TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 97

  Рет қаралды 15,611

Nkhalango Multimedia

Nkhalango Multimedia

Күн бұрын

Пікірлер: 115
@christophermsowoya741
@christophermsowoya741 6 ай бұрын
Good job guys i can see chaka chino tiwinaso ma awards
@yusufjaile5317
@yusufjaile5317 6 ай бұрын
Chiphwanya akuti iyeyo ndi bigiliman yamu family yakwawo😂😅😅😂😅
@Tawina0101
@Tawina0101 6 ай бұрын
guys pangani like Comment yanga cholinga muzindikumbutsa kuzaonelatso
@FlavianoThomo
@FlavianoThomo 6 ай бұрын
❤❤
@robertrichman9376
@robertrichman9376 6 ай бұрын
Muzionera big osadanda 😂
@graceLufan
@graceLufan 6 ай бұрын
P​@@robertrichman9376
@graceLufan
@graceLufan 6 ай бұрын
P😊😊0😊​@@robertrichman9376
@AlfredMakuwira
@AlfredMakuwira 6 ай бұрын
You make happy guys watching from cape town s.a
@EsteryHassan
@EsteryHassan 6 ай бұрын
Kkkkk chiphwanya sopano anakwatila kutali ndi malawi kukana zimenezo chiphwanya ndi man bigili pambumba Panja ❤❤❤❤❤
@LofraBywell
@LofraBywell 6 ай бұрын
Project, Project my house and my beautiful me. Mr chiphwanya, are you so funny 😂 continue entertaining us.
@StatesManP-zq4ic
@StatesManP-zq4ic 6 ай бұрын
Chiphwanya tsopanoooo Ali moneys ndizimene zikulankhula kkkkk look at Mr spider😂😂😂 Chiphwanya anafikapo ndithuuu Mr building 😅😅😅
@MadaWilly
@MadaWilly 6 ай бұрын
Mbilintengerenji 😂😂😂😂😂😂😂😂 eeeee maina abale
@chibambarichard22
@chibambarichard22 6 ай бұрын
KOMA EMMA AFANANA NDI GAGA BWANJI 😂😂😂😂😂
@AfickDaud
@AfickDaud 6 ай бұрын
Mbiritu nawe ndwe otengeka Dollah anabadwa choncho nawenso ubadwisa wako watonde zimveka azizazitama naenso😂
@justinenambazo6855
@justinenambazo6855 6 ай бұрын
A Chiphwanya mwagwira ntchito kumusukuluza Nagumbo asadzayambirenso. Nawonso a Chibiliti akanadikira mayi Phiri awaonetse mkazi winayo asiyanitse okha. Mai Phiri mmakwana. Achimwene a Zimveka inuyo ndi machine amwene. Wishing you all the best guys mumakwana.
@SteveNdawu
@SteveNdawu 6 ай бұрын
Chiphwanya,,,,you'll hear him water😂😂😂😂
@robertrichman9376
@robertrichman9376 6 ай бұрын
Muthinda wangoti mwayi wangawo 😂😂😂😂, I love you guys
@MadaloHolla
@MadaloHolla 6 ай бұрын
Níce big up
@rashiddeula5715
@rashiddeula5715 6 ай бұрын
Chiphwanya my man!! Nice one! Great advice! Kuwatsukuluza alamu ache! Wakumva wamva!
@danielantoniomsutu8736
@danielantoniomsutu8736 6 ай бұрын
Emma akundiwazaso naye more fire 🔥🔥 Emma ndakunyadila. Komanso osayiwala Nazimbiri.
