ZODABWITSA MNYAMATA WINA YEMWE ANAMWALIRA WADZUKASO NDIPO AKULONGOSOLA ZONSE KU MALAWI BOMA LA ZOMBA

  Рет қаралды 55,823

Grant Bandah

Grant Bandah

Күн бұрын

Пікірлер: 80
@JosephineMkandawire-b2s
@JosephineMkandawire-b2s 6 ай бұрын
Abel thank you for what you’re doing. Tadziwa zambiri zikuchitika,
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 6 ай бұрын
Koma Pena Mulungu zimene amapanga eeeh zodabwitsa ndithu🙌🙌
@MateusErasmoGastene
@MateusErasmoGastene 6 ай бұрын
Zonadi
@MateusErasmoGastene
@MateusErasmoGastene 6 ай бұрын
Ndi chissomo ca ambuye!❤
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 3 ай бұрын
Mulungu ndi wabwino nthawi zonse❤❤❤
@Ester-c6y9t
@Ester-c6y9t 12 күн бұрын
Munthuyi akunena zoona kumwamba kulandile ulemu amen
@ShadreckLevi
@ShadreckLevi 6 ай бұрын
Abelu zuranga I like him the the way he is doing his job
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 6 ай бұрын
Nkhani iyi ndi yoona kumene zathu wina adamwalira kuno ku South Africa koma adakapezeka ku Malawi ali moyo pano akufotokoza chilichose
@sarahgalleta9240
@sarahgalleta9240 4 ай бұрын
Kulakwa 😢chinamuchitikira ndichan?
@FrankKambwani
@FrankKambwani 6 ай бұрын
Yehova amayika njira popanda njira.Ambuye mulemekezeke amen
@FlamigosParrow
@FlamigosParrow 23 сағат бұрын
Amen 🙏 brother
@DaveKachala-of6hh
@DaveKachala-of6hh 6 ай бұрын
Amen and amen
@ezilamasaka3637
@ezilamasaka3637 6 ай бұрын
Ndinakumana naye mnyamata ameyu ku Lilongwe and andipemphandi chithazo, but malingana ndi mmene amaonekeradi ndinakana poti kunja unaopsa uku, umati ndikuthandidza munthu nati akupwyeteke
@ulemuchisale
@ulemuchisale 6 ай бұрын
Praise God ❤
@GreatChipande
@GreatChipande 4 күн бұрын
Ndipempheko...mukamafusa mafuso muztha kukhalako phee kupeleka mpata kwa ofusidwa afotokoze...osat pang'ono fuso fuso ayiii😮
@ASHI-TECH
@ASHI-TECH 4 ай бұрын
Amen
@CathyNyirenda-iw7ld
@CathyNyirenda-iw7ld 5 ай бұрын
Government must change this law ,it's the poor always fill the pain 😢😢
@FelixLingston
@FelixLingston 4 ай бұрын
😅😅😅 pena ndikuona ngati akunama mmayankhulidwe akewo😅😅😅
@chapsonchadewa1373
@chapsonchadewa1373 4 ай бұрын
Amen Amen yehova wapitilile kukutetezani alongosi
@AwetuAmidu-u2j
@AwetuAmidu-u2j 3 ай бұрын
Mulungu ndi mulungu
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 6 ай бұрын
Alihamudulillah
@EdisonNakulenga
@EdisonNakulenga 6 ай бұрын
Haleluya mulungudiodabwisa
@SamisonLevison-z5p
@SamisonLevison-z5p 2 ай бұрын
Ndili kuno ku Mozambique.Nkhani izi sizachilendo,kuno weki yatha anthu okwana 6 anapezeka atangokhala pa nsew.Akut anali atatopa nkuyenda.Anamwalila 14 yrs ago
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 6 ай бұрын
Ndipo inu ziko iri anthu achuma awa mlungu azawarange ngati chakwera uzarangidwa unamupha chirima osarakwa
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 6 ай бұрын
Iwe ndwe wachamb wav chilima nd ngzi chab kapen ulindiumbon chakwela alibe vuto km iwe
@RemzyMwenecho-oz5oc
@RemzyMwenecho-oz5oc 6 ай бұрын
akumanga ulinawo uboni
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka 4 ай бұрын
Enanu ndiye mwazilowetsaso ku ndale.
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka 4 ай бұрын
Idali Menjaitisi.Malungo akulu mmalo mokhala naye mchipatala iwo anathawa naye ulendo naye kwa sing'anga basi munthu mkumwalira.Lero mukusunga munthu wina mwati ndi wanu.
@EmoMphande-ui3xi
@EmoMphande-ui3xi 3 ай бұрын
