Zikomo CDEDI, we salute your leadership Mr Namiwa & team.
@AnnieNyirenda-d5t17 күн бұрын
Wauuuuuu namiwa ulemu wanu may God protect you and bless you more fire
@DonkumatePhiri17 күн бұрын
May God bless you sir Namiwa, and we release warrior Angels to protect you sir, we need people who can stand on the truth like this.
@JosephIsaac-s1c17 күн бұрын
As a Malawian we are tired of Chakwera is cruel and careless mn enough is enough must pack and go no mercy
@SherifaG.Mlelemba17 күн бұрын
Musowa....Chilungamotu chikuwawa,akusakani....GOD HAVE MERCY AND PROTECT YOU GUYZ
@MussaAli-h4i17 күн бұрын
Thanks namiwa god will bless you
@EmercianahKasiku-en6hl17 күн бұрын
Salute Mr Namiwa keep it up mpakana chilungamo chake chidziwike
@BenaSamuel17 күн бұрын
Koma kantande amandiwaza amapanga zithu ngat mwana wokulila mu ghetto zowonadi Koma gyz mumandipezesa chochita mukatulusa video yanu ❤❤❤❤❤❤
@DadTshepo17 күн бұрын
God Bless you Mr Namiwa
@ThomasSalaka17 күн бұрын
Keep up Namiwa , may the good.God continue to protect you
@GeraldChilundu-e3v17 күн бұрын
Namiwa big up. Apaneni amenewo. Ngozi anachita kukonza
@GeorgeChumah-l5h12 күн бұрын
God is with u mr Namiwa no fear
@mmadimmadi829717 күн бұрын
May God Almighty, please, save Comrade Namiwa. May He also make a million more Namiwas in our motherland!
@BurunoMbewu17 күн бұрын
Namiwa. Uja ndikatundu kwambili God bless you amalawi abomawa akutitoladi hvy
@BlessingsGama-j3r17 күн бұрын
More fire Apondeni pamtima. Aliyense wosapota mcp adapha nawo 😢
@CharityMkandawire-t8u17 күн бұрын
Akungo bwebwetatu azibale a anthu onse amene anatisiya sakugona tuloyi akupemphela kuti mulungu awawonese cheni cheni,big up namiwa
@ShinglaiAli-be3yn17 күн бұрын
Koma munthu guys mhu 🙌 kuyesesa kubisa ma umboni koma atah mulungu akukana 😂😂😂
@JACKSONHULUWA-j2n17 күн бұрын
May good Lord protect and protect you
@AbdulJohn-t7l17 күн бұрын
Mr Namiwa more fire apanikizeni awulule chomwe anthu awa anachita ma futso osewa ndi omveka bwino
@EryvinMhango-zl3oh12 күн бұрын
Rip biyeni😭😭😭😭😭
@JACKSONHULUWA-j2n17 күн бұрын
"Kodi maliro a kasambala anali opambana bwanji kuti ayendege pomwe ma politician Ena samapasidwa ndege akamwalira?" Best question
@PempheroMoleni16 күн бұрын
Anali Lawyer komaso zimawakhuza aboma zimenezo
@SliviaJosephy9 күн бұрын
Inali nyambo yofuna kuphera anthu
@ChristopherNikola15 күн бұрын
Namiwa more fire
@ibrahimbamusi10917 күн бұрын
Namiwa ndi number one
@MphatsoBasikolo17 күн бұрын
It would have been better if Namiwa remained in the commision chifukwa zomwe akufunsazi zikanapezeka mu report muja koma maganizo ake ochoka mu commision anapangitsa kuti report ituluke yosapsa.
@JJ-in-the-hut17 күн бұрын
His fellow commission of inquiry colleagues they were trying to programme him that's why he decided to quit.
@TriciaMalikebu17 күн бұрын
It was good that he didn’t, the Holy Spirit at work. He needed to be out for us to see the weakness of this report. It would have been very difficult for him to challenge the same report that he would have signed for.
