Mmbuyomu anthu a ku karonga nkhatabay dowa amakapezeka ku BT kuphatikiza ndi a kumwerako kucheza ndi president kusakanizana ndiye ubalewo, sikuti zinaenera a ku mangochi okha ayi.
@EddahKaunda4 күн бұрын
But don't worry about mcp mbolidzawo
@geraldtuwaga-iz6ll4 күн бұрын
Pa new year uzapite ku ndirande
@AdamJames-x7x4 күн бұрын
kkkkkk mpaka ma lorry 62? Ku mangochi ndi Kwa adad basi enawo akuzinamiza .
Inu anuwake ma radio station mumanena kuti kupeleka ndemanga pasakhale chipongwe kutukwana kunyoza, amene onyozawa mumawatani? Mumakondwera ndi zipongwezo?
Ngakhale mavote a counsellor zija amatenga Anthu ku Mozambique awa azabera mavote ndithu tisamale kkkkkkkk.
@AndersonBishop-i2t4 күн бұрын
Ineso ndi wa ku mangochi kuno ma truck wonyamula anthu ndithu ndie analipo kmaso anthu achilendo mpakana tinawafusa kuti km mwadya cnanga mwabwela kuzamulandila chakwera km mwadya Enaso mpakana afika usiku asananyamuke ma truck amanyamuka ma 7 ine ndinawona ndi maso angawa ndithu ma truck wonyamula anthuwo
@RiteRoderick4 күн бұрын
😂😂😂
@harrietmkusangombe4 күн бұрын
Zovutatu izi
@henryibrahimsailes46384 күн бұрын
😂😂😂 koma uyu chikangawayu ndi joker ndithu we don't have a president in Malawi
😂😂😂😂😂😂 koma chakwera uyu moti agure petulo mene wavutiramu shem
@hamiltonsolomon37564 күн бұрын
Mpaka Ma Lorry62😂😂😂😂😂
@MandalaChaonaКүн бұрын
Anakumenyera kampeni Kuti ukhale pa mpandopo Ndiye unamutafuna. Tikuonera chaka cha Mawa ndi Mfundo zako zozizirazo Kuti uzizati Chani, Blood Sucker mix Mikodzo Chakwera Munthu Woyipa iwe. Ukhalepotu mpaka 2050 tilipano kuonera. Mwana wa njoka iwe Mr SMARTMATIC
@WarriorKB-l3iКүн бұрын
Kkkk koma kumeneko mpaka kunyamula anthu ku dedza kupita nawo mmangochi timanena nthawi zonse kuti mangochi ndi y APM simwaona? Za manyazi mcp anthu olephela inu mungotaya nthawi ife tikudziwa kuti kulikonse mumapita ndi malole a wanthu mudzioneka ngati muli ndi molalo aaah za zii mwayaluka basi kumangochi angasapote mcp ndi ndani? Ca mzeru mwapanga inu mmangochi ndicani? Zisilu inu
@chrisboyce24 күн бұрын
😂😂😂😂😂 pajatu ku Mangochi sitimasunga Kape ngati Chakwera kuno tsopano ndi kwawo kwa APM ndipo tili naye limodzi pa page House 💙✅
Komanso tu mudziwe kuti, sionse amene amapita ku malo ngati uku akusapota amene wabwerayo, ena amapitira kusowa zochita ndipo ena kumakhala kuti akamuone galu amene akukhaulitsa anthu pa nthawi imeneyo!!!
Nde thawi yamavote athuoso azavota kuzela malolemo zaumbuli
@TrizaGeorge-q8w14 сағат бұрын
M,busa wasatana iwe waboza galu
@VictoriaKumwenda-k6o2 күн бұрын
Boza leni leni zisilu zaanthu zamaboza
@samdiverson9733Күн бұрын
Uyu mkapolo
@PatrickSomanje3 күн бұрын
Chikangawa group okupha iwe
@JamesRoben-dy7bx4 күн бұрын
Z,😂😂kuzinyenga ndi Chala uku alendo kulandilan okha okha
@marjoriefundi2 күн бұрын
Azimai a hijabu kulibe ngakhale azibambo a zikofiya
@chirwaellace1093Күн бұрын
Apule awa mmmm
@yusufbanda49804 күн бұрын
Nde kt an2 aku dedza anangopempha venyu ku mangochiko chfukwa nde eee pali gulu ku dedzako sakanakwanako ay achuluktsa komaso anaona kt akaguleko chambo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ineyo ndikuti ndalama zoyendetsera anthuwo ma lorry 62 ndi zaboma. A lot of money zaonongeka Inenso sindikufuna kuti anthu azivinira Atsogoleri ayi. This political culture of dancing should stop President asamunamize anthu andale potuta anthu