A DPP Mwafulumila Kulira Shafie Hassan

  Рет қаралды 1,636

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

On Nyasa VoiceBox, Shafie Hassan, also known as Comrade Nganga, tells the DPP that they are crying foul far too early. If they have grievances about how the MEC is conducting voter registration and preparing for the 2025 election, they can take these issues to court or return to Parliament to amend the law, as everything the MEC does is codified in Malawian law, which all MPs, including DPP MPs, are aware of. Press briefings are ineffective.
Ku Nyasa Voicebox, Shafie Hassan, yemwe amadziwikanso kuti Comrade Nganga, auza a DPP kuti afulumilia kulira. Ngati ali ndi madandaulo pa momwe bungwe la MEC likuyendetsera kalembera wa ovota komanso kukonzekera chisankho cha 2025, atha kutengera nkhanizi kukhoti kapena kubwerera ku Nyumba ya Malamulo kuti ikakonzenso lamuloli chifukwa zonse zomwe bungwe la MEC likuchita zimatsata malamulo a dziko la Malawi, zomwe aphungu onse. kuphatikizapo aphungu a DPP, akudziwa. Zokambirana za atolankhani sizothandiza.
#malawi wi

Пікірлер: 53
@RoseThindwa
@RoseThindwa Күн бұрын
Za Zii Ngati mwatumidwa Malawi's sitikufuna machine wo
@MulowokaBlessings
@MulowokaBlessings Күн бұрын
Ukunena zoona big DPP alibe nzeru nkhalamba zilibe nzeru 😂😂😂 DPP akuyiopa game yakulila
@Twayaibrahim
@Twayaibrahim Күн бұрын
Ayakhula bwno abambo awa crias koma bvuto akuoposition mangot munthu walandra ndalama Malo mobvetsera bwno bravo Mr
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo Күн бұрын
More 🔥🔥🔥🔥🔥Shafie DPP ikudziwiratu Kuti sazawina ndiye pachifukwa cha Ichi akungofuna kupasa anthu mmalawi Muno chiganizo oti masankho abeledwa pamene akudziwa Kuti zawo sizilibwino
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Mkulu uyu wandila ndalama ndipo ndi mbuzi yeniyeni ......chisilu cha munthu
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo Күн бұрын
Mkulu uyu ndiozindikila kwambiri
@StanleyMunthali-s1d
@StanleyMunthali-s1d Күн бұрын
These guys are just blindfolding us . They forget 2025 is around the corner , Malawians panopa anasamba mokweza. Now they telling Malawians as if they are Angels now .They too should confess their past sins and be born again!
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Mkulu iwe ndi mbuzi Kodi chipani chinali ku press briefing anali a Dpp okha ....mbuzi iyi
@ChimwemweSimwela
@ChimwemweSimwela Күн бұрын
Anganga mwayankhula bwino
@MartinLondon-l4l
@MartinLondon-l4l Күн бұрын
Comrade nganga shaffi hassan ulemu wako mumatha kuyang'ana mbali zonse
@yassinn5634
@yassinn5634 Күн бұрын
Ngati walandira ndiye kuti wachita bwino kuti aziphunzitse mbutuma kuti zizindikire kuti malamulo amapangidwa bwanji ndipo amapanga ndani? MP? KAPENA ATOLANKHANI?
@yassinn5634
@yassinn5634 Күн бұрын
NGANGA NDAKUTAYIRANI KAMTENGO NDINU MUNTHU OZINDIKIRA NGATI SI ABOMA LIMODZI NDI ACHINA SALLO.AUZE NA AMENE ANALOWA MKALASI AMVA.MBUTUMA ZITSALA .
