MALAWI ADABWA NAYE DAN -LU PA NYIMBO IYI NDIPOSO GALIMOTO YAKE IYI ~ NDALAMA ZO WAZITENGA KUTI?

  Рет қаралды 82,629

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 423
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i Ай бұрын
Ndizomwe akumpakulila nyembazo , more fire chimwendo
@JenniferMkandawire-i6t
@JenniferMkandawire-i6t Ай бұрын
Muchedwa naye dun lu mutulukeni angofuna ndalama sakuona amalawi akuvutika kwambiri
@MUSTAFAJAMES-km6yg
@MUSTAFAJAMES-km6yg Ай бұрын
Apm booma 🤞👌
@Cathy-oc7vd
@Cathy-oc7vd Ай бұрын
Boma ndi lomweli ❤ MCP is here to stay... beautiful song
@SteveDuncan-l7o
@SteveDuncan-l7o Ай бұрын
Kupusa kwen kwen
@AusmanYusuf
@AusmanYusuf Ай бұрын
Naweso Kamineni uko
@RichardNjoloma
@RichardNjoloma Ай бұрын
Iwe kuno ku Balaka kulibe akugwilizanai ndi manyi akowo wamva,DPP more 🔥
@danamoskwenda5825
@danamoskwenda5825 Ай бұрын
Balaka Mbera MCP boma ndilomweli
@moseswonganichipeta1166
@moseswonganichipeta1166 Ай бұрын
He is a musician he's making money, plus he's right boma ndilomweli, I like what chakwera is doing, let developing continue
@LennieNyirenda-w6p
@LennieNyirenda-w6p 10 күн бұрын
U like what is chakwera doing kukweza kwa zinthu ..tizidya miseu
@LonjezoChitseko-lx4qb
@LonjezoChitseko-lx4qb Ай бұрын
Kodi akuti nyimbo kapena kwaya , Awa Akuganiza za nkadzi wawoo wanyengedwa uja mchifukwa akuyimba kwaya
@PeterChipwaila
@PeterChipwaila Ай бұрын
Phurika chabe iwee kaimbe yako
@ThammyMoyo-p6s
@ThammyMoyo-p6s Ай бұрын
Kha ngati kwayadi😀
@JonesjamboCement.
@JonesjamboCement. Ай бұрын
Good music Bwana danlu ineso ndikuti Boma ndilomweli basi osasimthaso ayi A CHAKWELA your the best
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Ай бұрын
Boma ndilomweli tikumanena mobweleza bweleza kuti boma ndilomweli
@RichardAlick-o8k
@RichardAlick-o8k Ай бұрын
Nyimbo munaimba kale man Lozani zanu ija anakonza bro
@JumahJhanePhiri-e7p
@JumahJhanePhiri-e7p Ай бұрын
Mlibe fundo iliyose mnyimboyii aaaa akungofuna dolla ameney
@TrevaLackud-ok5ux
@TrevaLackud-ok5ux Ай бұрын
Gud music boma ndilomweli 🎉
@ThannabMtendere
@ThannabMtendere Ай бұрын
Nice song
@SPEARJAMES-r7y
@SPEARJAMES-r7y Ай бұрын
Ayenera kutero ndikomwe akupezeka ndalama koma ife ayiiii😮😮😮😮😢
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 Ай бұрын
Kulibwino muzivera nyimbo za praise worship songs, ndi ma gospel music, chifukwa makonda makonda siabwino,, chifukwa mukuyenda munyengo zowawa amalawi, musakhale mbuli muzivera nyimbo za uzimu, ndiposo muzi pemphera kuti Mulungu alisnthe dziko lanu, ngati simupanga zimenezi muzapamavuto ziko lanu osasintha chifukwa ndinu anthu amwano,, mumakosekerela zilizonse
@ShinglaiAli-be3yn
@ShinglaiAli-be3yn Ай бұрын
Ndiwachizungulire ameneyo 🤣🤣
@wisemankadzakumanja-f4c
@wisemankadzakumanja-f4c Ай бұрын
Nyimbo yopanda nzere imeneyi
@MisheckAselo
@MisheckAselo Ай бұрын
Bola anakangopwisa 😂😂😂😂
@AdissanQisico
@AdissanQisico Ай бұрын
Malawi akufuna Adadi DPP represent
@PackstonMussa
@PackstonMussa Ай бұрын
Aaaa adadi ?kkkkkk
@KelvinPhiri-z9d
@KelvinPhiri-z9d Ай бұрын
Iwe kwathu ku mulanje ayi ufufutepo pamenepo ife ayi sitimufuna kuno chakwera wakoyo zachibwana eet.
