Kkkkkk more fire more fire ma analyst opusa aja pa MBC
@OwenMindozo12 күн бұрын
Leadership is not a fearful tool, their work is to lead the people to green pastures and protection from evil and robbery. God give us a good leader to lead us, as you did with children of Israel on hardship in time pharaoh regime.
@MosesTangwe-q8o12 күн бұрын
Ka program kanyatwa kwambiri
@HabiboZimba12 күн бұрын
😂😂😂 chekobwe boom
@smartchisoni214311 күн бұрын
Koma ineyo kunena zoona chitukukoko cha misewu cbimakhala kut previous president anapanga kale zonse ..kusaina mapepala onse .. Moti chakwera kuchoka adzasiyanso zina obwerayo azamalizitsa ....
Koma nkhani ya feteleza wa NEEF akuti ndiwangongole ndiye anthu atenga ngongole ndiye andale akumakapereka ngati ndani? Nzoona anthu kuwakankhira kungongole za fetereza kapena awathandiza kubweza ngongole anthuwo. I do not understand this
@LimzeySande-b9n12 күн бұрын
Chirungamo ichi
@ChrissyBhima12 күн бұрын
Ai sizisiru koma akunena zowona,akabaza mukuwononga miyoyo yanthu
@GetiverMbewe11 күн бұрын
Bambo asikono Udasi isikaliot akungonangati afika kwa Cauta
@Godwin-xy9rg12 күн бұрын
Inu ndimawona ngati kulankhula za nzeru koma mkulimbananso ndi akabaza ndinu zisiru zed
@RebeccaChikalenda12 күн бұрын
Akuti vote yanga mayo
@AdyasiMaulana12 күн бұрын
Mcp ipakile yazuza anthu mokwana enough is enough
@mozesjackson63286 күн бұрын
Ndipo zoona amazayesa
@MathewKalinkhu12 күн бұрын
Zitsilu iziza MBC, Kasakula adzipita kwawo akimilele MCP pa chisankho.