@LeniaBanda-r9t
@LeniaBanda-r9t 6 ай бұрын
Mbili Dolla akangodziwa adzakuswa. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@StatesManP-zq4ic
@StatesManP-zq4ic 6 ай бұрын
Koma zimveka naye uuhule udzimuthera mmmm. Komanso muthinda walakwitsa potenga mwana osatsanzika mapeto ake anthu mitu iwakulira pomati mwana alikutiii komanso nanga mwana pamawa atadwala adzapanga bwanji
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 6 ай бұрын
Ameneyo ndiye zimveka mbiri watheka kale kkkk 😂😂😂😂 Koma zimveka ulindimankhwara akadzi onse amangokuvomera kkkk
@Charles-bg5ul
@Charles-bg5ul 6 ай бұрын
kkkk Muthinda wathawa ndi mwana kkkkk kukhala kusaka z mwana ameneyo. *Muzibweranso ndi next tiziona zomwe zibwere kutsogoloku*
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 6 ай бұрын
Kkkkkkkk muthinda wandisangalatsa kwambili tinganene kuti waba mwana ngati? Kkkkkkk munthu suba chako chomwe
@BensonLitta
@BensonLitta 6 ай бұрын
Kkkkkk look at Mr spider anabwera awachapatu anagubo😂😂😂😂😂😂
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 6 ай бұрын
Chiphwanya machine 😂😂
@CharlesJamboh
@CharlesJamboh 6 ай бұрын
Following from cape Town nice movie guyz
@sayidimisessa
@sayidimisessa 6 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Azinveka eee ndi hule lalimuna iiiiiii 😂😂😂😂😂😂 kutsoka masiketi😂😂😂 ulemuwanu ma member a Tonde wadula from south Africa 🇿🇦 Johannesburg
@JamesVicktor-yl4bj
@JamesVicktor-yl4bj 6 ай бұрын
Mwana kwa adad akamwe tea😂😂
@sayidimisessa
@sayidimisessa 6 ай бұрын
More more more guys tikukusatani from johannesburg
@FlavianoThomo
@FlavianoThomo 6 ай бұрын
Mmmm mumatikodweretsa❤😂
@RhodaMwanza-o5b
@RhodaMwanza-o5b 6 ай бұрын
Amyi phiri murindivuto mukuwafuna achibirit nanuso kkkkkkk
@FlavianoThomo
@FlavianoThomo 6 ай бұрын
Koma Zimveka alimbanaso ndi Tonde 🎉🎉🎉
@BensonLitta
@BensonLitta 6 ай бұрын
Kkkkkkkkk Mai phili akuwafunadi achibiliti 😂😂😂😂😂
@MusaMusa-d4d
@MusaMusa-d4d 6 ай бұрын
Komaa ziveka Inuyo 😂😂😂😂😂
@JohnstonKazembe
@JohnstonKazembe 6 ай бұрын
Zimveka best actor
@YopooTael
@YopooTael 3 ай бұрын
Zimveka man of moment
@DalitsoKocherani
@DalitsoKocherani 6 ай бұрын
Look at Mr spider😂😂😂
@BridgetGunde-w9c
@BridgetGunde-w9c 6 ай бұрын
Tsono muthinda wabwera kuzaba mwana kapena kuzamutenga😂😂😂
@yusufjaile5317
@yusufjaile5317 6 ай бұрын
Kuzaba koma 😅😅😅
@VenancioKeyala-rn5bm
@VenancioKeyala-rn5bm 6 ай бұрын
Tonde wadula fans let's gather here🎉
@MarianoRaulPhir
@MarianoRaulPhir 6 ай бұрын
😂😂😂😂kkkkk Aziveka kúnama
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 6 ай бұрын
Chipwanya 😂😂😂😂😂
@sayidimisessa
@sayidimisessa 6 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 mayi phiri mwandibanda kwabasi achibiritu adyesa khwakhwanana
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 ай бұрын
Eya kuyankha amati abeee Emma congrants
@MphatsoMakungyaja
@MphatsoMakungyaja 6 ай бұрын
Koma chizimveka uhule kkkkkk
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 6 ай бұрын
Chimphanya sazatheka mumandimvesa kukoma simunyengelera pomuuza munthu kkkkkk
@ShadreckMwija
@ShadreckMwija 6 ай бұрын
Chisomo usangokwatirana ndifarau bwanji akuonesatu chikondichake chose paiwe mwina ao akunamiza uzamukumbukiratu
@patricksoko1308
@patricksoko1308 6 ай бұрын
Keep it up guys timadikira ife 😊😊😊😊
@JOHNMARK-sl5ff
@JOHNMARK-sl5ff 6 ай бұрын
You are best gys
@GraceTwaibu-vr1qf
@GraceTwaibu-vr1qf 6 ай бұрын
More fire 🔥 guys
@GaudySamu
@GaudySamu 6 ай бұрын
Mmakwana chaaniii💪🥳🥳
@FraserNamaona
@FraserNamaona 6 ай бұрын
Koma kunena zowona Zimveka ndi dolo. Amatha kunena chilungamo
@KenedyJolamu-rs9xx
@KenedyJolamu-rs9xx 6 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥💪
@amoschataika7440
@amoschataika7440 6 ай бұрын
Big up to the Camera Man
@KassimRasheed
@KassimRasheed 6 ай бұрын
Koma azinveka ximakuphonyani zinthu? 😅😅😅😅😅😅😅
@benjulius6070
@benjulius6070 6 ай бұрын
akut manez kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
@AbdullahBullah-jj6bm
@AbdullahBullah-jj6bm 6 ай бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@limbanigivinala3210
@limbanigivinala3210 6 ай бұрын
Zimveka style of speaking imandisangalatsa.... Dobadoba#
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 ай бұрын
Kkkkkkk emma wabedwa ndi muthinda kkkkkkko
@RoseDaudi-g8i
@RoseDaudi-g8i 6 ай бұрын
Chiphanya ndi number one
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 6 ай бұрын
Nyc❤😂
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 6 ай бұрын
More 🔥🔥🔥🔥🔥
@shaibuJames-c3w
@shaibuJames-c3w 6 ай бұрын
zimveka ndakatundu mumakwana sir
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 ай бұрын
Kodi zimveka kufuna kumuyenda mmapazi tonde
@ChristianmwaleJudith
@ChristianmwaleJudith 6 ай бұрын
More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 ай бұрын
Tonde wadula more 🔥
@MathewsBanda-nu1ec
@MathewsBanda-nu1ec 6 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤ tonde
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 6 ай бұрын
kept up mabwana
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 6 ай бұрын
Ching'ax good advise ❤❤
@MalizinaKalilizo
@MalizinaKalilizo 6 ай бұрын
Zinveka cheu cheu cheu polankhula koma m kuluyu nditambwali kkkkkkkkkkkkkkk
@yusufjaile5317
@yusufjaile5317 6 ай бұрын
Zimveka ndigadabwali mapeto kunama too much 😅😅😅
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 6 ай бұрын
My home 😂😂
@LucasBetiasseJairosse
@LucasBetiasseJairosse 6 ай бұрын
KODI NCHIFUKWA CHIYANI MWAMUNA WAKE WACHISOMO SAKUONEKA.
@vatineseduwin
@vatineseduwin 6 ай бұрын
chiphwanya good point
@jameskazembe1123
@jameskazembe1123 6 ай бұрын
Welcome 🥳🥳🥳
@JOHNMARK-sl5ff
@JOHNMARK-sl5ff 6 ай бұрын
Zimveka my man😅
@BlessingsBanda-ih4th
@BlessingsBanda-ih4th 6 ай бұрын
❤❤❤😂
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 6 ай бұрын
Zimveka machine kkkkkkk
@RichardAmosi
@RichardAmosi 6 ай бұрын
😂😂😂 Emma waku Town
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 6 ай бұрын
Zimveka mpaka kufunsa mfunda wa mbili
@yusufjaile5317
@yusufjaile5317 6 ай бұрын
Zimveka nditabwali kwambiri 😂😂😂
@TiyaKanchiputu
@TiyaKanchiputu 6 ай бұрын
Bambo a Dola ndi deal
@danielantoniomsutu8736
@danielantoniomsutu8736 6 ай бұрын
Guys koma Chiphwanya muli upangilitu kkkkkk
@vatineseduwin
@vatineseduwin 6 ай бұрын
muthinda waba mwana
@jackbello2170
@jackbello2170 6 ай бұрын
Atibera mwana
@Siyanibauleni
@Siyanibauleni 6 ай бұрын
Pharaoh mutu wayima😂😂😂😂😂
@daviechibwana3137
@daviechibwana3137 6 ай бұрын
Chiphwanya more fire 😂😂😂😂
@yusufjaile5317
@yusufjaile5317 6 ай бұрын
Beautiful me😅😅😅😅😅
@Maria-nv8ev
@Maria-nv8ev 6 ай бұрын
Koma dora ndi asiatu asowatu
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 6 ай бұрын
Dave alipo koma?
