PRESIDENT CHAKWERA WAYANKHA MADANDAULO ONSE A AMALAWI PA SPEECH YAKE YA LERO PA 27 NOVEMBER IYI

  Рет қаралды 9,604

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 200
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 3 сағат бұрын
Ya Allah Mulungu modzi amene mumamva kulira kwa ana anu tipaseni sogoleri oopa inu wachikondi ndi anthu ake taonani dzikoli tataika chfukwa chausogoleri oipa ulipanowu tichosereni satan watizungulirayu ya Allah ameen🤲
@PatriciaChibwato
@PatriciaChibwato 3 сағат бұрын
Ameen
@whitephiri839
@whitephiri839 2 сағат бұрын
Ameen
@HishamMalikha
@HishamMalikha 2 сағат бұрын
Ameen
@EmmaEmma-q4u
@EmmaEmma-q4u 2 сағат бұрын
Amen
@RahimYusufu-u2b
@RahimYusufu-u2b Сағат бұрын
Aameen
@Loy_Solutions
@Loy_Solutions Сағат бұрын
Zimandiwawa ndi zokuti ambiri amene timakhala ndi nkwiyo sitilembesa kuti tichose ndi ballot paper
@matthewskatete4763
@matthewskatete4763 53 минут бұрын
Ndalembetsa ndipo uyu ndimuthothola ndi vote
@LawrenceKachisa
@LawrenceKachisa Сағат бұрын
mpunga wa ku lndia bwana tigawileni ana anu akufa ndi njala.Musatengere chipwni tonse ndi amalawi popeleka paja adapeka kwa amalawi osati wachipani chonde.Zilipowe zizingatinthandize ku Malawi zimene akupanga azathu ku Lilongwe ndikuonesa sankho pa mu dziko la democry.Pepani bwana tili ndi anthu wolumala,wokalamba ,amisala,ana komanso azimai sangathe kuthawa chonde .This is the home heart of Africa.Let us unit as one Nation one country
@AbdullahSaeed-tg1cm
@AbdullahSaeed-tg1cm 3 сағат бұрын
People lost their hope in u.....no matter how beautiful your English will be... never will pple believe u again .....
@LloydBotoman
@LloydBotoman 2 сағат бұрын
To be the honest mr president mwationongera dziko
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 2 сағат бұрын
Umadziitumikila wekha ndi Ana ako iwe
@ReinfordPatricNyondo
@ReinfordPatricNyondo Сағат бұрын
Chakwera dziwa zinthu izi Nyumba rent supeleka Madzi ku water board sulipila Magetsi sulipila Nsima/ndiwo sugula Umadya ndi kumwa misonkho ya amalawife. Ufulu wathu okhala kumalawi watiswera, tikati tiyankhule unatuma zigawenga plus apolice kuzatisokoneza. Vote yanga suzayiona mwana wa njoka iwe.
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo 3 сағат бұрын
Kodi butchery ija simumaziwa kuti zipangisa njala, izi zakukulilani bwana😀😀
@Msukwaprecel
@Msukwaprecel 2 сағат бұрын
Kodi mpunga wa ku India amene amalandilako pls tiuzeni
@umalimaganga
@umalimaganga 3 сағат бұрын
What about the stoppage to registration and firing the NRB and MEC chairs?
@JamesBlack-t6o
@JamesBlack-t6o Сағат бұрын
Zaziii za manyi mungopeleka mimba kwa Ana present wakuba ndi kupha uchoke we need malawi to be a better country like before
@YusufMasi
@YusufMasi 2 сағат бұрын
Paja munati mukazalepela kuyendesa mboma muzapanga lizainu nanga lelo 4 eyes Tulane udindo mwawulemu mwalephela kuyendesa zikomo chokani papando mulibe zelu zoyendesela ziko
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 сағат бұрын
Munthu wa kumudzi sangakwanitse kugula feteleza pa k120,000.00 thumba limodzi. Zinthu zadula × 20 since you took government. Wabweletsa umphawi iwe Chakwera.