@ShinglaiAli-be3yn17 күн бұрын
😂😂😂koma fada mpaka kufufuza ma pic ake akuukwati 🤣🤣🙌🙌🙌
Forsure they nes kuti ndege yikukagwa mhuuuu too bad
@louisbonongwe853712 күн бұрын
Namiwa sakufuna zopepela
@Mahamudu-q6b17 күн бұрын
🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼🙏🏼🤞🤞🤞Yes
@MackzineGoyaz10 күн бұрын
Awa ndakatundu
@lastonkamanga4072Күн бұрын
Very sad ku family yofeledwa
@rashidadan253317 күн бұрын
Mr Sylvester namiwa , muli mugulu losakidwa ndi mcp , akufuna akusemeleni zifukwa within this month of January .
@edsongeorge803217 күн бұрын
ndiwe munthu wopusa kwambiri Kodi ukusangalala ndizomwe zikuchitikazi m'dziko lino ukufuna kuti anthu asanalankhure this is a democratic country my friend
Wreakage ya ndege yogwa pa height 4.5m singaoneke chonchija. Anthu awa alibe manyazi a Chakwera. Angovomereza kuti this was a mission went wrong. Zikhale Ng'oma analakwitsa Chakwera ill advised
Iweyo Namiwa wandisangalatsa kwambiri chifukwa cha umboni umenewo ndiumene unkandipweteka kwambiri Koma mwana ameneyo mmsamalile kwambiri chonde
@calvinjamal711717 күн бұрын
Chilungamo chidziwika wina afune asafune
@Gtamvera71117 күн бұрын
Koma mwawufunisisatu udindo , iwe unalikuti kuti ukapeleke umboni wako? Pomaliza or utayakhula chotani sangadzukeso anthu anamwalila aja ungothapo mawu ako .
@MackzineGoyaz10 күн бұрын
Pangolin namiwa
@louisbonongwe853712 күн бұрын
Kkkkkkk ati even pa ukwati wake amaoneka chonchi.
@MrsokoMrsoko17 күн бұрын
Anamiwa mbambànde
@MackzineGoyaz10 күн бұрын
Ngakhale atola nkhani wo angofunsira mafunso polemekeza ganyu wawo koma the truth is that they had no questions 😂 coz mafunso onse got the answers already 😂
@PercyRoos17 күн бұрын
Namiwa Mulungu azikudalitsani
@InnocentnMbale-zq8pk17 күн бұрын
Wuyu apweteka Mcp sure
@KelvinDickson-c1x15 күн бұрын
Uku ndye kuimvesa kuwawa mcp
@JJ-in-the-hut17 күн бұрын
Koma zaka zino nzosilizadi, ulemu udatha ndithu😂😂😂😂
Muyambe kae mwaitanitsa kunkuyu akatuluse black box, mkulu wa asilikali mabodza amanena pa 10 June aja + plus chakwera iye mwini akanene amene anamuuza KT ndege inakafika ku MZ nkhan ndiya straight forward ngt inalidi ngozingozi , but the moment chakwera akungabe anthu onse mmaudindo omwe amayenera kuchosedwa chifukwa Cha ngozi imenei ndekt chakwera akudziwapo kanthu
@crytoniegrantliffa243117 күн бұрын
Inu mukuti chian? Chilima anachita kuphedwa ndi chakwera basi!!
@altonchikaoneka-684817 күн бұрын
@MzadziWanga kumkuyu sanapanjitse press briefing koma awa asamatisowetse mtendere pamene atasankhidwa ntchitoyo anayithawa zitipindulira chiyani ngati Ali ndi information bwanji osangobweretsa zomwe akuzidziwazo koma izizo sizothandiza koma tikudziwa kuti akudyera momwemo akulandira funding kudzera kuzipani amene Ali katangale chabwino afotokoze Kaye kuti funding ya press briefing iyiwo nanene komwe ayitenga .zomatipusitsa ife ayi ena akupeleka ma comments apawa ndi abungwe lawolomwe amadyeralimodzi
@altonchikaoneka-684817 күн бұрын
@crytoniegrantliffa2431 inu sitingalimbane nanu kagawanani zaumbulizo or inuyo kuti tikufuseni apapa umboni palibe chomwe munganene koma apa tingoti mbuli zikugawana uthenga
Iwe ananakusakha kt ukhale mu comeet muja chifukwa chani iwe unatulukamo . lero ukuyankhula ngat wanzeru. Zonsezi iwe unakazifufuza Amalawi tiye tizikhala pa chilungamo