THE COURT (Malawi)

  Рет қаралды 61,862

Malawi News Update

Malawi News Update

Күн бұрын

Пікірлер: 90
@AllenMsowoya
@AllenMsowoya 2 ай бұрын
Koma abambowa ndi omweoso ankati banja lithe chifukwa cha ma ARV , lero ndimboni yaboma🤣🤣🤣
@MadalitsoChasauka
@MadalitsoChasauka Ай бұрын
Ndiwomwewotu kaya
@ustintembo
@ustintembo 22 күн бұрын
This is acting sure.. 🤣🤣
@SaudaKennedy
@SaudaKennedy Ай бұрын
Kkkkk koma zinazi kusowa zochita kumalawi nkhona anthu akungonkhalila maboza zaziiiiiiii
@steveFelix-g4l
@steveFelix-g4l Ай бұрын
Galuyi akuti mboni yaboma akuti kwao mkwa chikowi ku Zomba mesa mulandu wina amati banja lithe ndipo kwao mku mulanje Acting yabwanji
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 2 ай бұрын
Muziika nkhani za nduna apa osati anthu opanda kathu,zachipongwe basi 😢😢😢
@KestonNGUBO
@KestonNGUBO 2 ай бұрын
Ndere imwe
@HenryLaidon-pl9ly
@HenryLaidon-pl9ly 2 ай бұрын
Paja ku court ndi kwa mphawi zopusa basi
@SuccesMaliro
@SuccesMaliro 2 ай бұрын
Kd bwanji simuyankhula Chichewa pakuti nose ndi aMalawi Ku South Africa tikalakwa timadikila Loyer kumalawiso ndiye kwanthu ndikuti zanchamba zimenezo
@AustinMwenda
@AustinMwenda 25 күн бұрын
Kkkkk adha nde kaya kwathu ndi kt kaya kma mw kkkkk
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 ай бұрын
Nkhani zooona zenizeni mukuzisiyaa. Chikangawa akusowatu
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 2 ай бұрын
Etieti
@isabelmartin7567
@isabelmartin7567 2 ай бұрын
Aaaaaaaaaa ndipo Malawi why 😢
@CharlesChilemba
@CharlesChilemba Ай бұрын
Koma adha awa 😂😂😂 asiya zawo lero ndi mboni ayi tathokoza, koma amayi musamamange koma apatseni ndalama akayambe bussness kuti azisamalira ana awowo
@SlyviaPhiri-bd9uu
@SlyviaPhiri-bd9uu 2 ай бұрын
Koma zovesa chisoni kwambiri azimayi ena alibe zeru kwambiri zoonadi kutuma Mwana kukamphempha 🙆🙆🙆💔💔💔
@rexfjonga6159
@rexfjonga6159 2 ай бұрын
Acting iy😂
@CharityGondwe-bw9gs
@CharityGondwe-bw9gs 2 ай бұрын
Talowesani khani yakuchikangawa menemo osati zimenezo. Zaziiiiii
@anastasiakalipalire6260
@anastasiakalipalire6260 2 ай бұрын
Kd abambo awa mesa last WK anali ndimulandu wawo,,,tchito yawo ndiyokharira Court,,,
@LinasMunthali-gb1md
@LinasMunthali-gb1md 2 ай бұрын
Nde tidziwa bwanji kuti chigamulo chinali bwanji?
@creativecassim4831
@creativecassim4831 2 ай бұрын
Kodi ilili ndi sewero chan?
@HalimuChisaka-o1t
@HalimuChisaka-o1t Ай бұрын
Kod simungapase chisamariro
@PaulNdala-kw3ob
@PaulNdala-kw3ob 2 ай бұрын
🎉 please next time finish the store komamso osamangoti tanvan sikukwanira kukhala title s
@isabelmartin7567
@isabelmartin7567 2 ай бұрын
Abambowa ndie ndikabwelebweletu ku court 😂
@GiftMkweza-lq4hw
@GiftMkweza-lq4hw 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 customer
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 2 ай бұрын
Bvuto ndi boma lipereke chochita Kwawanthu
@AbudulJohn
@AbudulJohn 2 ай бұрын
Ada awa ndi woipa mtima kwambili iyeyo atawona kuti amaiwa akutelo bwanji osatengapo mbali bwanji komaso Ada awa amayiwa amafuna
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
M, tendele ose wadziko la Malawi uli m, manja mwa chikangawa ndi nduna zake basi
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Vuto kumalawi kuno uphawi wachuluka olo atati azigulitsa masambao panopa palibe chikuyenda ndiy olo kholo langofika poti mutu sukugwila ndichifukwa athu akungozimangilila kusowa kuti apanga bwanji koma mulungu atikomele m,tima ndithu
@creativecassim4831
@creativecassim4831 2 ай бұрын
I have seen a guy with different names in two episodes
@BrownBanda-q3t
@BrownBanda-q3t Ай бұрын
Mmmmm malamulo enawa aziyenda ndithandizo nanga akanatani mayiwo??