@emmanuelkadzera1328
@emmanuelkadzera1328 2 сағат бұрын
The worst administration ever Palibe chanzeru apa. Zikungioonetseratu kuti Mzeru nzochepa
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 3 сағат бұрын
Kkkkk chakwela tangotulani udindo phasi palibe ukukamba apa waonetsa a malawi 🇲🇼 nyekwe iweyo, muthu opanda chisoni iweyo , ngati unamupha chilima anakumvela chisoni kuti ulowe boma, amalawi otsalafe utiona ngati ndani , galu iwe
@DendeyaMichael
@DendeyaMichael 3 сағат бұрын
Azavota ndi omwewo amene uwapade vingoma iwe kuno yay ndiwe waboza wanthu wafwawafwa ndipo ukt wawona mwahuno za njala aaaaaa kukoko
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 2 сағат бұрын
Ndipo dada uyu mutu wakhe ukwenda cha nimuzeleza chomene watisuziska mweee
@DanielKagona
@DanielKagona 3 сағат бұрын
My vote DPP ❤❤❤
@williamyusuf259
@williamyusuf259 2 сағат бұрын
Will vote you out
@clairelewis5309
@clairelewis5309 2 сағат бұрын
Which God he is thanking,god ya zinyau???????😮
@StewartGoma
@StewartGoma 3 сағат бұрын
Really chakwela u can address the nation with that silly speech how long people has dying with hunger empty brain
@clairelewis5309
@clairelewis5309 2 сағат бұрын
@Stewart very silly indeed.Nonsense Speech waste of time ,chikulilenji chimunthu kupha mwana SKC
@williamyusuf259
@williamyusuf259 2 сағат бұрын
Songiso ameneyu
@JustinChinombo-dy6tp
@JustinChinombo-dy6tp 2 сағат бұрын
Ngati president wokanika wopanda zeru nde uyu chakwera, ndipo amalawi lero titamva kuli national address timadikira kuti upanga resign mnthu woipa iwe
@MasaukoKatunga
@MasaukoKatunga 2 сағат бұрын
Achedwa kuyankhula nde zosadabwitsa mwina watuma kuti ayankhure
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 3 сағат бұрын
Akunama Chakwera osamunvera ameneyo akungodya ndi banja lake.
@EnerstManess
@EnerstManess 3 сағат бұрын
Mbuzi ya president
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 сағат бұрын
Udachimwila dziko la Malawi komaso kumwamba dziko lino silizayenda bwino unless tisithe msongoleri
@JosephKayira-j2p
@JosephKayira-j2p Сағат бұрын
But in karonga there was no drought 😥😥
@temwekamlenje4358
@temwekamlenje4358 Сағат бұрын
Chonsecho akudziwana ndi zigawengazo bwanji mukuyankhula lero atakudzudzulani kaye
@GanizaniNyson
@GanizaniNyson 3 сағат бұрын
Chilling cha sogoleli mphaka chikangawa chopusa mu Africa mose chitsilu cha president ndi Lazarus chikangawa chakwela mbuzi yamuthu
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 36 минут бұрын
Tikudikila leport yandege muyakhuleso sitinaiwale munapha athu osalakwa za say thank you zo tilinazo tchito
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman 2 сағат бұрын
Zazi Bolanso bon kalindo amayankhula zanzeru 😂😂,ukuona ngati ku Lutcheza ubwera ngati ungachite makani uzayenda mwauyo uyo.
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 2 сағат бұрын
His face is telling a big story Zaziiiiiii Tulani pasi udindo ayona inu
@clairelewis5309
@clairelewis5309 2 сағат бұрын
Depression face despite ngende yo kkkkk😅
@williamyusuf259
@williamyusuf259 2 сағат бұрын
Bwapini kkkkkkk
@NosiphoMazibuko-e9z
@NosiphoMazibuko-e9z 3 сағат бұрын
Mr president you failed 4years ndeno zomwe ukulangulasi ukwanisa kuzichita kodi now is two later mr president you should step down you failed already chikangawa
@SumayaOsman-de2dn
@SumayaOsman-de2dn 2 сағат бұрын
Choka iwe wakupa speech less dr mayenda yenda😮😅😮
@Msukwaprecel
@Msukwaprecel 2 сағат бұрын
Sinnaoneko munthu ofoila komanso upusa ngati uyu
@AliPonda-m4s
@AliPonda-m4s Сағат бұрын
Kkkkkk😂😂😂😂noses president nde zichachani zimenezo
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 2 сағат бұрын
Sitidya chizungu amalawi ukapume iwe 2025 watinzunza
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman 2 сағат бұрын
Zazii ,muziyankhula chichewa ,adakuvoterani ndi akumudzi siachizungu.