@Kondwanikanakana
@Kondwanikanakana Ай бұрын
Ine kwathu ndi kuneno koma Dan Lu asaname Ife yathu ndi DPP, ngat iyeyu ilindalama koma 2025 DPP Boma
@JoyfulKennedy
@JoyfulKennedy 29 күн бұрын
Boma ndilomweli sitikusitha ku gona ndi njala kwake kumeneku tikasithe palibe kusitha apa 📸🔥 ipase moto Dan lu🔥
@ScottTholo
@ScottTholo Ай бұрын
Ku MCP ko nyimbo zikukuvutan man Bolanso Zija za adadi
@MikeMoris-zp6yg
@MikeMoris-zp6yg 13 күн бұрын
Boma ndilomweri never change
@danielzitande5231
@danielzitande5231 25 күн бұрын
Kungoti munthu ngati uli wuli basi idzakhalabe mbuli ,this is just because, Dan lu iyi ndi nyimbo koma kuti ayende mmidzi anthu akuvutika kwambiri iye akudya za bwino mbudzi ya munthu Boma ndi lomweli koma tisintha basi ,idyani ndalama za kuba dzinjoya nadzooooo
@IsaacLuhanga-l4m
@IsaacLuhanga-l4m Ай бұрын
Akazipexa ndalama azidyabwino sogolo lithaposachedwa
@GideonPromice
@GideonPromice Ай бұрын
Nyimbo ziziyimbidwa km ife tapanganizo athu awawa akupita afune asafune ulendo ulipo
@vanSefu
@vanSefu Ай бұрын
Boma la dan lu lomukomela yekha uku mkazi wake akupakulitsa nyemba mu boma lomwelo manyazi ulibe ukamaimba za MCP
@KENNETHBTMAGEYA
@KENNETHBTMAGEYA Ай бұрын
Boma ndilomweri ndithu koma tikusitha Mtsogoleri uzakhaula iwe
@CharlesNyamula-r6g
@CharlesNyamula-r6g 26 күн бұрын
Nthawi yopanga ndalama koma mumtima akudziwa chilungamo
@GreevinMandala-z1d
@GreevinMandala-z1d Ай бұрын
Nyimbo yopanda mfumdo😅😅😅😅😅😅😅 yopanda chikoka
@TendaihMwenefumbo
@TendaihMwenefumbo Ай бұрын
Aaah iwe wagwilizana ndindani kumpoto kuno kuti Boma ndilomweli 😊😊😊 ine ndiye ayi ..... APM Boom ❤
@aminajuma-x9t
@aminajuma-x9t 14 күн бұрын
Ndikumva ngati akuti agwirizana adyera okhaokha? 🙄🙄🙄 Maluzi ndikanthu koipadi....
@SaidSamuden
@SaidSamuden Ай бұрын
Nyimbo ikhale boma ndilomweli basi ndiye kumati watulusa nyimbo
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 Ай бұрын
Ndilomwelidi Boma Koma tingosinthapo mtsogoleri basi
@PeterWillard-r3y
@PeterWillard-r3y Ай бұрын
Aliyense ali ndipodyera pake mulekeni adyenawo,azathawa yekha 2025
@juliussamson6212
@juliussamson6212 27 күн бұрын
DANI IWE M'BALE WANGA UNACHITA MISTAKE BKUROWA MCP YOU NEED TO GO BACK HOME ZISANAFIKE POIPA
@AchinaKellz
@AchinaKellz 25 күн бұрын
Mcp ikaluza tisakuoneso dziko muna ukapeze kwina ife tivina lozani zanu chiza udapha 😂iyi ungokakamiza😢
@RuthJopilo
@RuthJopilo 28 күн бұрын
Boma ndilomweli koma president yekhayo fired.
