KZ
bin
Негізгі бет
Қазірдің өзінде танымал
Тікелей эфир
Ұнаған бейнелер
Қайтадан қараңыз
Жазылымдар
Кіру
Тіркелу
Ең жақсы KZbin
Фильм және анимация
Автокөліктер мен көлік құралдары
Музыка
Үй жануарлары мен аңдар
Спорт
Ойындар
Комедия
Ойын-сауық
Тәжірибелік нұсқаулар және стиль
Ғылым және технология
MICHAEL USI WAULURA CHINSISI ICHI NDIPO ANTHU AMBIRI ADABWA NGATI ATAKHALEBE MU UTM KAPENA WATULUKA?
29:52
Team Of Promoters Faking the industry, Using my name to Scam Money from Gen Sale. Bosmic Otim react!
3:11
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Леон киллер и Оля Полякова 😹
00:42
Chain Game Strong ⛓️
00:21
When you have a very capricious child 😂😘👍
00:16
TANVANI ZOMWE WANENA MICHEAL USI LERO! ANTHU NDIWODABWA NDI ZIMENEZI
Рет қаралды 3,689
Facebook
Twitter
Жүктеу
1
Жазылу 22 М.
Dreams Media MW
Күн бұрын
Пікірлер
@cosmaschimwaza
2 күн бұрын
Ndiye ngati sanatsatile malamulo nchifukwa chani sunapangise convention yako yotsatila malamulowo 😂😂😂😂
@AlicksonMakata
2 күн бұрын
I ❤❤❤❤❤❤❤you vice president m Usi.
@BrightZionga
2 күн бұрын
Which God you are thanking manganya chikangawa dull
@BarnetMwanyula
2 күн бұрын
Inu akulu mukudwara koma sumudziwa.. ukaopa conversation iwe . End utm ngati itathe akuononga ndiameneyi bac
@Davis-qo4qp
2 күн бұрын
Usi mutu wake sugwira . Zikuwoneka kuti anapengapo!!
@RosinaPatel
2 күн бұрын
Ndiwe WA MCP
@SaidiMbawa-st6bj
2 күн бұрын
Usi alibe vuto ngati wina zikumuwawa apite akasume basi koma izi zili choncho
@innocentkalako7814
2 күн бұрын
nde pangani convention yolongosokayo ka
@StanleyChamasowa
2 күн бұрын
Uyu akungoyenela apondedwe coz akusokoneza
@ThaboyEst
2 күн бұрын
Mukupenga chani zaziiii mxiiii
@ELLENZAPS
2 күн бұрын
Amanganya tangonenani Kut ndinu a mcp komaso okupha ndi chakwera nzakoyo ndiwe chitsiru mmwamba ulimo ugwano anzako ukuwanyoza lelo udzawafuna galu iwe
@ShakiraBiton
2 күн бұрын
Akuluwa misala koma ilimo
@JamesBrown-gx8my
2 күн бұрын
Wapengatu uyu
@mayahIntias
2 күн бұрын
Bambo asikono mubwerere ku adra
@BreezeBarry
2 күн бұрын
Chitsilu chimenechi
@henryphiri6100
2 күн бұрын
Anakutenga kuti ukamuphetse iwe oipa galu Chilima wakoma lero.
@Thokozani-n6d
2 күн бұрын
Koma kweni kweni ari mbari iti saphura kathu ngati aribe mbari yeni yeni
@henryphiri6100
2 күн бұрын
Mkuluyu akungufuna kukhala vice president mpaka September. Munthuyu he oipa. Apatse ndani poti iwe siwa UTM
@RosinaPatel
2 күн бұрын
Munthu uyu mutu sukugwira..paja akumati Boma ndi lomwelitu...usi mukulimbana ndi DK
@PatrickSomanje
2 күн бұрын
Yudas ndiiwe ngalu wachabe
@HarryMsudzula
2 күн бұрын
Kkkkkkk nthawi Zina ndibwino madokotala afike mwachangu paja mwazi wamunthu ophedwa ukati ukuukire
@FrancisNyayi
2 күн бұрын
Congratulations usi pitilizan kutchukisa saulosi thanks
@PeterAkidu
2 күн бұрын
Uku kuyambisa nkhondo Koma sibwino kumavomelexa
@LameckBanda-gk6ri
2 күн бұрын
DPP 2 vs manganya kabambe kuba UTM ndikuyipitsa kuthyolo
@LawrenceBelson
2 күн бұрын
Machende ako maikolo usi unaphesa nzako kamba kofuna udindo komaso unanena wekha kuti umapita kwa chakwera kenako upite kwa chilima chilunga ukuchiziwa kufupika ngati mchimba
@brendachiwamira
2 күн бұрын
Constitution yake yomwei yoti boma ndilomweli.a Usi musasokoneze añthu.ngati muli dolo bwanji mudakanika kukaima nao ku convention.
