So many prophecies otsutsana are given as it was in 2019. Tiyeni tidikire 2025 chenicheni chizaziwika. Chachikulu ndi chakuti lets pray for our country kuti Mulungu alitsogolere komaso Mulungu yekha asankhe. Nnazindikira chinthu ichi, azibusaso ndi anthu and amakhala ndi zipani zomwe amazifuna.
@michaelantony60693 ай бұрын
Eeeeee ndipo live amwene izizi izi anthu ambiri asocherapo apa
@ChifuniroInnocent4 ай бұрын
I thank God coz he has given me wisdom to understand the difference between truth n personal interests
@xinalungu96163 ай бұрын
He has talked about ma hammer amene adawadutsa. You mean, God changed his mind because ma hammer anawadutsa in the last elections? Uuuuumh! Something fishy!!! All prophecies start or end by quating a direct speech from God pachichewa (Atero Ambuye). I never heard that in here
@GraceChikosa2 ай бұрын
God bless you Prophet 🎉🎉
@HestingsZiba-d6k3 ай бұрын
Mai joice banda sakufunika mumugwilizano this is powerful words
@RiteRoderick4 ай бұрын
Great man of God, Amen🛐
@MonijaKataika4 ай бұрын
U are right anthu anasiya kulalikira za ufumu wakumwambatu basi nkhani mulemera, ntchito yabwino,banja mupeza, miracle money etc ..zoti tikayenda muchiyero zonsezo automatically timapatsidwa komatu ayi ndithu..God bless u.
@LumbaniNeba-d9n4 ай бұрын
Please Son of living God help us in this country Malawi
@lyiemanganjira97084 ай бұрын
I pray that God should give you more vision for Malawi,, so that we can be saved
Muwalakwitsa inu anzanu,asiyeni apange za ndale,tatipatsani ulaliki wotitengera ku chipulumutso.
@hananianyirenda3 ай бұрын
Ulaliki wa lero ndiumenewu abusa? Sindinanvepo ubwino oyenda ndi yesu nanga bwaaa?🙌
@PatumaCassimu3 ай бұрын
😂😂😂
@AggieGeorge-s3v4 ай бұрын
Ambuye apitilize ku bvumbulusa zobisikazo
@YoungMwacho3 ай бұрын
True Man of God, PP ndi Joyce Banda asawalore, winanso ndi Timothy Mtambo they are devils asawalore mmugwirizano wawo.
@EssauChikope2 ай бұрын
Ndife atumiki achiyanjaniso 2ank 5v19
@ThandekaNyasulu3 ай бұрын
Oh Lord God have mercy on us
@StevekassimSteve2 ай бұрын
Ife tilipano kuvera
@hastingskayange4 ай бұрын
Apa tisabiseko Mau chipani Cha pp sikufunika mu mngwilizano wa Dpp,Afford,Udf ndi UTM...chonde amai osawalora ndi mvundula kuwiri...asatinamizepo ayi akhale ku mcp Koko,maiyu ndiwoipa
@YohanePaul4 ай бұрын
Amen
@FloraBanda-w7t4 ай бұрын
Apatu mwandisekula mmutu😮
@AngellaAnge-p7x4 ай бұрын
Ngakhale asaulule koma anthu adziwa kale kuti ndi amayiwa mvundula madzi ndipo adad sangawalole amayiwa mumgwilizano chifukwa akuwadziwa
Aaaaaaa kaivotele wekha ase nkhalamba yakoyo mxieew 😔
@MWayne03 ай бұрын
Kkkkkk
@TRUSTDAVID-yt5um3 ай бұрын
Mukatero basi mwadyetsera khosa za mulungu i azibusa masiku ano muli busy ndi zochitika za dziko lapasi umalo moti mulalikile za mfumu wa Ambuye yesu muli busy ndi ma prophetic ofuna kupeza ndalama kuchokera kuzipani
@JosephBotoman3 ай бұрын
Basi ku church kumalalikila zandale?
@AgnessKwenda3 ай бұрын
Aliyense akufuna matambala Malawi wavuta uyu😂😂
@Maxielyies3 ай бұрын
Amen Man Of God 🙏🙏🙏 thanks for the good revelations, the country really need APM back to government ❤❤❤
@SaidiMbawa-st6bj4 ай бұрын
Azimayi kwa ma prophet mumafunako chani makamaka
@SabitiChisawa-b6l4 ай бұрын
Azibambo ku mowa amafunako chani???
@ShamilahSaizi4 ай бұрын
Azibambo ku mowa ku mitala mumafunako chani
@EstherDebwe3 ай бұрын
@@SabitiChisawa-b6liiiih Ambuye ana anu atopa kunoo😂😂😂😂
Mbusa mulomwe angayankhule zonyoza Petro zaziiii zenizeni
@ClearKondowe-m3j4 ай бұрын
Ndi zoona atumiki chinthu chokakamila Chimakumphulikila ndi izo lero. Ndikungwilizana nanu Mulungu salakwitsa.
@BrianNantchengwa3 ай бұрын
Osati mukuti nkhalamba koma ndi nkhalamba.
