Akatundu awa!!!!! He is so courageous!!! speaking with no Fear,, he sounds like Chilima in his Bond of courageous.
@MasausoMsiska-rz3idАй бұрын
Munthu koma uyu speaking without fear....Big up Mr chihana
@lloydjeremiah2250Ай бұрын
eeee kma this man is so courageous
@user-fz3gu2ez1o26 күн бұрын
Eeeeee Koma SKC 😭😭😭😭 Ine imfa iyiyi.. Imandiwawa.. eeeeee
@JesusChristFollowers-ez9zuАй бұрын
Mr. Chihana is man of his word, ndipo zikupanga prove that he is the son of his father. Amenewa ndi amene anathema ndi kamuzu, apa chakwera akuchoka, ndavomereza anthufe sitimafa koma maonekedwe athu ndi amene amasintha
@arnoldkaikenkayangeАй бұрын
Afford my vote
@magex88719 күн бұрын
Koma ndiye.big up chihana❤
@iconiclife681123 күн бұрын
So powerful bwana We need this Energy in our country honestly achinyamata ambiri akufuna ngati iziiii
@HopeJaffariАй бұрын
Ramaphosa wanthu waku Malawi 💪💪
@NoluvuyoMatutuАй бұрын
😂😂😂😂even me I thought like that ndtaona pic yake poyamba
@memoryziyaya2593Ай бұрын
true ..they are resembling very 😅
@kusekejere29 күн бұрын
SKC has gone leaving a message that malawi is the land with possibilities but the problem are the leaders. What a humble guy. Rest well sir
@jonasmunthali848Ай бұрын
I didn't know dis guy can talk lyk dis🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥
@hopesato29 күн бұрын
Anthu akwiya mkoz
@jonasmunthali84829 күн бұрын
@@hopesato ndaonaso🙌
@luciatembo-e4f29 күн бұрын
Straight wise proud of you chihana🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@papelariareis.e.6 күн бұрын
This guy is very strong 💪 🎉🎉🎉
@amandamoyo7156Ай бұрын
God protect Mr Chihana....we love u
@HappyAbyssinianCat-xt2bmАй бұрын
Km ndi zoona chakwera popanda chilima sukanawina galu iwe chakwera unapanga ndiwolotse ndikakutafune galu iwe chakwera dzimaso dzako unatiphera ngoni wathu
Ndiye chilima popanda chakwera adakhala vp tisamalakhule mbali imodzi chilima tu adali vp from 2014 up to 2024 ineyo ndimafuna nditadziwa zomwe adapanga kapena ankadikila adzakhale President kuti inuyo mudzayamve kusangalala to me i don't know thanks God ineyo ndimadziyimila from nyumba ya maudzu to mansion bra inuyo dikuilani chiloma wina kuti moyo wanu udzasithe
Zomvetsatu chisoni kwambiri. Ndikanakonda a ku Banja akanaketsa Zopusa zimenezo. Chidziwika ndi chakuti SKC ndi CHIHANA were not Friends. Ngati zomwe akunenazo ndi zoona tione umboni wake. Atiuze nthawi, tsiku komanso Audio or ma message olemba. Musaiwale kuti ndi yomweyinso anabweretsa nkhani yonama ku Nyumba ya Malamulo atafunsidwa za umboni anakanika kupereka. SKC awuza bwanji iyeyo kusiya kuuza utm members?. CHIHANA ndi ONAMA kwambiri
achihana uko muli uko Pala pangawa mwayi mwizeko ku nkhatabay mkondezi area I beg
@smashingogden4236Ай бұрын
We soldier on!... very brave mr chihana junior 💪🏼🇲🇼... speak it like it is....
@ruthkundwe7448Ай бұрын
No rest for the wicked
@PemphelaniTchezaАй бұрын
Chilungamo sanong'onotu 😢😢with heart broken
@karenn296913 күн бұрын
True voice of a leader, thus why he was the first to demand enquiries into the death of Chilima
@ClaraMkandawire-d2k27 күн бұрын
Kuyankhula koma ukuuu aaaaseeeee👊😂
@PatrickKabudulaАй бұрын
You are not alone mr
@SigoMwАй бұрын
Ndipo simunati akanantchulidwabetu chilima mpaka mpaka muphulikeee amfiti inu
@user-jm8kw9gw2dАй бұрын
Aford the mother of all political parties in Malawi, it's your time Big Man, mcp is afraid of you in Jesus name
@shonmike-su7qk29 күн бұрын
Mcp inalakwitsa kwambiri kuphwanya lonjez ndipo izizi zimenez amalawi zatikwiitsa kwambiri from molongolo Tanzania
@user-ko1lk3br4r23 күн бұрын
Km Inu simudzalowapo mboma truth
@tumpalechihana5073Ай бұрын
Our own leader
@NysonStandy29 күн бұрын
Go ahead mr Cihana
@WAZAKILIBANDAАй бұрын
Kumeneko nde kulankhula dad🥰🥰🥰🥰🥰
@MirriamKambale29 күн бұрын
Chakwerayutu si m'busa anthunu mangosokoneza munthu uja ndi nthakati. Mfwiti ya tyala iliye na mzeru ingaphepese yai after those words pray hard angakusowetse
@user-dh8ho2qt4h21 күн бұрын
❤❤❤ love you dad. We all cry our vice president chilima.😢😢😢
@WilliamNyirenda-xq4km27 күн бұрын
Viphalileni bwana viwanthu voina mitu ivi you are my vote
@MadalitsoTamayenda-ez5pj28 күн бұрын
Powerful voice
@JusticeDamalekani13 күн бұрын
Akamuna awa❤ osati akapamba enawa😢
@user-oc9vl9xz8eАй бұрын
Kumeneku ndiye kuyankhula Kwa Mtsogoleli wadziko kuyankhula mosaipa wina aliyense
@PiliraniMalemia2 күн бұрын
God is watching from a distance
@RoseTaika7 күн бұрын
So courageous
@user-ty4pq5ub3qАй бұрын
RIP CHILIMA....😢😢. Auzeni live live..akapukuu ..nduna zokuda mbuuuuuuu
@unstorice4045Ай бұрын
Appreciate you chihana🎉🔥🔥🔥🐐
@ConnexMtika16 күн бұрын
Ilov AFORD leader fearless
@OsimanIbnAkimАй бұрын
Your the best speach 💪💪
@PemphelaniTchezaАй бұрын
We have lost a great leader SkS because useless party mcp😢😢
@WilsonMillion-p2u11 күн бұрын
Ndiye cadet wachabechabe uzithupsya amalawi kuya nkhula chilungamo.apa ngakhale wina azinama koma imfa ya chilima ipase phunziro