Eish ndakanika kugwira mtima koma kukhetsa msozi Ambuye akhudzeni mai Mary chilima 🙏
@tionetawenichakhwantha73772 ай бұрын
This is heart breaking, Lord comfort your daughter Mary.
@PreciousKatsokwe2 ай бұрын
😭😭😭😭 So sad But limban mtima madam Life ndichoncho😭😭😭😭
@mrsmkjb24112 ай бұрын
So so sorry about this heartbreak 😢😢. Very painful for Mary and the family. 💔💔😢😢. MHSRIP 🙏🏾 God Almighty will avenge this death. The devils have not won!
This is heartbreaking to see Mai Chilima crying like this!😭😭😭😭
@eunicesaiti2 ай бұрын
Pepani mama Mary Chilima, SKC Rip 😢😢😢
@StiveriaChikonga2 ай бұрын
Palibe chithu chopweteka ngati ku luza okondedwa wako ,😭😭😭😭
@ShameemMawindo2 ай бұрын
It's so emotional 😢
@violetpotani2 ай бұрын
Eeeh koma Mary kumvetsa chisoni ambuye mulimbitseni mtima mayiyu ife sitingathe, koma poti inu mmayiwalitsa muchitireni mary
@MaryPhoya2 ай бұрын
😢😢😢😢l can't stop crying, be strong madam chilima, only God knows
@JaphetSakala-pq4fl2 ай бұрын
Mayi mery chilima pepani.mau awa akhale pantima(1atesalonika4:13-18). Akubanja chonde kulila kwanu kwaveka koma be MULUNGU wa mwambayo AKUFUNA kupangisa manyazi anthu ena NDIPO wasankha kale madam mery. Chonde khalani ndi chiyembekezo mwa Ambuye.😊
@bernadettachirwa47282 ай бұрын
Why am I still crying for SKC??
@PrincessVifaloma2 ай бұрын
Same here, I can't hold my tears 😢💔🕊️
@GiftGift-d6u2 ай бұрын
Be strong Mary..God is wit you,, n you will never be alone
May our good Lord comfort you madam Mary tikulirabe Nanu limodzi
@Jessymsowoya2 ай бұрын
😭😭😭😭😭😭ifa yosayiwalika pamoyo wa amalawi 💔💔💔
@helenngwira7922 ай бұрын
Ambuye akutonthozeni Mayi chilima. Pepani ndithu
@LalonaKamanga2 ай бұрын
Izi koma mukanachepesako let the widow heal😢
@MosesBanda-h4x2 ай бұрын
Inde ndi zowawa mai Mary Chilima koma Mulungu akutonthozeni
@ChisomoBanda-jo4ix2 ай бұрын
Manganya uyo ndisatanaweniweni nd chakwera wake nkhope ngati wachison mu . Mtima akusangarara
@corretabanda76852 ай бұрын
I will vote because of anger with the death of Chilima. If he was alive mwina sinkanavota. RIP forever my president. Mr Usi, how do you feel mukamawona chithunzi cha a Chilima atafa komanso pampando womwe mukukhalawo? You will talk senseless things forever, and no one will take you serious sure.
@DoreenBanda-hg7oe2 ай бұрын
😭😭😭imfa iyi ikumvuta kuiwawa
@WisdomMaseko-fi5sv2 ай бұрын
God may you comfort this bereaved family
@PatriciaKanyanga2 ай бұрын
Mmhuuuu🙌🙌
@TiyamikeChinsembe2 ай бұрын
Mary abale😭😭😭😭😭 ambuye amutonthoze mmmmmmmm
@JogaJoseph2 ай бұрын
so painful 😢 but let god to be god 😢😢😢
@mrsmkjb24112 ай бұрын
Why did Usi even go there?? Just to mock mama Chilima? There really was no need for him to be there, even sitting on the chair like he’s a little king! Leave the widow to mourn her dear husband in peace. She DOES NOT need your fake comforting!😡😠
@StellaChizombo2 ай бұрын
Mmmmm ambuye athandize Aku banja la chilima
@serakillo86682 ай бұрын
Sorry Mary chilima mulungu alakwisa ndpo. Sanalakwisepo so be strongle
@godfreysawawa66362 ай бұрын
Preparing mama Mary This is so hard in life
@DolicahGift2 ай бұрын
Pepani mrs mary chirima 😢😢😢
@FateemahHamzah2 ай бұрын
Misodzi siikutha. Not easy kuluza omukonda. Mulumgu tipatseni kupilira
@Fatima-db8ut2 ай бұрын
Jesus look at Mary ,have mercy on her
@lusungumsiska22932 ай бұрын
😭😭 Pepani pepani pepani.