@MakawaPartrick
2 күн бұрын
Kufa kwa skc wapeza mpata onyobza
@qassimuajaba2512
2 күн бұрын
Usi panyapako
@StanleyChamasowa
2 күн бұрын
Manganya machende ake uyu wachamba galu olephela
@SliviaJosephy
2 күн бұрын
Uyu ofunika amenyedwe bcs ndi chisilu chamuthu,,anali kuti ku convection shupt man
@MathewsMakina-z6n
2 күн бұрын
Akufuna kusokoneza uyu watumidwa ndi chakera uyu satana wachabechabe
@edsonnyasulu5394
2 күн бұрын
Koma manganya uchisilu azafa nawo wasowa kolowela
@JamesChiphwanya-m4v
2 күн бұрын
Komatu ineyo manganya chilichose chomwe amapanga pano chondinyasa chifukwa ndimaona ngati kt ayiwala kuti anali ndani
@EthelKubalasa
2 күн бұрын
Kodi iwe usi lero ukukakamila kukhala wa UTM koma thawi yomwe malemu SKC anali moyo iwe somanusapota ngati running mate wake, mwanji sonayime nawo pa UTM conversion election, kuti athu akusakhe wokha, iwe ndiwe osokoneza, Mr drama king, tasiyilani ena nawo apitilize mosakhale ngati chakwela nzakoyo kukakamila pa undindo koma athu sakumufuna ata.
@emmanuelChitenje
2 күн бұрын
Alibe chipani mpake akukakamila zamasiye
@MichaelChimwala-m2b
2 күн бұрын
Uchoke
@ThomasShuga-z5p
2 күн бұрын
Chakwera anaganiza bwanji kutenga munthu wosagwira Mutu Kuti akhale VP wadziko?
@TakalaniGlenda
2 күн бұрын
Wamisala amanyengana ndi wamisala mnzake ndiye musadabwe akudziwana awiriwa ndithu
@AlfredNazombe-me2ly
2 күн бұрын
Manganya ndichitsiru chamunthu nchifukwa anamupeleka chilima
@JaneKadzuwa
2 күн бұрын
Ndiye ulibe chipani
29:52
MICHAEL USI WAULURA CHINSISI ICHI NDIPO ANTHU AMBIRI ADABWA NGATI ATAKHALEBE MU UTM KAPENA WATULUKA?
Makosana
Рет қаралды 36 М.
3:11
Team Of Promoters Faking the industry, Using my name to Scam Money from Gen Sale. Bosmic Otim react!
ACHOLI DAILY NEWS TV
Рет қаралды 799
00:32
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
00:42
Леон киллер и Оля Полякова 😹
Канал Смеха
Рет қаралды 4,7 МЛН
00:21
Chain Game Strong ⛓️
Anwar Jibawi
Рет қаралды 41 МЛН
00:16
When you have a very capricious child 😂😘👍
Like Asiya
Рет қаралды 18 МЛН
11:04
DR DAVID F MBEWE PULEZIDENT WACHIPANI CHA L.E.F KUTHANDIZA ANTHU AMENE AKHUDZIKA NDI NJALA MACHINGA
King Blesser
Рет қаралды 1,1 М.
18:58
MWAMVA? CHAPONDA ANATUMIDWA NDI MUTHARIKA ATI ANENE IZI LERO ~ NAYE KUMKUYU WANG’ALURA DPP YONSE EEH
BS Malawi
Рет қаралды 3,2 М.
29:55
MPAKA VICE PRESIDENT WADZIKO MICHAEL USI KUYANKHULA IZI PAMBALANGANDA?? UTM AKUIPITITSA KUTI KAYA
AM TV MALAWI
Рет қаралды 17 М.
12:07
Nkhani ya Blackbox si yokambirana; Anthu atopa ndi mabodza a kongeresi
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 58 М.
14:33
SAMEER SULEMAN WAMUNG’ALURA LERO RICHARD CHIMWENDO AKUTI ANANGOKULA MUTU NDI MIMBA KOMA ALIBE NZERU
Makosana
Рет қаралды 94 М.
9:11
Ssaabasajja nkuloopera abantu bo bano baakumaanjanga entakera - Katikkiro #NkuukaMasavu
BBS TEREFAYINA
Рет қаралды 10 М.
26:18
Nkhani Masana | 31 December 2024
Malawi News Update
Рет қаралды 11 М.
51:23
NDE MWAMVA? AKUTITU KUCHOSA MANGANYA KU UTM NDI MISTAKE ~ WAYISHOSHA KABAMBE AWONA IZI KU UTM KOMKO
BS Malawi
Рет қаралды 29 М.
24:34
Palibe Chinsinsi! Imfa ya Saulos Chilima 2025 Revelation.
Human Rights Consultants TV
Рет қаралды 8 М.
12:02
PATRICIA KALIATI ANATENGETSANA NDI JOURNALIST WA KU ZODIAK ATAMUFUNSA FUNSO LOVUTA ILI
Makosana
Рет қаралды 205 М.
00:32
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН