ZOMWE ZIKUCHITIKA KU BALAKA PADAKALI PANO PAMENE PRESIDENT CHAKWERA NDI VICE MICHAEL USI AFIKAKO

  Рет қаралды 60,865

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 262
@user-gd2kl1fx1q
@user-gd2kl1fx1q Ай бұрын
Balaka ppo mwachìta bwino osapitako keep it up
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Ай бұрын
MBAMBANDE
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya Ай бұрын
Ayi a Manganya mukuoneka okondwa, chasala nchiweruzo basi pa imfa ya nzanu, continue rest in peace SKC, tizakulira mpaka kale kale Biyeni
@bristonmwenga5286
@bristonmwenga5286 Ай бұрын
Mmmmmmm,,,koma Malawi,,,,z
@petroszgambo9949
@petroszgambo9949 Ай бұрын
Manganya is a happy man nowadays, he is exactly where he wanted to be all along. RIP CHILIMA.
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z Ай бұрын
Ndiposoo
@stephancommercial580
@stephancommercial580 Ай бұрын
He is more than happy
@user-cs3lq5mr9t
@user-cs3lq5mr9t Ай бұрын
He is just a puppet wa apule uyu😅😅 kd anthu simukuona what's going on... 😅😅 8:35
@user-ep7gu2td6y
@user-ep7gu2td6y Ай бұрын
He got opportunity he was looking for 😢😢
@vukanifracksonchinkonde7324
@vukanifracksonchinkonde7324 Ай бұрын
You guys are unrealistic,you expect him to always morn....remember you can not keep crying for a workmate as if it's your mam and Dad. Why shouldn't he be VP ?
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb Ай бұрын
Mr chikangawa ndemwawondatu nde mkuwonda pano lbani kaye zomaliza nthwi lripo agogowo alibe chochita china muboma lakupha lanuro mzit zikomo chilima mwawulawa udindo ndikumuphaso ziko lapasi koma 😢😢 pitilizani kupuma bwana chilima
@user-lu5db5qk2o
@user-lu5db5qk2o Ай бұрын
Koma anthu aku Balaka congratulations mumatha anthu amenewa tisawaoase mpata please.
@StevenMjMbama
@StevenMjMbama Ай бұрын
Good job Mr president and vis wanu limbikitsa ndinthu ulimi umenewuu
@user-rz8qp8tj8e
@user-rz8qp8tj8e Ай бұрын
Koma guys sindikufuna kuseka ati monica imeneyi wig yanji 😂😂😂😂😂😂😂😂😂ndakomoka ❤Dr chikangawa woyeee and mr short chakwera ndi manganya mukuvala mochititse manyazi bwanji Kwachema ndi ku Balaka no people 🙌🙌🙌
@user-mv1ho9pp7o
@user-mv1ho9pp7o Ай бұрын
Mamie ndiye mumangolondora kuli konse mulibe zochita zanu ndiyekut eti achakwerawo ndiye ayamba kuondatu chonsecho akudya misokho ya malawi or mutero chaka cha mawa muchoka mudyeretu misokho ya malawiyo paja dzina lina ndi chikangawa 😂😂😂😂😂😂
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 koma akuliziwa dzinali LA chikagawali
@user-cs3lq5mr9t
@user-cs3lq5mr9t Ай бұрын
Ndipo pansana pawo ndithu😅😅😅
@prettytambala5687
@prettytambala5687 Ай бұрын
Kumaka, dad asayende okha angayambe kukodwa ndi ana anjoka😅
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Ай бұрын
Ka msanje bwa???? Mix ti atsikana tosezenzedwa ma unduna tili ku mcp kkkk kuopa kulandidwa
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Ай бұрын
Ulibe manyazi manganya kuchenjera konsekuja kumupha nzanu ngat galu ndi chikangawa nzakoyo,anthu akakuona akumakumvera chison chifukwa mawa ndiwe.utm yake itiyo yomwe uli iweyo,popeza chilima ali Moyo sunasapotepo utm.anthu amagazi mmanja
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Ай бұрын
With or without anthu program yachitika basi. Zomwe amakapanga president ndizothandiza anthu omwewo. Kupanda nzeru eti. Ndale zanji zimenezi. Nsanje paMalawi
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb Ай бұрын
Amanganya mwamasuka pano mukumva kukoma mutamuphesa chilima ndi abraz anuwo lnuso muzafa mutu kuwumawo ngt nguli
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j Ай бұрын
Kunganakhala ku maliro tikanati angokhala po ananfedwa okha
@ThokoGomeza
@ThokoGomeza Ай бұрын
Kuononga ndala kukayendera nyemba basi ndi matumba angat achimanga mukanagura kupasa anthu akusowa chakudya 😢😢😢😢😢
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f Ай бұрын
Watching from Johannesburg
@yusufbakali
@yusufbakali Ай бұрын
❤ Maiko usi a chakwela pano a kuyendela nzeru za Maiko usi
@yusufbakali
@yusufbakali Ай бұрын
Akugofuna kumugwilitsa ntchito then asamuphe mcp plan
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Ай бұрын
Bolanso kukanapita anduna okha mwinako kukanakhala anthu not as it is manyazi bwanji koma!!