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 Ай бұрын
Ati taaa sizikukoma olo pang'ono nyimbo ndizomwe zija mudayimba Lozano zanu osati izi olo chimodzi
@YOUNGSONSAMBO
@YOUNGSONSAMBO 28 күн бұрын
Boma dilomwero palibe munthu angalimbane ndi mcp 2025 wooool
@RobertGambuleni
@RobertGambuleni 16 күн бұрын
Iwe uli phee kudya machenji achakwera koma samala kumangochi kuno sitingavotere mcp ukungodzivutitsa iweyo ndi ana ako udzavotere mcp ngati uli umphawi peza njira ina akupusitsa
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 Ай бұрын
Chitsiru Dan Lu wanu, mwana wachigororo
@JoePrecious-j7o
@JoePrecious-j7o 23 күн бұрын
Mkuluyu maluzi adamukwapula apapa at least akudzitolera ndipo sangaleke apeze kaye izo akuziona kt azipezazo
@paulmartin8165
@paulmartin8165 Ай бұрын
Mulungu anapatsa munthu mpandoyi ndicholinga, nthawi ya chakwela akunama nd zinthu zovuta kwambili. Ndi mwana wa mulungu uyu. Boma ndilomweli basi
@ModestoLedissone
@ModestoLedissone 14 күн бұрын
Dan. Lu. Hoye
@vanSefu
@vanSefu Ай бұрын
Dan lu sukunama boma ndilomwedi silisintha koma tingosintha president
@SylvesterWyson
@SylvesterWyson Ай бұрын
DPP wooyeeeeee!!
@KIDNAPHIWA
@KIDNAPHIWA Ай бұрын
DAN LU, wagwilizana nda amalawi ake akuti zomawanamizila anthu zoo sizabwino
@PaulManyamba
@PaulManyamba Ай бұрын
Ndipo ukuona ngati unganamize kumwela kwake kuti kwa chiyenda Utsiku kapena palibepo zanyimbo apa wagwa nayo
@MikeSanthe-w1f
@MikeSanthe-w1f Ай бұрын
DPP yayi tinatopa ife ndi nyasi za DPP kmso tsakho banja limodzi .
@AnnahZimba-v8i
@AnnahZimba-v8i Ай бұрын
More fire mr chimwendo ulemu wanu
@chrispinchirwa9563
@chrispinchirwa9563 Ай бұрын
A Dan lu mukuyimba mokakamizidwa kuopa mukasintha muona chikangawa unakodwa Iwe ungatani
@HoracioJoaowaissone
@HoracioJoaowaissone Ай бұрын
Athu ngati inuo ndie muter km amene akudxiwa kuipa kwa MCP sangakambe kt ndilomwel
@BrinoJob
@BrinoJob Ай бұрын
Eya ndichoncho basi ndilomweli
@DanielMatt-ib1eb
@DanielMatt-ib1eb Ай бұрын
Zoyimbaso zakezo sizikumvekaso bwino azayaluka ameneyo 2025 ndi ambuye akewo.
@NekhasonLarkim
@NekhasonLarkim Ай бұрын
Kasungu chotsapo zopusa zakozo ife nd dpp
@NeliahWiseman
@NeliahWiseman 5 күн бұрын
Ife sitisintha
@PeterLazario
@PeterLazario Ай бұрын
2025 yafika kale tiziona vote ndi mumtima basi
@SaideSamson
@SaideSamson 16 күн бұрын
Aaa angozivituta awa
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
How can you say Boma ndilomweli yet there is no: Food Folex Passport Fertilizer Drugs Inu oyimba tamakhalani ndi manyazi, posankha owayimbira nyimbo.