@AulivinChaula
@AulivinChaula 2 ай бұрын
Abambowa ndaboza mesa ndiomwe anabweras ndi yawo kt anthetse banja iiiiyaaa nkhan za bonza
@MerryWayson
@MerryWayson 2 ай бұрын
Program iyitu ndaikonda, tamphunzila kwambiri kuziwa udindo Wa Mwana komaso Mai pakhomo kkkkkk komano Mai mzangayu ndichisilu chamunthu Mai wanzelu kutumiza Mwana ndithu komapemphesa ngat wamisala zowona aàa Alandile chilango
@michealchilemba3149
@michealchilemba3149 2 ай бұрын
Onse a Malawi choyankhulira English ndi chiani ngati muli Azumgu ku Court ko
@CHAPITASINGINI
@CHAPITASINGINI 2 ай бұрын
Ugalu basi ndiye kupepha ndi kuba chabwino ndichani mukusiya milandu ikuluikulu kumakamba zithu zaziiii uchitsilu et dikilani ndimuwuze JB akutukwaneni mapwala
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 2 ай бұрын
Zaziii osabweresa poyera aja apezeka ndindalama kubwalo landege ku Zambia aja
@FragsonChimpanda-so4ft
@FragsonChimpanda-so4ft 2 ай бұрын
Ili ndi sewero sizenizeni
@GiboTakondwa
@GiboTakondwa 2 ай бұрын
Neva iwe chimene ukadachita ukadapeza njira zoti mayiyu athandizidwe pazimene akusowa pakhomo ndiye APA mwamanga mayiyu mwanayo pakhomopo azikhalapo ndindani munasowa nzeru pachiyambi neba
@IssahAluba
@IssahAluba 2 ай бұрын
Iwe neba uzafera zayeni ugowona mene akukuoneramo iiiii zilikotu 😅😅
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 ай бұрын
Vuto lokwatiwa ndicholinga choti mamuna azikudyetsani ndilimelo. Kuntumiza mwana ku umasikini malo momutumiza kusukulu. Pezani chochita, mamuna akamakukwatirani mukupanga ka geni kangachepe. Ndi izi amuna kukuthawani basi inu simudya. Olo ntchito yochapa malainimu simungagwire? Olo business ya masamba simungapange? Mwanayo tsogolo lake mukuliganizira? Mwangokhala amai opusa, opepela, ndipo ankhanza. Pitani mukailawe ndende mai.
@AnnieKazembe-ic5vp
@AnnieKazembe-ic5vp 2 ай бұрын
Ndiudindo waketu umenewo zimangotengera ndimamuna amene wakumana naye kuti kodi mapezedwe ake ndiotani akazifetu ndichongothandizirq osati tingatenge udindo onse wazibambo ayi
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 2 ай бұрын
Akuvutik kulankhul chichewayo ndi mchew oimbidwa mland mchew kom ndikumufun munthu win mchewanso kut azimasulir pal nzer yanj tsono kungonong nthawi
@ALLIEDAUDI
@ALLIEDAUDI 2 ай бұрын
Neba neba neba mutu sukungwira ❤😂😂😂
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer 2 ай бұрын
Km iyi nd nkhan yen yen kapn sewelo pot abambowa ngt Tinawaonas week yatha pa nkhan yinas yokhuzanas za banja
@FragsonChimpanda-so4ft
@FragsonChimpanda-so4ft 2 ай бұрын
Ndisewerotu ili
@CliveChikaphonya
@CliveChikaphonya 2 ай бұрын
Owooo Nd sewero et ndmadabwat
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 2 ай бұрын
Aboma inu ndinu zisilu
@edgarmsofi589
@edgarmsofi589 2 ай бұрын
Judgement: suspended sentence. A tengerepu phunziro basi.