@CleverJosafat
@CleverJosafat Ай бұрын
Ai zikomo anthu aku Baraka ❤❤❤❤❤
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi Ай бұрын
Km ndie kuli chinamtindi cha anthu!!! Kkkkkkk
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Fanz mphwanga
@marryphili5419
@marryphili5419 Ай бұрын
Keep it up balaka people mupitilize wosapitako achikangawa akamabwera kumeneko
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f Ай бұрын
My district ,keep it up
@user-io2uw2me9f
@user-io2uw2me9f Ай бұрын
Manganya or utavala zofafana ndi chilima sungamake 😂😂😂kod apule mwachedwa nazotu nthawi yonseyi munalikut
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Ай бұрын
Ndipo live ife tikufuna chilima basi
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr Ай бұрын
Ndipo inu galu manganya Kwa basi ufiti basi kulakwa Koma chomumohela munthu ndichani mmmmmmmmm takaoneni kufupika
@stevezulu2108
@stevezulu2108 Ай бұрын
African countries need different type of Democracy designed by Africans them self. The one we follow now has a lot of European influence, control, and interest. It contains ideas whose goals are to control and pin down developing. countries. China has its own type, and Russia has its own. Many European countries have what fit them better. While in Africa, we are controlled by the West. People who shared our continent among themselves in 1884 without involving any African representative. So, let's not blame our leaders so much. But let's fix come up with our own type of Democracy.
@LindaKeston
@LindaKeston Ай бұрын
Sapato ya madam yo eeh😅
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Ku Balakatu anthu anafika kukenani mkona mwapeza kulibeko😂😂😂
@HannahBandah-ks1uh
@HannahBandah-ks1uh Ай бұрын
😂😂😂
@SteveriaNyalugwe
@SteveriaNyalugwe Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no Ай бұрын
Athu kod alikuti zukhala bwanji kumeneko😂😂😂😂
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Kaya alikutiko kkkkkk
@CleverJosafat
@CleverJosafat Ай бұрын
Inu simukuwona noka akuwopa kuti akawagesa
@RhodrickBanda
@RhodrickBanda Ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 koma Malawi penapake zimaoneka ngat ena tidakali muzaka zamma 1980 nanga tikamunene munthu chifukwa choti wavala mofanana ndiwina wake kkkkkkk 🛌🛌🛌🛌🛌🛌🛌
@Lee-lee-w1r
@Lee-lee-w1r Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@RachelNkhoma-vn2jo
@RachelNkhoma-vn2jo Ай бұрын
Kkkkkkkkkk koma kuli anthu kapena kuli achina yudasi okhaokha?😂😂😂😂😂😂😂mbali yakuno chikangawa yomweyo msonkhano wa Mr chikangawa.Balaka number one pitilizani mtima umenewu❤❤❤❤❤❤ ndakukondani ndife abanja limodzi zigawengazo mutalikile Nazi zingakupheni zili ndi poison
@MonyaNtchona
@MonyaNtchona Ай бұрын
A Malawi chenjerani chakwerayo ali ndi asilikali akulwan
@MonyaNtchona
@MonyaNtchona Ай бұрын
A Malawi chenjerani chakwerayo ali ndi asilikali akulwan
@RachelNkhoma-vn2jo
@RachelNkhoma-vn2jo Ай бұрын
Ok
@BenjaminMtima
@BenjaminMtima Ай бұрын
Kodi sound yanuyo mukumveka ngati muli nchigubu bwanji?
