Awa akuziluma okha kosungira katundu aikako bwanji mpaka akaika ma computer office table why anthu Inu somunati mulungu akuikanidi poyera somunati,it's my prayer kuti muchitedi manyazi.
@eliffagondewe8214Ай бұрын
A Sambo ndinu munthu wa bodza kwambiri mukupangazi ndiupandu mukuononga dziko lanthu mavote mukuberadi musakanee ayi... Koyamba mu history ya malawi mpaka mukapanga ku ja🙌
@mishecksipolo7153Ай бұрын
It doesnt make sense ngati ma khadi akucjokera kunja to the ware house how come kukupezeka a lilongwe okha Okha? Nanga ma gadgets akutaniko ku ware house instead of kwa DC? Is warehousing processing? Futseki NRB
Eeeedi ife a kumwera ndife atsiru.koma musaiwale ndife a Malawi big!!!!!
@YusufMtendereАй бұрын
Kumangidwa Suleiman wina afa
@0wenNkhambuleАй бұрын
Suleman big man 100%❤
@LastonChamilaАй бұрын
Am Laston from nkhotakota ndinapangwisa ID pa dwangwa center first month koma mpaka pano stikulandilandila I'd kani akusingila ma I'd kunkhokwe kosungila zakudya
@ExcitedBreakingWaves-oh3zbАй бұрын
Chiphatso ndi ukapolo kwa anthu achikuda..sisitimu yanu ndiyolakwika.musindikiza bwanji national ID mdziko la ena.
@esterechamba9343Ай бұрын
Pamenepo??????
@miriammvanda3404Ай бұрын
zitheka bwanji Kupezeka a lilongwe okha aaa uyu ndikatakwe zosaveka
@JosephMedson-q1lАй бұрын
Ati ifeyo monga aboma kkkk nrb ya MCP iyi, awa ndiye atipezelera bwanji.
@HenryManda-c4iАй бұрын
Kodi akuyankha zosemphana ndimafunso bwanj?? Aaaaaaah koma this NRB guy is suspicious 😂😂😂
@MosesNgombeyayera-tc3ruАй бұрын
All these warehouses in Lilongwe what's the point of sorting cards in nfra warehouse nanga Ku mpoto akuwerengera kuti?
@watsonmhango8794Ай бұрын
Transparency apa palibepo akunanama Sambo ndi wakuba😅😅😅😅😅
@StanleyChamasowaАй бұрын
Ku Lilongwe kulibe office ya DC??
@zayedmitawa8345Ай бұрын
NRB simafunika kukhala busy panopa kuposa MEC chifukwa NRB ndi office yachitsegulidwe through out the year.Why they're panic panopa,chinachake sichili bwino. NRB panopa bwenzi ikungopanga ma final touches osati kuo sort ndi kugawa ID Nthawi ino ndi ya MEC,kupanga register komanso verifying voters. NRB bwenzi ikumati almost nzika zambiri zinalandira kale ma ID. Chilipochilipo apa.I wonder why MCP is not commenting anything in the matters of ID and Smartmatic,are they ok that their fans have registered and Smartmatic wont affect them?
Thanzi likuvutanso mbali imenei kapena sindikuona bwino 😎😎😎
@Jamilahchinyama-y9bАй бұрын
Akulandira panado ameneyo simukuonayi
@MagretMakuwiraАй бұрын
😂😂😂😂😂
@RaphaelWinford-t7uАй бұрын
NRB Mukugwila tchito mopusa kwambiri 😊😊😊😊
@Spaw-BTheGogoBoyАй бұрын
NRB KUYALUKA kwamtundu wanji kumeneko
@MasterBlack-r2nАй бұрын
Zaka zonsenzi zimayenda bwino Koma ulamuliro uwu chilichonse chinasintha Anthuwa alibe pabwino pot munthu utha kunena kuti bolamkoni aka?😭😭😭😭😭
@AbdulIbrahim-b6vАй бұрын
A sambo vomelezani pomwe palakwika Lilongwe is national head of tale center so anything that the do must have been noted to all the political party in advance before moved to a private place like ku malo a chimanga pomwe muli ndi good big offices at MEC
@MfumuNgwenyaАй бұрын
Katole eeeeeh😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌
@TelezaNtodwaАй бұрын
Anthu aline ma card Iwo akungowasunga bwanji?
@RodneyTomatoАй бұрын
Suleman respect OSAOPA OSAFOKA OSATOPA
@joebrown1158Ай бұрын
Mutu wankhani apa mwa guidance.
@ConexKamulole-be5bpАй бұрын
Bwana wamkulu mr Sambo mukufuna muthandawuze kuti ma warehouse a NRB ali busy moti simunga kwan e ma ID awanthu a😜🧐🧐kumalawi ndiye ndichifukwa chani mumayamba bungwe limeneli 😂😂😂😂😂😂😂😭😭😭😭😭😭😭🙃🙃🙃
@MvenaMagaletaАй бұрын
Keep it up Mr Suleman
@SydneyKhakonaАй бұрын
Ine ndie palibe angandilese kumvera bakili muluzi tv
Iweyo samba ukungwilisidwa chito molakwika pleas muziwe kuti zizukulu za ana Anu mukuziyika pa moto pleas muzilingaliya songolo ya Malawi
@farmupmalawiАй бұрын
Ine chiphatso changa kuti chitheke ndinali pilau 40 pin +transport
@StevenGoodson-kn7ugАй бұрын
Kkkkkk Koma tayankhani zomwe mukufuzidwa
@RonaldGama-gz9ugАй бұрын
Ngati warehouse ngati amatha kumasungirako mankhwala ..Does that means they can do packaging at warehouse
@TruthReigns6Ай бұрын
Ma ID asochera bwanji and yet ukoko akuti ama sorter ko ma iD wo?
@cassimdanielАй бұрын
Mmm NRB itipweteka
@esterechamba9343Ай бұрын
Bambo sulemani go deeper for this issue akutitola asambo pamodzi ndi chipani cha MCP
@ellensambo6323Ай бұрын
Akudziwapo kanthu asambowo aaaa
@alfordchirwa3587Ай бұрын
Is the building lebled?
@GabieBlackАй бұрын
Fire Suleman
@user-mx7oj1vx3lАй бұрын
Koma Boma la france ndiloyipa kwambriri yomatsindikiza ma ID aku Lilongwe wokha wokha basi dziko lonse la Malawi 😮😢shem on you! ndi mabodza ako wopanda nawo manyazi😅
@EmmanuelPharaohАй бұрын
Ndpo inu mmmhhh😢
@IreenMughogho-z6fАй бұрын
Kumeneko ndikusa kwambiri iwo wa NRB ine mwana wanga since 2022 up to now sanatenge akungoti sizinatuluke vyauchindere ivo vinthu vikwenda makola yayi
@MusaLion-os1lxАй бұрын
Ndipo Selemani ndimachine kwambiri uyu ndimuthu
@ibrahimalfred6539Ай бұрын
Asambo Mulungu akuyendeleni komaso next year kundende ndialo mukakhale moyo wanu onse
@LameckDanken-tm4rtАй бұрын
Vote tisagwilise chiphaso make another way iyaaaa
@michaelkallyz2425Ай бұрын
Anthu ambiri anabwezedwa Kuma Center mpakana sazavhota. Kodi zimenezi zitithandiza?
@bridgetmajor3646Ай бұрын
Amene tinataya ma I'd..anatipasa ma pepar..oti tizarembesa za chisoni kutikana....akuona ngati azabera...anya kunjakuno kuli Mulungu😢😢
@AbdulMmadimwanyalisiАй бұрын
NRB,ili limodzi ndi mcp ,ndipo ili sibungwe loyima palokha ayi.ili ndi bungwe La mcp .
@SuleimanRabsonMkhungaАй бұрын
Suleimana makwana
@JosephChiccoNkhulandeАй бұрын
Funso kanga ndiloti kodi Malayini a Times TV amamveka kumwela kokhakokha ndipo anthu ake amodzimodzi pali chilungamo apa
@InnocentNgulube-f5cАй бұрын
Akulepherela kuyankhatu matunso a Malawi chimene chikusonyeza kt pali kena kake pakat pa boma NRB ndi meck ndye ngt sasamala chisankho sichizakhala cha mtendere
Boma limeneli ndilmanyaka, why do this Stupid NRB is working in favour of MCP without working with all political parties. We will see when governments change.
Sambo pokhapo walephera kuyankha funso lomaliza la Suleman, zaonetseratu kuti you are hiding something,,, mwachidule ndiwe wa MCP, pafunika mukatuluka m'boma ukaseweze kumaula.
@GibsonKasabolaАй бұрын
Chifukwa chani a chimwendo banda akumayakhila a NRB? Sambo ndiwe wa bodza akumakutuma a MCP iwe
@SamuelKanongwa-k6hАй бұрын
Kunali kupanga reduce anthu ovota through ma delays tactics
@AgnesNjikhoАй бұрын
Koma ziliko anthu akamakuchemerera ziwa kt wachenjeresa azako wasiyana nawo patali azako akukusgoza iwe uzichita zovutisa koma azako ose alido iwowo sakupanga ndare wekha mupaliyameti wekha ku NRb azanu kulibe
@TonyMhoneАй бұрын
Uyu Amati Sambo uyu Koma akutenga a Malawife Ngati ciani? Mbuli kapena anthu a nzeru zawo. Iiiiiiiii zotsakhala bwino idzi. Mpaka kukhokwe yosungira chimanga kwasanduka kusungira ma ID mmmhuuu!!!
Mchifukwa chani sanatcheke ngati ma id Ali kukanengowo sanalembesedwe mu system ya MEC?
@GranceChirhwaАй бұрын
Kundirande post office anthu sakwapasa ma card angowayendesa anthu osapasa chonde tatithandizeni kumeneko prease
@MfumuNgwenyaАй бұрын
Nsambo wapanikizka ndi mafuso 🤣🤣😂 bodza likuonekeratu😂
@esterechamba9343Ай бұрын
Mphatso Sambo mukapsa chifukwa cha bodza nenani chomwe mumakapanga Ku warehouse yachimanga musatiputsitse diso likuona zomwe mukupanga ife amalawi sitikufunani tulani pansi udindo Ena aimepo
@ClementZintula-wi4tzАй бұрын
NRB under panic
@NadeemKhan-sh9jsАй бұрын
Ine ndimaona ngat ma ID wo amafunikira kut eniake apasidwe ndi cholinga choti akadurire vote nde zipezeka bwanji ndiowawa
@WarriorKB-l3iАй бұрын
Inu palibe ca mzeru ciliconse angatiuze mwana wa cikangawayi apapa a sulemani ndi azanu mwagwila wakuba.Mcp ndi yakuba panyoo pake nsambo ndi anabelo.
@PreciousGomiwaАй бұрын
Akuti ma ID ndi ochuluka mma center anthu sakutenga komanso akuti ma ID ndi ochepa mma center akutengedwa... Ndiye timve ziti kkkkk
@TecnoPop3-k2cАй бұрын
Akunama asambowo kuno kumpoto ku ekwendeni ma Id sanafike anthu ambiri akudandaura ndeiwowa akuti akugwira bwino nangabwanji anthuena sanarandire ziphasozao
@robertnamangale3504Ай бұрын
NRB si ya mcp ayi,bwanji sanawauze a opposition ngati ma stakeholder a election? anthu anayamba kale kudandaula za NRB bwanji a Sambo akulephera kuvomereza kuti sizikuyenda?
@HaroldFodyaАй бұрын
Compromised nrb
@GoodsonRastonАй бұрын
Asambowo sakugwira ntchito yawo moyenelera,chinyengo chawakulira and amenewo Ali mbali ya mcp,akupangazo zibwelesa nkhondo mmalawi muno,Mr suleman ulemu wanu bwana,ndne goodson laston kuno ku nsanama boma la MACHINGA