Best way our president must resign and gave this chance to others maybe we can survive but if we wait until next year mmmmmm I'm telling something will happen ndithu. Kusowa kwa mafuta, kusowa kwa ndalama, kukwera kwa zinthu then njala. Malawi next year akhala otani? Zandikwana. No way to survive.
@ChimsyUlemu8 сағат бұрын
Mcp must resign, we are sick n tired with you mafiya s, lakukanikani dziko kuyendetsa
@rashidadan25337 сағат бұрын
After chakwela another ldiot person in malawi is lbrahim matola , Kulila kwa achule mu nsinje sikungalepheletse njovu kumwa madzi , izi adayankhula lbrahim matolayo poikila kumbuyo MCP kuti ikuchitabwinopa ground , Ndiye lelo akuti sakugona tulo likuwasowa chifukwa choti mafuta asowa ?? ayambano kudziwa kuti zinthu sizilibwino kumalawi kuno ???
@thulanimpphiri68739 сағат бұрын
Malawi wake up please. Ziko lilebe atsogoleri tili ndi zikwangwane basi. Anthu akuvutika kome amene mukuti ndi atsogoleri salary yawo ikuyenda koma anthu akuvutika mafuta kodi salary imene akulandila azitsogoleri azikwangwani awa ntchito akugwira kuti? Ali busy kuyenda mumisonkhano kuononga ndalama afunika kuwawumbuza kuwagenda anthu ombwambwana
@ChimsyUlemu8 сағат бұрын
Akagwele uko matolayo asatione ngati ndiye opepela kuti azingotibwatika ndi bodza we will sort u out next year
@MiddayDeleza9 сағат бұрын
Nde zikuchitika tikusendera ku zisankho choncho nde inu a Mcp mungawine? Ndinkona mukungoganiza zodzabera chisankho
Mmalawi muno zinthu sizili pabwino antaa! Cikangawa ndi nduna zace aba folex yonse ndrama ndi zija amagulira oimba simwaona? Dan lu kumenya kugwetsa mumanena ndizimenezi? Iwe cisilu kwambiri ndicifukwa akunyengela mkazi .oyimba nonse munagudwa pa ucisilu pa manu ndi cikangawa wanuo ndanena ndine
@mukhalacheteluhanga60699 сағат бұрын
Izi ndi mbuzi zikulu zikulu kwambiri
@KennethJere-n1d8 сағат бұрын
Panopa tikugula 5ls k40,000
@ChimsyUlemu8 сағат бұрын
Mcp must resign, we are sick n tired with you mafiya s, lakukanikani dziko kuyendetsa