Otitengera ku Cannan aja asintha akutitengera ku BAGAMOYO
@SimonBanda-b1f4 күн бұрын
Anthu amavala bwino pamsewu koma kubwera MCP kugula ID ndi 2000 kwacha basi akulola. Anthu opusa kwambiri. Komanso fertilizer wa subsidy anthu kuvomera kujambulitsa mutasinzina za chamba kwambiri
@AchinaKellz4 күн бұрын
ndaona zibwana koma sichibwana koma kupusa koma muziwe kumwamba kudakana look at Mozambique now next malawi
@Zebron-kg2qz4 күн бұрын
Guys falitsani uthenga uwu MCP 💔😭 Yapangana ndizigawenga ZAKE kuti MADEMO yakubwerawa zigawenga zija zika join nikumaphwanya ma shops nicholinga CHOTI anamizire opposition
@SimonGondwe-o2o4 күн бұрын
This is politics.
@AjidahZmachemba4 күн бұрын
Kodi mafuta omwe mukuyendera kumapita nawo ku msonkhano wa ma battery wo mukuwatenga kuti? Ndinu adindo omvetsa chisoni kwambiri.
@HestingsEdward4 күн бұрын
BOMA la MCP tawonga ndi achinyamata pomagwira ganya wazikwanje Malo mwa nchito one million