@Mastonlebiam
@Mastonlebiam Ай бұрын
Ndani luu ndiongani booh dpp zaka 80kuno ayi ku amereca bieden wafa Kodi uu pita muzinyamula azalamula ndi chisale ife sitimuopa ndani owinna ndiwe
@AneFombe
@AneFombe Ай бұрын
Koma olo muntima mwake chilungamo akuchiziwa lakula ndi dyela basi koma apm 2025 bomaaaa
@JonathanChinomba
@JonathanChinomba Ай бұрын
Dan akuseka maso sukuona sekula maso nupenye patali
@JnrHastingsMatola
@JnrHastingsMatola Ай бұрын
Chimene akuchita sakudziwa kumunyengela mkazi wake uja sakumvesa mofelamo
@GloriaSalijen-v8c
@GloriaSalijen-v8c 9 күн бұрын
KD iye Danyo mavuto omwe zko likukumana nawo kuchokela 2020 kfkla lelo 2025 sakuona aziwe izi zonse zomwe akuziwa achite kma ife tdalila mulungu tzakumana skulo likazafka
@MartinMwanganda
@MartinMwanganda Ай бұрын
Boma 5lit ya chimanga yafika 6pin tiuzen kod izi zidachitikapo
@LeonardDavid-x7u
@LeonardDavid-x7u Ай бұрын
Mcp si makape iwo amapereka ndalama zaulele izi
@winstonmulenga6940
@winstonmulenga6940 Ай бұрын
Choonadi chili mu mtima mwake. Mind you, uyuyu akupanga business chabe .
@AlifSaber-d9y
@AlifSaber-d9y Ай бұрын
Mapaziako
@AbdulKapinga
@AbdulKapinga Ай бұрын
Pantumbo pako iwe
@UPCChisomoChoir
@UPCChisomoChoir Ай бұрын
Mchifukwa chake ukukutumula iwe mix kukudyeraso mkadi uziona sunati muzayankha nthawi ikubwera
@AmisiDytoni
@AmisiDytoni Ай бұрын
Tingosintha nsigoleli bas
@jaimcatungue87
@jaimcatungue87 Ай бұрын
Achisilu awa ndipamene kadzi wake akuchindidwa akuwona
@DripCagemw196
@DripCagemw196 Ай бұрын
Nyero wake kapolo ameney pantumbo pamake sathanso kuimba nyapapi
@ReginaPhiri-u7d
@ReginaPhiri-u7d 28 күн бұрын
Kod akamat tagwirizana akunena ndani sitiku kana boma ndiromweri koma president tisitha mwanamizana ndi chakwera wa koyo tiku ona chaka cham'mawa
@EnerstMwitha
@EnerstMwitha Ай бұрын
Athu okonda ndalama inu ndiye mugwela limodzi ndichakwala wakoyo apa Dan lulu mwatha
@yasiniKalonga
@yasiniKalonga Ай бұрын
Tisintha tsogoleli koma boma ndilomweli pajatu boma ndi anthu
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba Ай бұрын
Kodi Dan lu akali kugonabe chifukwa cha titandala tomwe alinatoto zaziii chakwera sazaona boma 2025 Dan lu ukunama azachoka chothawa
@JoyceBowman-x7o
@JoyceBowman-x7o Ай бұрын
Dan lu ndale zake wafika nazo popusa iiiiiiih ai waonjeza afuna kudya nawo basi iyi ndinyimbo chabe ife boma tisitha ndivote yathu not nyimbo
@ChristopherMunlo
@ChristopherMunlo Ай бұрын
Koma mcp ikazangoluza iwe Dan lu suzathawa?