@FrankKamundi-l1s
@FrankKamundi-l1s Сағат бұрын
Dzipani dzonse munapanga nadzo mgwirizano dzinakuthawani anthu oyipa pamaso ngati anthu mumtimamo athakati eni eni
@AssanShaibu-s8b
@AssanShaibu-s8b Сағат бұрын
Ha nanga monse muja mumasiya zinthu zikuonongeka Inu munali kt
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 46 минут бұрын
Kalembela wake uti mbuzi iwe? Tinakuza kuti smart matic icoke sufuna, mec icoke sufuna colinga mubele mavoti nde tikukuza kuti tiyamba kumanga iwe ni cimwendo cifukwa ndinu munatuma dzigawenga zija anthu oipa inu2025 mukupita zausilu mmalawi muno sitifuna
@temwekamlenje4358
@temwekamlenje4358 Сағат бұрын
Chinderelite ukunamiza ndani
@JudithMbuba
@JudithMbuba 2 сағат бұрын
Ndipo sachoka ngat smutha chizungu dikiran chichewa apm anu aja amyakula chichewa mbbuzi inu
@HerbertTchautchau
@HerbertTchautchau Сағат бұрын
Km ichichi ndiichisiru kwambiri ndithu ndipo uzakafa ukuzapsa moyo wakoonse Ambuye sazakukhululukirayi ena paka panopo ku zomba kuno sanalandire paka panpo
@attaufeeqmuhammad718
@attaufeeqmuhammad718 2 сағат бұрын
Kape okutha kuyankhula chizungu koma mmutumo phala lokhalokha
@RehannaZenus
@RehannaZenus 50 минут бұрын
Mcp my vote ❤❤❤❤❤
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 47 минут бұрын
Aah u are 1 out of 1 million 😂
@AssanShaibu-s8b
@AssanShaibu-s8b Сағат бұрын
Aise tulan pansi udindo chifukwa iwe ndi wakupha komanso ozudza opanda chisoni ngati iwe , gule ngati iwe, kd gule angayendese dziko
@AssanShaibu-s8b
@AssanShaibu-s8b 56 минут бұрын
Chokani apiseni adad akulandiren
@GustinoKamanga
@GustinoKamanga 3 сағат бұрын
Machende ako Lazarus wanva pakamwa pobwafukapo😂😂
@DendeyaMichael
@DendeyaMichael 3 сағат бұрын
Kkkkkkkkk
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 2 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@MosesDaniel-h7w
@MosesDaniel-h7w 2 сағат бұрын
Palibe chanzeru mwakamba achimwene. Pitani muzikadya za chankhumi ku assembles
@YamzyNedson
@YamzyNedson 2 сағат бұрын
Uyuu akungofunika ma demo anyooo kut achokepo pampando coz Malawi is now worst than ever before.😢
@HestingsSalimon
@HestingsSalimon 3 сағат бұрын
Azikwanje amayenda ndi apolice ndiye zigwawengazo agwila zake ndani
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 2 сағат бұрын
Uyu ndi wabodza asakidwa bwanji yet apolise anachita kuuzidwa kuti asalimbane ndi azikwanje
@allieadam3235
@allieadam3235 3 сағат бұрын
Not loosing hope til when mr President?
@AssanShaibu-s8b
@AssanShaibu-s8b 55 минут бұрын
Yomweyo Galu iwe
@donnetbandamichael5233
@donnetbandamichael5233 Сағат бұрын
Nice English language ❤❤
@chachaamoah3592
@chachaamoah3592 57 минут бұрын
Nice English koma brain nje
@JudithMbuba
@JudithMbuba 2 сағат бұрын
Apm awakuwiza kumwanza akut mwakula.