@NditajiMaxwell-cz8ir
@NditajiMaxwell-cz8ir 6 ай бұрын
Km zimveka ndiza sewero
@YalediGondwe
@YalediGondwe 6 ай бұрын
Chiphwanya 🔥🔥
@khumbophiri9006
@khumbophiri9006 6 ай бұрын
Zimveka sazatheka ndithu
@issadinala125
@issadinala125 6 ай бұрын
Zinasiya kukoma izi mukumangobweleza bwanji aaaaaa😢
@nkhalangomultimedia
@nkhalangomultimedia 6 ай бұрын
Ndie ndiinu nokhatu omwe simukumva kukoma, kapena mwangotutumukira mwayankhula?
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 ай бұрын
Zinasiya kukoma koma nkumaonerabe hehehe shame
@MrsleeLutepo
@MrsleeLutepo 6 ай бұрын
Komanso tiwafunse awa Iwo angapange zokoma kupotsa tonde??. kkkkkk zamanyazi
@EdythGloryNamponya
@EdythGloryNamponya 6 ай бұрын
Auzeni mwabwinobwino...zomwe akunena ndizoona koma kuyankhula sanayankhule bwino...chepetsani zobweleza
@WilliamKapena
@WilliamKapena 6 ай бұрын
Dora alikut abale amasangalasa
@MaggieBanda-o2p
@MaggieBanda-o2p 6 ай бұрын
😊😊😊
@MavutoJackson-j3v
@MavutoJackson-j3v 6 ай бұрын
Mbiri wagwelamo bad😂😂😂😂😂😂
@DominicMbondo-u9s
@DominicMbondo-u9s 6 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂musamenye theche thumba la cement 😂😂😂😂
@thomaschipinda6952
@thomaschipinda6952 6 ай бұрын
Mai phiri ingonenani kuti ndinu nomwe 😂😂😂
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 6 ай бұрын
Zamphamvu
@LucasBetiasseJairosse
@LucasBetiasseJairosse 6 ай бұрын
PEOPLE HEAR ME WATER.
@faisaliqbal5625
@faisaliqbal5625 6 ай бұрын
Zimveka unadza
@kinggomani2676
@kinggomani2676 6 ай бұрын
Tiwonele zimenezi
@GeorgeGeorge-bu6cy
@GeorgeGeorge-bu6cy 6 ай бұрын
Zilibwino
@JamesMalango
@JamesMalango 6 ай бұрын
Mabuilding
@TasieManda
@TasieManda 6 ай бұрын
Chiphwanya iwe ndimachine wakumva wamvadi
@patrickmadukani4314
@patrickmadukani4314 6 ай бұрын
Ndafika
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 98
27:54
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 20 М.
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 34 МЛН
😜 #aminkavitaminka #aminokka #аминкавитаминка
00:14
Аминка Витаминка
Рет қаралды 1,9 МЛН
Бенчик, пора купаться! 🛁 #бенчик #арти #симбочка
00:34
Симбочка Пимпочка
Рет қаралды 3,7 МЛН
This mother's baby is too unreliable.
00:13
FUNNY XIAOTING 666
Рет қаралды 42 МЛН
Pray For Chiwenga Before It's Too Late😭
15:20
Kulliant Tv
Рет қаралды 16 М.
KUYANKHULAPO PA NKHANI YA KUMANGIDWA KWA PATRICIA KALIATI
7:06
Malawi Extra
Рет қаралды 7 М.
B'ella (Malawian feature film with eng subtitles)
1:28:53
Tereza Mirovicova
Рет қаралды 53 М.
OTSATIRA CHIPANI CHA UTM AFIKA KALE KU POLICE KOMWE AKUSUNGAKO KALIATI
1:44
Jane apange bundle ya mowa
5:37
Jimmy & Jane TV
Рет қаралды 1,3 М.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 100
27:56
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 21 М.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 125
27:37
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 15 М.
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 34 МЛН