Kamuzu Kuwauza Anthu A Ku Tanzania Mosaopa Kuti Nyanja Ndi Ya A Malawi

  Рет қаралды 3,831

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

Пікірлер: 30
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u 3 сағат бұрын
That's speaking of the leaders ✊
@MMK-p3y
@MMK-p3y 2 сағат бұрын
Chakwera Koma wamvera kameneka kapena akukonzanso ulendo wopita dziko lina kukacheza?
@rashirdbanda8204
@rashirdbanda8204 7 сағат бұрын
Chakwera akuononga dziko la Malawi icho ndichoti tiziwe
@MoffatBinali-pp8hi
@MoffatBinali-pp8hi 5 сағат бұрын
He was the real giant,very amazing man nothing fear was in him.
@TimothyKamanga-t2z
@TimothyKamanga-t2z 5 сағат бұрын
Kamuzu was very wise , courageous, patriotic leader
@BilalAliyah-k1f
@BilalAliyah-k1f 5 сағат бұрын
That's great voice
@PiassDayit
@PiassDayit 5 сағат бұрын
zikoli laling'onokale ligawidweso Mmmm 😭😭 Koma chakwela mmmmm mwafika
@stevezulu2108
@stevezulu2108 20 минут бұрын
Malawi without the lake is nothing
@markmalunga6185
@markmalunga6185 58 минут бұрын
Ma British anapanga zofoila kulemba malire amaiko awiri using that Lake. There is no way people from Tanzania can avoid using the Lake
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 4 сағат бұрын
Chakwela chilichonse amangoti yes, yes president opanda kuthekela
@DeboErikalo
@DeboErikalo Сағат бұрын
Those days Malawi ngat dziko linali ndi phanvu zapadeladela osati zaleloz
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 4 сағат бұрын
Nzimai wagonjetsa chakwela Nzimai tu
@stevezulu2108
@stevezulu2108 21 минут бұрын
Messing up with him meant messing up with south african. Chakwera is on his own. He only has Nyau back up. Unfortunately.
@liz9425
@liz9425 56 минут бұрын
Indeed he was not a Malawian 🇲🇼 murder Chakwera also copy how he speaks maybe that’s why also that’s why naye akupha athu ngati nkhuku
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov 6 сағат бұрын
Kamuzu anali munthu oteteza dziko lake even malankhulidwe ake anali eni eni okwiya koma chakwelayu kwao kweni kweni ndikut?
@finchiadriano
@finchiadriano 7 сағат бұрын
Watching from Mozambique
@StevenJosphat-q9t
@StevenJosphat-q9t 6 сағат бұрын
❤❤❤
@stevezulu2108
@stevezulu2108 23 минут бұрын
Kamuzu was a real doctor, not Chakwera, a pastor. He also had back up from the apartheid regime of South african.
@LucksonChipofya
@LucksonChipofya 7 сағат бұрын
Uyu chakwera sanabwere ngati mpulumutsi wa dziko mulungu watiwonetsa atumiki ake kuti ndiwonyenga mawu a malemu chilima yakwana nthawi yoti tisiye kumakhulupilira azibutsa kuchokera 2022 chilima adabwera poyera kudandaula kuti ambiri akalimbikitsa kuti chakwera atsogole adali mazibutsa koma munasankhanso kukhala chete osayankhapo or mwina kungotsutsana naye malemu chilima lero ndi izi chilima alimumanda tiziti ndinudi azibutsa kapena atumiki adakana.
@wellskhoriyo8586
@wellskhoriyo8586 6 сағат бұрын
We should not allow this kind of nonsense lake malawi is ours.
@DivineMercy-df2pu
@DivineMercy-df2pu 53 минут бұрын
Chakwera is a useless president just Wait for Mozambique ibwera nayo poyela kuzapanga claim Likoma Island.If Chakwera will win 2025 MALAWI we are doomed.
@wellskhoriyo8586
@wellskhoriyo8586 6 сағат бұрын
We should not allow this kind of nonsense lake malawi is ours,this is cryz
@YusufuKaifa-r2y
@YusufuKaifa-r2y 7 сағат бұрын
Chakwera is not Malawian coming from another country come in malawi to distroy malawi only nows nothing about malawi
@MikeMbewe-mb9it
@MikeMbewe-mb9it 4 сағат бұрын
JuniorHal Muwafuse athu omwe amamu votera chakwera iyee alingant khoro lathu koma ndikholo lanji rosava kuwawa ana ake akamalila kholo lomwe ine ndimaliziwa mwana akalila limathamaga kufusa kut wakumenya ndani koma chakwela dziko munoaliyese akudandaula iyezosamukhula or
@petertaulo8014
@petertaulo8014 5 сағат бұрын
Ngati amakonda ndalama kwambili azigullisa Ana ake
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@GabrielGasiyo-k3o
@GabrielGasiyo-k3o 6 сағат бұрын
Tanzania tingomenyana nayo kuti nkhani iyambire pamenepo
@CHIMWEMWEKASANGAA
@CHIMWEMWEKASANGAA Сағат бұрын
Mungamenyane ndi Tanzania inu 😂😂 mukayambira pati anthu oti or ndege mulibe , machita kubwereka
@wellskhoriyo8586
@wellskhoriyo8586 6 сағат бұрын
We should not allow this kind of nonsense lake malawi is ours,this is cryz
小丑女COCO的审判。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:53
超人不会飞
Рет қаралды 16 МЛН
СИНИЙ ИНЕЙ УЖЕ ВЫШЕЛ!❄️
01:01
DO$HIK
Рет қаралды 3,3 МЛН
Quando A Diferença De Altura É Muito Grande 😲😂
00:12
Mari Maria
Рет қаралды 45 МЛН
A Chakwera Mwalola Nyanja Ipite? - Bon Kalindo
15:40
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 728
Ku Ndirande A Kabambe Alandilidwa 100 Percent
2:10
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,6 М.
Atupele Muluzi Boma - Nyimbo Za Ndale
4:47
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,3 М.
Boma La Chakwera Limakomela Anthu Olimbikila - Mzika
1:57
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 157
小丑女COCO的审判。#天使 #小丑 #超人不会飞
00:53
超人不会飞
Рет қаралды 16 МЛН