@FundoNdeketeya
@FundoNdeketeya 3 сағат бұрын
You don't think my friend keep fooling Malawians the Wil come after you soon 😂😂😂
@wacksoniron
@wacksoniron 2 сағат бұрын
Kalata imene awelenga apuly walemba ndi kunkuyu ndi chinwendo
@ChimwemweW.Chibisa
@ChimwemweW.Chibisa 2 сағат бұрын
But all the support you're citing here are nowhere to be seen
@BrianJoe-z7u
@BrianJoe-z7u Сағат бұрын
Chimuthu chopanda manyazi ndiku lakhula bodza ngati uyu Sina muonepo koma chakwela chakwela eeeee ayii
@ReubenMgaiwa-e1g
@ReubenMgaiwa-e1g 2 сағат бұрын
Mwati nthandizo lonse mwalengezesa apali mwapitusa maboma mwatumizako ndiangati mwa 25 mwawatchulawa
@YunusuMaulidi
@YunusuMaulidi Сағат бұрын
Mmalawi muno anapita ku
@OusmanBen-f4o
@OusmanBen-f4o 2 сағат бұрын
Very powerful and meaningless speach for not being fulfill the promises speach,l'm tired of u Mr president Chakwela Chikangawa
@KodwaniWeston
@KodwaniWeston Сағат бұрын
Kagule matewela paja wapeleka mimba usatibowe apa
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 2 сағат бұрын
Uyi ndiofunika kumukoka khutu chisiru chimenechi chationongela dziko
@WiltonSingini
@WiltonSingini 2 сағат бұрын
Muziyakhula chichewa inu malawi ndife achewa tumbuka Tonga not chizungu chanu
@mkandawirem610
@mkandawirem610 2 сағат бұрын
Osathawira chizungu tiyankhureni chichewa so that anthu a kumudzi aja azimva zomwe mukuyankhulazo,,,
@P.Bilali
@P.Bilali 2 сағат бұрын
National address 😂
@DysonKamama-yh7hq
@DysonKamama-yh7hq 3 сағат бұрын
The help is on the way,mmene unayambilamuja kumangolankhula with 0 action kuyambila pa campaign ya 2019 up to now nothing tangible
@AusteenSumael
@AusteenSumael 3 сағат бұрын
And this is mumu pro max 😢😮😢
@FrancissMackson
@FrancissMackson 2 сағат бұрын
Vot ili mumtima wusawone ngat tos nda utm asee akakhala pitala sulamulilo wake tinawuwona kale nde manyaka bolaso amweyu
@GregoryMchinyira
@GregoryMchinyira 3 сағат бұрын
Mbuzi yagalu iyi palibe amadziwa koma Kuba misonkho nkumapha anthu ndi njala
@user-nt5yn2im6t
@user-nt5yn2im6t 3 сағат бұрын
You are a great lair where were you distibuting this maize? Had you have used all this monies malawians couldn't reach this stage don't cheat the doners looking for another more money to pocket them
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 сағат бұрын
Too much lies mr. President, you talk nice but on the ground 0.
@temwarachaelkhonje3733
@temwarachaelkhonje3733 3 сағат бұрын
Akulu........tayankhulani fundo zeno zeni mchichewa inu.......za slang izi sizithandiza....aaaaaaaah bodza leni leni
@clairelewis5309
@clairelewis5309 2 сағат бұрын
Slang ,nkhope ndi chimtima choyipa sizikugwilizana ,mxiíiiiii
@IbruraAmadu
@IbruraAmadu 3 сағат бұрын
Machende ako....
@MartinMartin-d3g
@MartinMartin-d3g 2 сағат бұрын
Machendeko wamva namachende iwe pa nyelopako
@Sofi-p1v
@Sofi-p1v 3 сағат бұрын
Anakuika ndani galu iwe Unalowera. Chifukwa chama demo
@DeeHMugonya
@DeeHMugonya 2 сағат бұрын
Sipano STIMA ija mumati ndimafuta mmesa
@MaggieMasiano
@MaggieMasiano 3 сағат бұрын
Mr president you are very stupit let us vote by manual and let obsevars to come we are very tied with you.