@AREFRIEDNELSON
@AREFRIEDNELSON 2 ай бұрын
Nde ndimene lilidzikoli lathu li china chili chonse ndichovuta kupeza nde mumafuna kuti atani mmene dziko lilimu mfunso langa ndilakuti chomunjaJila mulandu Chifukwa chani
@jameskamanga628
@jameskamanga628 2 ай бұрын
Koma ziliko 🙌😋
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 2 ай бұрын
Kodi ana amasiye woynaglidwa ndi a ma bungwe,amafunika kuti azigwira ntchito yolima minda??? Kuno ku mudzikwarhu kuno tikuwona ana amasiye akulima Munda,zikumandimvesta chisoni
@Esther-r8c
@Esther-r8c 2 ай бұрын
Mmm iwe sunawathandize bwanji
@Esther-r8c
@Esther-r8c 2 ай бұрын
Neba uyu mesa ndi uja anamangitsa nkazi wake kuti wamupasira matenda
@ethelkamwendo702
@ethelkamwendo702 2 ай бұрын
Also me i think so
@AnnieKazembe-ic5vp
@AnnieKazembe-ic5vp 2 ай бұрын
Boma limanga bwanji maiyu pomwe ana ake amavutika nawo okha opanda otengako mbali even bomalo siliwathandiza ,ine nde anaanga munthu wina sangandiuze zochitatu pokhapokha ngati amandithandiza atha kutengapo mbali
@vincentmpighu1080
@vincentmpighu1080 2 ай бұрын
Eti amwene aaah osakamanga bambo awo bwa
@PatrickLuis-g2c
@PatrickLuis-g2c 2 ай бұрын
Neba wamaboza
@AndileyaMkandawire-x8r
@AndileyaMkandawire-x8r 2 ай бұрын
Aneba mukanapanga njila kuti muzimayiyu azipezela chakudya chifukwa akamangidya anao avutikabe ndiye asambuka oyendanyendao chifukwa aziwa kuti njila yomwe amamuuza mayio ndiyolondola kom siyorondola tiyeni tizipasana zelu zokhwima khani isana fike poyipa, naweso mayi ukanauvomela mulandoo pachithu choona sitimakana akanakuthandizani zelu yopezela chakudwacho eeee zovesa chisoni chifukwa mbali zose sizinali bwino bamafunika oyimilila waphavu kuthesa votolo
@FireKajambe
@FireKajambe 2 ай бұрын
Court's Powerful are from dark kingdom
@jahmanmakwinja-ef7zn
@jahmanmakwinja-ef7zn 2 ай бұрын
Ndye akusamalidwa nindan panopa mutamumanga mzimayiyu?
@aurorethomas5814
@aurorethomas5814 2 ай бұрын
Muzimalizitsa tinve chigamulocho
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 2 ай бұрын
Vuto ndi njala MCP ndiyomwe ikubwelesa mavuto amenewa maboma apita mbuyomu kunalibe zimenezi
@NellieMsamala
@NellieMsamala 2 ай бұрын
Tufuna za chifunga ife osati izizi ayi
@ForsterThawan
@ForsterThawan 2 ай бұрын
Ada awaso ndiopa ntima kwambili
@Margaret-t7m
@Margaret-t7m 2 ай бұрын
Kodi nkhani izi bwanji zumakhala za anthu amodzi modzi? Ndi drama mwina? Onsewa aliapawa amabwela ndi nkhani zosiyana siyana
@TakondwaSaidi
@TakondwaSaidi 2 ай бұрын
Eya
@egreymkumba-tj5ji
@egreymkumba-tj5ji 2 ай бұрын
Anthu ake angokhala omwewo kodi ndi drama eti
@gladysmanthimba7851
@gladysmanthimba7851 2 ай бұрын
Bambo a mwana amangidwe
@mphatsomaluwa
@mphatsomaluwa 2 ай бұрын
Tiziyakhulanapo chichewa apa
@BillySaukani
@BillySaukani 2 ай бұрын
Ku nzunza mwana kumpatsa udido pamene suli wake
@MalackPatrick-jt4hk
@MalackPatrick-jt4hk 2 ай бұрын
Koma maniwa atava anachitapo chani ndiompenga ameneyi
@CliveChikaphonya
@CliveChikaphonya 2 ай бұрын
Kd mboniyi ikupezeka bwanj pa nkhan zambir
@HalimuChisaka-o1t
@HalimuChisaka-o1t Ай бұрын
😂
@wezzieneba9238
@wezzieneba9238 2 ай бұрын
She is so innocent, please, forgive her and tell her what is supposed to be done. She has said that she didn’t know. Even God will punish us on what we know. She doesn’t know what it means, the so called constitution. She is there to be forgiven and tell her what to doing. What she did or she was doing is just the consequence of poverty and neglect from her husband. Yes, it wasn’t right, but she needs to be guided and not penalized. My food for thought. Thank you.