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb Күн бұрын
Chisulu chadyera ichi
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb Күн бұрын
Dyera galu uyu
@YamieManda
@YamieManda 21 сағат бұрын
Macadet akufuna Jane Assah
@MulowokaBlessings
@MulowokaBlessings Күн бұрын
Taonani akungotukwana basi a DPP ndiye kutukwana mukutukwamako mwati muzaiona vote mmmmmm ndakayika chifukwa anthu inu ulemu milibe kuyambila magogo Anu aja opanda Manu mukamwa zochitanso chimozizi 😂😂😂 anthu simungalamulile ziko ndinu okanika komanso otembeleledwa MCP 2025 ikuwina whether you like or not
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo Күн бұрын
DPP afford ndi UTM alira kale 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 bwanji bosangonena Kuti a MCP apitilize Kuti ndalama zisaonongeke
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Күн бұрын
Atupele uja osazamuphwekesa UDF sitilola kukhala munkhwapa mwa MCP or DPP sitikuifuna tipita tokha kumasakho win or lose period ❤❤❤
@Twayaibrahim
@Twayaibrahim Күн бұрын
Wazxiwa het? 😂
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Күн бұрын
Malawi mayi ako iwe mapwala ako anamvomera ndani mapwala ako ndi kumangochi kwanuko andu osapita ku school akumangochi mwafikapo ndi umbuli wanuwo koma ine kumangochi bwanji kodi ayao awa
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 21 сағат бұрын
Zoona zoti kuli opposition suzimaziwika ali nziiii kuopa kuti angayalusidwenso nawonso ali ndi Magazi mmanja mwawo ndiye nkivuta kudzuzula Malawi anainongeka basi
@AssanMwapi
@AssanMwapi Күн бұрын
Kulakhula mwazeru nganga
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe Күн бұрын
Okay chabwino koma ifeee chakwera sitifuna aiiiiiiiii
@HusseinBinali-z1s
@HusseinBinali-z1s 19 сағат бұрын
Wawo pe olo ryawo soni mmwee ilipyala mkawecheta soni yepyala yenuyo nambo soni Naga tummanye timtoche mmangochi muno
@christopherchikankhen
@christopherchikankhen Күн бұрын
Mau ndithu
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 Күн бұрын
Iwe sia DPP okha galu iwe uzinva,,,, 😂😂😂😂
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li Күн бұрын
Pansete.... Pako... nganga. ku... mangochi ko..... wamva
@FranksonKennethChipande
@FranksonKennethChipande Күн бұрын
Awa a DPP game akuiopa aona kuti palibe chawo 2025
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Күн бұрын
Inunso muli ndi bodza muli mbali iti kweni kweni dpp 2025 boma
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li Күн бұрын
Nanunso.. angaang. . mumalitenga..... mbali.... ya. Mcp.... Osaganiza ... Zidzukulu .. zako. . bwanji ........
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Anthu opusa omwecamalandila ndalama .... Zopusa zenizeni ......iweyo ukuona ngati ku dpp kuli mbuli eti ....akulu inu ndi mbuli yeniyeni ndipo simukuziwa zomwe zikuchitika
@DerickChudza
@DerickChudza Күн бұрын
Sakunama anthu aku dpp akuganiza ngati Ana, achina chaponda anakalamba musaiwale munthu akakula zelu zimabwelela a maganiza ngati mwana wazaka ziwili
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px Күн бұрын
mkuluyi akunena Zowona koma poti ma supporters a DPP adazolowera kutukwana apa mutukwanaso, MCP ikungokudodani ili pheee, ndiye musadatitu mulimbe kutukwanaku mpaka 2030 woooo.
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Күн бұрын
Garu iwe kape weni weni waiona ndi DPP basi zakokhalira basi pamtumbo pako chsru chidebe chamunthu osamakadya ndalam zo uko bwanji nyani palukundu penipo mpikene mwedyo anambwa
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u Күн бұрын
Kulirako kukufunika panopa Chifukwa zisankhozo is around the corner Kodi Achakwera adalowela machine Achakwera sadalowere ma vote Achakwera adalowera ma demo Tingopanga ma demo basi kuti atuluke boma
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Күн бұрын
Iwe namachede ngati watumidwa pwala lako ife machine awa sitikuwafuna manya pako iwe hassan
@ISMAELNKWATULANKWATULA
@ISMAELNKWATULANKWATULA Күн бұрын
Kape akungobwelenza kulakhula kopusa komanso kunali zipani zingapo ukungochula DPP chifukwa chiyani? akuti zikomo kwambiri muchomeyi kkkkkkk dzoba iwe
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Kodi mkulu ameneyi mdiwakuti .....chisilu cha munthu ochi
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Күн бұрын
Akuti ku Mangochi
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr Күн бұрын
Zoti majority rules umayimvetsetsa koma, odambana mkamwa iwe? Mboliyako
@PrinceChapola
@PrinceChapola 16 сағат бұрын
Kodi inu adpp munthu akakuzuzulani inu mukungoti wapasidwa ndrama Kodi inuyo bwanji mupite Nanu mukalandile ndramazo bwanji inu anthu opusa inu Kodi inu simumszuzulidwa panja ndinu anthu osakhululuka ngati nkhalamba yanu ija inuyo kutani Kodi?? Mumafunakuti zikoli muzingolamula inu nokha basi anthu osowa fundo inu dziko lidakukanikani anthu muwauza chani kuti akumveleni nkhani pa nsonkhano kumangotukwsna basi zaziiii
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr Күн бұрын
Wakutuma Mtenje?
