MCP Ikusewera Game Yapasipasi

  Рет қаралды 8,797

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

Пікірлер
@RoseThindwa
@RoseThindwa 15 күн бұрын
Agree with you 💯 we can't just sit here n do nothing,we have to take action .
@FadahMatola
@FadahMatola 14 күн бұрын
Uyuyu akukamba zoona
@YoungMwacho
@YoungMwacho 12 күн бұрын
Zoona, vuto limene limakhalapo kuchosa boma loti munaliyikapo nokha ndi limeneli polanda boma lakale ndi limeneli.
@Onex-z6s
@Onex-z6s 15 күн бұрын
Apapa tisalambalale,nkhani ndiyoti tiyeni tipange mademo......
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 11 күн бұрын
DZIMEDZO NDE FUNDO ASACHEDWE NDIKUTI AMUTIMANGA KUTHANA NDIKUMANGIDWAKU NDI KUCHOTSA MCP BOMA BASI BEST WAS
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g 15 күн бұрын
Ndipo ukunena zoona aise
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 13 күн бұрын
Survage chikangawa anayesa kuyendetsa boma kuli ngati kukumba mbewa
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 15 күн бұрын
Good Message Mr Brother
@RexKamwendo
@RexKamwendo 14 күн бұрын
Chimachine sichikugwila ntchito 😂😂zavuta a Mcp
@SolomonMbewe
@SolomonMbewe 15 күн бұрын
Zowonadi,mwalankhula bwino.
@anusahjenala1063
@anusahjenala1063 14 күн бұрын
Ndipodi ndi zoona akunena uyuzi tiziona ngati za ku mozambigue😊
@tasmania527
@tasmania527 14 күн бұрын
Simungamuchose Mtalimanja mwachepa. Even khoti likupangani reject, mwauponda kkkkk
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 14 күн бұрын
Koma mu tinnganizile ife Malawi osaku kumbali ya chakudya ku Malawi kuno zavuta and chili chose chakwela koma adona Kuma Nena mowona mtima chakwela palibe chimene wa chita pa zaka 4 Ine ndi damuvotela kuti mwina atichotse kulamulilo wa DPP koma panopa ine chiyembekezo Cha mcp chikupanga bolaso DPP yomwe ija inu mazila 350 soya pisesi 600 and chimanga 7000 5ritaz 😭😭 mwina ndinu ma bwana bolani
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 14 күн бұрын
Chikangawa team sisowa
@Twaibuishmael-j4v
@Twaibuishmael-j4v 14 күн бұрын
Ndithu ndi zoona ngati sitikupanga umodzi amalawi pakadali pano tiona mavuto
@frankkaipa8925
@frankkaipa8925 15 күн бұрын
Sukunama akufuna tiyiwale za chimachini chopusacho
@MarySinjirani
@MarySinjirani 13 күн бұрын
Nkhaniyi ndi yoona brother
@dalitson3558
@dalitson3558 15 күн бұрын
Agree with you, these are all facts
@edgarmsofi589
@edgarmsofi589 13 күн бұрын
Chamba chakupweteka iwe, milomo yotuwayo.
@innocentmtungambera4905
@innocentmtungambera4905 14 күн бұрын
Kkkkkk Chingerezi chilimo ndithu
@JkBanda-c3j
@JkBanda-c3j 13 күн бұрын
Boma ndiromweri
@MrGcellrepairsnlaptops
@MrGcellrepairsnlaptops 15 күн бұрын
Let's meet and we agree one thing
@MajorCharles-z4l
@MajorCharles-z4l 15 күн бұрын
Yes focus on that issue
@MphatsoJameschipali
@MphatsoJameschipali 15 күн бұрын
Indeed comrade
@Maxielyies
@Maxielyies 15 күн бұрын
Powerful message
@SandPhiri
@SandPhiri 13 күн бұрын
Mtalimanja wavala tsapato yayikulu game yamukulira sangabele wachepa
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 15 күн бұрын
That's true anthu awa ndima mafia..
@AustinGomani
@AustinGomani 14 күн бұрын
Zoonadi comrade
@ManzyNgoleka
@ManzyNgoleka 15 күн бұрын
Nkhani ndiyastraight iyi
@MynessChirwa
@MynessChirwa 14 күн бұрын
Zoonadi
@jackalview7491
@jackalview7491 15 күн бұрын
Black box ananena yekha Moses kunkuyu pano akufuna tiyiwale
@LukeMapukusa
@LukeMapukusa 15 күн бұрын
Ndipo zoonad zimenezo
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 14 күн бұрын
ndipo zowona
@YasinKamanga
@YasinKamanga 15 күн бұрын
mau awa ndioona
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp 15 күн бұрын
Zoyona tayiwara Kuti kuri cimarmatic
@JackMvura
