Koma kumeneko! A cina cimwendo ndi amene amafuna kunyengana nae nde yapheduka makape a mcp, nkhani ndimenei yoti akufuna kubela mavoti.Ndicifukwa cani amati sanagudwe pamene anali atugudwa cimene amabisacho chimenecho koma akunama sitisiyana umakwana comrade program ikhale choncho comrade manyo×2 basi palibe kubela.