@EuniseMasuku3 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣kma ndaseka kkkkkkkkk a prophet mu church😂😂😂😂😂😂😂
@MathewsNgozo3 ай бұрын
Cadet Wallowa mutchalitchi😂
@DicksonLuka-q2d3 ай бұрын
Chipani #5 ndi pp, sikufunika mugwirizano.
@CharlesBenLongwe3 ай бұрын
Palibepo uzimu apa and sizikumveka😂
@JimmyHau-n4z3 ай бұрын
Kodi imeneyi ndi gospel?
@ThomasChiwaya-qx9mf4 ай бұрын
Truth
@xinalungu96163 ай бұрын
Prophecy ya utsogoleri ikamachoka kwa Mulungu imadziwika. 1) Nrchenjezo lake imakhala ndi CHIPHUNZITSO. Apa chiphunzitso palibe. 2) Prophecy IMAKOMELA or KUDZUDZULA ana a Mulungu. Apa sindinamve 3) Proohecy IMAKHALA MU MAU (Scripture). Apa palibe 4) Prophecy SIICHOKA MU BONGO. Apa sadanenepo sentence yotsatilidwa ndi ATERO AMBUYE 5) Prophecy siisankha mitundu. Koma apa AKUPHA MA ALBINO ndi amene akukondeledwa POTI AKUCHOKERA KUCHIGAWO CHAKWAWO. UUUUU, Abale! Apapa abale, prophecy yalephereka
@HopeMartinKamwana3 ай бұрын
Very
@AlexanderYovatiKhumalo2 ай бұрын
Ulosi obwabwatika.
@chimwemwelungu19344 ай бұрын
I stand to be corrected but This is zakuthupi. The Holy Ghost that I know, I doubt if Angakhale busy saying this. Mulungu akanafuna bwenz DPP ikulamulabe. Zilipo zonyansa zomwe Boma linkapanga under DPP regime which is also happening under MCP regime. Politics is a spirit. Regardless of chipani be it UTM, MCP, PP, PDP, AFORD etc ndale ndi principality and muli zambiri zoipa zomwe zimachitika. Bottom line is that Malawi as a nation we Need Jesus Christ and the Help of the Holy Spirit to deliver this country. We can't bank our hope mwa president or chipani. Tafatsan naye Mulungu and spend Alot of time with Him, azakuululirani zinsinsi zimene inunso zizakusinthani kutumikira kwanu. Mukayamba kusanthula za zipani n atsogoleri Ake you will miss The Voice of God. Mulungu azalephera kukudalirani ndikukugwiritsan ntchito mokuya poona mtima wanu ndi malingaliro anu. Tiyeni timusiye Mulungu. Amadziwa chimene akupanga. Whether president is from God or not koma ngati walolera kuti munthuyo alamulire zilipo zomwe zimachitirabe ubwino iwo akumkonda ndikukhulupilira Mulunguyo. Palibe chipani or president wa muyaya or wa 100%. When you go deeper into the Things of God, Mulungu azakudalirani ndi zinthu zazikulu. Your calling and spiritual gift is more valuable to God than preaching politics. Shalom.
@amosimunthali13683 ай бұрын
Iwe ndiye wanena Chilungamo❤
@LuciusLungu4 ай бұрын
Ndiye wang'alulansoo ngati Nancy ndi Che nkhope.
@JosephBotoman3 ай бұрын
Prophet sakhala wandale
@irenemakwecha7224 ай бұрын
mmm inu tamalalikani za ku mwamba
@MeltonChilambula3 ай бұрын
Muzikauza akazi anu Inu
@BrianNantchengwa3 ай бұрын
Kodi amuna sasonkhana nawo ku mpingo kwanuko. 😅😅😅😅😅
Chi joice banda chisankharemo mmungeilizano wa azizake ndicha kumpha chisatanic
@FlovenaScreenprinters2 ай бұрын
Mmmmmm mwadyatu zambili
@PreciousNeba3 ай бұрын
Uku nde kupusako mulungu sanakuonetselen zakuchikangawa bwanji kufuna kutamika et?
@FranksonKennethChipande3 ай бұрын
Azibusa asiya kutumikira Mulungu pano akupanga ndale
@DayzmondBakker2 ай бұрын
Wa dpp iwe ndachita kuona blue paliponse
@user-ii9ch7oz8n3 ай бұрын
Kodi zinthuzi mukuyendesa bwanji mwasiya za mulungu mukupanga za ndale mukufunako ndalama kuti mumalizise church pitani direct kuwapempha ife boma sitisintha
@tembompeta11073 ай бұрын
😢😢😢😢😢🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
@Felixbanda-q6p3 ай бұрын
izomwe mukunenadzo ndizona and ndinalota ndikuyakhulidwa kut bushiri ali paudani ndimulungu waukulu
@PAULKAMAJOWA-u5k3 ай бұрын
Is that prophecy or politics? Bible says there is no one adzayendese bwino zikoli nd mulungu yekha, so please akhilistu titsegule maso ndkuchapa ubongo.
@MosesDzonzi-em5px2 ай бұрын
Mwanena Zowona achimwene
@BrianNantchengwa3 ай бұрын
Anthuwa muziwaphunzitsa za ufumu wa Mulungu osati kampeni ya dpp mupangayo
@Collingschawanda4 ай бұрын
Iwe usatiyakhulise molakwika Mpando usike koma guys eish!