@RachelNkhoma-vn2jo
@RachelNkhoma-vn2jo Ай бұрын
Mwamuona pharaoh ndi Yudasi anthu oipa kwambiri bola winayo asasanduke Chulu Cha mchere
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e Ай бұрын
Kodi ku Balaka anthu anapita kuti kukumangowoneka asilikali okha ndi Chakwela zikukhala bwanji
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Anafika kukenani mesa
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d Ай бұрын
Anthu ali busy kupanga zaphindu osati kukaona Chikangawa ngati ndi anawafera 😂
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw Ай бұрын
Balaka ndikumene inayambila referendum thawi ya kamuzu balaka siyogonatu ayi
@ManuelMalunga-mb4hr
@ManuelMalunga-mb4hr Ай бұрын
Watching from Capetown
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v Ай бұрын
Anthu aku balaka Mulungu akudalitseni kwambiri ndinu okonda dziko lanu anthu tikuvutika palibe chifukwa chokhalira busy ndi anthu amagazi mmanja
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Ай бұрын
Bala wooooye mwachita bwino Mr chikangawa ndi Mr chifunga osapitako
@user-ol1hf7ru1v
@user-ol1hf7ru1v Ай бұрын
Kkkkkkkk
@iangondwe6857
@iangondwe6857 Ай бұрын
leave chakwera and usi God bless them
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Koma guyz kkkkk anthu alikutiko kwangoti ziiii😊😊😊
@EviChio
@EviChio Ай бұрын
Ndipo ameneyu olo mavoti osadzamupatsa galu ameneyu. Tikuvutika
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Ай бұрын
Kkkkk Koma ndiye kwadza zatu anthu 😂😂😂😂😂😂 chikangawa yomweyo
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Munthu paliponse
@user-co6sc8om5n
@user-co6sc8om5n Ай бұрын
Aaa uchisilu basi 4 years munali kuti afiti inu Dr chikangawa ndi mr chikangawa
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 Ай бұрын
Mfiti za zikuru zikuru zikufuna kunamiza anthu zakupha anthu opanda chifukwa, akatura pasi udondo sadzawonaso ma vote ameneyu chikangawa
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 Ай бұрын
Sizoba khahlera landuku laba banthu bazonya, tinabangoni hakisabe bayabeda, kumafunika kuzayamba yamaja
@Lucy-p5s
@Lucy-p5s Ай бұрын
Great
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Manganya kutalika kwakeko😂😂😂😅😅😅
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Ай бұрын
😅😅😅😅😂😂😂😂😂😅😅😅Balaka woyee 😅😅😅😅😅😂😂😂
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 2 күн бұрын
Amalawi tiyeni tipitilize kuchita ngati zachita anthu akubalaka osamasekerera NG, onazi zikumatha anthu mkumaziseketera aziona sizinati munthu osaweluzika ndalama kumangoononga osamva chisoni amalawi akufa ndi njala otembereredwa inuu
@RobertChimenya
@RobertChimenya Ай бұрын
Chisiru Cha president ichi nchewa paja sayendatu ndye apa mwai wapezeka ayenderetu 😂😂😂😂😂😂
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Ай бұрын
Udzaziona wakula watha
@ajasikalonga3210
@ajasikalonga3210 Ай бұрын
Nosence where were you all these days
@user-ww4ei5fb7d
@user-ww4ei5fb7d Ай бұрын
Kkkkkk anthu muli kuti guys 😂😂😂😂. Yomweyo Chikangawa 😅😅😅
@JesseKanjanga
@JesseKanjanga Ай бұрын
Koma SKC udindo wauVP umkamukhala osati zinazi
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 Ай бұрын
Kodi ndiye mwati ku farm ya Demeter ku amakataniko. This farm has been there b4 iyeyu kulowa m'boma.
@user-mw8dq4is6k
@user-mw8dq4is6k Ай бұрын
Mr chikangawa ndi VP nde akuyendatu ngat campaign yayambika kale😮
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 Ай бұрын
Sikulina anthu azapanga transfer ena Azapita ku Zambia ena ku Tanzania 🇹🇿 chifukwa cha mavuto boma silibwino ndalama zimabedwa kwambiri chithandizo palibe
@prettytambala5687
@prettytambala5687 Ай бұрын
Koma mpaka kukayendera nyemba like seriously apule?
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Ай бұрын
Kusowa chochita
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON Ай бұрын
Mukufuna kumangoba zitukuko chamuthu chabe osati ndi boma linalima zimenezo mabodza basi 😅😅😅😅😅😅😅😅 koma azitsogoleri Enawa eeeti
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON Ай бұрын
Sazidziwa zawulimi mukungo tha mawu palibe chomwe chikulowa mmakutumo. Koma zomwe akuganiza akachoka kumeneko ndi kukaba mitsonkho ya thu avutika ba mutamuwuza zamitsokho nde nde eeeeeee sngajowejowetu Tsinzina mntole mr Raza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@muhammadisaid3968
@muhammadisaid3968 Ай бұрын
Zachita bwino osapita anthu, chipani chokupha chimenecho, chondee ma boma ena mutengelepo phudzilo osawasekelera akanganya amenewa , I'm White Willison from machinga T/A chamba , Lulindi villege
@DavisonKambia
@DavisonKambia Ай бұрын
Bomaloooooo!¡!!