Mommy mupaka kuopseza kuti akumanga 😂😂😂😂 ndipo ndaseka amanga ndani galu ameneyo muuze azamange ine chakwera koma ayesese kubwera ndi apolisi ose akumalawi kuphatikiza aku Israel, chabe ali mu mumadzi Meneyo ​@@RemzyMwenecho-oz5oc
@sakalameck
@sakalameck 6 ай бұрын
Zabwino zonse Willy!!
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 6 ай бұрын
Abele wakumana nazotu apa chilungamo munthuyo akufotokoza
@PleasantKamwana
@PleasantKamwana 4 ай бұрын
aaaa koma akuyankha zosiyana ndi funso, ndiye ife tigwile ziti kwenikweni
@EllenKapinga-rm9zm
@EllenKapinga-rm9zm 7 күн бұрын
Abel uzimusiyako kuti alongosole, ukuchulukitsa nkhani
@chicconambesa4973
@chicconambesa4973 3 ай бұрын
Wow
@TsakhoChimwala
@TsakhoChimwala Ай бұрын
Ameni
@TopG-h4l
@TopG-h4l 5 ай бұрын
Zoonadi zimenezo kusalima zinachhika pano pakana pano adabeleka mwana
@ChippaKaira-g6h
@ChippaKaira-g6h 4 ай бұрын
Ndithokoze Mulungu mwatilibikisa
@BlessingsUndih
@BlessingsUndih 2 ай бұрын
Pamenapa kukanakhala kotheka achipatala ndikofunika atengepo mbali poyedza magazi
@eunicethokomanda8911
@eunicethokomanda8911 4 ай бұрын
Mmm kaya ndakayika ngti akunena xoona
@DanChimaliro-j7f
@DanChimaliro-j7f Ай бұрын
Mulungu akule ife tichepe
@EllenKapinga-rm9zm
@EllenKapinga-rm9zm 7 күн бұрын
Abel ukulankhula kwambiri sukumupatsa mpata munthuyo kuti atifotokozere bwino
@TriciaDeborah
@TriciaDeborah 5 ай бұрын
Yooooo zithu zake
@ChrissyZima
@ChrissyZima 3 ай бұрын
Ineso ndikuona ngati akunama bwanji sakufotokoza bwino
@ElickGeorge-l5w
@ElickGeorge-l5w 6 күн бұрын
Komano poyamba pajatu mumati kuli matenda Amazon nde patsaxikana ndi afumu mwagwilana
@TamalaKambanje
@TamalaKambanje Ай бұрын
Abelo ndimafuna number yako ndikufuna ndinthandize munthuyu
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 4 ай бұрын
Kofi bwanji osangofotokoza za mmene unabwerela kudziko kuno ukungobwerezabwereza zoti ufiti kulibe,ife tikufikilira za mmene iwe unafikira kukhomo kwamakolo ako ukungoti kumalawi ufiti kulibe mobwerezabwereza
@Laugh-l8s
@Laugh-l8s 4 ай бұрын
Ine ndikuona ngati nkhani yonseyi ndiyabodza aah
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 4 ай бұрын
@@Laugh-l8s eti amwali?olo ine sizikundigwura mtima antaa
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 2 ай бұрын
Zizakhala zowona zikazachitika kwanu,,,ine ndili ndichikhulupililo chonse
@PeterHartzeberg
@PeterHartzeberg 6 ай бұрын
Kwa mulungu wamoyo kulibe chobisika,, mulungu apitize kugwila ntchito yake
@nelsonmwanache8692
@nelsonmwanache8692 2 ай бұрын
Ku Malawi kulibe ufiti...nkhani yake yokha yokha...kumalawi kulibe ufiti
@FrankYohane
@FrankYohane 6 ай бұрын
Mulimekeze Yehova dzikoli likupita kuti tilikumapeto
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 4 ай бұрын
Ukanafotokoza bwinobwinooo zammene unabwelera kuno kudziko kuno osamangofotokoza zaufitizo iyayi kambani zakubwera kwanu anthu titolepo fundo yogwilika chifukwa chochulutsa zotankhulayankhula anthu sangakukhulupilire
@AfricanChina-im1op
@AfricanChina-im1op 3 ай бұрын
Ngat ndizoona akuziwa ndimulungu
@frankchiwawa4795
@frankchiwawa4795 5 ай бұрын
Eish
@ListerMkandawire
@ListerMkandawire 6 ай бұрын
Last days
@IdaChiwanda-i2f
@IdaChiwanda-i2f 9 күн бұрын
Zikundikaikitsa, sakufotokoza bwino uyu
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka 4 ай бұрын
Palibe akupereka umboni owona apa.akusunga munthu wa eni awa
@FauzaTabu
@FauzaTabu 3 ай бұрын