@MiddayDeleza2 ай бұрын
Pepani kwambiri Mary Chilima Mulungu akutonthozeni ndithu
@PrinceBlessings-bv5bs2 ай бұрын
So painful 😭😭😭😭 indeed
@monicahmtambalika26112 ай бұрын
Mmmmm zomvetsa chisoni
@MercyKatongo-p9b2 ай бұрын
Unbelievable Mr chilima
@anastanziaelia-gk3tt2 ай бұрын
Mai ali mu Nkhalango awa mmmmmm Ambuye yekha ndiye angathe kuwatonthoza zokhudza kwambiri izi
@QueenMkandawire-sg4df2 ай бұрын
Mmmm moyowu. May his soul RIP
@AnnetteKadzombe2 ай бұрын
Pepani Mai Mary Chilima pepani mai
@CharlesFalakeza2 ай бұрын
Michael usi unampititsadi Chilima ngati bodza
@CathreenKadwala2 ай бұрын
Sorry marry 😭😭💔
@IanAllstal2 ай бұрын
Umasie ochita kumupangira munthu 😢😢 Koma zoona ? Mukumva bwanji mukaona Mai akurila momvesa chisoni chotele? Ai Baezekani Tero
@YassinAmbali2 ай бұрын
Marry akundivesa Chisoni 😭😭😭😭😭😭😭
@LoyceMisomali2 ай бұрын
May God wipe your tears mama Mary
@AndrinaMnthaliАй бұрын
Sorry mama nzopweteka
@stevenkambuku2 ай бұрын
Very sad, Mhsrip
@beatricenkhoma11092 ай бұрын
God is good
@MarthaZakaria-l5e2 ай бұрын
😭😭
@KettieCHAVINDA10 күн бұрын
😢😢
@JoyceChaima2 ай бұрын
Mmmmmm mhuuu
@JosephinePhiri-zh2li2 ай бұрын
Mmmmmm sambi😭😭😭😭😭😭
@ShillahChisi2 ай бұрын
😭
@JoyceBAllubi2 ай бұрын
Imfa yowawa yosayiwalika
@LindaKapeta-u6d2 ай бұрын
Mayi akumva kuwawa uyu
@MartinKapanga-q6m2 ай бұрын
anthu aa mcp anakulakwila koma mulungu azaziwa kuti ndindani
@MercyKatongo-p9b2 ай бұрын
So sad for sure
@jeanmatiya73472 ай бұрын
Ambuye inuuuu😢
@SlyviaPhiri-bd9uu2 ай бұрын
😭😭😭😭😭
@VictoriaKumwenda-k6o2 ай бұрын
Pepani mai mulungu akufungatileni
@PatrickHaward2 ай бұрын
Mu zonse muyamikeni Mulungu Mayi
@Martha-m6e2 ай бұрын
Mulungu akutothozeni nonse.
@SydneyMwale-u9w2 ай бұрын
Usi na chikangawa chakwera musakafe
@mikesandali84252 ай бұрын
Akubanja paja akuti musamatokote zaboza
@GraceGonani2 ай бұрын
Koma abale😭😭😭😭😭😭
@SabinaNkhoma-sf7kz2 ай бұрын
Mary watililitsa
@DOLADAUSI2 ай бұрын
Mwamva
@AndersonBazale2 ай бұрын
Koma!!! Mmmmm
@directorvjshiiz71042 ай бұрын
Ngati bodza
@MeriaMasinga2 ай бұрын
Chakwera Mulungu akuwone
@ElinatyChakwera2 ай бұрын
Don't judge people like that, the Chakwera you are talking about might be innocent, unless you got the proof and evidence at hand that he is the one who did it...... the Chilima family is not happy with these types of comments. If you know much better about this incident, challenge the whole country and let them know the whole story. Am not a politician rather an individual with all morals intact, not brankrupt