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e Ай бұрын
Utsi watengekatu nawenso ukwela ndege pompano nd zigawenga zimenez😅
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke Ай бұрын
Kubalaka kuno tinali busy kusaka ya thumba lachimanga mpata opita Kwa apulesidenti sitinaupese😂
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Ай бұрын
Abale azanga musiyen manganya ,usamunyoze zakutsogolo sizidziwika , adzatero Ali ana anu Ali pa mpando wa up resident
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Ай бұрын
Ife tidya masambao za ziii munali kuti nthawi yoseyi aaaaa ife si zisilu
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Ай бұрын
Ulimu wanu ma pulezdent athu ❤❤❤❤❤❤
@bristonmwenga5286
@bristonmwenga5286 Ай бұрын
Wow!what a good initiative
@NellieMaulidiChimanda-p5t
@NellieMaulidiChimanda-p5t Ай бұрын
Tiyeni titenge ngongole za Neef kuti titukule Business zathu ndi magulu a business Ndalama zimene akhazikitsa a President
@user-im8bv2el9b
@user-im8bv2el9b Ай бұрын
Kodi Michael usi wavala kut afanane ndi big akunamatu uyu komanso iye kuzavula chipewa. Manganya iwe ndiwa map to see tikuziwa
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 Ай бұрын
Mr chikagawa akuondatu mzimu wachilima ukuzuguza
@FrankKambwani
@FrankKambwani Ай бұрын
Idzidzi sidzingapangitse kutsitsa katundu ndi kukweza mphavu Kwacha
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Ай бұрын
Ngati ndinu mbuli ingokhalani musaonetse umbuli wani
@FrankKambwani
@FrankKambwani Ай бұрын
Inuyo kuzindikira kwanuko kulipati?
@giftblack7690
@giftblack7690 Ай бұрын
Chakwela akumukonda manganya Chifukwa choti akudziwa kuti sangamusokoneze olo zinthu zikulakwika akudziwa kuti yemwe akanandisokoneza ndi chilima anamupha uja munthu wachabe uyu zoti ndale ndi mfundo wowinayo awine koma osati kuphana nde paliso ndale ngati mukuphana atsogoleli kusokoneza ndale kumeneko
@user-qb4pj5yy5b
@user-qb4pj5yy5b Ай бұрын
Balaka! Balaka! Balaka! How many times have I called you?😂
@UsumanLuwayo
@UsumanLuwayo Ай бұрын
Muwaudze akadulitse magalasi ofanana ndi nkhope yawo a vice president, ma galasi akuwpatsa busy
@hesidomi
@hesidomi Ай бұрын
Komaso kodi mwati nkwawa zunguwa akatero azizakamba ngat Iwo apa
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Ай бұрын
Chikangawa ndi chifunga akuti akukayendela chiani
@MeriaMasinga
@MeriaMasinga Ай бұрын
Mayi chakwera ndakaika ngati akuvanawo
@BlessingsSeleman
@BlessingsSeleman Ай бұрын
Kod zolimadzo zoti zalimidwa kuchokera kundalama yatu yamisoko kapena dzida ngati zimenezi zoti sizadzungu koma tagula toka nditimisoko tathu tiziona Lori poti mukulimbika kuonesa mukuti mamega famu kod ndi anthu kapena angelezi
@user-ss9sr7bi6f
@user-ss9sr7bi6f Ай бұрын
Ulimi ndiwabwino kwabasi kananji othilira umapindula mwachangu
@bristonmwenga5286
@bristonmwenga5286 Ай бұрын
Ngati sanapite so what?good show a PULE
@AmosMilanzi
@AmosMilanzi Ай бұрын
Boma la MCP kukamba mowona mtima labwera kudzakhala komanso kuthandidza a Malawi.
@PraiseMitton
@PraiseMitton Ай бұрын
Kodi tinene kuti a chakwera akuonda ndichani makamaka 😂 mwina ndi bakili muluzi tv eti kkkkkk achoke!! achoke!! Chakwera achoke!! Achoke.
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y Ай бұрын
Kapoli wankulu adafika mu Mbalaka 😢😢😢 uyo wamfupiyo Yudas 😢. Ayi zikomo 😢😢😢
@magex887
@magex887 Ай бұрын
Chikangawa crue
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Ай бұрын
Athu sangapiteko akulira maliro a chilima NDI Lucius Banda
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Ай бұрын
Madam Ake a VP ndioukilatu
@BMDMasulani
@BMDMasulani Ай бұрын
Mufuti yonseyo ngati mukupita ...kunkhondo zikumakoma bwana usi akayenda okha ulimi ukuchita kukongola koma bwanji mifuti choncho?