@AUFIMADENGU
@AUFIMADENGU 2 ай бұрын
KHANI YAVEKA KOMA VUTO NDIMAVUTO BOMA LIKUYENERA KUKHARA NDI NDONDOMEKO YO PHUZISA MIZI KUTI KUTERO KULAKWILA MALAMURO IZI ZAPANGIKA CHIFUKWA CHOSAZIWA ZIKOMO
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje 2 ай бұрын
Ma number ama athu oona zakhaza zanawo tipaseko 😢
@HarryChikandira
@HarryChikandira 2 ай бұрын
Ndi program yodziwitsa anthu za malamulo okhudza ana Komanso chilango chomwe chimaperekedwa Kwa olakwa.Program imatenga nkhani zenizeni zomwe zimachitika mmalo momwe tikukhalamu bwana wanga ndithu ACC mene munafunsa kuti ndi drama kodi nanga bwanji anthu ake as mangokhala Omwe omweomwewo.
@AnnieKazembe-ic5vp
@AnnieKazembe-ic5vp 2 ай бұрын
Aziwisa bwanji Ngati amatengako udindo okithandizira
@joma5327
@joma5327 2 ай бұрын
Stupid program bwanji simumaonetsa the conclusion of the case chigamuro
@IkhenaCalvin
@IkhenaCalvin 2 ай бұрын
Kwambili owe unatumiza nkhaniyi plus just check out for this woman maybe we can help her
@jahmanmakwinja-ef7zn
@jahmanmakwinja-ef7zn 2 ай бұрын
Neba oipa iwee
@Uncle_B265
@Uncle_B265 2 ай бұрын
Mwano mulibe podaliraa
@EusébioLucianoGaiondo
@EusébioLucianoGaiondo 2 ай бұрын
Aaaa
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 ай бұрын
❤❤❤
@amaliphiri1846
@amaliphiri1846 2 ай бұрын
😂
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Vuto ndi MCP fertilize ndi wodura china chilichose chakwera ndiye amuna akuthawa banja chifukwa akusowa mtengo wogwira
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 2 ай бұрын
Neba munakangopita ndithumba lachimanga basi kut maiwa achite manyazi
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 2 ай бұрын
Can you send me that number for she's number kuti tiwathandize Tiwapatse ndalama kuti ayambe business pepani pa izi plz
@g_deonm5793
@g_deonm5793 2 ай бұрын
Chokani apa...mungofuna muwapange ujeni........
The Court | Malawi (30 September  2024)
23:25
Malawi News Update
Рет қаралды 12 М.
Ku court
9:20
Chikoko Comedy
Рет қаралды 7 М.
Flipping Robot vs Heavier And Heavier Objects
00:34
Mark Rober
Рет қаралды 59 МЛН
My Daughter's Dumplings Are Filled With Coins #funny #cute #comedy
00:18
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 33 МЛН
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Malawi News Update
Рет қаралды 278 М.
MALAWI COURT...(PART YOTSATIRA)
23:39
Malawi News Update
Рет қаралды 16 М.
THE COURT (Next part) Malawi
28:38
Malawi News Update
Рет қаралды 21 М.
CRUISE 5 WITH SHEPHERD BUSHIRI ECG   PART 1
53:15
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 200 М.
The Court Of Malawi
24:32
Jimmy Chimera
Рет қаралды 57 М.
THE COURT (Malawi)🤔
25:31
Malawi News Update
Рет қаралды 11 М.
THE COURT (IYI NDE MUSAIPHONYE!!) Malawi
22:07
Malawi News Update
Рет қаралды 63 М.
THE COURT (NEXT PART) Malawi
25:02
Malawi News Update
Рет қаралды 3,1 М.
Flipping Robot vs Heavier And Heavier Objects
00:34
Mark Rober
Рет қаралды 59 МЛН