@JackMvura 15 күн бұрын
Mbuli yachilomwe muzipita kwanu Mozambique sikwanu kuno anyani inu
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 15 күн бұрын
Panyero pako wamva alomwe ananyera ndi amako pakholo pamako wamva ukati mulomwe ndye kuti chani
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 15 күн бұрын
Muli mbuuu kusapota usatana omwe Chakwera akupanga even mphka yemweyi mulibe alomwe ndye kuti chni alomweo akapita ku Mozambique iweyo upindula chni ndwe chsru chotheratu wamva ndne muyawo koma wayankhula zopusa garu iweeeee tiye nazo mwe alukundu
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 15 күн бұрын
Ndine Mchewa koma MCP izipita yandinyasa heavy. Chipani Cha mbuli.
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 15 күн бұрын
Sopano ngati alomwe kwawo kuli Ku Mozambique inuyo anyau kwanu NDI KUTI? Zakuti nyau zonse Ku Malawi sikwanu izi mukuziziwa? Inutu anyau munachokera Ku zaire ndipo muzipita kwanu pam'nya pako.
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 15 күн бұрын
Wina aliyese amene amaikila chakwela kumbuyo Ali ndi tsoka lalikulu kwambili ndipo sazauza m, tendele
@GladysBonongwe-p6b
@GladysBonongwe-p6b 15 күн бұрын
Yes brooh true
@WhyteSmart
@WhyteSmart 15 күн бұрын
Ndipo live
@MacdonaldMajohn
@MacdonaldMajohn 10 күн бұрын
Kodi dpp dza smart martic ikutipo bwanji kampeni yofuula mawu ilibe ntchito tisanafike nthawi yovota tidziwe results ya smartmatic
@AngeloGerman-p3c
@AngeloGerman-p3c 15 күн бұрын
Tell us the fact, what can we do to remove simatimartik,
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 15 күн бұрын
Am agree
@DoreenMaida
@DoreenMaida 15 күн бұрын
So what can we do about it
@RoseThindwa
@RoseThindwa 15 күн бұрын
Lets demonstrate
@GladysBonongwe-p6b
@GladysBonongwe-p6b 15 күн бұрын
Let us unit
@RoseThindwa
@RoseThindwa 15 күн бұрын
@GladysBonongwe-p6b for sure
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 15 күн бұрын
100%comrade ❤
@RonaldChirombo
@RonaldChirombo 13 күн бұрын
Komat muli ndimaitanidwe amphuno phiri.ngat bowo la toilet yokumba.😢😢
@LeonardNapwanga
@LeonardNapwanga 13 күн бұрын
Mwana wanzanu?
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 15 күн бұрын
Usamati a Malawi uziti alomwe nokha ndi anthu akumwera komweko osat kuno enafe mutichosemo
@MarkMasangwa
@MarkMasangwa 15 күн бұрын
MCP ikuchoka ufune usafune galu iwe
@AliNtolera
@AliNtolera 15 күн бұрын
Iwe ndi mboro basi mcp ndikachani
@MarkMasangwa
@MarkMasangwa 15 күн бұрын
@@AliNtolera ndipo ameneyi mboli yache
@symoldicky
@symoldicky 15 күн бұрын
​@@MarkMasangwaine ndi wapakati pompano koma sindikusapota nyasi zomwe MCP ikupanga just bcz njapakat Pano nzopusa kod mwana wanga adzanva kuwawa bwanji mawa ngat ine lero ndikunva kuwawa ndipo ndikusekelera
@symoldicky
@symoldicky 15 күн бұрын
ndine wapakati pompano ndipo sindikusapotaso MCP kachikena cuz yopanga zofoyira zosaganizira anthu Ake komaso sogolo Kadziko nde nsafele kut MCP imachokera komwe ndimachokera nzopusa
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 15 күн бұрын
Osasiya.agaluo.big
Zomwe Wayankhula Atupele Kumangochi, Ndipo Anthu Ndiodabwa...
5:41
Sam Malvitha
Рет қаралды 31 М.
When you have a very capricious child 😂😘👍
00:16
Like Asiya
Рет қаралды 18 МЛН
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
Chakwera akufunika ku mental hospital akamuyeze ubongo
14:21
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 104 М.
GWEDE GWEDE | 23 JANUARY 2025
30:55
Malawi News Update
Рет қаралды 10 М.
Oyimba Akugulidwa Ndi MCP
6:22
Sam Malvitha
Рет қаралды 64 М.
Mk party made sure anc won't get kzn again
19:14
MusaN
Рет қаралды 153
ZOMWE AYANKHULA MAI KALIATI 😱 😱 __17 January 2025
27:20