Amayi amakanao amakhala kuti amadziwapo kanthu
@EmoMphande-ui3xi
@EmoMphande-ui3xi 3 ай бұрын
Koma zangovuta popeza ufiti kumalawi amati ufiti kulibe, akanapempheratu uyu asalawo kutulukaso
@LevisNyasulu
@LevisNyasulu 4 ай бұрын
Uzamupitile alape akapitiliza aziwone nayee
@marryrobert7092
@marryrobert7092 6 ай бұрын
Wamaboza nyamatayo aaaaaa
@IssacMateyo
@IssacMateyo 6 ай бұрын
Wabodza ndiweyo kaya palibepo chimene chikukukhudzapo kaya iweyo kwako ndikuvela basi
@SevioursAbson
@SevioursAbson 5 ай бұрын
Fiti iweyo usatipusitsepo apa
@SevioursAbson
@SevioursAbson 5 ай бұрын
Wabodza bwanji umbon oseu
@EmoMphande-ui3xi
@EmoMphande-ui3xi 3 ай бұрын
Galu ameneyo mwana wa chikangawa uyo umboni oseu ukat zaboza? Ukufunika kuzakuphera kamwana kako iwe
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka 4 ай бұрын
Dramma yeniyeni.
@BenedictChikaoneka
@BenedictChikaoneka 4 ай бұрын
Kodi anthu enanu bwanji??? Nkhani imeneyi siyoona ndi bodza lapoyerayera.koma enanu mpaka kumakhulupilira zimenezi? Kukhulupirira za matsenga basi.Khulupilirani Mulungu wamoyo basi zinazi ayi
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 2 ай бұрын
Mulungu akukhululukile iwe kwanu ko sizinayambe zachitikapo but me ndikukhulupilila ndi mtima wanga onse
@LacksonLungu-e2q
@LacksonLungu-e2q 6 ай бұрын
Tingawapeze bwanji
@MtenjeHassan
@MtenjeHassan 6 ай бұрын
Nyamatayi akundionekera ochenjera kwambir, watumidwa ameneyi... iyaaa
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 4 ай бұрын
Ineso akundibowa mmalo mofotikoza zamabweredwe ake akungokimbikira zakuti kumalawi ufiti kulibe mmene wayambilaa akubowaso kobasi
@AlinaphyChavuta
@AlinaphyChavuta 4 ай бұрын
Ai ndikusagwila kwa mutu uyu but Zina akukambazo ndizoona inuu anthu amapanga chipongwe ana adzawo
@MonicaMtambalika
@MonicaMtambalika 3 ай бұрын
Uyu ndye ndiwabwno bwno,
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 6 ай бұрын
Zoonadi anthu awa akufanana koma akafukule mandamo DN a
@Zamwano
@Zamwano 6 ай бұрын
Km Ambuye atichitire chifundo
@phillkaunda5623
@phillkaunda5623 3 ай бұрын
I don't believe this man.this is not true
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 2 ай бұрын
Ukadzaziwona kwanu uzavomereza but ithink iweyo ukudziwapo kathu
@EllenKapinga-rm9zm
@EllenKapinga-rm9zm 7 күн бұрын
inu pitani ku chigwiri mukatenge njinga zopita kwa a Chala anthu akufa mwamatsenga akudzuka uku, nthawi yakwana Mulungu akuyika pa.mbalambana za umfiti
@FrancisZuru
@FrancisZuru 6 ай бұрын
Amen and Amen
Omwalira apezeka wa moyo
48:05
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 85 М.
Правильный подход к детям
00:18
Beatrise
Рет қаралды 11 МЛН
黑天使被操控了#short #angel #clown
00:40
Super Beauty team
Рет қаралды 61 МЛН
Ogulitsa Ziwalo Xa Anthu  Agwida Ku Thyolo.
1:27:49
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 248 М.
CRUISE 5   ELIYA NZERU WILLIAM
1:20:13
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 430 М.
Chegutu : Ruvimbo wekuurairwa $100 onzi opfuka asati avigwa
1:03:06
CYCLONE FREDDY FUNDRAISING DRAMA #malawi
1:31:45
Kanema Online
Рет қаралды 545 М.
Mubarak Munyagwa Today; Enkalu Ku Mulambo Gwa Ssegirinya
38:22
Inside Story Uganda
Рет қаралды 1,7 М.
NKHANI ZA MA BOMA 1 APRIL MALAWI 2023
11:15
KWACHA TV
Рет қаралды 8 М.
Continu.. Part 2
37:28
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 174 М.
Правильный подход к детям
00:18
Beatrise
Рет қаралды 11 МЛН