Apa mwapepela akulu, nanga bwanji mukupepesa ku dpp?
@DeMu-t2v16 сағат бұрын
Kunali anxanu owopsa kuposa inu
@MahometAli-e8w15 сағат бұрын
Komatu Bakili muluzi atcheya amkanena kuti amalawi mumaiwala msanga inu mukudziwa bwino dpp zinayamba kuwavuta nikumkota nimene munati musinthe boma munasintha zikupita worthy nde mukuti libwerenso dpp dziwani izi any president amene analowamo first term imayenda bwino even nthawi ya Tcheya ni Bingu ni APM nde musegule mmaso