Powerful skefa. You can't hate your leaders and say you love your nation. Respect to skefa for taking part to spice up this event, one love, peace for mother Malawi. I love you Mr President
@RhulaniMukasi5 ай бұрын
Skefa wachita bwino ndalamazo ndizaife amalawi osazisiira mphavazo ay udyenawo aise umakwana zkatuluka nboma uzaimbeso nyimbo yowaseka agaluo❤
@yusufjaile53175 ай бұрын
This is end of beautiful talent my brother Skeffa Go and ask Nkasa kuti anatha bwanji
@francisfanwellmwanza89275 ай бұрын
How,....? Music is business boss and obviously he was paid handsomely
@GeoffreyMthiko5 ай бұрын
Skeffa akusokola cash mmati akhala bwanji pa Malawi 😂😂😂❤❤
@vukanifracksonchinkonde73245 ай бұрын
Anyone who is against skefa for singing ku convention you are probably faulty in thinking,he sings as business,so he can not fail to go for it because some Malawian who is anti MCP will hate it😂😂😂😂😂😂
Ma biggey kusungunula mafuta mthupi 😂😂mimba kugwelela muja motie kotooooooo😂😂😂😂😂
@RonnMtafya4 ай бұрын
Bartimeus wa ku CHIKANGAWA
@DeliaKaduya5 ай бұрын
Koma ndalama😢😢😢 ayi zikomo SKC what people are doing now in front of your grave? Ambuye imvani kulira kwathu ife a Malawi chifukwa cha imfa yowawa ya abale athu ku Chikangawa kuja, tikudziwa kuti sizatisiya tokha pa ballot paper paja, zaimeni ndi mMalawi aliyense patsiku lachitsankho
@LinesiKanzota-fw7sj4 ай бұрын
Koma zowona Muthu ungamamusapote fumu yoyipa Mmmm
@RitaBan-t7c5 ай бұрын
Wakwiya ndi kamanjekete wagwanayo ndalama ndizomwe waonongazo 😂
@JOHNOlesmasCosmas5 ай бұрын
mukubera nyimbo za DDP a Skefa chimoto aaah ndakutulukan basi
@ShabaniKuswere5 ай бұрын
Bola Chakwera ndi anyamata anzake atambala titha kuti mzachidziwikire kuti akunva kuotcha ,koma sindikudziwa Kuti achina , Nankhumwa,change golo,Ken msonda,Dausi ndi ena aja anachotsedwa muchipani chokoma cha DPP aja akunva bwanji kumeneko aliko😂😂😂😂
@OMEXTWAIBU5 ай бұрын
Dan Lu ndiye tsogolo lake lilipo poti amayimbila Dpp? Inu kodi ndi Mulungu? Tsogolo la Skeffa ili mmanja mwa Mulungu, osati mwa munthu
@SalumNakanjila4 ай бұрын
Ine or skeffa atadzasiya kuyimba koma ndidzaMkondabe chifukwa nyimbo zimene wayimba iyeyo zasintha moyo kwambr
@Randy-er2xo5 ай бұрын
Zaziiiii😂😂😂😂
@ellensambo63235 ай бұрын
Woyimba alibe mbali ❤❤
@collienkapombe86784 ай бұрын
In jesus name , 😢😢😢😢
@JemaxChibwanazulu3 ай бұрын
Kukagwira Dala mabaterry a Mkango utagona uku kkkkkkkkkk
@AyebhoMfumu5 ай бұрын
Koma ndalama.., inaphadi yesu . Skeffa wabwino bwino uja wapenga.😅
@CrinitHaziwelo5 ай бұрын
Eeeee ndalama ndisatana yoo
@WanangwaMfune5 ай бұрын
Nyimbo siyachipani Nanu kkkkkkk koma anthu ena awa
Kodi mesa ankati siwandale?gays let's listen again the Grace chinga's speach,just praying malawi gays🙏🙏🙏uti ndi nkhondo ya kuthupi tiyeni timenye ya uzimu
@SamsonSolomon-rc4ef5 ай бұрын
Ndakutulukani a skeffa
@Felista-m4q4 ай бұрын
Mmmmmm mukuzinamiza
@FelixMngomba5 ай бұрын
Musiyeni muthu akusokola chakudya cha banjalake
@MatressKanyenga-f1z5 ай бұрын
Kutha kwa luso asikefa 😂😂
@MarriamBakalie5 ай бұрын
Skeffa u r finished I'm watching you...