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma Ай бұрын
Ndiliweli❤
@KingsleyKapanga
@KingsleyKapanga Ай бұрын
Dan Lu ndichisiru koma sakuziwa azaithawa malawi asakufuna
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma Ай бұрын
Azoona palibe wazelu angavotele chinkhalamba ngati chimunthalika
@SammiesJohansson
@SammiesJohansson Ай бұрын
Ineso mawa ndpeka nyimbo ya afit nde kut ndpeza cash..
@JosephSiyame
@JosephSiyame Ай бұрын
Boma ndilomweli koma president ndiame tisinthe
@JOHNSANGWALI-n2f
@JOHNSANGWALI-n2f Ай бұрын
Anatha awaaa zikugowomeka Kuti akupangila Wina Kuti amusangalase
@MistonNyati
@MistonNyati 13 күн бұрын
sakunam ay
@GodfreyMagombo
@GodfreyMagombo Ай бұрын
Boma ndlomweli tngosintha president Nd chipan DPP 2025
@PhillipChisanu-k3r
@PhillipChisanu-k3r Ай бұрын
Ndilomwelidi bomali,tingosintha tsogoleri bas,abakukwerelabe mkaziwakoyo Kachitsilu iwe!
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz Ай бұрын
Chakwera wake yemweyu akungokuwidwayu??????za ziiiiii sangawine ndi vote yako yokha muzingodya nawo misonkhoyo
@PeterMwakihana
@PeterMwakihana Ай бұрын
Ubwino wake ndiwoti iyoyo ndinyimbo koma ovota akuziwa amene akapase vote lake.😂
@DopegeeIneastAfrica
@DopegeeIneastAfrica Ай бұрын
Ndibombocrat Amanyengetsa kuthako ndiposo pantumbo pamayake 👊
@TimeAbilu
@TimeAbilu Ай бұрын
Boma zoona ndlomwero koma tisinda apule ndi chipani
@catherinenihorowa-x3c
@catherinenihorowa-x3c Ай бұрын
Ubwino wake munthu atha kumasapota chipani china koma kukavotera wina, aliyense vote yake ili mumtima
@ElsaMalunga
@ElsaMalunga Ай бұрын
Ndiye cn kuyimba kuyakhula aaaa inuso ndiye zitukwi moti nkumati munthu woimba kpn ndakatulo aaaaaa
@JuliusMtimbula
@JuliusMtimbula Ай бұрын
Adan lu ndiopusa ndmthera kuwiri uyo
@AnneChakhame
@AnneChakhame Ай бұрын
kufuna pofela tiyeni tidzingopenya game imeney azatha movuta
@TimothyvascoVasco-j6d
@TimothyvascoVasco-j6d Ай бұрын
Chitsilu ichi kusaphunzila kwambili mkovutaso adzava manyazi kwambili
@Mastonlebiam
@Mastonlebiam Ай бұрын
Ndan luu ndikatundu pitiliza kuno kwakauma olembetsa takeana 11thouzand tonse chakwera osabwerela mbuyo mulungu akudalitse Dan ndipo mcp mukuyenels kumupasa ulemu wapadera Dan tikafutsa ndionse omwe atithandiza chonde ankasa sekefa nyemba nyemba azanye bwino komaso akauma afzawakweze kukhala sta kauma
Giboh Pearson - Adzamwa (Official Music Video)
4:17
Giboh Pearson Phalombe Musik
Рет қаралды 539 М.
Triple M Ft Driemo - Follow (Official Music Video)
4:57
Triple M Zambia
Рет қаралды 11 МЛН
요즘유행 찍는법
0:34
오마이비키 OMV
Рет қаралды 12 МЛН
Vampire SUCKS Human Energy 🧛🏻‍♂️🪫 (ft. @StevenHe )
0:34
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 138 МЛН
The Last Fishing Boat - a film by Shemu Joyah
1:49:51
C. Shemu Joyah
Рет қаралды 371 М.
Top 10 Ya Azimayi Olemera Kwambiri Ku Malawi
9:51
Sam Malvitha
Рет қаралды 140 М.