@yassinn5634
@yassinn5634 Күн бұрын
PALI MWAMBI WAKUTI TUMIZANI MBAVA IKAGWIRE MBAVA. DPP NDI MBAVA POKHUDZA NKHANI YAZISANKHO. UMBONI ULIPO PITANI MUKAONE UMBONIWO KUKHOTHI KUTI ANABELA ZISANKHO.NDIYE CHIFUKWA CHAKE AKUOPA ANZAO APANGA ZOMWE ANABELA IWOWO.
@yassinn5634
@yassinn5634 Күн бұрын
Ngangatu mukuoneka kuti ndinu munthu odziwa kuchita analyse zinthu. Nganga inuyo ofunika kuchoka ku Mangochi chifukwa ndinu munthu oyang"ana patali. Chifukwatu ku meneko anthu ambiri amangotsatira ziri zonse zomwe yakamba DPP. ONSE AKUKUTUKWANANI APA KUTI MWAFUFUZE MUPEZA AMBIRI NDI MBUTUMA MKALASI NDIYE KUTI ANATHERA MU STD
@yassinn5634
@yassinn5634 Күн бұрын
Atupeletu mdi OPHUNZIRA NDIPONSO NDI OZINDIKIRA. KUNGOTI VUTO NDI ANTHU AMATSOGOLERAWO. A BAKILI ANANENA KALE ZOKHUDZA OTSATIRA CHIPANI CHA UDF NDISACHITE KUBWEREZA PANO ANAZIMVERA OKHA
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Күн бұрын
Kodi iweyo ukunena zopusaz osaganizra ana ako otuwa aja adzakhal bwanji mwe alukundu pathako pako
@yassinn5634
@yassinn5634 Күн бұрын
A Shamimu za anthu OSAMBA IZI
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Күн бұрын
@@yassinn5634 amakobiri osati za anthu osauka ngt ine panopa eyetu zokomera andlama inu nanga kampopa ngolo mphawi otheratu okudya zotoleza ngt ine pano mkumatan dziko ndilanu ili znse mzanu zmwe
@JoelKacheche-x6i
@JoelKacheche-x6i Күн бұрын
Mwayankhula zoona lemi wanu anthu oganiza mwachilungamo ngati inu ndiwomwe tikuwafuna,dpp ndichipani chama propaganda komanso kusokoneza,sangakane makina ovotera komanso kumukana chairman wa electrol commission siku la lero,malamulo aziko lino anapereka kale mphamvu kwa chairman kugula makina amenewa,ntambo asakupusiseni nayenso ndiwosokonekera kwambiri
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Күн бұрын
Chili kwa anzanu chaipa mbuzi iwe. Sudziwa ntchito yoitanira atola nkhan kut ndikufuna uthenga ufike palipose... Am not member of dpp but if I lose my data listening stupit story from MCP members.... Mmmmm I feel bored... Therefore I just say had I know before I couldn't open it
@eliasMwamba-q5f
@eliasMwamba-q5f Күн бұрын
Pansetepako nyapapi
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Күн бұрын
iwe mapwala ako iwe mbunzi yachabe chabe
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Күн бұрын
Patumbo pako iwe ukuziwa chani iwe
BILLY MALATA UJA WAONA ZOKUDA - CHAKWERA NDI KALINDO WABODZA NDI CHAKWERA
13:37
Help Me Celebrate! 😍🙏
00:35
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 87 МЛН
Don't look down on anyone#devil  #lilith  #funny  #shorts
00:12
Devil Lilith
Рет қаралды 47 МЛН
Will A Basketball Boat Hold My Weight?
00:30
MrBeast
Рет қаралды 89 МЛН
Fake watermelon by Secret Vlog
00:16
Secret Vlog
Рет қаралды 18 МЛН
DPP SENDERA SISTERS_AYAMBA KALE KUNJENJEMELA
4:37
DEMOCRATIC PROGRESSIVE PARTY - DPP TV
Рет қаралды 1,6 М.
SENDERA SISTERS_TUWASAKA_ 2024
4:47
DEMOCRATIC PROGRESSIVE PARTY - DPP TV
Рет қаралды 2,1 М.
A DPP System Ya MEC Amalowetsa Data Ya Fake - Ken Msonda
4:09
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,7 М.
Enough Is Enough - Bon Kalindo
15:44
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1 М.
Machine obera chisankho anafika kale mdziko muno
12:27
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 17 М.
Help Me Celebrate! 😍🙏
00:35
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 87 МЛН