere ndege iliyonse koma pofuna ma allowance anakwera. Onse amene anafa mundege anali a UTM amene anaphedwa ndi MCP.
@actuarialscience22835 ай бұрын
@@ancientnkhata1137 Chakwera analemba abale ake okha zomwe Pter sanapange. 90% ya nduna ndi za ku Lilongwe, Zomwe Peter sanapange. 100% ya olembedwa ku MEC ndi a ku Lilongwe ndi Ntchisi. Oyendetsa MEC ndi mwana wa John Tembo. MRA ikuyendetsedwa ndi mwana wa Chakwera. Immigration mwana wa Chakwera. NoCMA mwana wa Chakwera. Unduna wina ndi MG2 wa chakwera. 👈This is 100% tribalism. Mac-Hendie-son iwe.
@HaroldMkanthama5 ай бұрын
Cotton. Bakili sold David whitehead and sons.
@Patrickgomani5 ай бұрын
It makes sense 🎉
@BrightKandengere5 ай бұрын
Powerful
@HalisonSolomon5 ай бұрын
AAAAAAAA INU UYU SO NDI MBAVA YOTHERATU NDAMENE ANASOKONEZANSO NDALAMA YA RESERVE BANK KULIBE MUNTHU AMENE ANGALIOMBOLE DZIKO LATHU CHIFUKWA ONSE AMENE AKUFUNA MPANDO NDI ANTHU OTI ATCHUKAPO NDI UMBAVA IYAAAAA
@JaneMapazi-ex6bb3 күн бұрын
Mabodza AWA ku reserve bank ankalemba aku Thyolo okha okha,
@VaidaSidreckАй бұрын
Abambe umakwana
@AliceNaphiyo5 ай бұрын
What about Reserve Bank. Yes you are dreaming.
@rasheedhoward35 ай бұрын
vuto agaluwa amakhala azeru akakhala outside koma akhala kati amasamala za uphawi akula nawo mufuse chakwera
@retirementtoafrica5 ай бұрын
Nanga zathera panjira bwanjinso?
@kadijachilwan9675 ай бұрын
This can happen only if there's no corrupt mawu amphamvu kwambiri ndipo othandiza
@elishangalu58525 ай бұрын
We have great thinkers,but to do ...dololoo
@UssenNjirinah5 ай бұрын
Ndizaka zingati Ali mboma lolamula bwanji samakambirana zonsezi.... Chakwera number apezeka