Keep up Brian ukamafunsa munthu suopa umafuna tidziwe chilungamo
@frackisonlogah41654 жыл бұрын
Mr Briana musalimbane ndi uyu ndi cadet wa dpp kuti muve Zambili za imfa ya Robart mufunse black Moses akuuzani chulungamo
@denniskhalamba96554 жыл бұрын
King wa ma cadet uyu.
@hajiwayison87482 жыл бұрын
Mafuso abwino komaso ndithokoze bambo mike chitete n'mene akuyankhira mafuso komaso ndithokoze wires ya times pomatigawila nkhani zosiyana siyana GOD bless you brian banda with mike chitete good bye👍
@rossferg19874 жыл бұрын
Wa cadet ameneyo
@vincentlamanmathebulamwana56974 жыл бұрын
Mr Brian ntayeni uyu koma mau amodzi kwa nkuluyu ndi awa kukula nthupi,kunyamula zitsulo sikuthandauza kuti ndinu odziwa kupha, mupite pa mirror mukaziyang'ane bhobho kuti mwina kukula nthupiko mwina mulinso ndi manso kumbuyo, koma ngati mulibe muzikhala ndi mantha coz minga ndi munthu tikachitenga chachikulu ndiye ndi munthuyo komatu minga imabaya munthu
Maik mpwanga iwe ndi achitsiru mwanva?kuyanka kwa Sirius? Kkkkk mwakulatu!
@Littlefair73 жыл бұрын
Brian, interview iyi sinali level yako, kuyankhula ndi mphwepwa, ife timadziwa kuti Brian amayankhula ndi anthu oganiza, odziwa chimene akunena osati izi za ziiii.
@chesterphiri75234 жыл бұрын
Kkkkkkk inetu ndikumvatu kwa inuyo.🤣🤣🤣🤣🤣
@chesterphiri75234 жыл бұрын
But do you really have peace mind ?????
@mrwh.mwalimumrwh.mwalimu43974 жыл бұрын
Brian ndi yemweyo ndi jomo wakwatopwa. amaziwona ngati madolo malawi muno koma Thawi izawafika