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w 2 сағат бұрын
Zavuta awa😂😂😂
@PatrickKapendo
@PatrickKapendo 2 сағат бұрын
Kodi a malawi tikakhala m'makukamu rikumawona atsogoleli wowopa Mulubgu alikuti?Ndafusa izi daladala palibe ndi munthu m'modzi angabwele kuti akuzaombola a malawi ai chokela omenyela ufulu akumenyela m'nyimba mwawo kuti akayiteme ndi ana awo mawailesi nawoso akugwira manyumba kuti moyo uzifewa ife anthu ovoti timachosa mtsogoleri papando ndivoti koma tikumka tivuti chifukwa cha anthu omwe ali otsogola pa maphuzilo ndiomwe akubwelesa kusakhazikika kwa kayendesedwe ka dziko lathuli chifukwa tnotse amene mukuoneka kuti ndinu anzeru zakupguzira mukulimbana ndi dziko lanu mukhale atsogoleri pamene malawi ndimodzi uyu koma zonse zichitika mavuro sali kwa inu muli ndizochitanu ai koma ife omwe tili kutali nanu ndipo mukulimba mtima kulakalaka nkhondo cholinga mukwanilise zikumbokumbo zanu koma amalawi sali mwakufuna nkhondo ai koma ana awanthu omwe ali gulu lakuzindikila kupembera chimenecho koma Mulungu alipo
@PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
@PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 2 сағат бұрын
Muchite manyazi ndi mwana uyu wa zaka 36 Ibrahim wa ku Burkina Faso for only two years he has transferred his country and he is recovering many support from developed countries...you can't learn from this young man? Too late to save Jerusalem
@PetrusTlhokwane
@PetrusTlhokwane 3 сағат бұрын
Sidzayiwala president wamisala ngati uyu ku Malawi kuno chimunthu choipa ichi
@FatimaSamson-d7w
@FatimaSamson-d7w 2 сағат бұрын
Pasana pake chikangawa
@PetrusTlhokwane
@PetrusTlhokwane 3 сағат бұрын
Ndipo kumafunika kuchipangira mademo anyooo chichakwelacho chituluke basi
@JohnJumah-yf7qt
@JohnJumah-yf7qt 2 сағат бұрын
Chokani achisilu inu palibe chomwe mungatiuse
@JudithMbuba
@JudithMbuba 2 сағат бұрын
Ndipo sachoka muzawona inu ozunza ma albino
@courageouslondo1986
@courageouslondo1986 3 сағат бұрын
Amayamikila maiko not kupanga adress people of Malawi
@franksalanje9191
@franksalanje9191 3 сағат бұрын
Unabwelesa njala mayesandiwe ndiye ukutichani apa
@crytoniegrantliffa2431
@crytoniegrantliffa2431 3 сағат бұрын
Koma chakwera ndi president wopanda mzeru ndithu Aaaaà awa ndiye bolani mayi Joice banda
@clairelewis5309
@clairelewis5309 2 сағат бұрын
Mamina okhaokha
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 23 минут бұрын
Fiti uyu galu kwabasi ntchewe iyi chili kukoma chilima ndicho ichi
@HildaMbizi
@HildaMbizi 2 сағат бұрын
Vyaziiiiii vyambula na fundo utm ndiyo nizamuvotera
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 2 сағат бұрын
Ndipo chinafundo cha chizeleza ichi palije na kamo ako ayowoyapo kazelu Ntchewe iyi
@AlexanderKamanga-i2l
@AlexanderKamanga-i2l 3 сағат бұрын
Ndife amalawi choncho sindife azungu,uchisilu uja ndi umenewu
@KingstonPhiri-g5h
@KingstonPhiri-g5h 3 сағат бұрын
Kumango namiza anthu koma iweyo chalakwe kkkkkkkk
@cosmaschisale-z7k
@cosmaschisale-z7k 3 сағат бұрын
Muwagwire nokha poti ndi anthu Anu omwe azikwanjewo
@SuperBuild-k9s
@SuperBuild-k9s 3 сағат бұрын
Bwanji nditukwane kamwa ngati ponyelela pa bakha
@EdsonKamwendo
@EdsonKamwendo 3 сағат бұрын
Chimene ukukakamilira pa mpando ndi chiyani mfiti iwe
@HanifuKalenje
@HanifuKalenje 3 сағат бұрын
Manyaka a president mbudzi
@EnerstManess
@EnerstManess 3 сағат бұрын
Kukhozedweso mademo tione ngat sikuzalephelesedwaso
Results awaited as Swapo faces strong opposition
12:31
Newzroom Afrika
Рет қаралды 1,7 М.
Twin Telepathy Challenge!
00:23
Stokes Twins
Рет қаралды 119 МЛН
How Much Tape To Stop A Lamborghini?
00:15
MrBeast
Рет қаралды 235 МЛН
Farmer narrowly escapes tiger attack
00:20
CTV News
Рет қаралды 11 МЛН
Чистка воды совком от денег
00:32
FD Vasya
Рет қаралды 2,7 МЛН
Didablk And R.Rei & Gums - umgido
2:35
Didablk
Рет қаралды 36
Electricity Minister updates on KRN 2 prepaid meters
18:14
SABC News
Рет қаралды 12 М.
Eksklusif: Prabowo Subianto Bicara | Mata Najwa
1:49:52
Najwa Shihab
Рет қаралды 23 МЛН
Twin Telepathy Challenge!
00:23
Stokes Twins
Рет қаралды 119 МЛН