@MaryNgola5 ай бұрын
Km ndrama tiona zinthu 2024🙌
@MosesDzonzi-em5px5 ай бұрын
MCP yanyamukadi apa pa social media pano timapusitsidwa go pa ground anthu ayambaso kuchikonda Chipani cha Mcp Kaya mukufuna Kaya titukwana bwanji koma Chakwera alamulliraso mpaka 2030, pa social media pano pakutipusitsa amalawi Kkkkkk kooomaaaaaa!!!!!!!!!
@Rabeccakaliyati5 ай бұрын
Everyone has got a right tu du wat he/she wants...ndi mene wazionela skeffa minding his own biznes.....
@calvinkhonje6935 ай бұрын
Askeffa be careful zandale zimagwetsa career yamunthu
@LevisoniBandawe5 ай бұрын
Skeffa my artist, apa mwabesa ma fans anu, uziona
@DeenesNurudMeke5 ай бұрын
Ndipo kwambiri
@kangungufoundation20205 ай бұрын
Amalawi muli ndi vuto yamikirani chabe skeffa akuyimbira ziko la malawi kuwonesa chikondi basi amalawi ma jealous ndi ufiti wachuluka
@patricknzima602828 күн бұрын
zoona
@EnipherAyami5 ай бұрын
Mmmmm kma dziko lamalawi kuvetsa chisoni
@jamesjillan96875 ай бұрын
Ndimaona ngati nkasa yekhatu
@SamuyeleJayilosi5 ай бұрын
Brother skeffa malowa ndale u know meaning ya ndale wait koma osazauza anthu osapupuluma posaka ndalama
@ThomsonHarry5 ай бұрын
Ndamutuluka
@EnipherAyami5 ай бұрын
Mmmmmm plz skeffa don'tsupport chakwera plz 😢
@EstherTumanni5 ай бұрын
Safuna ndalama ndindan inu.. Olo muli bread winner mungatan.. Ana atupe ma offers alipo? Nzanu ali mu office mwake,azisake basi
@Josephchiunjila5 ай бұрын
Wakwiya ndindani?
@EmmyYafete5 ай бұрын
Kd skeffa wa ndi wa mcp?iye akugoimba basi kusangalatsa anthu,ndemwat bwa??
@ronaldchirwa25065 ай бұрын
Skeffa this skeffa that aaa inu mwatan kod. .. are u gonna pay his bills? Everyone is hunting for salt
@ChimwemweGwape5 ай бұрын
Skeffa ndakutuluka ndiwe chikangawa part 2
@PetuloJoji5 ай бұрын
Zoonaaaaaaa!Mcp yomweyo
@BillyChisale-m1z4 ай бұрын
Inu uyu siwoyamba kumakayimba mmisokhano ya ndale kunali a Lucious Banda komalizila kwake akut akuyimila UDF a Joseph Tembo nawo ndikuyimila DPP naye uyu skeffa Muva nayeso ndufuna kuyima pa MP sizachilendo fanz izi
@FrancisNyayi5 ай бұрын
Skeffa uja
@LockeEudora-p8p3 ай бұрын
Cassandra Dale
@RittaB0ti5 ай бұрын
Koma ndalama tiona zithu mu 2024
@GeoffreyMthiko5 ай бұрын
Luso ligwire ntchito malipilo ake ndi money basitu