@HaliJana
@HaliJana Ай бұрын
😂😂😂😂 ZIKUTANTHAUZA KUTI CHAKWERA AKAMUVOTELE NDI ASILIKALI NDI APOLIC AKEO KKKK CHIKANGAWA YOMWEYO
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Ай бұрын
Ku mangochi aja avotera councilor wa mcp ndi asirikali?
@brownpetroscoplandmalemia1551
@brownpetroscoplandmalemia1551 Ай бұрын
Wasting Tax payers money
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Ausi zobvalazo sizikukukhalani bola Chilima zimamukhala😂
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
😅😂😂😂
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms Ай бұрын
Kulibeko anthu bwanji kodi
@RebeccaNvenya
@RebeccaNvenya Ай бұрын
Chikangawa ikungoononga ndalama ndinu agalu kwabasi
@BlessingsBanda-ol2pg
@BlessingsBanda-ol2pg Ай бұрын
Azalira chikangawa😂😂😂😂😂😂😂
@user-rz6vf9wh5c
@user-rz6vf9wh5c Ай бұрын
Chakwera ndiwowinawina palibe angamake
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Ай бұрын
Mudzafa ndi ukapolo onyaweza kadzinyoza , mwina umapwza mphoto
@williamsalexmbonga
@williamsalexmbonga Ай бұрын
Zama big izi guys ndipo MCP siikugonja amtaaa
@AlexMlenga-kc5cz
@AlexMlenga-kc5cz Ай бұрын
😂😂😂😂 km monica yekha ulusi amayika sangachite kufuna phunzitsi 😂😂😂😂😂😂
@MeriaMasinga
@MeriaMasinga Ай бұрын
Balaka ndiyozindikira siphwekesa akupherani mayi shanil zimbii
@MphatsoMhoney-xn2ft
@MphatsoMhoney-xn2ft Ай бұрын
Amanganya oro kuvara jombo osatalikabe
@stevenbanda6665
@stevenbanda6665 Ай бұрын
Kwanti ziiiii anthu akubalaka ulemu wanu ndinthu
@finiasmtete
@finiasmtete Ай бұрын
Gwilani ntchito yanu yabwino a Vp.Mwayamba bwino
@YohaneColumbus
@YohaneColumbus Ай бұрын
Dr. Chikangawa Chifunga mwapeza nyekhwe, balaka siimasekelera zopusa. Rest in peace Dr. Saulos klaus chilima
@barnettbmphanda108
@barnettbmphanda108 Ай бұрын
Olemba zoyipanu kalembani nsanje ikakula ndi choncho
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Ай бұрын
Yakuli andu ambili 😂😂😂 2024 mtionazindu 😂
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Ай бұрын
Koma mavalidwe amonica yooooo9😂😂😂😂
@TinoCharamba-hr9el
@TinoCharamba-hr9el Ай бұрын
Kkkkk km zilikotu mangabya kuuluka ulusi monga malemu chilima
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Ай бұрын
Anthu aku Balaka mumakwana, mumaopadi mulungu
@MarvellousTech-kz6no
@MarvellousTech-kz6no Ай бұрын
Unyozawe ukamaliza kunyoza mphoto imene ulandire utionetse
Touching Act of Kindness Brings Hope to the Homeless #shorts
00:18
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 18 МЛН
❌Разве такое возможно? #story
01:00
Кэри Найс
Рет қаралды 6 МЛН
At the end of the video, deadpool did this #harleyquinn #deadpool3 #wolverin #shorts
00:15
Anastasyia Prichinina. Actress. Cosplayer.
Рет қаралды 16 МЛН
TIKUFERANJI 18SEP2015
27:06
Edson Gunsalu
Рет қаралды 84 М.
Vice President Chilima's visit to the SVTP (Chichewa Interview)
1:47
Shire Valley Transformation Programme
Рет қаралды 64 М.
A MOSES KUNKUYU KU PROGRAM YA KULINJI
39:13
HOT 265
Рет қаралды 18 М.
VICE PRESIDENT CHILIMA'S VISIT TO THE SVTP (Meeting and Interview)
9:34
Shire Valley Transformation Programme
Рет қаралды 2,7 М.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Zodiak Malawi
Рет қаралды 86 М.
HOT CURRENT KUNG'ALULA MOSAONA NKHOPE 1 September 2024
55:12